Za ziii aaaaaaa ife si ana tikuziwa mukutipusitsa waziwa liti ndipo mutuluse ma lipoti a ife ya chilima atuluka munachita kunpha 2025 zikuntha zimenezo feti ameneyo
Musatitukwanisepo apa ..sitinakhalepo ndi a vp aafupi choncho... Awa. Pompano abwerera ku ntchito yawo ku Tikuferanji.. Kutiphera muthu yemwe anabadwa ndi utsogoleri even maonekedwe ake amamuchitira umboni ...
Michael usi siwa UTM koma wa MCP ndipo sakudziwa ntchito yake because akugwila ntchito ya minister Lero ngati iye ndi minister,,,,,,,,,ali pa u minister samkagwila bwanji,,,,,,,,,,wayamba mwaphuma ndipo akusewela ndi mkango mcp,,,,,,,,aziona because Malo akusewelawo siake ndi a bushiri
Koma sindingagwemo chifukwa Cha izi unless ndikuone usi uli limodzi ndi kaliati ndi ena onse omwe kaliyat akugwila nawo ntchito falling which sindiwe wa utm .ndanena ndanena sindikukhuluoilila ine ndipo zakozo sindinganve koma utagwilana manja ndi kaliati ndi ena mmmm ulemu wanga ukupezani ndithu koma mukupangazi mmmm mwavala Makaka a utm kunja nkati muli mcp
Usi ndimukonda ndipo ankandiwaza even malemu Chilima pomusankha anamukhulupilira koma anasintha atayamba kugwira ntchito ndi boma ndipo anadya bazi and akungoyankhula zambali yaboma not zolimbikitsa chipani cha Utm. Ndipo ukoko samagwira ntchito zaboma ndebwanji sanavale makaka achipani? Akunamatu Usi ndiwachabe l dont trust him
Manganya si wa UTM uyu, nanu mungowombera mmanja zilizonse mxiew! Tamusiyeni azipanga za MCP zakezo tatuwache Sikono wanuyo, SKC continue rest in peace, your still our president even in heaven will vote for you 😢
Dr Michael Usi ngatiti ndi wa UTM bwanji sakubvala makaka a UTM mmene ankachitira malemu Dr Chilima😢
I love Dr Usi very very much❤❤❤❤
Tiyeni timusapote mzathuyo ali chisanzo chabwino kwa inafe.
Vuto amalawi kumangoombela mmanja zinazilizonse angokupusisani basi😂
ndipo kwawo konko aziwapusitsa choncho
Za ziii aaaaaaa ife si ana tikuziwa mukutipusitsa waziwa liti ndipo mutuluse ma lipoti a ife ya chilima atuluka munachita kunpha 2025 zikuntha zimenezo feti ameneyo
Only in Malawi president is Ex pastor vice is Ex comedian
What a joke of a country
Very nice words and building words with love
Viva maiko usi Viva 😊
Zaziiii
Nde bwanji kose kumene akuyenda akulankhura zangongoli ndimumene anakhalira pampando 😢😢😢😢 Malawi sazatukuka nkhani kugawana ndrama zaboma basi😢😢😢
Michael Usi siwa UTM and he will never be in UTM again, we don't want him
Awa si a UTM bwanji sakubvala makaka a UTM
Musatitukwanisepo apa ..sitinakhalepo ndi a vp aafupi choncho... Awa. Pompano abwerera ku ntchito yawo ku Tikuferanji.. Kutiphera muthu yemwe anabadwa ndi utsogoleri even maonekedwe ake amamuchitira umboni ...
