Wapanga bwino kuyimba ndi jetu wamva nda download chifukwa Cha feat ndi jetu osaziwa kuti iwe Fred mw muli uthenga ndukupanga follow Zowonadi mvuto ndi nyumbamu nkhani ndi nyumbamu Favorite song Zowonadi anthu amakhala masiku atatu osapanga even ka 4times kamakwana km eeh Fred mw
I was in min bus this other day,, nyimbo iyiyi ndiyomwe inayamba kuimba I was just smiling 😁..the story telling chemistry between you two was just wow... this is good song Man Fred
Overall, there is a big difference with your previous songs.. Hard working pays brother .However ,your far to reach there but wth dedication and perseverance you can reach there our young star.... Take note that there are ups and downs in a every industry , therefore focus on your hustle and move . Proud of you 🎉
Who else is here after watching Chakwaza and Wakalamba wafuna
Meee😂❤
😂😂😂anthu inu bwanji ko
Me 😂😂
ine pano 🤣
Me😂😂😂
Ndasiya ka comment ka kuti anthu akapanga like zibwelanso kuzaonela❤
Nyimbo zoyenera ma awards and proper recognitions ndizimenezi. Legit🤜🤛🔥💯
Ndipo sukumana
I support
Who's here for Jetu too
Ine
Ine
❤❤❤❤❤❤@@user-xp2wg1to5w
I am
From chakwaza tikubwera kuno😂
🎉🎉🎉🎉 I love this song thank you guys
Jetu wabwera kudzakhala uyu ,💞💞💞💞
Chikangiti ine ndi JETUUU umangodziwiratu
Nice tune
Nice song Jetu go ahead osabwelera mbuyo ayi ndi anthu asanjewa chifukwa aliyese ali ndichimwemwe kuona lunso limene wabweletsa kwaife amalawi ambuye akudalise Jetu
when you come here in 2063 the time that Malawi will get rich just know i was here on 2024 watching this video 📸
😂😂😂😂when Malawi get rich 🙌
Wapanga bwino kuyimba ndi jetu wamva nda download chifukwa Cha feat ndi jetu osaziwa kuti iwe Fred mw muli uthenga ndukupanga follow
Zowonadi mvuto ndi nyumbamu nkhani ndi nyumbamu
Favorite song
Zowonadi anthu amakhala masiku atatu osapanga even ka 4times kamakwana km eeh
Fred mw
I will be watching daily to hit Million views
Am with you good people ❤
Tiyeni ifike 1m 🔥🔥uyu fred amatha kuimba
Akulu apa ndiye mwafika basi , ndipo inu ndi oyimba basi.
Team Fred Mw let's gather here to witness this hit song, a song we love to watch daily❤
Nurse
Voice ya Fred on point
Ine ndindan kuti nsayamikile,,,,,,mwapha guys,,mnyumbamu Ili mwala❤
queen of amapiano jetu.. 3stop🎉😂
Ase Fred osafooka ndi gogo sten jatu mwagwilana bho pangan crew #FJ
Fred umakwana upgraded big up bho
Nyimboyi yaphedwa za ntchito ❤
am here for Jetu .....gives vibe♥
Jetu lovers let's gather here ❤
Jetu 0:30
Milonde Makuwa Music,,, New Style 😂😂😂😂iyiyi Fred nde wachapa❤❤❤❤❤
This is becoming my favourite artist now Fred umatha
Big time
@Fred mw am your top fan nyimbo iliyonse imakhala bomba kwaine koma tsiku lina mzakumana nawe dzedi ndikukugwira chanza👐👐👐
composure yabwino, big up, video directing and production zili super
Moo fire modern pack balaka
amazing one I like the song and the information
Fred uli pa bill yanga jetu musiye zako azipuma 👌💓💯💯💯💯
Umakwa Fred Mw, Milonde Makuwa music to the world 🔥
Madolo ovinira mmatha heavy kkkkk
Nice beat
Beat yabho
Kunena zoona ana ama 2000 Mungobwela nditi ma bomba toposa ndi tsikhu wanu keep it Guys moto kuti buu
Good song and voice fred.....mulungu akupatse luso latsogolo
I like it ❤
Milonde music to the world 🔥🔥🔥
Road to 1 million 😊😊
Pure Malawian Sounds 🔥🔥🔥🔥❤️
AJetu mwafikapo.
