ZOMWE ZACHITIKA KU MOZAMBIC ZIKHALE CHENJEZO KU MALAWI KUPANDA KUSAMALA ZITHA KUCHITIKA KU MASANKHO

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 14 ธ.ค. 2024

ความคิดเห็น • 182

  • @khasimMusa-d3w
    @khasimMusa-d3w หลายเดือนก่อน +13

    Chkangawa Mutu ophwanyika uja tizagenda

  • @DaudBonomali
    @DaudBonomali หลายเดือนก่อน +11

    Ndipo zizaposa zaku Mozambique ndi kenya

  • @InnocentEdasi
    @InnocentEdasi หลายเดือนก่อน +8

    Ndipo chakwera asayelekeze kubela zimavuta ndithu ndipo sitizalola kt Chikangawah alamuliso munoh

    • @SiphamandlaNcaphayi
      @SiphamandlaNcaphayi หลายเดือนก่อน

      Mudzaonatu sitikubera Koma kuwina mwa nyooo

    • @JessicaManda-zm1ug
      @JessicaManda-zm1ug หลายเดือนก่อน

      Kuyankhula mopusa uku mwina nanu muli tuuuu pamenepo iyaaaaa👆​@@SiphamandlaNcaphayi

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu หลายเดือนก่อน +3

    Ku Malawi zidzachotika mosakaika, chakwera, Chimwendo, kunkuyu ndi Kabwira adziwe zimenezo, palibe amene angawavotele. Useless government ever in Malawi. Rubbish government.

  • @LuciusPatrick-f2c
    @LuciusPatrick-f2c หลายเดือนก่อน +6

    Zimenezi zikuyembekeza kuchitikaso kuno chifukwa mcp ikufuna nkhondo ndiye amalawi atopa ngati sakusintha ndondomeko zomwe akugwirisa ntchito pano zikuno kudzabvuta

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick หลายเดือนก่อน +4

    Aliyense akudziwa kuti MCP kwawo kwatha ndipo any results fovoured to them malawi tiluzamuyatsa moto koopsa ndipo kuzachema zedi Coz Chakwera ndioluza kale

    • @SiphamandlaNcaphayi
      @SiphamandlaNcaphayi หลายเดือนก่อน

      Mudzasauka nokha muli ndichani inu kumeneko mbuzi inu

  • @AffectionateGondola-cv7qj
    @AffectionateGondola-cv7qj หลายเดือนก่อน +1

    Don't worry kwanthu kuno sizizachitika before the counting is over Peter will congratulate chakwera

  • @imranstivini1226
    @imranstivini1226 หลายเดือนก่อน +2

    Ndipo chakwela sakuloledwa ku lamulilanso dziko la malawi
    Mavuto adzakhalanso kumalawi

  • @austenbushiri-cx1kh
    @austenbushiri-cx1kh หลายเดือนก่อน +4

    Anthu atopa bac ndi anthu andale next year osatizitenga bwino kunoso zizachitika ndinthu

  • @JamesRoben-dy7bx
    @JamesRoben-dy7bx หลายเดือนก่อน +2

    Mcp samalan kodzekan kuipa kun

  • @Japlennthondowa
    @Japlennthondowa หลายเดือนก่อน +5

    Kusavana kwa tsitsi kudapangitsa kukamera Malo osiyana

  • @EmmanuelSambani
    @EmmanuelSambani หลายเดือนก่อน +2

    Kukamba mwakuya kwambiri bwana ndipo zoona zake zimenezo.

  • @RichardImuran
    @RichardImuran หลายเดือนก่อน +2

    ❤❤mwalangula bwino my brother

  • @JosephChingombe-o3i
    @JosephChingombe-o3i หลายเดือนก่อน +2

    Ndipo tizaphana muno chakwera akazangobela cs ifeyo sitikumufuna

  • @AmosScott-z9x
    @AmosScott-z9x หลายเดือนก่อน +4

    Osakaika ansundwe aja kuchepa

  • @Nangayivuza
    @Nangayivuza หลายเดือนก่อน +4

    Kagame ameneo ku Mozambique🇲🇿

  • @ThokoMsonkho-hy4uc
    @ThokoMsonkho-hy4uc หลายเดือนก่อน +1

    If MEC will use smartmatic system,opposition parties must forget about victory .

