NTHAWI YA UMBULI KUIMBIRA MFITI MMANJA SH.ABOU SUFIAN KHATWEEB DAWOOD

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 27 ส.ค. 2024

ความคิดเห็น • 18

  • @MariamJaffali
    @MariamJaffali หลายเดือนก่อน

    Naam sheikh ma shaa Allah ndipo anthu amaopa kukhala kuqibula Allah awakhululukire zofooka zawo

  • @UseniMailosi
    @UseniMailosi หลายเดือนก่อน

    Ameen inshaah Allah

  • @Musa-cz1nm
    @Musa-cz1nm หลายเดือนก่อน

    Ma shaallah ma shaallah ma shaallah

  • @user-gk6bf7xe9g
    @user-gk6bf7xe9g หลายเดือนก่อน

    ❤❤❤❤

  • @user-lf5qw7mk3h
    @user-lf5qw7mk3h หลายเดือนก่อน

    Km this kind of lecturing sometimes zumandikhuxa bwanj
    Mmalo moti muzapephelera amzanu chikhululuko bas muli busy achibekete
    Panopat kumalawik kuli zambil zoti kalel sizimachitikai inuo ophuziran muthawi yanu samasephan pakhan ya eid km lero ikangofik mumangotukwanizana apa
    Be humble muziwapephera amzanu chikhululuk jaman kozan zomwe zilipoz pano a a jaman

  • @user-rl5zq1qr4d
    @user-rl5zq1qr4d หลายเดือนก่อน

    Ulaliki wabwino ndithu koma kuchula mbiri ya munthu omwalira kuti anali wa shirik its very unfortunate mukanangokhonza zimene inu munaziwona kuti ndizolakwika in directily not directily nkutheka ena analowa chisalam kuchokera kuzimene iye amapangazo inde tiwalemekeze ndi amene anasunga deen inu ozindikiranu musanabwere choncho tiyeni tiwapemphere chikhululuko osati kuwapepusa MAY ALLAH SHOWERS US ALL WITH BLESSINGS FOR BEING MUSLIMS

  • @IsmaelBilal-lh1pi
    @IsmaelBilal-lh1pi หลายเดือนก่อน

    Tiyeni tiwapangile ma duwah mwina kutheka amaizichita mu umbuli. Allah awakululukire chifukwa anatisungira Deen

  • @edwardedo6798
    @edwardedo6798 15 วันที่ผ่านมา

    Sheikh uyu zikufunika kupita nae kuchipata for mental issue , Allah azikukhululukirani pa umbuli wanu, Ameen

    • @Qassimcedrick
      @Qassimcedrick  9 วันที่ผ่านมา

      @@edwardedo6798 deen siiyendera mmene mukuganizira imeneyo nde misala yofunika ku mental yo ndipo ukanakhala umamuopa allah mberera izi ukanasisunga muubongo mwakomo
      Allah akuongole

  • @JohnAsendi
    @JohnAsendi หลายเดือนก่อน +1

    Koma amwene ndi makusati mukulankhulana kwanu kwaonesa kuti wabwera kuzalimbana ndi anthu omwe anaphunzira kale kodi tizinena kuti muli PA chiwongoko ndiinu choti muziwe ndi chakuti dini ndi ntchito sizingagwilizane mupite Kwame e mukuwanyozawo samalandila ndalama kutha kwamwezi pomwe Ena inu mumalandila ndiye kumati uza zabwino zomwe akuchita ungokhala zonse ndizolakwika alibe zabwino zomwe akuchita

    • @Qassimcedrick
      @Qassimcedrick  หลายเดือนก่อน

      Sheikh kodi mitiuza mu Quran pomwe aletsa kulandira ndalama ukagwira ntchito ya Deen pakati panu ndi ife pali Quran ndi MA hadith atumiki basi palibe zokangana

    • @JohnAsendi
      @JohnAsendi หลายเดือนก่อน

      @@Qassimcedrick mumalandila ndiinu ingo ndiuzani lembalo mu qraan

    • @JohnAsendi
      @JohnAsendi หลายเดือนก่อน

      @@Qassimcedrick mumalandila ndiinu ingo ndi uza lemba mu quraan

  • @MoneyTiririMgwagwa
    @MoneyTiririMgwagwa หลายเดือนก่อน

    Munakakamba zoonadi koma osatchula muthu ngat inu mwazindikila muchoonadi munakalalikila pazomwe inu mwazindikila ndi mene mwaphuzilila

  • @AdamYas-ec9oc
    @AdamYas-ec9oc หลายเดือนก่อน

    Uyu sadayange mafuso amene ana fusidwa komaso tingopemba allah kuti abwelere kudarassa chifukwa hukum ya deen mutu mwawu mulibe