MCHEWA WINA WADABWITSA ANTHU ATASAMBWADZA CHIPANI CHA MCP POYERA

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 1 ธ.ค. 2024

ความคิดเห็น • 16

  • @JulioChiwalo-t4f
    @JulioChiwalo-t4f 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Chilungamo chenicheni Kaya wina a fune asafune

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Bigg mwanena zoona cifukwa tikamanena anthu amati ndikudana ndi ocewa ai. Panopa mtundu uliwonse mmalawi muno ukuona nyekhwe za mcp zomwe zija za 1930 zija.mwanena cilungamo cikangawa mtima wake ngwa nyau, 2025 amalawi cilombo cimeneci cidzipita ku kasiya catizuza.

  • @LoyceChipwaila
    @LoyceChipwaila ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndipo anthu akamati chakwera ndi mcp akuchita bwino ndipo ndikuchita kudabwa nawo ndithu... zokhumudwitsatu zedii.

  • @Frederick-s4h
    @Frederick-s4h 11 นาทีที่ผ่านมา

    Mcp yagwakale apa utumize katundu wake kwasathe adzipita bs kkkk apm ndlkatundu pachitukuko amakwana anakoza mesiya wakumalawi apm muthallka

  • @VitumbikoKaunga
    @VitumbikoKaunga 58 นาทีที่ผ่านมา

    Chilungamo chipose apa

  • @Blessings-b7h
    @Blessings-b7h 15 นาทีที่ผ่านมา

    Zovuta kwambiri kuti anthu ena sakudziwa zimenezo.

  • @ZakeyoPhiri-s6n
    @ZakeyoPhiri-s6n 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zakale zimenezo akale sanunkha manyi

  • @EmmanuelChavulla
    @EmmanuelChavulla 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Akulu inu uku ndiye kuyankhula zoona osabakila mtundu koma kunena zoona zenizeni. Mwanditsangalatsa.

  • @WilliamNhlane-fd9hi
    @WilliamNhlane-fd9hi 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    🙏🙏🙏

  • @giftevans2957
    @giftevans2957 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Sure

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ntokoto km zoonadi zenizeni mchewa siwabwino mm

  • @DavieNkhoma-tf3ir
    @DavieNkhoma-tf3ir 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Sikuti ukakhala nchewa ndekuti ukuyenela kukonda mcp ayi..alipo achewa a opposition.chimodzi modzi alomwenso alipo ena a mcp...nde apa palibe chomwe ndumvapo

  • @elijahkasawala9122
    @elijahkasawala9122 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Alomwe simudziwa ndale that's why mwayamba zogawanisa mitundu. Koma mwayabazizi zimukwanisa chifukwa Malawi sakupanga zosangalasa inu.

    • @Blessings-b7h
      @Blessings-b7h 17 นาทีที่ผ่านมา

      Kkkkk achewa ndie oipa kwambiri ogawanitsa anthu

    • @elijahkasawala9122
      @elijahkasawala9122 4 นาทีที่ผ่านมา

      @Blessings-b7h anapangapo kuti. Mfundo mulibe mwayamba kukokela mitundu ya anthu. That's a shame. DPP silowanso boma kuganiza kwake kukakhala ukuku. U must know you are a minority people you need people to win elections.

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Sure