COMRADE NTANYIWA KU STATE HOUSE KWAVUTA ZIGOLOLO MOTI AGWILANA ALI MALISECHE AKUPANGA ZAOZO

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 2 ก.พ. 2025

ความคิดเห็น • 152

  • @ChristinaMdeza
    @ChristinaMdeza 12 วันที่ผ่านมา +15

    Yakwiya ndi mzimu bas ku chikangwa kuja. ndiye jasse kumati boma ndilomweli zopusa bas zikom comrade wathu ntanyiwa. we love you ❤❤ God bless you

  • @LeyvanSamuel-pe5tc
    @LeyvanSamuel-pe5tc 12 วันที่ผ่านมา +6

    Keep it up good work 😇 comrade ntanyiwa chikangawa akapuma kumwamba 😅

  • @VictorChunga-f1g
    @VictorChunga-f1g 11 วันที่ผ่านมา +3

    Osamatalikisa nkhan enafe after nkhanga zaona timathamangilanso kut tikamverenso history the best teacher

  • @SalomeManda-c1i
    @SalomeManda-c1i 11 วันที่ผ่านมา +1

    Respect to You Mr ntanyiwa

  • @RuthMsosa-c4r
    @RuthMsosa-c4r 12 วันที่ผ่านมา +3

    Just resign Mr pule eish zatikwana muli buzy kunyoza Mutharika izitu anthu Anu Aja azikambiranenso pa MBC ,galu wasekatu apa

  • @DauglasBowa
    @DauglasBowa 12 วันที่ผ่านมา +3

    Koditu saulosi chilima uja osamamutengera kuntoso tionatu zinthu mu 2025 comrade ntanyiwa forever

  • @charlesmphatsokazembe1480
    @charlesmphatsokazembe1480 11 วันที่ผ่านมา +3

    Try kumalankhulako mofulumira komanso to the point. But I really like your contribution

    • @PatrickZinenanie
      @PatrickZinenanie 11 วันที่ผ่านมา

      Yes nane ndizomwe ndinanena kuti akulu awa antanyiwa akumatenga nthawi kuti ayankhule mfundo timankonda but azingohita the nail basi akumatithera bandle

  • @McDonaldbeketeNkhata-n4l
    @McDonaldbeketeNkhata-n4l 12 วันที่ผ่านมา +3

    A Chakwera Mulungu Awakwira Ndibwino Kuvomereza Kutula Pasi Udindo

  • @EnockLichenya
    @EnockLichenya 12 วันที่ผ่านมา +4

    Akapitiliza zolubwa lubwa tiponya ma pic 😂😂😂😂😂 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣

  • @TasiyanaChinula
    @TasiyanaChinula 11 วันที่ผ่านมา +2

    Eeeeeeee koma.
    Zamaliseche zo nde ayi aaaa
    Umve umenewo,,,,chimanga chingakule bwino choncho 😂😂😂😂...Tapolamilidwa😮

  • @dorrahChilimampunga-e3y
    @dorrahChilimampunga-e3y 11 วันที่ผ่านมา +1

    Limpopo mbambande ❤❤

  • @muhammadstaubi4604
    @muhammadstaubi4604 8 วันที่ผ่านมา

    Rudo ?like mother like daughter.like daughter like John tembe.mashona mahule, pakaipa apa shamwari.

  • @SetmatherPeter
    @SetmatherPeter 3 วันที่ผ่านมา

    Ehehehe iiiiiiii koma musatisiye tokha ambuye🙏🙏

  • @EnerstMwitha
    @EnerstMwitha 12 วันที่ผ่านมา +2

    Pepani mr chikangawa tulani pansi udindo tsoka iyi minyama iyi ndithu mizimu yathu 9 yakwa basi asa mwayesa hotel kapena kongona basi misikho athu koma athu kuvutika kwambili inu kungonana basi ma hule muchoka nose makape inu buzi zawathu