  • @BerthaKasambala-y5k
    @BerthaKasambala-y5k หลายเดือนก่อน +2

    Kwasara iwe chikangawa basopu

  • @MuhammadAlie-u5n
    @MuhammadAlie-u5n หลายเดือนก่อน +1

    Ndipo asazayelekeze kupanga chopusa chilichose kt azabele olo atanenakuti wawina tizamuloza athuake siife ndizamutumizila njuchi😅😅🎉

  • @AwaliShaibu-n6e
    @AwaliShaibu-n6e หลายเดือนก่อน +2

    Zoonad abro kumalawi zichitika zimenezo chaka chikubwerachi

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm หลายเดือนก่อน +3

    Nao amalawi atengere phunziro ndpo akadzangobera achakwera adzaona nyekhwe

  • @ClementMunyolowa
    @ClementMunyolowa หลายเดือนก่อน +4

    Anthu ambiri ma ID sanalandire ndie akawonesa chani kukalemberako

    • @SiphamandlaNcaphayi
      @SiphamandlaNcaphayi หลายเดือนก่อน

      Chimbolo chakocho chosadula chonunkha gaga

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 หลายเดือนก่อน +1

    Kuno ku Malawi tikufuna asazangwilise ntchito machine chifukwa machinewo ndiwobera zisakho 😎😎

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm หลายเดือนก่อน +2

    Chikangawa achoke sitikumufuna

  • @munashemoyo4190
    @munashemoyo4190 หลายเดือนก่อน +3

    Ife tikufuna mavoti azawelengedwe pamanja bs osat machine awowo kuno mayaz kuzavuta zed

  • @mabvutomichaelpanagona1949
    @mabvutomichaelpanagona1949 หลายเดือนก่อน +1

    Amene apha loya amenewo ndi aku malawi walamula zimenezo ndi chikangawa basi

    • @SiphamandlaNcaphayi
      @SiphamandlaNcaphayi หลายเดือนก่อน

      Kupusa ndikupanda mzeru kumeneko chakwera chikunukhudzapo ndichani iweyo ngokugwa khunyu eti

  • @MadalitsoMarcos
    @MadalitsoMarcos หลายเดือนก่อน

    Ndipo mademo adakalipo bas madalitso from Mozambique 🇲🇿🇲🇿

  • @IbrahimUseni-p8f
    @IbrahimUseni-p8f หลายเดือนก่อน +1

    Ziwawa ndizosafunsa,boma ngati sasintha smatimatic ,,kuno ndiye kuzayaka kuposa Ku mozambiqueko

  • @esaMoha-dm4kj
    @esaMoha-dm4kj หลายเดือนก่อน +2

    shinkangawaw asashita nkutawa nkulisindu 2025

  • @BlaiseskSk
    @BlaiseskSk 17 วันที่ผ่านมา

    Venanciyo akufunidwa ndianthu kwsmbir now akudikira tsiku lina next month alengezeso kt wawina ndan

  • @BonexMaruanha
    @BonexMaruanha หลายเดือนก่อน +1

    Sanachite ngozi koma waphedwa ife tili konkuno ndipo tikuona sense. Achita kumupha, ndipo dzina lake elvino

  • @zacariasjoselemessonelemes9562
    @zacariasjoselemessonelemes9562 หลายเดือนก่อน +1

    Ndipo zikuchitikadi, kuli zipolowe za nyooo. Nkhondo itha kuyambikamso.

