Ulemu wanu big up Comrade Ntanyiwa may God bless you bra Osasiya ana ankhandwe amenewa till a Malawi aupeze mpumulo We're so proud of you guys Bakili Muluzi tv, Born Kalindo concluding you Comrade Ntanyiwa keep it up guys
Hy Mr Mtanyiwa, Bakili Muluzi TV ndi The DC Boooon Kalindo president wa aphawi nonse ndimakudyadirani MCP singamake pa Inu Ndipo kukupezani inuyo our brothers you both stay safe and blessed ❤❤❤❤❤❤❤❤
Ulemu wanu brother Ntanyiwa ifetu timakunyadirani nonse Bakili Muluzi TV ,the D.C and crew yonse pa Limpopo FM osaiwala brother Salo .DJ munyanane komaso Mr Samuel
Ndi madoro team imeneyi onse the Dc bakiri muluzi TV comrade ntanyita brother salo sangawakwanisse team imeneyi ndi poison kwambili amene angamalimbane nawo azivaya yekha one buy one
Mr Comrade ntanyiwa Allah azikudarisanu mpaka crocodile utuluke mu boma komaso chilungom tichiziwe basi Allah adalise dziko rathu kuti chipani cha Satana cha mcp chituluke mu boma crocodile team
mutanyuwa ndmakunyadla heavy andp ndmakukonda kwabc...kmn chonde usamawauze anyapapiwa zot munakumana mene wanenelamu angakuphe chonde we are expecting alot from you...
Musayerekeze Kupanga ubwezi ndi Big Joe akupanga nyambo afuna akupusitseni amenewo ndi gulu la agape khombe limenerolo malume chilombo cha mudzi chimenecho
Chilungamo amalawi tinachiziwa kale kuti kufa kwa achilima ndi gulu la Richard chimwendo kuteogozedwa ndi achakwera,ngakhale mwana wazaka 10 iyi ndi history
Ulemu wanu big up Comrade Ntanyiwa may God bless you bra
Osasiya ana ankhandwe amenewa till a Malawi aupeze mpumulo
We're so proud of you guys Bakili Muluzi tv, Born Kalindo concluding you Comrade Ntanyiwa keep it up guys
Hy Mr Mtanyiwa, Bakili Muluzi TV ndi The DC Boooon Kalindo president wa aphawi nonse ndimakudyadirani MCP singamake pa Inu Ndipo kukupezani inuyo our brothers you both stay safe and blessed ❤❤❤❤❤❤❤❤
Papa ntanyiwa, papa Kalindo, papa muluzi TV, brother nsalo we Love you so much our kings keep it up we will continue praying for you guys mumatiimila.
You forgotten Shamba I need his contact or his wife, let's help him
@@AchinaKellz u mean pastor shumba?
Ntanyiwa mulungu akusungeni ndimoyo komanso anzizako awili amene sindinawatchule maina
All praises to Yahweh for all these revelations, proud of you comrade Ntanyiwa, be safe and protected always
Ulemu wanu brother Ntanyiwa ifetu timakunyadirani nonse Bakili Muluzi TV ,the D.C and crew yonse pa Limpopo FM osaiwala brother Salo .DJ munyanane komaso Mr Samuel
Welcum broh eeee koma basi bola kumapita ku Burkina Fasso kumakakhal kuli president odzindikira osati izi zoyendera jackson ngt nkhuku zachtopazi
100% support brother, keep it up, atsekuleni maso a Malawi.
God bless you all guys,,, Comrade Ntanyiwa, Bakili Muluzi TV and the DC Bon Kalindo
THOSE WHO LOVE LIMPOPO FM WITH COMRADE NTANYIWA LETS ALL GATHER HERE,LETS ALL SHOW SOME LOVE❤❤❤❤❤❤
Am proud with you guys papa ntanyiwa papa Bakili muluzi tv papa Kalindo papa brother salo ndi papa DJ mnyanane 🎉🎉🎉🎉
Allah alipo mpaka chilungamo tichiziwe basi akuona ngati akuchenjera koma akunama akunamizira kudwala cholinga choti thawi izidusa ndiye akuzinamiza
Inuyo ndi 1 Boss Koma plz pa you tube muziponya mwachangu
Kkkkkk koma comred ntanyiwa ndi dolo komano osamaulura azakutolani 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂❤❤❤❤❤❤
Ndi madoro team imeneyi onse the Dc bakiri muluzi TV comrade ntanyita brother salo sangawakwanisse team imeneyi ndi poison kwambili amene angamalimbane nawo azivaya yekha one buy one
Stay safe comrade tanyiwa we love you
Ndiye akapha azingowonjezera kuipa mmalo mochapa mbiri akupitiliza nyasi
Mtanyiwa yemweyo.....kuti huu ....kuti huu... kuti huuuuu kkkkkk. We love u all
Sangaimake Ntanyiwa,The DC Bakili TV, Sallo
Brother ntanyuwa inu ndi katundu ana sangamake
Ulemu wanu Mr ntanyiwa
Timakunyadilani always bro osanyengelela anthu oipa awa ationongela dziko akuba koipa
God bless u guys u're doing great job weldone
Mr Comrade ntanyiwa Allah azikudarisanu mpaka crocodile utuluke mu boma komaso chilungom tichiziwe basi
Allah adalise dziko rathu kuti chipani cha Satana cha mcp chituluke mu boma crocodile team
Umakwana mr ntanyiwa
Ku mcp zoti anthu akupitila ndalama zomwe zaphwekazo president sakuziwabe, keep it up guys
Kma mumandiwaza timu yanu mumandimvetsa kukma
Palibe choyipa ingakhare cholanga chidzakuy andikireni nonse u r the eyes and ears of malawian ,may God protect u all
Koma bola inu a Mtanyiwa mukhale naye patali big G .Mwina ndi nyambo yoti inu muganize zokumana naye kenako azakupelekeni.😅
Big man Mulungu akumenyereni nkhondo opanda inu bakili muludzi tv and born kalindo nose amene mukutiziwitsa tikulephera kuthokodza
Akupatseni moyo wautali mulungu
Ntanyiwa
Chimwendo ndie President wa mcp.