  • @LimzeySande-b9n
    @LimzeySande-b9n 12 วันที่ผ่านมา +3

    Ku MCP kuli uhule wayooo

  • @MISHECKBANDAH-m3h
    @MISHECKBANDAH-m3h 12 วันที่ผ่านมา +1

    Waza comrade yomweyooo chikangawa crew

  • @JimmyMhone-b5p
    @JimmyMhone-b5p 12 วันที่ผ่านมา +3

    Ntchito za satana ndizomwezo

  • @GraceMasiye
    @GraceMasiye 7 วันที่ผ่านมา

    jessie kabwira akumafunsira ana ndikumawavulira realityx2😂🤣🤣🤣ziyalu ziyaluu

  • @phillipchimalizeni2656
    @phillipchimalizeni2656 11 วันที่ผ่านมา

    More fireeeeee comrade 🔥🔥🔥🔥🔥

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 8 วันที่ผ่านมา

    ZACHISONI CHAKWERA IWE MUTU MWAKO MULIBE CHILICHOSE CHAZERU AMAI MAI OMWE AKUFU WOYEMBEKEZERA ZIPATALIWA NDIWO WOFUNIKILA KWAMBILI NDIWO AMAGWILA NTCHITO YAYIKULU KUBWERETSA MA DOCTORS MA NESI MUNO MUDZIKO KOMA IWE CHIFUKWA SUNABWERE NDI CHOLINGA CHABWINO PAMPANDOWU UNABWERA KUDZAPHA ANTHU CHIFUKWA CHAKE UKUPANGA IZI KOMATU UDZAYANKHA ONE DAY

  • @EstherLuka-m4r
    @EstherLuka-m4r 12 วันที่ผ่านมา +2

    Koma ndie kwalowa sewerotu ku State House. Nthawi yovota ikuchedwa mwamvaaa

  • @LouisChabwera-y2w
    @LouisChabwera-y2w 12 วันที่ผ่านมา +3

    Koma antanyiwaaaa aaah izixi mumaziziwa bwanji

  • @alfredmongola900
    @alfredmongola900 8 วันที่ผ่านมา

    Mzimayi oimba mwaluso gospel Rudo mkukupa wagwidwa ndi chigololo ku state house
    Kodi mwanva!!!!!!!!!!!
    Zamanyazi kwqmbiri mkazi wa nick chakwera

  • @TrinityKangombe-z7f
    @TrinityKangombe-z7f 6 วันที่ผ่านมา

    Kaya ndizabodza koma wamwanyidwabe Rudo yo basi😂😂😂

  • @ThomasMlowoka
    @ThomasMlowoka 11 วันที่ผ่านมา

    Limpopo fm 🔥🔥🔥
    Mzimu yakwiya

  • @ianganiza
    @ianganiza 12 วันที่ผ่านมา +1

    haibo comrade,, mwati wakhimbidwayo ndani...

    • @supa4dupa
      @supa4dupa 11 วันที่ผ่านมา

      😂😂😂😂😂

  • @natashamathala8715
    @natashamathala8715 12 วันที่ผ่านมา +1

    Lubwani a MBC monga mwa khalidwe lanu hahahaha koma nde zilijoooooo nyasiiiiiiii

  • @mussakapalamula1990
    @mussakapalamula1990 11 วันที่ผ่านมา +1

    Ku State House kwabadwa mwana dzina lake Lazarus Gwenembe 😂😂😂😂😂😂 mwana otembeleredwa ndi dzinalo.

  • @FurakGeoffrey-l5s
    @FurakGeoffrey-l5s 11 วันที่ผ่านมา

    Abusa chonde chonde zisiyeni mukunyazisa dzina lamulungu chonde abusa achakwela timakudalilan2 kumpingoku bwelani musatye ntima saulo anasithatu kukhala saulo thawing ilipo ambuye akukufunani mupitilize tchito yake slalom shalom

  • @ellahmwams831
    @ellahmwams831 12 วันที่ผ่านมา +2

    Koma abale dziko ili likupita kuti 😂😂

  • @AnnieMpenda-vx5wb
    @AnnieMpenda-vx5wb 7 วันที่ผ่านมา

    Things follow apart

  • @EmmanuelSanganiza
    @EmmanuelSanganiza 8 วันที่ผ่านมา

    Kkkkk koma Ku state kwavuta sidzikuthandiza bwino ndipo tikuona kuchedwa September 16

