Pitilizani chonchiyo. koma popita Ku katola nkhani muzikhala ndi equipamentos komano calachá monga mwa malamulo ake!!!! I m by Alexandre zimpita fromu mapanje localidade d banga.koma ndili Ku Tete!!!
Ine ndimakuonerani kuchokela ku Durban koma kumudzi ndi kumalawi boma la nkhotakota inu ntchito ya bwino mukuigwila yesesani kupitiliza kusakasaka nkhani
Continuo,bom trabalho mumati zosiyana siyana zam'maiko zochitika Thanx
Keep up the good work thanks so much
Continue good job watching you from south Africa
Thanks
Continuo Govat and sizito
Paine zilibhoo. G&C🔥
Kuno Ku Jon ndimakusataninso kwambili pitilizan 🎉🎉🎉 happy new year
Watching from Katete Zambia
Zikomo
Mumatidalisa pa ntchito yanu especially yautola nkhaniyo. All the way from Cape Town 🇿🇦
Pitilizani anyamata muli booo!!!,🥰👍🔥
am in zambia obrigando
live from NB
Happy new year
Happy happy New year
Pitilizani happy new year
Ine Duncan Kandaya kuno ku Ntcheu Secondary school Malawi 🇲🇼 ndimakukondani anyamata nonse a Channel chathu chokoma cha BS. Happy new year kwa nonse.
Mudasowa2
Zilibwino, pitilizani
Anyamata mudasowatu welcome
xap ndimakufilani kwambili Agovati ine ndili Joz
Azibambo pitirizani!!
Nkhani niyakuti mokupemphani tiikileni nyimbo za Godseez chonde
Ndi programou yabwino kwambiri, pempho langa ngati Muthu ndimafuna mutamabweletsa ma luso a wathu akumudzi oti akhoza kuthandiza achinyamata (criação)
Juno kutchetsa ndikunthukwi timakunyadilani
Timakunyadirani anyamata a Balanço semanal
Pitilizani chonchiyo. koma popita Ku katola nkhani muzikhala ndi equipamentos komano calachá monga mwa malamulo ake!!!! I m by Alexandre zimpita fromu mapanje localidade d banga.koma ndili Ku Tete!!!
Ine ndimakuonerani kuchokela ku Durban koma kumudzi ndi kumalawi boma la nkhotakota inu ntchito ya bwino mukuigwila yesesani kupitiliza kusakasaka nkhani
Pitilizani ndithu
Pena ngati mukufotokoza ZA ndalama please yakhulani muchiyakhulo chanu kmso chichewa
OK
Bs chanel pitilizani ntchito yabwino potipatsa nkhani zabwino, lyford vasco kampira, bs moto kuti buuuuuuuuu
Lyford vasco kampira mzimba Malawi
Pitilizani ndithu
Thanks