BON KALINDO LERO PA 30 OCTOBER WANG’ALURA CHAKWERA PONAMIZA AMALAWI ZOKHUNZA MAFUTA

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 29 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 83

  • @FosterPhandama
    @FosterPhandama 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา +8

    The guy is so courageous and akalankhula i feel sorry for my country Malawi

  • @EliaSiska-n6r
    @EliaSiska-n6r 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา +6

    Very true Bon. Take example Britain had changed priministers several times

  • @PraiseMt-l6f
    @PraiseMt-l6f ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Amalawi axanga tixacangamuka lit kd aaaa gyx plx gyx kalindo nduyu amatisegula masoyu km ife aaaaa😢

  • @mishecksipolo7153
    @mishecksipolo7153 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา +6

    Pa private sector po ndi maganizo abwino kwambiri

  • @KendrickLuckyc
    @KendrickLuckyc 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Keep it up Mr B k

  • @AlexanderBaluti
    @AlexanderBaluti 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    More fire the DC❤❤ kukumverani big from Capetown...

  • @GiftGwaza
    @GiftGwaza ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Big up auzeni apubwawa

  • @abgi.doctor.august
    @abgi.doctor.august 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mavuto osatha amenewa Mulungu atithandize kutiolosa Nyanja yofiyirayi 2025 Chauta Mulungu wamphamvuzonse akuwamiza ndi ankhondo a Farao ndi magareta awo omwe the DC Boooon Kalindo president wa aphawi 🔥🔥🔥🔥❤❤

  • @FrankCon-j3i
    @FrankCon-j3i 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Watch from Argentina

  • @HAJIUBAYIDABLACK-q7n
    @HAJIUBAYIDABLACK-q7n 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Nkhani ndiyakuti tiyeni tipange mademo
    Bon Kalindo amayesesa kutiwunikila koma ife amalawi timagona kwambiri

  • @BlessingsZudi-mx7tj
    @BlessingsZudi-mx7tj 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา +5

  • @JafaliChiwimbi
    @JafaliChiwimbi 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Boooooon kalindo ❤❤

  • @peterthawi
    @peterthawi 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    this guy speaks zinthu zanzeru kwambili.Only if people litsened to him..

  • @AnnieChikango
    @AnnieChikango 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    😊Izo ndizoona moto kuti buuuuu

  • @AndersonDPaul
    @AndersonDPaul 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    m'Malawi muli zitsiru Kalindo paja ankanenatu kuti train ija idanyamula molasses.Koma achina boma ndilomweli munkatsutsa.Mxweew!!

  • @BlessingsChimango-e3t
    @BlessingsChimango-e3t 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kulakhura mwachindunji mwa tchutchu tchu abooni kalindo the Dc

  • @GiftNgwira-e8l
    @GiftNgwira-e8l 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Bon kalindo akunena zoonadi amalawi ife ndinapepera kwambiri maiko ena zinthu ngati zimenezi sizingachitike kumangosekerera zopusa

  • @ReginaMulipa
    @ReginaMulipa 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    😂😂😂😂ati kwinako sindipitiliza ifeso zikuti bowa zikupanga a dpp tu sukunama kalindo

  • @happyluhanga3387
    @happyluhanga3387 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kkk kumeneko ndi ma spider man azi dumpha muma building

  • @dalitson3558
    @dalitson3558 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    A opposition ndi a chisiru kwambiri makamaka a dpp ndi anthu oyaluka kwambiri ukufuna azizalila,

  • @LawrenceMataka-h1i
    @LawrenceMataka-h1i 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Munthuyu amalakhula mosabisa koma ena satsangalasidwa ndizomwe amanena DC

  • @RaphaelWinford-t7u
    @RaphaelWinford-t7u 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Be blessed Mr kalindo❤❤❤❤

  • @IsaacBauti
    @IsaacBauti 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mwana oooooopsaaaaa kwambr

  • @JosephyMangwaya-d8i
    @JosephyMangwaya-d8i 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Uyu anabwera

  • @FelixMachika
    @FelixMachika 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    It's vyendeee eeeeeee for me 😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😆😆😆😆😆😆😆😆😆😆

  • @kennedybanda
    @kennedybanda 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Being a motional speaker it doesn't mean you can become a "CEO".