Musamuyandikire big Joe ikhoza kukhala nyambo,
mutanyuwa ndmakunyadla heavy andp ndmakukonda kwabc...kmn chonde usamawauze anyapapiwa zot munakumana mene wanenelamu angakuphe chonde we are expecting alot from you...
Leaving no stone unturned. Kuika chilichonse poyera ❤
Azibambo sopano❤
A kongeresi sangakukonde Ntanyiwa kkkkkk ndi awa akutukwanawa sakusowanso......
Ntanyiwa samalan ndi big jooo
😂😂😂😂 inu ndi dolo big man ulemu wanu
Love you guys mmatiyimirila😅
Musayerekeze Kupanga ubwezi ndi Big Joe akupanga nyambo afuna akupusitseni amenewo ndi gulu la agape khombe limenerolo malume chilombo cha mudzi chimenecho
Mr ntanyiwa please osayelekeza kukumana ndi Big Joe asakunamizeni apa plan imene cholinga mukhale ngati mulilimodzi kuti akupheni please samalani izi
Tinaifufuta chifukwa audio inali yosakwanira...tipepese now zonse zakonzedwa.
Enjoy.
Apology accpted but keep moving we r tired with this nonsense leadership may God almighty protect u guyz where u r God bless u
Mumve kunanala a Mtanyiwa komwe muliko
❤❤❤❤ love you more thanyiwa
Komadi apule chibweleleni kuunga sadayankhule nzimene adapitila
Timakunyadirani gyz olimbana ndinu angotaya nthawi A malawi tonse tili pa mbuyo
😂😂😂 big up to you comrade
Koma samalani Ntanyiwa sionse amati ambuye ambuye omwe akalowe ku mwamba
Kubwebweta koma pa ground 0 ndipo mulila zenizeni
Nde iweyo ps ground po wapangachani??? Devaluation akupanga ambuyako chomwe ukunyadira
Wasemphana nacho chikwama 😂😂, wanya nayoooooooooooooooooooooo!!!
Timakunyadilani madolononse
❤❤❤❤ 3 in 1 alkaidah network
Ndipo mulungu awalengele mpedzepeze paliponse pomwe adziyenda😅😅😅😅😂😂😂
Ulibe zochita Zina galu iwe
😂😂😂😂 kwachematu
Inu ndiwakulu bro
Chilungamo amalawi tinachiziwa kale kuti kufa kwa achilima ndi gulu la Richard chimwendo kuteogozedwa ndi achakwera,ngakhale mwana wazaka 10 iyi ndi history
Mr ntanyiwa please take care eya asafikedi nthawi yamambvoti akudzitenga ngati madolo ayiwala kuti kunja kuno kuli mulungu adziwona
Ati muzipita mmodzi mmodzi mutatha kusaza magazi😅😅😅😅😅😅
Ine ndinachiziwa ndichowona patali kkkkkkkkk😂
"Mbalame ikauluka kwambiri imapitirira chisa" beware ndiwe mwana udzalilitsa makolo.
Ululan chilungamo dxitsilu dzimenedxi dziyaluke 😅😅😂😂
Big joe ulemu wako umenewo timati umunthu,mcp anthu akupha,Ntanyiwa,kalindo,bakili TV anyamata inu mumatiyimilira
Big up big joe
❤ my vot DPP
Aaaaa zanu zinada kale inu zeru mulibe ndi ma boza anu anthu c timakukhulupilirani!
😂😂😂😂 anthu ake ati uziti iweyo, simamukhulupilira kma daily ukumavera ma bodza omwe ndekt mntanyiwa amakusangalatsa ndipo umaikondaso program imenei
Nde mupezekelanji kuno
Umadzichemelera nkhani yake imeneyo kupanda nzeru Amtanyiwa fundo mulibe mbala iwe
Mwayamba kuwapatsa ma Tip TU ot akugwireni😂😂
Opposition mkumandadi😊😊
❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Apolice akumalawi ndimbava
comrade mtanyiwa inuyo ndi one
Good job nyilongo
Umakwanaa boss
Kkkkk oyess zoonadi anthu oyipa kwambiri mcp
Sitikudandaula naye ndi munthu opanda phindu.
Akangobela zisakho tizavotaso
Wa Bodza uyo akukupanga punsi punsi Big Joe usamuvere za mabodza zo kuti afuna akukope ni man ndi poison amene yo walandira za mbiri ku mcp
Mbambande comrde ntanyiwa
Mbambande Mtanyiwa
Big joe palibeso
Amasuleni big
Ndipo chilima sakupita ulele musazinamize kuti yatha
😂😂😂😂😂😂❤❤❤❤❤
Ndimava nanu kukoma akomrade ntanyiwa
Reply toTambala
Zopusa zenizeni.
Mumatha inuyo 3guys
❤❤🎉🎉🎉
Ok takumvaaq
Kma samalabe bale wanga asakuchosele moyo anazikambewa
😅😅😅😅😅 Athu osokoneza chabeee inu..
❤
Koma achimwendowa amawona ngati adzafa?
Wanyanayoooooooooooooo
Zanziii
Igweeeee
Ana achepa
Inuyo ndi kathundu ndithu
Mumatiyi milila❤