When a hyena wants to eat it's own young ones, it first accuses them of smelling like goats! But this guy is not smelling like Bakili Muluzi TV. This guy is genius ndiye mungofuna kumupezera zifukwa zomuphera. Musavuka ndi ufiti wanuyo. Sakani wina oti mumutafune uyuyu ndakaniza!
Mmm wa BAKILI MULUZI TV simunthu wamba ndipo mawu ake enieni si amene amaveka aja ayi.Ndipo musataye nthawi nkumaganiza ngati angamalankhule mawu ofanana apa audio ndi mau apa live? Aaa mwanama.
When a hyena wants to eat it's own young ones, it first accuses them of smelling like goats! But this guy is not smelling like Bakili Muluzi TV. This guy is genius ndiye mungofuna kumupezera zifukwa zomuphera. Musavuka ndi ufiti wanuyo. Sakani wina oti mumutafune uyuyu ndakaniza!
Sakufanana olo pang'ono,mwayambapo amalawi kiti mumuphetse munthu
Ai Mau sakufanana kutalitali
Mantha chabetu awa
A visionary man
Mufuna amagwidwe?
Kulakwa
Amalawi anzanga, iyayi. Denis Mahata mau ake akumvekeratu kuti uyu ndi wa ku Ntcheu. Bakili Muluzi TV guy, ndi wa ku Phalombe.
Ma voice ndi osiyana akanyimbi inu amene mukufuna mwazi wa munthu basi
Akusiyana kwambiri anthunu musamakolezele Moto Kwa munthu
Sangakugwireni Boss wambwita ameneye😂😂
Olo mpang'Ono pomwe bwana
Bakili muluzi azakafa akwanu uzakhaleso busy chonchi
musamuphetu mwanayu. ali ndi sogolo uyu. mwayambatu
Sizikufanana
Ameneyo mwambwitaso, musafafanize ndiameneyo ayi😂😂😂😂
Uyu yekha tilekereni
Bakili muluzi tv sangayime dala pa mibawa tv akusiwa kuti akhufunika ndi boma
Ine ndili nayo speech ya bakili muluz yalive😊 ndipo mmh sakufanana mau antaa
Watumidwa uyu.
Mmmm inu sizikufanana konse ,,musamupwetekese mwana
Wa bakili muluzi TV uja osazamuphwekesa 😂😂😂
Kupepera mupangaku "Mawu sakufanana or pang'ono"
Mwauponda
Mahata akukamba za IMF nanga inu????😂😂😂😂 malawi okomera tonse??😢😢😢😢😢😭😭😭😭
Osaika mwana wa eni ake pachiophyezo chonde
Sizikugwilizana ma voice awa
Akunama uyu
Apa akufuna atiphele mahata wathu mulungu akuteteze mahata
Big up brother man!!
Osaopa!! Bakili Muluzi tv simunthu wamba. Ndikatundu. CIA
Inuso mukufuna musokoneze zinthu musiyeni mpulumutsi wathu
Mmm wa BAKILI MULUZI TV simunthu wamba ndipo mawu ake enieni si amene amaveka aja ayi.Ndipo musataye nthawi nkumaganiza ngati angamalankhule mawu ofanana apa audio ndi mau apa live? Aaa mwanama.
Koma uyu ngat angayime amalawi nose amene mumavota ngat muli ndizelu oti malawi asithe please zavoten ameneyi ndithu malawi azasitha?
Zikusiyana sakufananayi mawuwa
Aaaaa palibe zofanana mau apa iya
Ayi simenewo ndipo sakufanana kutali tali
Voice yosiana kwambili
Mukufuna muphetse munthuyu mcp ndiyakuphatu
Mwayamba potu
Chomwe timafuna a malawi sitimachiziwa ndithu
Mmmm mwayambapotu,zikugwilizana bwanji?musiyeni Munthu😢
Ayi sizikufana
I think he is the one
Sakufanana ai
Wapezeka
Alibe mavuto
Kape iwe
Kutalitali sakufanana mpang'ono pomwe.
