Very nice and colourful dance from chichiri prison.We celebrate you president Nyusi and Lazarus maccarthy chakwera as you are presiding the official opening of Malawian trade fair.Achakwera palipose mungayende timakukondani kwambiri ndinu mtsogoleri wamaso mphenya aakuru kukonzanso ziko la malawi kuti libwelere mwakale ndipo zaysmba kale kuchitika.Osusa ali mmazi.
Now it makes sense, kani ndi a kaidi eti. Nde kuwaveka uniform ya mabwana awo kuti chani. Mabwana mwawavula kaye uniform kuti a kaidi a kavinile. Koma uchitsirunso
I'm one of moz which agriculture is in Mozambique? Akunena kafarm kalipaVuanduzi , ndikaAzungu wosati Nyusi
Very nice and colourful dance from chichiri prison.We celebrate you president Nyusi and Lazarus maccarthy chakwera as you are presiding the official opening of Malawian trade fair.Achakwera palipose mungayende timakukondani kwambiri ndinu mtsogoleri wamaso mphenya aakuru kukonzanso ziko la malawi kuti libwelere mwakale ndipo zaysmba kale kuchitika.Osusa ali mmazi.
Ngati asilikali ake a 1949 tu, uniform ikuchita kukana thupi. Kaya anadya liti kaya.
Tawatulusani akaone ana ndende imaphweka muli mwana wanzako kma siziziwika m'mawa ndiwako
Aaa nawo akaidi akufuna adye nao za cikangawao
Ndye akaware akufana nda Anyusi
Koma ubale ulipati pachikwera ndiNyusi ulipatiko, fit yazuza athu kuMozambique ibwere kuno ngati zanzeru 😢
Zaziiiiii chiwongolelo chophela anthu paseu mukudya kumeneko kunkhuta et kuli njala simudziwa
Better these days timavutika mages,mafuta ndiye polankhula kumafunika kuganiza komwe mwachokera kaye
Akayidi akufuna mutuluka kikkkkk
Nice
Now it makes sense, kani ndi a kaidi eti. Nde kuwaveka uniform ya mabwana awo kuti chani. Mabwana mwawavula kaye uniform kuti a kaidi a kavinile. Koma uchitsirunso
Zazii zeni zeni
😢😢😢😢😢 chose so mukugona NDI njara amalawi😢😢😢😢
Kkkk manyasa sitizatheka basi busy basi ndi chikangawa kkk
Akuti mwatenge bwino akumalizani chikangawa akwezaso mitengo
Iye nkumasekera izi
Mbuzi zokha zokha zakuman
Ok
Osauka akati avine
Shikangawa nayeso kusatizila kuvina kkkkk😂😅😅
Rlp 😢😢😢 The white chewa
Catholic priest
You preserved our culture well 😢😢😢😢
Chodzivutitsila kuvinila anthu okuzunzani ndichani? Amvekele mwetu ngati zeni zeni mxwiiiii
Makape ndarama samalandila zooneka
Ndalamah anakonza anthu akuvutika awah....,,
Mmm
Malawi
Akayidi koma
Angowakhululukira ma inmates wa
Comment reserved kudzazionesera kuti ndife asilikali titumizeni kuja mumanena
Koma eee anthu akuwondako ku ndende uku
Awa sabwerako
Awawa zifukwa zowankhululukira mzokwana anyamata avina bwino kobasi kkkk
Kaye kunvesa chisoni
A prison nda security amphawi awa onvesa chisoni
Ngati zikukuvuta kwa mako ukuganiza kuti aliyese zikumuvuta zeru muzikhala nazo polakhura
NOSE INU MAVINALA CHAKWERA NOSE NDINU ZITSILU
Koma zikoli momwelikuyendela paliso chifukwa chomakavinila pamaso pa chakwela
Dziko lokongora koma mwaliononga agalu no makape
asilikali wiosaziwa chimene ali mmalo mongopempha ndipakamwa koma kumaziyalusa choncho zomvesa chisoni kwambili zaziiiiiiii
Za chibwana kufuna ndalama basi maluzi wa
Camera mbora
Nthawi yomweeyo ndikulamula Kuti amasuleni milandu yawo yathetsedwa, nkhothi liyime
Km guys umbawi sizindu guys kumavina motero kufuna ndalama
😂😂😂 zaugaru basi
Zobheba
Takatungeni magazi ku mozambikiko mubwezele Bushiri magazi ake mutenge ena a abale anu ife ayi mutisiye tokha.
Achokela limodzi asiyen
Koma😂😂😂 level yachina las dema
Kufuna ndalama uku koma kulikufa chakachino inu chomavinira ndichani inu
Osangothawa pamenepo bwanji
Kkkkkkkk anthuwo kuwonda kumeneko iiiii
Za ziiiii ku prisonikonso kulibe ufa
Akaidiwa aimba nyimboyi akuopa kt awaphera komko chikangawayo ndi mfiti inzakeyo
Kufuna ndalama tawonani wapolice kuwonda
Koma anthu muli ndi mphanvu zobvinira eti
😂😂😂😂Koma
😂😂😂
😂😂😂😂😂😂