NKHANI YA LAWYER ALEXIUS KAMANGILA IJA YAVUTA MA BUNGWE ENA ALOWELERA NDIPO LERO APANGISA CONFERENCE

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 13 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 45

  • @RhoxinahMalamba
    @RhoxinahMalamba 20 นาทีที่ผ่านมา +1

    Bravo!! Mr. Kamangira
    Dzuka Malawi Dzuka.
    Ma youths this is the right way to fight for our country osati kutumidwa kuyambitsa zisokonezo. Nthawi yakwana kuti achinyamata atenge udindo to shape their future. This is very commendable. More fire bwana Kamangira.

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +8

    Me too , I will in front... Amalawi nthawi yakwana kuti Malawi yopulumuke ku muchitidwe wobela amalawi aumphawi

  • @KingDavedNkhata
    @KingDavedNkhata 37 นาทีที่ผ่านมา

    Congratulations brother Kamangira
    Mulungu akhale nanu nthawi zonse
    angakhale khamu la wanthu limadana ndi chilungamo
    pambuyo panu ngangangaaaa timakunyadirani kopotsa zedi

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx 25 นาทีที่ผ่านมา

    Truth is a spirit from God. No one can attack the truth because it's a product of Holly spirit.
    No matter how much the corrupt judges would try to silence the truth, they cannot win.
    Kamangila is a God sent lawyer to save justice at it's extreme level

  • @ziwani3682
    @ziwani3682 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Powerful message

  • @PhiriChiyambi
    @PhiriChiyambi 57 นาทีที่ผ่านมา

    Let all Malawi'an tigwilane manja timusspote mu njira ili yonse chinyengo chikuchuluka kundende angopezeka osauka okha mbava zikuluzikulu zolemela sazimanga Kaya ndalama let's lez fund to support this laywer

  • @MariaGatoma
    @MariaGatoma 33 นาทีที่ผ่านมา

    Mr kamangila pitilizani kukoza Malawi wathu,,,wakutumani ndi mulungu,,anthu akufa osalakwa,,,kumangidwa,,okuba ali khale chifukwa ali ndi ndalama,,mulungu wakutumani kuti mupulumuse anthu osauka

  • @emmanuelchirwa3420
    @emmanuelchirwa3420 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Well done ✅ guys good job thanks, again well done guys together we can make Malawi better place for all,,

    • @twaibupatrick-k1n
      @twaibupatrick-k1n ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Komaso ukunena zooona kuyamikaso ndikwabwino kwayamika anthu amenewa

  • @MrMagombo
    @MrMagombo 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Apa Justice wo alowe mu khoti ndi a kamangilawo. Ndipo ikhale pa radio.
    Mlandu omveledwe ndipo ma CSO ndi ma Judge atatu amvele mlandu wo.
    Guys dziko limene athu akukayikila ma Court limakhala Lawlessness.

  • @JamesALLi-m8i
    @JamesALLi-m8i ชั่วโมงที่ผ่านมา

    More fire 👦 🔥 guys 🇲🇼 Malawi is badly now 😫 😢 😩 be strong 💪 👏 we trust you guys 👦 more fire 👦 🔥 again

  • @FredKanyerere
    @FredKanyerere ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Well done brother kamangila.

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Powerful massage

  • @GodfreyKamphiripiri
    @GodfreyKamphiripiri 59 นาทีที่ผ่านมา

    Powerful message ❤❤❤

  • @alickkachepa3801
    @alickkachepa3801 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Let's protect this property ❤

  • @SymonKachala-b2y
    @SymonKachala-b2y ชั่วโมงที่ผ่านมา

    😊😊😊😊
    I totally support this statement

  • @peterbakuwo1249
    @peterbakuwo1249 6 นาทีที่ผ่านมา

    I can sense seriousness in these guys...
    Go,guys go and bite hard.

  • @ChikumbutsoJohn-rs4tt
    @ChikumbutsoJohn-rs4tt ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    IT IS TIME TO RESTORE MALAWI BELOVED COUNTRY

  • @JosephIsaac-s1c
    @JosephIsaac-s1c ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    I see changes in Malawi 10-15 years come

  • @CharityChikomo-hl1gz
    @CharityChikomo-hl1gz 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Well done

  • @Felie-p7l
    @Felie-p7l ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Asasowetu ameneyo

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Even the devil knows that justice is sold in the country 's courts .

