Nkhanga zaona: Achakwera akupita ku Israeli akalipire omwe ndege ya Chilima

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 11 ก.ย. 2024

ความคิดเห็น • 160

  • @ernestphiri5507
    @ernestphiri5507 หลายเดือนก่อน +26

    A Usi azungulira mutu alibe nzeru its true Chilima is still winning may his soul rest in peace

    • @EllinaBitto
      @EllinaBitto หลายเดือนก่อน +1

      Ameen😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭

    • @ProsperGondwe-ju5fw
      @ProsperGondwe-ju5fw หลายเดือนก่อน

      Kkk km Malawi

  • @GanizaniKamvazaana
    @GanizaniKamvazaana หลายเดือนก่อน +20

    Ife timakondana chilima osati za usi zii achitsiru ausi awona ngati basi zomwe akupanga zo akubebetsa never wanya nayotuuu

  • @JuniorHala-vf9ov
    @JuniorHala-vf9ov หลายเดือนก่อน +2

    Ntanyiwa mau oti usogoleli ndi mphatso thank you so much for that fantastic word chakwela mulibemo mphatso ya usogoleli even manganyao, chilima adali ndi mphatso yochokela kwa yehova osagawa ndalama koma anthu ankamukonda heavy because of that gift he has given from god not zama copyright it was special mphatso

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole หลายเดือนก่อน +9

    Kutengera zimene zakhala zikuchitika ndi zimene zikuchitika psychologically Michael usi is a betrayal Akuziwapo kanthu ife si Ana mwanyanya kujijilika .

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 หลายเดือนก่อน +2

    Keep the fire burning bro, mwainu amalawi kudalila kuwuzidwa zoona, pitilizani ndithu ndipo MULUNGU azikuyang'anilani, kukutetezelani kwa oyipayo komanso akupaseni moyo wautali amwene ❤❤❤

  • @user-ky4ce9gb6j
    @user-ky4ce9gb6j หลายเดือนก่อน +8

    Skc still In our hearts

  • @lyiemanganjira9708
    @lyiemanganjira9708 หลายเดือนก่อน +6

    Comrade Ntanyiwa for president 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @Musa1828-l5d
    @Musa1828-l5d หลายเดือนก่อน +7

    Manganya akuona ngati akupanga zopambana kwambri azindikila machende alibe ndigalu kwambri

  • @esaMoha-dm4kj
    @esaMoha-dm4kj หลายเดือนก่อน +7

    Mr president mtanyiwwa ulemu wanuw mulungu adalise inuyyo nosse nkumene mulinko 🎉🎉🎉

    • @esaMoha-dm4kj
      @esaMoha-dm4kj หลายเดือนก่อน

      That's good news thank you for the sampot

  • @FestonBuka
    @FestonBuka หลายเดือนก่อน +4

    Akapita kumeneko ,chonde hamas ndege yo muione mwapaderadera 🙏🙏

    • @sakalameck
      @sakalameck หลายเดือนก่อน

      🤣

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz หลายเดือนก่อน +3

    Chimene sanachokele a skc ndi ichi kutengera ndi interview ya manganya zikusonyeza kuti achilima adakhulupirira osaziwa kuti adalithira kuwiri panja musayiwale amati pakakhala kusagwirizana akuti akathamanga mbali zonse ziwiri, Zoti chilima akabwera akufuna akumane ndi raph akadziwa set yamalo anakambuka raph usi amaziwa zisisizonse manganya amaziwa osati wina aliyense mu utm set yonse idayambira PA usi chilima adali wa dzeru or raph adali shasha mufune musafune kuti mjomvuzi ziphedwe mwini Film ndi manganya wina afune asafune padali pomvuta kuti anthu awa aphedwe, ma Master adalipo atatu owukira mcp modzi adathawa ndikuwulura plot yonse musamuyiwale manganya musewero amamunena nkhwari,chakwera zamukhuza inde popeza koma angakhare amafuna njira yoti amuphere padali pomvuta popanda manganya uthengawu ali mpopo

  • @PaulKalambo
    @PaulKalambo หลายเดือนก่อน +5

    Bon kalindooooooo ananena kale kut Michael usi manganya ndi kape 😂😂😂 akut Ali ku Canaan kkkk koma the DC amaona patali

  • @MosesKalenge
    @MosesKalenge หลายเดือนก่อน

    Nthanyiwa. ULEMU WANU MR ❤❤❤❤💪💪💪💪💪🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @PhilbertoChaimah
    @PhilbertoChaimah หลายเดือนก่อน