  • @EmilyBanda-e1f
    @EmilyBanda-e1f หลายเดือนก่อน +1

    tikuyenda onthawa nthawa ife Kuno mpaka 7days akuti Moçambique wavuta Kuno 🇲🇼

  • @JimmyMhone-b5p
    @JimmyMhone-b5p หลายเดือนก่อน +2

    Amalawi tawiyala kuti kuli mulungu anthu akutamanda fano lotchedwa chakwera

    • @ShamimuBisani
      @ShamimuBisani หลายเดือนก่อน

      Ndpo inuyo inu siyani nkhaniyo

  • @sarahfernando3674
    @sarahfernando3674 หลายเดือนก่อน

    Yes. Brothers this is what is happening in our country.
    Now 4 Million people are to the capital town till the white house. The president have tô uswer us some questions

  • @MandalaChaona
    @MandalaChaona หลายเดือนก่อน +2

    Vuto la kugwiritsa Ntchito SmartMatic machine.
    Kungomva Kuti Boma silimaludza zinali kale Zimenezo.
    Malawi MCP ikuyenda yotibuka kale ndipo singalamulire .

    • @RiteRoderick
      @RiteRoderick หลายเดือนก่อน +1

      Ndipo koopsa zedi

  • @edwinnyasulu2088
    @edwinnyasulu2088 หลายเดือนก่อน +1

    Nice analysis

  • @PatrickgawaniGawani
    @PatrickgawaniGawani หลายเดือนก่อน +2

    Chakwela ngati ali ndi nzuru aphuzile kenakake apa

  • @austenbushiri-cx1kh
    @austenbushiri-cx1kh หลายเดือนก่อน +2

    Umakwana asy

  • @AnnastasiaChakwiya
    @AnnastasiaChakwiya หลายเดือนก่อน +2

    Tiyeni tidzuke A malawi

  • @Blessings-td4cr
    @Blessings-td4cr หลายเดือนก่อน +1

    This will also be done this coming year,,, MEC will be the cause,,,, with this smartmatic machine tapanga download ife system iyiyi Ku Philippines yakanika kugwira bwino ndiso maiko ena it has been disqualified why here in Malawi gonna use this busheet machine they are planning to bring chaos in Malawi this government chikangawa.

  • @ciprianopedro3590
    @ciprianopedro3590 หลายเดือนก่อน +1

    Osati ngozi koma wawomberedwa ndi apólice awili zipolopolo 25 aluza moyo anthu awili ndi nzimayi m,modzi wavulala mwa kayakaya

  • @talandilabenedicto
    @talandilabenedicto หลายเดือนก่อน +1

    Anthu akatopananu koma inu mkumakakamirabe kuti tikulamulirani, zotsatira zake zimakhala ngati zimenezi

  • @isaaczuze
    @isaaczuze หลายเดือนก่อน

    Ineyo ndikufunizisa kwambili kuti zimene zokuchitika ku Mozambique zichitikenso kuno kumalawi

  • @isaaczuze
    @isaaczuze หลายเดือนก่อน

    Ndipo chakwera akhalebe president ndiye kuti ziko ili lionongeka osakhala masewela

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule หลายเดือนก่อน +1

    Very good

  • @CollingsMbira
    @CollingsMbira หลายเดือนก่อน +1

    Ndikukaika kuti tidzachita ma demo ,ma demo akadachitika pa imfa ya chilima😢😢😢RIP comrades..opposition yathu ndiyogona

  • @ZecaFranqueMarioMario
    @ZecaFranqueMarioMario หลายเดือนก่อน

    Loya sanachite ngozi koma adaombelebwa ndi a polince usiku.