Anena kale bakili amalawi sachedwa kuiwala uhmmm mmalawi adakhala bwanji kma iii
Akuwanamiza anzake a utm uyu ndiwa mcp akuopa bwana wake chakwera kuti akamuona atavala za utm sagwilizanapo 😂😂😂😂
Ngati makaba zawuphawi ndiye mwapanga chani kodi zaka zomwe chakwera wakhara mboma uphawi awuwone rero
Kodi nyimboyi ndayam,bwiza guys paja akuluwa amakonda m,bwiza
Zaziii,,,,
Kudzikoku kunalibe mbalume kkkk onowakewo kupingasitsa manja mmm ai zikomo 😮😮😮😮😮
Koma si wa UTM bwanji sapezeka ku misokhano ya utm
Ati ndimunthu oopa mulungu pamene wakhala akuvula mapanti azimai
😁😁😁😂😂😂😂
Koma Malawi ndikuombera m'manja
Zaziiii zenizeni
Azakakuyezeka ndiyamene uzaziwe pomwe uli ndale timapanga usiku
Azimayi koma kugundika, Pali chanzeru kt ndikuimbila mmanja
Manganya Zima grace ndizazikulu vurani kakhope kowumako yudasi lwe
Kkkkkkk...muuzeni.....kkkk..ndi m'banga umenewu..😅😅😅
Ndiye ndizako nanga Kodi kkkkk
UTM itha mukangomulola Usi kutenga UTM
Michael usi si wa UTM ayi
Network yukugayaninso Makosana
Mmm koma akuluwatu Che machokola mbwelera za chuluka😂
Zoombela manjazake zazii
Usi anagulitsa chilima ndpo uyo Siwa utm ai ndpo musamupangire anapangira dima nzake munthu oyipisisa kwambiri ndpo ine akundinyasa manganya
Tigwilane manja nayani mambala iwe
Mary chilima akuchita kuoneka kuti she is still in deep pain chifukwa cha anthu ofuna udindo ngati iwe ukamuona ukumva bwanji mumtima mwako?
Ndiponso abare mmmm
Umakwana
Akuzutsireni avice president pamene iyeyo way I'ma mgalimoto amuzutsa bwanji?
Akulephera kutsika mgalimotomo???....😅😅😅😅😅
Akufuna kutalika ndi zakeyutu paja
Ife sitikufuna maik usi fiti imeneyo inamupelek chilima 😢😢😢😢
Ineyo ndiri ndi fuso kodi ndiye kuti samawakonda amalawi?
Fuso lina kodi titati tiwayike pasikelo anthu awiliwa chilima ndi Usi angalemele ndi uti
Fuso lina kodi Chilima pa dzaka 4 chamulephelesa ndichani zonse zomwe amalonjeza zinja sizinatheke chifukwa chani?
Sewero la tikuferanji kkkkk
Koma ausi asakhale ndimutima iwili
Usi mwati mdiwoyipa abwino mulungu ndiye wabwino
Good
Akupha inu mbuzi zaanthu shupit
Chisuru iwe chokapo palibe chair mbuz
😅😅
Michael usi ndi wa bodza
😄😄😂Koma manganya ndiwamasewero uyu🤣🤣
Wansanje alowa mbotolo
Ndiwe oipa kwambiri garu iwe
ameneyo ndamene anaphesa chilima kuti akhalepo ndiyeyo akuti ali ndi mthiko utm
Mzimu wa SKC ndi anthu wonse 8 munawapha aja ukuzunzani
Anthu akupha inu zipita ku Mcp kwao uko
Usawanamize anthu akwahuwo ay nanuso kumaombela manja zomwezo apanga chan bambo wa sikonowo
Michael usi siwa UTM koma wa MCP ndipo sakudziwa ntchito yake because akugwila ntchito ya minister Lero ngati iye ndi minister,,,,,,,,,ali pa u minister samkagwila bwanji,,,,,,,,,,wayamba mwaphuma ndipo akusewela ndi mkango mcp,,,,,,,,aziona because Malo akusewelawo siake ndi a bushiri
Unamupereka chilima kumupha kufuna udindo km manganya mulungu akukathe plz mulungu mukantheni manganya ndichakwera ndipemphero langa
Kuombela mmanja za ziii. Usi siwa UTM uyu koma ndi wa MCP asatipusise aMalawi
otukula si amcp ayi ndiokupha amenewo
Nonsense
Ciphe usi