    Mr mtanyiwa Ambuye akusungeni ndimoyo wautali kwanbiri ❤❤

  • @souzajoaquim571
    @souzajoaquim571 หลายเดือนก่อน +13

    Angoima bakiliyo bass timuvotela

  • @BarwickSalanje
    @BarwickSalanje หลายเดือนก่อน +4

    Atcheya woyeeeeeeeeeee.....President yemwe analamulira dziko lino mosayang'ana nkhope...tipemphe mulungu atichitile chifundo atipatse mtsogoleri wabwino

  • @user-st6bt5vv9c
    @user-st6bt5vv9c หลายเดือนก่อน +3

    Manganya ndi wa MCP muone tayi yake red red you can see Bakili yellow it's his colour kodi tayi colour ya UTM ni red iiii

  • @lyiemax
    @lyiemax หลายเดือนก่อน +2

    Powerful 💪 comrade Ntanyiwa ❤❤❤

  • @Henry-vw2cz
    @Henry-vw2cz หลายเดือนก่อน +5

    Chikangawa 😂😂😂😂 mbudzi ya munthu chakwela

  • @samchibenene4458
    @samchibenene4458 หลายเดือนก่อน +4

    Amake sikono tawayimbireni phone amuna anu😂😂😂😂😂

  • @AiameAdamo-su1nt
    @AiameAdamo-su1nt หลายเดือนก่อน +3

    Keep it up Mr Ntanyiwa.

  • @RitaKainga
    @RitaKainga หลายเดือนก่อน +2

    Mzimu wa Chilima ukanthe wina aliyense ochita moipila dzina lake la Chilima

  • @LouisKanje
    @LouisKanje หลายเดือนก่อน +4

    Amunongera

  • @shenwaahabdulhakim
    @shenwaahabdulhakim หลายเดือนก่อน +1

    A chakwera akuona ngati tikamuona Usi tiziona Chilima uja ndi manganya ndithu zeru zake ndiza mthiko bas chakwera and Usi ose akufunika ku prison

  • @user-ik5sz8hc6f
    @user-ik5sz8hc6f หลายเดือนก่อน

    Ndalama akukalipila zigawenga zinzake Malo mogwiritsa ntchito yoyenelera podziwa kuti dziko lathe likusowa zambiri.Amudziwe Yesu chikangawayo

  • @Lingstone-r3z
    @Lingstone-r3z หลายเดือนก่อน

    We are still going to vote for next year and we never know,,,, who will be?????

  • @MwenyeCheNsoma-gb2yz
    @MwenyeCheNsoma-gb2yz หลายเดือนก่อน

    Dr. Bakili F. Muluzi musiyeni abapuma please.

  • @Margaret-t7m
    @Margaret-t7m หลายเดือนก่อน +3

    Zovuta kwambiri, achatsika akanapakila koma hiyaaa atikwana kwambiri

  • @PeterMvula-o5v
    @PeterMvula-o5v หลายเดือนก่อน +2

    Koma guys kkk...that's for real 😂 I second that with no doubt

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of หลายเดือนก่อน +2

    Pamabodza FM lelo khani alibe akapeka ena atiuza😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @emmammatsa1284
    @emmammatsa1284 หลายเดือนก่อน +1

    Wow😮 manganya anali asanavalepodi skc t-shirt...it is sad now that he is doing this. Mwanena bwino mfiti amazigwiritsa yekha ndipo wakupha amalira kwambiri

  • @DevisonHala
    @DevisonHala หลายเดือนก่อน +4

    Manganya adapereka chilima chifukwa amafuna udindo zidali zogwirizana ndi chakwera mr chikangawa mcp

  • @BENSONRANGWANI
    @BENSONRANGWANI หลายเดือนก่อน +3

    Chakwela wamupha chilima zasala zosatila Zach

  • @augustMag
    @augustMag หลายเดือนก่อน

    Mtanyiwa FM 🔥🎉🎉🎉🎉mumatiyimilira❤❤

  • @HiltonZaone
    @HiltonZaone หลายเดือนก่อน +1

    Utsogoleri ndi mpatso yochokera Kwa mulungu 12:43

  • @MarthaMbewe-uk5nn
    @MarthaMbewe-uk5nn หลายเดือนก่อน +2

    Manganya akugawa ndalama kwa gulu la ODYA DZKE ALIBE MULANDU osati a UTM wagwidwa njakata YUDASI

  • @KamizaElizabeth
    @KamizaElizabeth หลายเดือนก่อน +3

    Haha hahaha bambo asikono ...... Mbolo yake

  • @WilliamNhlane-fd9hi
    @WilliamNhlane-fd9hi หลายเดือนก่อน

    President Bakili muluzi please come back and sort out these mess .