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu หลายเดือนก่อน +1

    Ku malawi 🇲🇼 kuno chotsani za machine tipange chinsakho cha lokolo

  • @AbdulrazaqHussain
    @AbdulrazaqHussain หลายเดือนก่อน +1

    Let's hope it want come to that

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 หลายเดือนก่อน +1

    Ndipo azasiya zopusa zomwe akuchitazi

  • @ThokoMsonkho-hy4uc
    @ThokoMsonkho-hy4uc หลายเดือนก่อน +1

    Vuto logwiritsa mchito smartmatic machine ndi limenelo.
    Amatha kufunsa mkulu wa chisankho kuti mbali yako ndi itiyo kuti popanga seti machine apange zoti akondele chipani cha mkulu wa bungwe la zisankho.
    In this case,Malawi MEC chair is belonging to MCP, therefore oposition parties must refuse smartmatic system.
    This is bad SYSTEM ever

  • @ChimsyUlemu
    @ChimsyUlemu หลายเดือนก่อน +2

    Kuno zidzapotsa pamenepo anthu atopa ndi chikangawa and they must remember this is 2024 not 1964

  • @MemoryZiyaya
    @MemoryZiyaya หลายเดือนก่อน

    Uuuuhm Ambuye atithandize 😢😢

  • @JosephPhiri-p7b
    @JosephPhiri-p7b หลายเดือนก่อน

    Asayelekeze chakwera kudzavuta koooopya

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 หลายเดือนก่อน +1

    Ndipo kunoko olo atawina mwachilungamo mcp yatikwana kwambili ingokhala ngati yalamulatso zaka 33 mmmm

  • @EdwardSteven-t6h
    @EdwardSteven-t6h หลายเดือนก่อน +1

    Evil politicians

  • @HusseinsaidiSelemani
    @HusseinsaidiSelemani หลายเดือนก่อน

    Ife kuno tinaiwala kare mantha ndipo zomwe timafuna ndi zomwe timapanga MOTi inuyo ku Malawi ko zukani menyerani ufulu ana anU🇲🇿

  • @JamesALLi-m8i
    @JamesALLi-m8i หลายเดือนก่อน

    Ife nde zitilora kuti chakwera alamulire dziko la Malawi again we don't need this government again tiwonezana chaka cha 2025 more fire 🔥 guys 🇲🇼 we love Malawi ❤️ guys 🇲🇼

  • @SamuelLiwonde
    @SamuelLiwonde หลายเดือนก่อน +1

    chaka cha mawa ndataya moyo wanga bac

  • @WillianBanda-p7d
    @WillianBanda-p7d หลายเดือนก่อน +1

    Malawi becareful

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 หลายเดือนก่อน +1

    Mcp olo itazabela mavoti siingazawine

  • @MonyaSaka
    @MonyaSaka หลายเดือนก่อน

    Ndipo amene akatenge vote yake kuvotela chikangawa ndekt simalawi yemwe akudya chiteze dziko layipa kumalawi muzaka zochepa zomwezi mmmm

  • @LameckGamah
    @LameckGamah หลายเดือนก่อน

    Chakwera 2025 Sakupitiliza kulamulira dziko tili nd chikhulupiliro choti akufunisisa kma Sakupitilizabe Kuba misokho ya amalawi.

  • @MoosaSame
    @MoosaSame หลายเดือนก่อน

    Ndipo tidzadula mamchende achakwera chaka cha mawachi ndipo asayerekeze chikangawa

  • @PriscillaKhumbanyiwa-i1d
    @PriscillaKhumbanyiwa-i1d หลายเดือนก่อน

    Bwana ndi tambasule bwino nkhani ya ku mozambique sigozi koma lawyer amuwombela zipolopolo 25 panthupi lake ndi chifukwa chimene cha kwiyisa anthu

  • @RargieMediaclassic
    @RargieMediaclassic หลายเดือนก่อน +1

    Tikungoona kuchedwa pakadali pano

  • @ThomasSalaka
    @ThomasSalaka หลายเดือนก่อน

    Ndimaonakuti iyi ndi nthawi yoti Mukulu woyendesa zisankho Kuno Ku malawi a Anabel mtalimanja amphizile chinachake b4; it's too late

  • @georgeraphael8198
    @georgeraphael8198 หลายเดือนก่อน +2

    Malawi ndi Mozambique ndi zosiyana,a Malawi ndi ife mantha......