Pezani zina zochita
Apatu nde mwaphonya
Musamuphese tu future president wathu
Musaphese zanu😂
Amene muku panga izi ndinu asatana mukufuna kuphesa munthu wosalakwa ndinu agalu
Ayi sakifanana olo
Sameneyu
Aaaah Mahata's voice is totally different ndi Bakili Muluzi TV....
Sakufanana 😮😮
Pangani zochita dzina km
Not marching
Sakufana olo pang'ong'ono, ukungofuna umuphetse muthu osalakwa
Kkkkkkkk muuzeni
Sakufanana mwakhuta mgaiwa eti
Palibe chikufanana, mwina nzeru zokha.
Ai alibe shofafa apa
Sakufanana
Mmmmh a Malawi chonde musaphe munthu
Mukufuna kumupwetekesa muthuyu eti ma voice sakufanana mukunama
Mukatero mukufuna mumumange 😂😂😂 panyapake chakwerayo
Amene anayambitsa zofananitsa mauwo cholinga chake iyeyo ndi chani makamaka?
Cholinga mumuphe muziti ndiwa bakili mulizi zitsiru mukusowa okupha tsopano anthu akutulukila chakwera kumtumbo kwako konukha pagulu
Olo pang'ono sizikufana
Sakufanana, koma Malawi anatembeleledwa
Voice siyikufanana ai, ilo ndi bodza adzangomupha Mahata a MCP.
Mukungofuna kuphetsa munthu osalakwa , wa Bakili Muluzi TV simunthu wakuda ngati iyeyo mix he is not staying in Malawi right now
Mwasowa zofanizila et palibe kufanana apa
Sakufana mukufuna mummnge munthu osalakwa bwanji
Nanga bakili mulizi tv amalakwa chani anthunu mwasowa zochita mmbomamo
Iwe oipa
Mukungofuna kumupwetejetsa mwana wanzanu
Ndipo olo sizikugwirizana olo pang'ono
Akupanga izi ndani asiyeni achinyamata wa ndi anthu
MUNTHU UYU AKUFANANA MAU ND BAKILI MULUZ TV
Sakufanana
They aren't the same
Zikufanana patii
M mmmmmmmm. 😂😂😂😂😂😂😂 mwadeya palibe kufanana kulikonse
Msiyen Mahata ndi sogolo lanthu
Kkkkk muphweteketse nzanu sinchoncho!
Mmmmmm ayi sakufanana konse
Uuum sizikufanana antaaa
Iiiii musiyeni mwanayu aphure dzikoli musamusowetse inu achina ujeni
Mungofuna pomuphela akutumani azungu kut mupezele ma plan omuphela akwapasa theng'eneng'e azungu end mawu anayakhula kale yekha kut ukazindikila umaphedwa mukufuna kumupha masanasana 4:11
Mwangosowa ntchito pezan ina agalu inu
Kkkkk
Ine bakili ndikumuziwa Si uyuyu
😂😂😂😂😂
Mawu akumveka kuti Denis ndi Nchewa pomwe pakili muluzi TV amayankhula Bobo musamusakile zifukwa anthuwa akusiyana kwambili mawu
Bakili muluzi tv mau ake ndi computerized pamene mahata is original voice so musampweteke mahata plz ndi mmoz yekhayo yemwe tasala naye
😂😂😂😂😂 komatu anthu ayi mumaganiza mochedwa kwambili
Sizikufanana olo pang'ono
Suzugwilizana mahata ndi BTV
Kungofanana anthuwa ndi ophunzila kwambiri ndipo ndi ozisata
Mwanama gyz
FAR FARRRRRR FROM IT
Mumuphesa mwana wa eniake
Zoonad mukufuna kumuphesa munthuyi mau sakufanana
Ndpo kutaltali sizikufana
Mau sakufanana or pang'ono