❤🎉😊
Eee very nice song❤❤❤ akuti ngani ndinyumbamu🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Jetu to the world...
That's exhausting
Iwe ndi Dolo Fred mw fire 🔥 umatha iweyo 🔥
Kod kaniii 😃😃😃
Very nice guyz more 🔥
Beautiful and nice hits
😂😂😂😂😂😂 eeeeh koma sound yaphulitsidwa iyii. Big up to producer and jetu
Jetu ndidolo ofcourse koma man mukutha
Jetu to the world
Anthu amakhala ooo masiku atatu
Koma inu pasiku mukufuna katatu😅😅🏃🏃🏃
Zoopya pasiku katatu
The song is great... Wapha ayise.
Fred ndiwe katakwe ace🔥🔥
Jetu am your fan for life. I want to meet and celebrate yiur COURAGEOUS attempt at Fame iwedi ndi JETU!!!!
😅😅😅😅😅 😂😂😂 I don't no why am happy kkkkk but this song jetu Ali nyumbamo
Mwana wakwathu keep it up milonde more
Give thanks to whom u like much like Fred mw
Kani mzokoma chonchi❤❤❤❤😂unabwera iweyo gogo Jetu
Big up magogo jutu from Uganda
Afunamu khare ndimapasa atatu
Jetu to the world ❤🔥🔥🔥🔥
Tiyeni road to 1 million
Njila mumakwana basi apaa ndakuwonani zabwino zose🎉
Hahaha Mukandiwona ndikutha Nkhani ndi Mnyumbamu one of my favorite song ❤❤❤❤
I like this song sooo much
I love my country Malawi I miss home
Fred uli bho kwambiri ❤
Who's chilling the song
Eeeeh koma chinyimbo ichi chokha nde chasinjidwa yooooo❤
Mbambande njira umatha 🔥🔥🔥🔥🎧📻🎥
I love this song even l can I can repeat it again
Very grateful song ❤❤❤❤
Let's hit million this song
Ma shasha akumana ❣️
This is a nice song.
Am here for Jetu
Je
2:06 tu
I love this song,seriously🎉🎉🎉🎉our very own Milonde boy
I was in min bus this other day,, nyimbo iyiyi ndiyomwe inayamba kuimba I was just smiling 😁..the story telling chemistry between you two was just wow... this is good song Man Fred
Jetu woyeee
This song is so fine! Production plus concept
Nice song kweni muyikeso zasono zila akulu a kaima ndine kam'dumukire ❤❤❤
Anjila atokwanajetu iwoo
Umatha ase
i once underrated this track didn't know it was tgis dope🤣🤣🤣
Superb 🔥🔥🔥
I love the energy in this song
My guy come on ,Jetu heroiness Pitilizan
Nice song🎉
Hit!!
Getu more fire
🎉 from Zambia
ipase moto
Ife ndye sinatikwanebe, tumaonera daily katatu ngat treatment 😅😅😅😅
Continue working hard my brother.. 🔥 Milonde-Makuwa-Music 🎶 to the world
Wapeza top fan apapa Fred🔥🔥🔥🔥
I love this song with powerful meaning
Akuti unandiputa wekha kwathu 🤣🤣🤣🤣 nanenso ndiyamba uhuletu ,zili bwino mayi ft fred keep it up🫡🫡
WAITHA MFANA MORE FIRE
Eeeeee u kill it
I like your music Fred from Luviri, Mzimba❤
Overall, there is a big difference with your previous songs.. Hard working pays brother .However ,your far to reach there but wth dedication and perseverance you can reach there our young star.... Take note that there are ups and downs in a every industry , therefore focus on your hustle and move . Proud of you 🎉
😊😊0000
HR wachilembatu
❤❤❤❤❤
I love the song
On repeat
Jetu sakukhuta greatfull 👏👏
Khani ndi nyumbamu mwaipha sure❤
Nice one Guys. Keep it up.....MALAWI MUSIC AT ITS BEST