    • @DaudBonomali
      @DaudBonomali หลายเดือนก่อน +1

      @@georgeraphael8198 komano manthawo mukupanga pano 2019 or 2020 munalibe manthawo munthalika amatilera etiii koma naulendo uno adziwanso

    • @RiteRoderick
      @RiteRoderick หลายเดือนก่อน +1

      Anthu amafika potopa

  • @PhilemonLloydGalawanda-tz2zb
    @PhilemonLloydGalawanda-tz2zb หลายเดือนก่อน +1

    MEC siyikufuna kumva madandaulo a zipani koma ili pa tsogolo kupha ufulu wa mzika za Malawi kuti zisakavotele....mukazaona referee akupanga maganizo ayiye yekha osamva maganizo a ma team omwe Ali okhudziwa ndi maseerawo dabwani naye.....chodabwitsa nchakuti ndi chifukwa chiyani akukana kuwerengera mavoti manual, ndi chifukwa chiyani akukana ma external auditor? Vuto lawo la MEC ndi chiyani? Ndi chifukwa MEC yapanoyi ndi ya makani komanso onse ogwira ntchito kumeneko ndi ochokera chigawo chimodzi cha pakati? Zingondikumbutsa ndi ulosi wa Grace Chinga......a Malawi akufuna kwabwino tiyeni tichilimike tigwirane manja popempherera dziko lathuli lino kuti Yehova Mulungu wathu wa moyo alowererepo ... Ambuye akudalitseni Inu nonse omwe mutenge mbari mugawo la mapemphero osemphana dziko lathuli... Amen

  • @HiryChimalizeni-z2n
    @HiryChimalizeni-z2n หลายเดือนก่อน

    Nkhaniyo ndiyowona amubera.

  • @allahslave7177
    @allahslave7177 หลายเดือนก่อน +2

    Anthu amene akudziwa zomwe akuyenera kupanga ndinso kupanga express ufulu wawo osati malawi ugunatayi, kumuphera vp wawo koma kuli ziiiiii

  • @AnyuxyJulias
    @AnyuxyJulias หลายเดือนก่อน +1

    Ya ma id niikanikayo

  • @MasiyeChirwa-i3l
    @MasiyeChirwa-i3l หลายเดือนก่อน

    Exactly this will happen to malawi

  • @andiwochishadreck3753
    @andiwochishadreck3753 หลายเดือนก่อน +1

    Work up malawi

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm หลายเดือนก่อน

    Wakutsina khutu ndi mnansi . Mubvi oyang"anira umalowa mmanso . MCP ikubisala pachipande .

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile หลายเดือนก่อน

    Kulikonse zipani zolamula zimaba zinayamba kale kuchokera munthawi ya udf, dpp onse amaba ndichoncho

  • @amalauantonioantonio4056
    @amalauantonioantonio4056 หลายเดือนก่อน

    Si ngozi ayi, koma anaphedwa ndi zipolopolo 25 pa ATM

  • @PaulNkhata-c3b
    @PaulNkhata-c3b หลายเดือนก่อน

    Ngizoona coz amene ali muboma panopawa ndianthu oipa mitima komanso akudziwa bwino lomwe kuti akakhalapo ena pampandopo azakhala pamavuto 99%

  • @WilfredGunya1
    @WilfredGunya1 หลายเดือนก่อน +1

    Ndipo kuno zichitikad musakaike gat mcp sisamara

  • @EsnartGirivin
    @EsnartGirivin หลายเดือนก่อน +1

    Chakwela turned adzalakalaka kuthawa dziko lokhala lake lomwe kungobela

  • @AusterMuyila
    @AusterMuyila หลายเดือนก่อน

    Chakwera azawina mosanyengerera osusa okundikurirà kwa adzanthu kalembeseni not kumbwembweta simupindula naza

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile หลายเดือนก่อน

    A Malawi ife tili pa easy boma ndilomweri sitikusintha

  • @HiryChimalizeni-z2n
    @HiryChimalizeni-z2n หลายเดือนก่อน

    Ndipo adzazionatu paja akut sakuchoka muboma nkuru wa electrol commission ndi wachibare wachikangawa