    • @SymonKachala-b2y
      @SymonKachala-b2y ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Nkhani ndiyayikulu iyi

  • @GladysndilimbiraBonongwe-g6c
    @GladysndilimbiraBonongwe-g6c นาทีที่ผ่านมา

    Nthawi yakwana

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Aaa mamvuto TIKUKOMANA NAWO LELLO AMALAWI NDIWOMWE AMABWALO LAMILANDIKU KUGAMULA MWA DZIPHUPHU LELO MALAW ALI PAMOTO APA AGALU KWABASI

  • @SprianoJeke
    @SprianoJeke นาทีที่ผ่านมา

    Restoration

  • @giftmakoyo1441
    @giftmakoyo1441 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Chilungamo chibwere poyera basi

  • @CharlesChagudubuka-rm6bh
    @CharlesChagudubuka-rm6bh ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Dziko lidaipa ili it's better maiko anzathu adaonongeka koma ku zachuma adasunthako,koma sikwathu kuno umphawi wa thoo koma kumangopondeleza anthu osuka Iwo nkumalemera modabwitsa why Malawi??? For example njala ili muziko muno sibwino kumafinyana tokhatokha pofuna kusangalatsa anthu oononga dziko ndi odzikonda 😢😢😢

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Osawanyengera a justice lenani Manda atumbukawo kuopitsa mtundu wao..ife a malawi tatopa ndi zachinyengo zimene atumbukawa amachita mma office a bomawo..kodi ndi umphawi kodi ? Nkuona Dr H kamuzu Banda anawathamingitsa atumbuka onse azipita kwao in 1987..cos they are all corrupt .them are thieves.. ndiye apa akapitiliza onse atumbuka adzipita kwao not live in the southernbregion or the central region.

  • @promixphotography8056
    @promixphotography8056 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Vuto lomwe tili nalo ife aMalawi ndi matha chifukwa zinthu zambiri zikukhala zovuta chonchi tiyeni tione maiko ena akupangira kutuluka sikukutengera kuti atipha ai, ndipo sangaphe tonse ai.lets open our 👂 ndikuonaso

    • @BeatriceSaulosi
      @BeatriceSaulosi 2 นาทีที่ผ่านมา

      Ndipo Nkhaniyo ndiyoona a Malawi tili ndi matha anyooo

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ma judge akakhala kuti ndi achinyengo dziko so silimalongosoka, komanso ma judge akumalawi panopa ali mbali ndi boma

  • @YasmeenYalabi-b2c
    @YasmeenYalabi-b2c 4 นาทีที่ผ่านมา

    Ayitu uyu yekha simukhwasula akuimila amphawife ma judge ena ndiomwe agudwa ndi boma cholinga azathandizile kubela chisankho

  • @SprianoJeke
    @SprianoJeke 3 นาทีที่ผ่านมา

    Kwatentha 😂 palibe kucheza

  • @MissoutNiceday
    @MissoutNiceday ชั่วโมงที่ผ่านมา

    These people the dont have ashame ,when the west money for poor people.

  • @JerieWytonTengani
    @JerieWytonTengani 16 นาทีที่ผ่านมา

    Zikomo kwambiri pothandiza dziko lino kwa Malawi aliens kuti tiziziwa chilungamo kwa anthu akuba ndalama za misonkho Mexico la Malawi.Wabayo asathawe ndipo tiwadziwe ndithu poyera.

    • @JerieWytonTengani
      @JerieWytonTengani 6 นาทีที่ผ่านมา

      DONT LET THEM,BUT WE NEED THE TRUTH TO FOCUS IN OUR NATION .INDEED IT IS HAPPENING IN OUR GORVERMENT OF MALAWI.START WITH CHAKWERA AND ALL MINISTERS,JUDICIAL ,AND ALL DEPARTEMENTS.

  • @BENSONRANGWANI
    @BENSONRANGWANI ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chakwela wamupha chilima zasala zosatila Zach

  • @ChifundoGalusa
    @ChifundoGalusa ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Corruption Corruption

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Judiciary is wrong, you think kamangila is mentally ill... judiciary is rotten

  • @WarriorKB-u3k
    @WarriorKB-u3k ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kamangila anaconda dziko lake wachita bwino kuyalutsa a galu amenewa kamangila suli wekha tili pambuyo pako ndinthawi yoti chilungamo chiyende ngati madzi coz chikangawa akuononga malawi

  • @Yamikanilikolome
    @Yamikanilikolome 5 นาทีที่ผ่านมา

    Following