Iweyo utsi, Ndi amene udamverana Ndi Chakwera Kuti Chilima aphedwe,mo womberedwa NKU mali zidwa motemedwa nchikwanje olo,mubise koma kunja Kuno zaululika Kale, Wanthu aja muda Chita kuwa phadi, mbolo za makolo anu,nyini za makolo anu,ndiwe ndani wobadwa moipa ngati iwe,kuipa Ndi Mtima womwe muziwe masiku achepe, achuluke,muzaphedwa chimodzi modzi.ndipo wina Aliyense amene akuku landira iweyo chigawenga Yudasi Utsi Panyero pa Make, Munthu woipa iwe, Ndipo Chilima,Wosama mu tchula misonkhano yanuyo.agalu ,ndiwe waku Mulanje iweyo, koma uziwe wakupha ndilu panga nayenso azafa ndilu panga nkhope yonyansa yo Wanthu Nonse Mulipo pamenepo namu imbira m'manja vanthu muni va Mayo
Uyu ndi wa mcp
Manganya uyu inu
Aaaaaaaaa,tangomalizani timiyezi tanu tasalato muchoke
Malawi wanga watha basi paka manganya ndikumamuti bwana
Ndichifukwa timati osamanyoza Muthu chifukwa sudziwa zamawa eetu😂😂😂
Aaaaaa iweyo zot manganya ndi Boss man moti wadziwa pompano 😂😂😂😂 koma osauka kudelera ma biggy 😂😂😂
Wa mcp nakudziwa
Siwa UTM uyu usatipusitse .satana ndi emwe anamuyika uyu anapha Chilima
Manganya kumpeleka chilima kufuna udindo wa 10 months okha, Mary chilima uja ukamuona sakukumvetsa chisoni? Mulungu asakusiye ndi mtendere iwee
Koma sindingagwemo chifukwa Cha izi unless ndikuone usi uli limodzi ndi kaliati ndi ena onse omwe kaliyat akugwila nawo ntchito falling which sindiwe wa utm .ndanena ndanena sindikukhuluoilila ine ndipo zakozo sindinganve koma utagwilana manja ndi kaliati ndi ena mmmm ulemu wanga ukupezani ndithu koma mukupangazi mmmm mwavala Makaka a utm kunja nkati muli mcp
Munthu ndi president wa UTM koma or tsiku limodzi kuvala makaka a UTM?
Adpp asyireni autm msasokoneze ai anthu ansanje inu
Yudasiyo
Afumuwa, ndi agalu kwabasi
😂😂😂😂😂😂zopanda pake
Zazii
Inu palibe mukuchita apa zatepurale izi 2025 zikutha izi
Or. U. VP. Sukumukhala or ndipang'ono pomwe golf shirt yake imeneyo
Osafuna usi akufuna udindo,bwanji kare chirima sanakusankheni,chirima anariwachikondi,m,zimu wake uwusemum,tendere m nyamata wanthu
Unapereka chirima
Sopano magalasiwo mukuwaphunzila kumagowagwilagwila akulemela zoziwonela kukulu
😂😂😂😂😂
Choka iwe mthera kuwili iwe, unamupereka mzako kumuphesa chilima chifukwa cha unthera kuwiri .
UTM yanji yopanda SG??
Usi ndimukonda ndipo ankandiwaza even malemu Chilima pomusankha anamukhulupilira koma anasintha atayamba kugwira ntchito ndi boma ndipo anadya bazi and akungoyankhula zambali yaboma not zolimbikitsa chipani cha Utm. Ndipo ukoko samagwira ntchito zaboma ndebwanji sanavale makaka achipani? Akunamatu Usi ndiwachabe l dont trust him
Mbolo yake manganyayo
Ndiposo pamtumbo pake
Zilibwini kungoreko mwina antha maludzi
Manganya si wa UTM uyu, nanu mungowombera mmanja zilizonse mxiew! Tamusiyeni azipanga za MCP zakezo tatuwache Sikono wanuyo, SKC continue rest in peace, your still our president even in heaven will vote for you 😢
Zofoila basi u vp wake uti
Drama yeniyeni
Za ziiiiiii
Zochititsa manyazi
Manganya VP amaufuna ndikale wa satanic
Ka usi ka galu kwabasi kanamupeleka nzake chilima
Sizikukoma ataaa
Manyo Ako usi
Akuziona ngati akulotatu basi zomwe umafuna ndi zimenezo kuti uzitulusa mutu pamwamba pa galimoto 😅😅😅😅
😂😂😂😂😂
Koma malawi
Palibe mwachita inu naanu mwangogwera zaini amangamya thawi yatha mcp idxipita yatilanga mpakana kuchotsa miyoyo??? Rest in peace saulos
Koma ineyo sinamuonepo atavala za utm uyuyu
Wakhupha
Chitsiru iwe
Galu iwe kwabasi
Aaaaaaaaaaaaaa
Kodi magalasi amangoti wagwira kuwabvula kuwavala amamulemera?
😂😂😂😂ati ubwana
What I hate bad comments,