  • @MemoryKamanga-jv4jh
    @MemoryKamanga-jv4jh หลายเดือนก่อน +5

    True Mr ntanyiwa

  • @user-nb1ns6ye1v
    @user-nb1ns6ye1v หลายเดือนก่อน

    Mizimu ya anthu omwalilira pa ngoz ya ndege yiwambwambwaze agalu amene usi ndi chakwera makape

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl หลายเดือนก่อน +3

    Afuseni amanganyawo 😂😂😂😂😂😂

  • @blessingsbandah-pu3kw
    @blessingsbandah-pu3kw หลายเดือนก่อน +2

    Mntanyiwa umakwana

  • @JayKawereMw-po5go
    @JayKawereMw-po5go หลายเดือนก่อน +4

    😂😂😂😂Chakwera

  • @Thembokatuli
    @Thembokatuli หลายเดือนก่อน +2

    Anthuwatu kuluza vote by vote sangawine koma azangwiritsa ntchito mphavu azaphaso amalawi ambiri kukamiza

  • @user-be5fc3ed1i
    @user-be5fc3ed1i หลายเดือนก่อน +2

    Welcom ntanyiwa 😅😅

  • @hissimajohn965
    @hissimajohn965 หลายเดือนก่อน +2

    Ine ndilibe chipani komano olo a chili a alipo palibe zomwe anachitapo

  • @MathiasEgama
    @MathiasEgama หลายเดือนก่อน +2

    Kodi chilima anali musogoleri wa ndani?

  • @ruthkundwe7448
    @ruthkundwe7448 หลายเดือนก่อน +2

    God is watching,u will face judgement

  • @PatienceChumba-jc5mc
    @PatienceChumba-jc5mc หลายเดือนก่อน +2

    This world come to an end

  • @Drlufani
    @Drlufani หลายเดือนก่อน +3

    Koditu awawa olo kupanga mpikisano ndimtembo ukhoza kuwina mtembo wakufa

  • @rexphiri7242
    @rexphiri7242 หลายเดือนก่อน

    Antanyiwa mundperekele mon kuchikangawako

  • @mbewemisoyaanenenji1908
    @mbewemisoyaanenenji1908 หลายเดือนก่อน

    Powerful comrade, ause mu mtendere Chilima, usi ndi stupid sell out and traitor, uyuyu olo u MP ku Mulanje sangawine ata

  • @LukaEthibwi
    @LukaEthibwi 18 วันที่ผ่านมา

    Abwerere achair awina

  • @GoldenNamanguya-q9u
    @GoldenNamanguya-q9u หลายเดือนก่อน +2

    Mafuso opusa chifuka mukuziwa kuti malamulo sakulola amuluzi kuyima

    • @InessMchenga
      @InessMchenga หลายเดือนก่อน

      Inuyo mwamva kuti ayimiranso Kkkkkkk? Kapena akuti atati Dr Muluzi aimenso atha kuwina popanda kapeni. Ndi suggestion chabe imeneyo akudziwa kale kuti sangaimilire malamulo akumuletsa.

  • @ayamikasamba-lx4eo
    @ayamikasamba-lx4eo หลายเดือนก่อน +2

    bwaji osasisa feteleza bwaji ausi

  • @MchachaGoodson
    @MchachaGoodson หลายเดือนก่อน +1

    Malawi bwanji tichotse Nyansi before election phamvu kwa Anthu

  • @alickmodi6449
    @alickmodi6449 หลายเดือนก่อน

    Manganya ndichitsiru,tinamupanga trust koma pano mmm mbuzi yeniyeni

  • @LouisKanje
    @LouisKanje หลายเดือนก่อน +2

    Amuwongera tsogolo rake raulemu

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 หลายเดือนก่อน

    Usi analipidwa kale. Pano akupanga kampeni ya MCPigs.