  • @StewartGoma
    @StewartGoma 11 วันที่ผ่านมา

    Let them do whatsoever they want no one is concerns

  • @FathimaMhlongo
    @FathimaMhlongo 8 วันที่ผ่านมา

    Bwelani pano zilipo zokumva kupweteketsa mutu,zimvere mtolo iwe wa MCP

  • @PatrishaMwale
    @PatrishaMwale 12 วันที่ผ่านมา +1

    Apa murungu afuna aonetse ukuruwake

  • @ElliottBelon
    @ElliottBelon 11 วันที่ผ่านมา

    Nyasi zanji izi ku state house zoona 😂😂😂

  • @RuthMsosa-c4r
    @RuthMsosa-c4r 12 วันที่ผ่านมา

    Hahaha nkhanga zaona,Boma ndi lomwelo MCP woyeeeeee😂

  • @VeroMaster-lo1mu
    @VeroMaster-lo1mu 11 วันที่ผ่านมา +1

    Mulungu wakwiya nawo anthuwa sure

  • @FathimaMhlongo
    @FathimaMhlongo 8 วันที่ผ่านมา

    A M.r President zamanyazi galu wachabechabe

  • @NoelSenzani-r4g
    @NoelSenzani-r4g 11 วันที่ผ่านมา +1

    Mizimu ya anthu anafa kuchikangawa mtanyiwa moto patsogolo

  • @MosesMbale
    @MosesMbale 11 วันที่ผ่านมา

    Boma ndilomweli koma likufunika kuchotsa chakwera, adzukulu ake onse ndi chipani cha MCP osawanyengerera ndipo ngati pakufunika makofi kuchita nawo basi 😅😅😅😅😅

  • @EnockLichenya
    @EnockLichenya 12 วันที่ผ่านมา +1

    😂😂😅 zithupsaaaaaa Kuti phuli!!!!!!!! Bible linati tiberekane Ngati mchenga he,,,,,,he Koma ziliko

  • @EliasLungo
    @EliasLungo 11 วันที่ผ่านมา

    Limpopo kuti moto🔥🔥🔥

  • @PeterThomas-f4p
    @PeterThomas-f4p 8 วันที่ผ่านมา

    Koma nde mayalutu muzayenda nyambwali nyambwali umakwana
    Tanyiwa

  • @patriciajangaza675
    @patriciajangaza675 9 วันที่ผ่านมา

    Kkkkkkm ndaseka Boma loyaluka ili zoona kumangodyana bwanda Ku zopusa bwanji

  • @PatrickZinenanie
    @PatrickZinenanie 11 วันที่ผ่านมา

    Eiiishi mpaka shown kampondeni chipongozi chinatha ndi chikangawa mwachita bwino mwatiziwita sitimaxiwa

  • @ulemummangisa3150
    @ulemummangisa3150 8 วันที่ผ่านมา

    Yakwiya ndi miZimu baci kumwamba kwakana 😢ufulu waesedwa ndipo walephera

  • @PatrickZinenanie
    @PatrickZinenanie 11 วันที่ผ่านมา

    Tatumizani maliseche a rudo Tembo tiwaone akuyenera kuti Ali ndi ndata chimulu

  • @FavouredgrivinChikanda
    @FavouredgrivinChikanda 10 วันที่ผ่านมา

    CHIKANGAWA party zakuvutani bas Mulungu wakwiya nanu,,Zamanyazi

  • @Musa1828-l5d
    @Musa1828-l5d 11 วันที่ผ่านมา

    Rudo amuthila mbola uku boma lazitsiru achewa onukha kuthako

  • @ThoccoChimbali-h6g
    @ThoccoChimbali-h6g 11 วันที่ผ่านมา

    Prince wadya mwa Rudo eti?🤣🤣🤣🤣🤣

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 11 วันที่ผ่านมา

    Mu boku la miyambo muli mawu akuti ngati mutsogoleri ndichisiru nduna zakeso zimakhala zisiru

  • @AlexKaunda-w7l
    @AlexKaunda-w7l 11 วันที่ผ่านมา

    Komaso vuto ndi lakuti awa anthu ochita bwino ku ndalama ..samatha kuchinda kuchinda siyilana anthu osauka mamama😂😂😂