  • @Stellamalimero
    @Stellamalimero 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Tipange mademo basi mwina zinthu nkusitha

  • @ShownMboma
    @ShownMboma 59 นาทีที่ผ่านมา

    Ndipo boma ilili ndi boma lotanii😢

  • @BazukaChikungaM23
    @BazukaChikungaM23 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา +4

    Mumuuze Mafia chakwera Kuti milandu ija anamanganayo Patricia kaliti ndiyochepa kwambili amange Malawi yonse chifukwa tonse timafuna titamupha kumene akuopa iyeyo kufa 😮

    • @ChisomoChigaga
      @ChisomoChigaga 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      😂😂😂😂😂

  • @phoenexkachingwe2753
    @phoenexkachingwe2753 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    .
    Bon kalindo

  • @hamiltonsolomon3756
    @hamiltonsolomon3756 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    ❤❤❤❤❤❤

  • @lindadzaoneni
    @lindadzaoneni 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Fault yeniyeni yi ya magetsi tikumatha 2 weeks, 3weeks osabwera a Escom

  • @paulbanda9638
    @paulbanda9638 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Anthu a MCP akudabwisa kwambiri, a chakwera delivery ili kuti, tulani pasi udindo a chakwera, izi sizikukuyenerani ayi,resign resign

  • @WilfredKazembe-i6q
    @WilfredKazembe-i6q 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kodi dziko limenelo president tizapha ngati mbuzi ponchosa abele mavotiwo

  • @RemitterFlik1130
    @RemitterFlik1130 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Akuti tizigula ma polo amagesi kuti akafike panyumba Pako kaya akufunika ma polo 10 ugule wekha zili ku mzuzu kuno

  • @mishecksipolo7153
    @mishecksipolo7153 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    MCP Ana feliya Ana feliya😂

  • @ElizabethsBanda
    @ElizabethsBanda 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mwana oopsa kwambiri

  • @alexandermeke6994
    @alexandermeke6994 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mafuta adzasowa tsiku lina dziko lonse lapansi kaya ndiye mudzati wabwino ndi ndani anthu a khungu inu 😅😅😅😅 mbuli zophumzila

  • @NEBRA-lm7ji
    @NEBRA-lm7ji 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ati kuonda😂

  • @ShegSamosa
    @ShegSamosa 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    🔥🔥💥💥

  • @Kenmoney-xp7tz
    @Kenmoney-xp7tz 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Gentlemen wait a minute, kodi chakwera ndi nduna zake akumayenda kuti, akumathira chani mgalimoto zawo, ma que akumakhala munsewuwa sakumawaona?

  • @BeatriceBeattie
    @BeatriceBeattie 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    BON KALINDO 30

  • @harrispheleni2205
    @harrispheleni2205 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    God papa nde wa zoona 😅😂

  • @GodfreyKamphiripiri
    @GodfreyKamphiripiri 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    ❤❤❤❤❤Fireeeeeeeeee Fireeeeeeeeee DC

  • @EmmanuelDanitsa
    @EmmanuelDanitsa 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Andale amatitoradi ndife dzitsiru

  • @lysonkaselema7321
    @lysonkaselema7321 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nyoo sopano

  • @ZikwendaAlizk
    @ZikwendaAlizk 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Vuto zmangothera mtown moo Ife akumuzi ai why

  • @MartinMajola
    @MartinMajola 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chakwela mbuzii sakuziwa kanthu chisilu chamunthu

  • @gabbymagwaya5836
    @gabbymagwaya5836 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    dpp yafikapo kugona

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Boranso kwa Igpto komkuja timadya bola tibwelere basi

  • @WonganiKatchale
    @WonganiKatchale 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Tapita ukagone paseu ngati sakuponda ndigalimoto

  • @AlexanderYovatiKhumalo
    @AlexanderYovatiKhumalo 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ukakhala kuti unali mg'gulu lotola tola, ndiye kutolako kukavuta sititha kuyamika zimene ena akuchita ayi, let's learn to contribute how we can develop our country Malawi, kungokhala onyoza nthawi zonse kunyoza pa radio basi?