  • @yowasschitsosa5348
    @yowasschitsosa5348 หลายเดือนก่อน

    Mungodzivuta inu ndi mabodza anuwo mungodzivuta, bwelani pa ground mesa kumangochi mwaluza

  • @MulowokaBlessings
    @MulowokaBlessings หลายเดือนก่อน +2

    Anaononga dziko

  • @BrunoChakukuma
    @BrunoChakukuma หลายเดือนก่อน

    Antanyiwa tabwerani muzatiwombole chikangawa wavuta

  • @MarryUnyolo
    @MarryUnyolo หลายเดือนก่อน

    Ine ndytu ndi wa APM awa azipita umunthu unawachokera

  • @PeterMvula-o5v
    @PeterMvula-o5v หลายเดือนก่อน +1

    Koma ntanyiwa adakonza ndi umunthu womwe basi 😂😂

  • @suzenmeja
    @suzenmeja หลายเดือนก่อน +2

    kkkkkk kuseka Sawina zoonad

  • @BlessingsmadalitsoShumba
    @BlessingsmadalitsoShumba หลายเดือนก่อน

    Exactly 💯

  • @AARONCHISUKAMZION-we3vp
    @AARONCHISUKAMZION-we3vp หลายเดือนก่อน

    KAMBA NGATI MWALA,AMBUYE MUCHILITSE DZIKO LA MALAWI,KODI MUKAMAGAWA NDALAMAZO NGATI TOMATO MUMAFIKIRA BWINOBWINO ANA A MASIYE,OPUNDUKA,AMAYI ALI PA UCHOKOLO,OSAUKA,OKALAMBA,NDIPO OSAKANGOPEREKAKO KUMA COMPANY BWAAA KUTI MUMIZIMU NAFE TINGAMWEKO TIYI PACKET KUKHALA K800,KAPEREKENI NDALAMAZO KU COMPANY YA FETELEZA KUTHEKA MZINDA UZATHANDIZIDWA OSATI KUPEREKA KWA MUNTHU MMODZI.KOMA MALAWI.NDANGOSIYILA PANJIRA

  • @leonardmalirana7423
    @leonardmalirana7423 หลายเดือนก่อน

    Muluzi Naye anali ndi zake bingu atamulanda chipani ndikuyambitsa dpp muluzi anatuma brown mpinganjira kupita ku Mozambique kwa chisano chifukwa anali mzake kuti akaletse kupeleka mpata wopeleka mwayi ku dziko la Malawi kuti likhale ndi dock ,basi chisano sanavomele basi lero tikuvutika dock langokhala

  • @user-kr1tf2tu7s
    @user-kr1tf2tu7s หลายเดือนก่อน +2

    Satana iwe ,,mumafuna azilamulila achigawochanu, ndiye musanati mukhaula zenizeni

    • @user-un6qv6sj3h
      @user-un6qv6sj3h หลายเดือนก่อน

      Mmmm malume zina tizivomeleza moto saphimbitsa Malaya amapsya

  • @BFWCPHIRI1978
    @BFWCPHIRI1978 หลายเดือนก่อน

    CHA UMUNTHU ADACHICHOTSA BUSHIRI CHIFUKWA MGWILIZANO WAO WA MAGAZI SAKUKWINILITSA A MCP

  • @LiyayaNyamula-j3b
    @LiyayaNyamula-j3b หลายเดือนก่อน +1

    Atsongoleli omwe anali ndi phatso ya utsongoleli bingu wa muthalika bakili mulunzi ndi chilima awawa ndeeee ndi bola

  • @AnusaNkhoma
    @AnusaNkhoma หลายเดือนก่อน

    Ndipo manganya mmmmm akupala kuno bambo asikono

  • @LumbaniPolowani
    @LumbaniPolowani หลายเดือนก่อน

    Ndigaileni number ya Usi nane andigaile andigaile ndalamanzo

  • @PhilbertoChaimah
    @PhilbertoChaimah หลายเดือนก่อน

    Chikangawa anampha mbiyeni kkk

  • @MustafaHenderson
    @MustafaHenderson หลายเดือนก่อน

    Kodi Achakwela vutonchani lipotila ndege tikulifuna

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 หลายเดือนก่อน +1

    Aaaa ndalama za amalawi OCHULUKA amene akudya ochepa iii koma MCP nyasi zachipani manganya chisilu chamunthu galu kwabasi ndi MCP yakoyo