  • @GonçalvesXavier-l3z
    @GonçalvesXavier-l3z 8 วันที่ผ่านมา

    Nkaziyu ndi hule basi 😂😂😂😂😂 wapakulitsa nanyati,,nyemba

  • @MaxonKambazithe
    @MaxonKambazithe 12 วันที่ผ่านมา +1

    Ngati nizoona eeeee zopasa manyazi and chisoni, matha

  • @ZimhungaEsther
    @ZimhungaEsther 7 วันที่ผ่านมา

    Alekeni azipwetekana

  • @PeterCHAGUNDA
    @PeterCHAGUNDA 11 วันที่ผ่านมา

    Comrade tandipaseni manamba amayi kabwirawo mwina nane ndiwapakule nyemba basi

  • @JonasMponda
    @JonasMponda 8 วันที่ผ่านมา

    Chakwera ndi nfiti anapha sidik chilima ndi anthu ochulukanso

  • @UmaliMmussa
    @UmaliMmussa 11 วันที่ผ่านมา

    Kupakura kwa khan khan

  • @FurakGeoffrey-l5s
    @FurakGeoffrey-l5s 11 วันที่ผ่านมา

    Timanena ife kugwa mmanja mwachauta ndaiminyama siizi kma abusa inu

  • @DaudBonomali
    @DaudBonomali 11 วันที่ผ่านมา

    Ndiye bambo anali mfiti chigawenga chakupha anthu kubeleka ana ndi mahule Komanso ena ufiti osamva za anthu

  • @FestonMpwepwe-zq7hk
    @FestonMpwepwe-zq7hk 8 วันที่ผ่านมา

    Komano muzichitako ka summary. Mukuchedwa kufika pa point

  • @kennedybanda
    @kennedybanda 11 วันที่ผ่านมา

    Mulungu wakwiya....... Ndipo abale muoneko Luka 4:1- - - -

  • @frankdomingo1109
    @frankdomingo1109 11 วันที่ผ่านมา

    A curse is upon that house

  • @MatiasNgambi
    @MatiasNgambi 11 วันที่ผ่านมา

    Koma azimayi amafuna chani dollar ndibwe Kwa nick mufuna chani azimayi

  • @Andrew265Kalingo
    @Andrew265Kalingo 11 วันที่ผ่านมา

    Mwatimasula antanyiwav 😂😂😂😂😂😂

  • @CharlesMphweya
    @CharlesMphweya 11 วันที่ผ่านมา

    China nchipande powomola😅😅😅😅

  • @PatrickZinenanie
    @PatrickZinenanie 11 วันที่ผ่านมา

    Ntanyiwa usazafe uzangosowa umatiziwitsa zobisika

  • @MartinNgoma-tp2jk
    @MartinNgoma-tp2jk 8 วันที่ผ่านมา

    Gibo peasorn ananena galu ndine.diye galu ndife tevotela imbwa sad news

  • @Harrychokanda
    @Harrychokanda 11 วันที่ผ่านมา

    Ntanyiwa umakwana 💪

  • @Leo-fj6gz
    @Leo-fj6gz 11 วันที่ผ่านมา

    Koma nde izi ndi nyasi ☹️🙌🏾

  • @Amina-gg5gr
    @Amina-gg5gr 11 วันที่ผ่านมา

    Kwalowa usilu ku state house

  • @RosinaPatel
    @RosinaPatel 11 วันที่ผ่านมา

    Comrade kuseka kumeneku mupha nako anthu ndi BP

  • @ReginaSeunda
    @ReginaSeunda 8 วันที่ผ่านมา

    Nthawi yatha tiyeni tipemphere kwambiri

  • @ulemummangisa3150
    @ulemummangisa3150 8 วันที่ผ่านมา

    Wakwiya ndi mfiti ha ha ha ha ena zuwawa ATI nkhani zabodza ha ha ha ha muchira koma mochedwa

  • @Biath-m4b
    @Biath-m4b 8 วันที่ผ่านมา

    Ntchito imene tinakusankhilan ndi imenei?zoti anthu akufa ndi njala simungadzwed koma muli bzy ndi izi

