ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Comedy iyi ndimawonela chifukwa cha anthu awa chuma,mercy, mdyangu ndi shokoshoko
Chuma man of the moment 😂😂😂
chuma kuseka kwa ma game kumeneko😂😂😂
Chuma ndi 1 😅😅😅😅
Ma pant ndi bra mkatimo alibwanji 😂😂😂 ....Mercy❤
Well done chuma keep it up ❤❤❤❤❤ mdyangu wooyee
Mnyanyiwa muva naye kuwawa, tifane wakumana nazo
Chuma amandisangalasa koma😂😂😂😂
Koma Mercy umasemphana ndimakofi😂😂😂😂😂😂😂
Kutafulila tifane mwana wankango
Queen welcome back 😂😂😂😂 Mercy you're the best 🙏 congratulations guys 👏👏👏
bola short uyu osat za junior zijaa,,asazabweleso amene ujaa
Live
Thanks bro
Chuma is improving alot
😂😂😂😂 koma chuma 😂😂😂😂
Mercy wamaboza kwambri 😂😂😂😂
akut tadzipwekekaso bwanj 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Mercy chipongwe amangwetu 😂
Chuma dolo kanayi....👌👌
😂😂😂😂😂😂😂 Chuma umandiwaza
Mercy wakumana nazo😂
Mercy kukonda zolandira landirandira 😅
Achuma munakakhala oliza mpila....lukhwela lanulo mukuniwaza man
Koma chuma iweyo aaaa umatha
Queen tinakusowa
Mercy wakumana nazo ali dzuwa lindiwalire iweso undiwalire kkkj
Chuma ❤
Kod gys chuma ndiwachibwibwidi😢
Ayi ndiwaboboh
Koma chuma 😂😂😂😂😂😂
Mwana wa kango ndiku chimbuzi koma
Chuma ndiwamwano😅
Shokoshoko ndi dolo kwabasi
Walowa basi kuchipinda
Chuma😂😂😂
Mercy ndiwa mtopola
Kkkk chuma
Kodi chuma yo ndiwachibwibwidi kapena ndi sewero chabe?
Ndiwaboboh its just acting
Chuma ungozipasa mambama
Umatha chuma
Kkkkkkk koma chuma
Mumatha guys
Koma chumayo kkkk
Komatu lero chuma unakonzeka
Chuma amatha koma chichokele achina chipwanya pano dolo ndi chuma
Chuma kutalikitsa khani kkkk
CDM YOUR RELIABLE CAR DEALER