  • @jamessheki4293
    @jamessheki4293 หลายเดือนก่อน

    Kunonso kuli atsogoleri ofanana ndi a Mozambique akufuna kuti kunonso tivutike

  • @JosephAlikanjelo
    @JosephAlikanjelo หลายเดือนก่อน

    Tiyeni tkavote mwaunyinji. Chakwera akuwinaso

  • @RajaAlicky
    @RajaAlicky หลายเดือนก่อน

    Achipan chosusa Ali nd lingaliro lofuna kubela mchifukwa chake sakufuna kucntha zna zomwe mtundu wa a Malawi ukufuna km pangatalike pangafupike zomwe zachitika Ku Mozambique azaziona zkuchitka ndpo asakaike

  • @KingfrahMachado
    @KingfrahMachado หลายเดือนก่อน

    Ndipo za live brother akuyenela aphunzile apa ndthu maka maka A mec ndienao

  • @JamesALLi-m8i
    @JamesALLi-m8i หลายเดือนก่อน

    Kkkkkk tizambitsana pa kumwa chaka cha m'mawa chakwera kodzekani you have to know that we don't need 💯 you ✋️ to be president of this country 😀 😄 🙌 🙄

  • @NelsonKasanga-b6q
    @NelsonKasanga-b6q หลายเดือนก่อน

    Ee zosa yenda kom tikapanda usamala zizachitike ndizimeneso eeeezosay
    enda

  • @rexphiri7242
    @rexphiri7242 หลายเดือนก่อน

    Chakwera get ready for Malawians we're not kids😢

  • @Akobandabandabanda-j2g
    @Akobandabandabanda-j2g หลายเดือนก่อน

    Uku ndikusalolelana zomwe zosafunika.

  • @JumatayaDavie
    @JumatayaDavie หลายเดือนก่อน

    Chikawa akangoyelekeza kubela chisankho azawona zomwe kuzankhala kumenyana ndipo anthu azafa ndinthu

  • @AntwezFadiga
    @AntwezFadiga หลายเดือนก่อน +1

    Ndili komwwkuno Nampula koma kwavuta kwambiri kuno😊

    • @SiphamandlaNcaphayi
      @SiphamandlaNcaphayi หลายเดือนก่อน

      Ndiye Nampula ndi Malawi?kamunthu kopusa iwe

  • @RodgersPhiri-ju1eo
    @RodgersPhiri-ju1eo หลายเดือนก่อน

    Yaa kumalawi sipanakhalepo zisankho zosabelana koma vuto likhala ndi inu anthu adalila boma kwa anthu ozidalila paokha alibe vuto kuma kwainu amene mumadalila boma lizizakugailani chimanga mulipavuto loopya komanso ena mwainu muzafa kufela munthuwina kuti azikadya bwino chonsecho or atakhala pampando sazizakuyang'anani ndipo mufa chaka chake ndichamawachi ubwino wa anthu andalamawa samapitako kumakapanga nao zopusa ngati zioneselo ndizina zotele amatuma inuyo ali osalola tiyeni kunsewu or iye atakhala kuti wapitako iye amakatetezedwa enanu opanda chitetezo muzikaphedwa kuonjezelaso mavuto ena pakwanu

  • @MarkKaliati
    @MarkKaliati หลายเดือนก่อน

    Umakwana fadah

  • @EmilySinjani-wg2gy
    @EmilySinjani-wg2gy หลายเดือนก่อน

    Kee praying for our malawi....

  • @DeenesNurudMeke
    @DeenesNurudMeke หลายเดือนก่อน

    Kumalawi kuno ndikutha kuona anthu akupanga straight

  • @GersonMbumba
    @GersonMbumba หลายเดือนก่อน

    A tule pasi udindo atiphetsa chakwara

  • @AnyuxyJulias
    @AnyuxyJulias หลายเดือนก่อน +1

    Apanga mademo atopa