  • @BrownMatonyola-xi3lb
    @BrownMatonyola-xi3lb 11 วันที่ผ่านมา

    Nkhani ya beans winanso wa MCP analemba I think ndiyoona

  • @PatrickZinenanie
    @PatrickZinenanie 11 วันที่ผ่านมา

    Ndiye kaponda mgagayo nyemba ya rudo amakapakulira kuti tatiuzeni tiziwe

  • @patriciajangaza675
    @patriciajangaza675 9 วันที่ผ่านมา

    Mmmmmm zafikapotu kkkkk mmalo moyebdetsa Boma bzy kupakura bwanda

  • @ChimwemweSauka
    @ChimwemweSauka 11 วันที่ผ่านมา

    Angochindana ngati nkhuku kkkkkkkkkkkk chikangawa uyooo

  • @YounusWabullah
    @YounusWabullah 12 วันที่ผ่านมา +1

    Kwachema ndi kumalawi

  • @AhmedJali-xf3rw
    @AhmedJali-xf3rw 11 วันที่ผ่านมา

    Akuyenera nkaziyo kutero ndie kuti amuna akewo ndi ama busy vx sangafunde nayo blangert

  • @LookmanAdamu
    @LookmanAdamu 11 วันที่ผ่านมา

    Komakwachema😂😂😂😂😂😂

  • @TasiyanaChinula
    @TasiyanaChinula 11 วันที่ผ่านมา

    😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
    Watchedwa ndani?????????

  • @PhiriVictor-e9l
    @PhiriVictor-e9l 11 วันที่ผ่านมา

    Kodi amatenga banja lonse kupita Ku state house? Nde tones tachita manyazi

  • @arafatMtyala-bo8ev
    @arafatMtyala-bo8ev 12 วันที่ผ่านมา

    Basi azithilana ma batter kumyedzi yasalayi nakha atani?

  • @PeterCHAGUNDA
    @PeterCHAGUNDA 11 วันที่ผ่านมา

    Kodi mpongozi wachakwera ampakulanso nyemba, koma anali ndi zokoka

  • @JoefreyGongoni
    @JoefreyGongoni 11 วันที่ผ่านมา

    Atume azikwanje akape akamkakawo , 😅😅😅😅😅tsoka ndiiro

  • @JoseMasulan
    @JoseMasulan 12 วันที่ผ่านมา +1

    Athu apakula nyemb eeee kom abare

  • @RosinaPatel
    @RosinaPatel 11 วันที่ผ่านมา

    Koma ambuye mulungu inu mukule ife tichepe

  • @PaulMBKathumba
    @PaulMBKathumba 12 วันที่ผ่านมา +1

    Ma pictures ambwandawo ndilinawo ndiponya pompano akalimbalimba

    • @mussakapalamula1990
      @mussakapalamula1990 11 วันที่ผ่านมา

      Ponyani tione mbwanda yoitengela ku State House 😂😂😂😂

  • @IdressaMussa
    @IdressaMussa 11 วันที่ผ่านมา

    Yosavesa chisoni zachita bwino Kuti kulowe pugwepugwe aziphana okha okha

  • @ChikupizgaKajawaMkandawire
    @ChikupizgaKajawaMkandawire 11 วันที่ผ่านมา +1

    Koma ndiye muli pa ntchito yofalitsa nkhani za bodza mukatele mwaso wa chopanga post

  • @VeronicaChirwa-ct4os
    @VeronicaChirwa-ct4os 11 วันที่ผ่านมา

    Kalikonse tikamva ndipo tikawona very shame

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 11 วันที่ผ่านมา

    😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂yomweyo Chikangawa party

  • @chrispinchirwa9563
    @chrispinchirwa9563 12 วันที่ผ่านมา

    Katsakula ,Mvula ndi anzanu nkhani ndi yimeneyo ya ma bwana anu tiyenayoni

    • @VeronicaChirwa-ct4os
      @VeronicaChirwa-ct4os 11 วันที่ผ่านมา +1

      Sanganene kanthu Kasakula ndi azimzake achina mvula makape

  • @HawardKalipande
    @HawardKalipande 11 วันที่ผ่านมา

    Koma ku state house kapena ku Rest house??

  • @PaulMBKathumba
    @PaulMBKathumba 12 วันที่ผ่านมา

    Kodi ndiye kuti chipani cha MCP chazeru chimene akuchiona ndikuphana ndikupakulana basi

    • @TamikaKaponya
      @TamikaKaponya 11 วันที่ผ่านมา

      Basitu😂😂😂😂😂

  • @EmmanuelkpPraise
    @EmmanuelkpPraise 11 วันที่ผ่านมา +1

    Kasongo eeee!!!!

  • @MussaAli-h4i
    @MussaAli-h4i 12 วันที่ผ่านมา

    ❤❤❤