  • @NizigiyimanaChantal-c2p
    @NizigiyimanaChantal-c2p หลายเดือนก่อน

    Maibwa Mulungu achite nawo modabwitsamo ife tikadalira wathu chilima

  • @muyabasamson
    @muyabasamson หลายเดือนก่อน +2

    Usi nigalu kwabasi

  • @user-ky4ce9gb6j
    @user-ky4ce9gb6j หลายเดือนก่อน +1

    Akuti kuagula anthu mmm koma anthu atopa tu oho

  • @ManninLongwe
    @ManninLongwe หลายเดือนก่อน

    Abakili muluzi ànagulisa chipani kwaku bingu wamutalika

  • @PhilbertoChaimah
    @PhilbertoChaimah หลายเดือนก่อน

    Chikangawa anampha mbiyeni

  • @user-kf3qm3or8l
    @user-kf3qm3or8l หลายเดือนก่อน +2

    Zowonadi

  • @user-ky4ce9gb6j
    @user-ky4ce9gb6j หลายเดือนก่อน +1

    Zomvesa chisoni kwambiri dziko linolo GUYS mmm

  • @ErnestChansa
    @ErnestChansa หลายเดือนก่อน

    President wa kumalawi ndi bon kalindo osati chakwela chikangawa ai chakwela ndi maike usi ndi konyelela kumavi onukha

  • @user-wg8tp8in1v
    @user-wg8tp8in1v หลายเดือนก่อน

    Koma anthu amasatila zomwe mumaulusa kapena zimathela pompano? Nanga zikuthekaso bwanji kut madela ena MCP ikumatenga mipando chosecho muli pano kufotokoza zoyipa za MCP kodi anthuwa akumva koma mwina muli nokha

  • @mbewemisoyaanenenji1908
    @mbewemisoyaanenenji1908 หลายเดือนก่อน

    Mlomwe opusa uyu sindinamuwonepo ine, Mulungu amuchitire chifundo

  • @anusahjenala1063
    @anusahjenala1063 หลายเดือนก่อน +1

    A usi or zomwe akupanga zija ndi zichani ali pa drama

  • @GabrielMzich
    @GabrielMzich หลายเดือนก่อน

    Manganya ndi fiti yokwanila chiyudas cheni cheni

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo หลายเดือนก่อน

    Galu iweyo pathako pako musiye mr usi

  • @user-re7fo3be2z
    @user-re7fo3be2z หลายเดือนก่อน

    Fact

  • @eliaskachali-xn2ve
    @eliaskachali-xn2ve หลายเดือนก่อน

    Chakwera dzina Lake ndi chikangawa.kukumbukila Kuti chakwera anamupha chilima. Tikati chikangawa tikuti chakwera

  • @GabrielMzich
    @GabrielMzich หลายเดือนก่อน

    SITIKUFUNA CHI PRESIDENT CHAKUPHA

  • @HaliJana
    @HaliJana หลายเดือนก่อน

    BAKILI MULUZI NDI KUCHITUNDA ,MUSAFANIZILE NDI MBOLO ZOSADULAZO CHAKWERA WAKUPHA WAKUBA MUTU WAKE WAZAZA MAMINA BASI

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile หลายเดือนก่อน +2

    Ntanyiwa pano tinakutuluka ndiwe wa boza

    • @MEGANABIGAILMNTHALI
      @MEGANABIGAILMNTHALI หลายเดือนก่อน

      Olo atatuluka munthu mmodzi sizingapangise anthu 1 million kumusatila. We Love you our pangolin ntanyiwa keep it up ambuye azikusamalalila n the whole members of limpopo. Timakunyadilani

    • @user-hl3vl9nt1b
      @user-hl3vl9nt1b หลายเดือนก่อน

      Wamutuluka wekha mbudzi yamiyendo iwili iwe

  • @peterchitimbe7610
    @peterchitimbe7610 หลายเดือนก่อน

    Eet bwanji nyasi saphimba munthu umasowa2 mtendere

  • @jamessheki4293
    @jamessheki4293 หลายเดือนก่อน

    Wina amugenda kuseriku

  • @SahilluYusuf-sk7es
    @SahilluYusuf-sk7es หลายเดือนก่อน

    Using ndi chitsiru galu wamunthi

  • @SydneyMwale-u9w
    @SydneyMwale-u9w หลายเดือนก่อน

    Chikangawa chakwera hiiii yai

  • @AminAbbasi-xc4qk
    @AminAbbasi-xc4qk หลายเดือนก่อน +1

    🎉🎉🎉🎉🎉

  • @MichaelKachiboo
    @MichaelKachiboo หลายเดือนก่อน

    Koma dzikoli uhu