    • @JosephLemani-qq1is
      @JosephLemani-qq1is 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Kuyamika anthu akufu kusowa mafuta owatengera ku chipatala kapena mukutanthauza motani

  • @chrisboyce2
    @chrisboyce2 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Kunena Zoona Mr kalindo achenjeza kokwanira ku opposition ndipo kukakhala kusamva ndi kwawo Koma a Malawi Kumudzi akufuna Boma lankhazari lichoke latikwana. (Wake up opposition)

  • @ChimzyWesley
    @ChimzyWesley 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Sukunama bon ngankhale chakwera kupita ku Blantyre anthu ochuluka akumukomdabe kaya akumukondela chifukwa chani chimene wachitila sindiziwa

    • @FrancisNyayi
      @FrancisNyayi 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Better asamankhare ndiblove yapamaso

  • @HeyGehhe
    @HeyGehhe 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mcp kwatikwana ndipo mwatitila kwambili

  • @OdettaLowrence
    @OdettaLowrence 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Osusa onse akugona ndie kya awawinitse ndi ndani

  • @smartchisoni2143
    @smartchisoni2143 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Apeze athu olemera awabelenso aaaaaaa

  • @IslamMapepa
    @IslamMapepa 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koditu pamene zafika akayakhula chakwela tizingomunvela chifukwa zilizose ndizaboza

  • @MayesoBikefa
    @MayesoBikefa 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Dc

  • @NormanKaphamtengo
    @NormanKaphamtengo 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Fadah munabwera inuyo auzeni amenewa zawavuta badi

  • @CharlesMwachande
    @CharlesMwachande 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Anthufe tikuzunzika kugwila ntchito koma phindu palibe Kwacha ikungogwa aaaa pls pls apule tiganizilen

    • @mishecksipolo7153
      @mishecksipolo7153 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

      Sadziwa chilichose cha Economy Palibe angaganize he is just a local pastor.

    • @ShamimuBisani
      @ShamimuBisani 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Exactly koma usogoleri opanda Mulungu kukhalam zikuvuta chil chonse

    • @MaureenNgoma-p7l
      @MaureenNgoma-p7l 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Pena ngati ungosiya ntchito

    • @ShamimuBisani
      @ShamimuBisani 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      @MaureenNgoma-p7l ss kusiyas ntchto sidzingaende choncho wapereka Mulungu zikhala zmwez basi

  • @InnocentBanda-ze8de
    @InnocentBanda-ze8de 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zoona Bon 🤝

  • @happyluhanga3387
    @happyluhanga3387 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ku LLs kuli ma hustlers

  • @ZikwendaAlizk
    @ZikwendaAlizk 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mmmmmmm

  • @BrianAmos-s2k
    @BrianAmos-s2k 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kodi chimdzimayi chosavuka chija chinkavinila sitima yopanda kanthu nkumati muli mafuta ija ali kuti pano?

  • @johnhaynes5286
    @johnhaynes5286 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Dc😂

  • @BazukaChikungaM23
    @BazukaChikungaM23 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Bhohn Mwana oopsa kwambili kkkkkkkkkkk

  • @JamesSingini-t4j
    @JamesSingini-t4j 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Mpaka 2030 ukupangabe ma audio akowa kkkkkkkkkkk Boma ndilomweli

    • @chilembwekanjirawaya4296
      @chilembwekanjirawaya4296 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Akulu misala muziona Malo apangila mavuto ndi atose

    • @GeorgeKholongo-ew4qc
      @GeorgeKholongo-ew4qc 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Are you not ashamed of yourself brother?

    • @kingsleymsampha2260
      @kingsleymsampha2260 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      MCP members are not suffering eeeti? Sugar, fuel etc zanu zikutheka kwambiri. Mwalemeratu ndi mcp anzathu.

    • @MosesMasina
      @MosesMasina 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      😂😂😂😂😂 ukunama Iwe

    • @chimwemwechikwawa
      @chimwemwechikwawa 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Kuwaona akuti boma ndilomweliwo mmmh ambuye alowelelepo ndithu

  • @funnynyirendafunny7888
    @funnynyirendafunny7888 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Tinganenekuti please a bambo athu ife timadalira Inu. Ndamene mmatimenyera. Nkhondo. Nde oyambisaso mademo ndinuyonanga. Poti maso anthu Ali painu . Enawa ndi athu chabe. Mantha achulukira . please help Malawi I like always you do! Please

  • @graceofgodlivingchurch.
    @graceofgodlivingchurch. 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma abale

  • @InnocentvagabondTembo
    @InnocentvagabondTembo 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    ❤❤❤❤