MCP AING'ALURA NDIPO SANACHIOPE KUTI NDI CHIPANI CHOLAMULA |

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 8 ก.ย. 2024

ความคิดเห็น • 17

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus หลายเดือนก่อน

    Guys....let's be proud with our courts...they are independent😅...salute

  • @matiasphungwako
    @matiasphungwako หลายเดือนก่อน +1

    awatu anazolowera chipani chimodzi za demokalase akuchita kukakamizidwa

  • @JeanBanda-zy6wu
    @JeanBanda-zy6wu หลายเดือนก่อน

    A mcp ichi ndi chifukwa chimene anamuphela chilima mukuyalukatu

  • @WitnessKamoto-bf4pu
    @WitnessKamoto-bf4pu หลายเดือนก่อน +1

    Anthu inu mungofuna kuba bas mulibe malingaliro othandiza

  • @DensyHone
    @DensyHone หลายเดือนก่อน

    Achina chikangawa tikumana 2025. Bas😂😂

  • @SueWahna
    @SueWahna หลายเดือนก่อน +1

    Kom Kuli zithu 😮

  • @Martha-m6e
    @Martha-m6e หลายเดือนก่อน

    MCP chilichonse chowavuta basi.mitu sikungwira.

  • @Lazarus-qo1sl
    @Lazarus-qo1sl หลายเดือนก่อน

    Ziliko mawa pansewu

  • @StevenAjusugama
    @StevenAjusugama หลายเดือนก่อน +2

    Kodi Inu mumankhala kuthi pa mavuto adziko kappena idzi pali wakupasani ndalama

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 หลายเดือนก่อน

    Malamulo akuswa kale chakwera. Iyeyo panopa akuseva kale third term ku MCP.

  • @nessiemfunie
    @nessiemfunie หลายเดือนก่อน

    A mr chikangawa tizaonana mu 2025

  • @JamesIbrah-jp5zr
    @JamesIbrah-jp5zr หลายเดือนก่อน

    Muli busy kulingosola izi za mcp pomwe Mavuto alitho mzikomuno

    • @JosephMaduka-i9s
      @JosephMaduka-i9s หลายเดือนก่อน

      Ndie ufuna mcp isadzudzulidwe

  • @josephkafupa
    @josephkafupa หลายเดือนก่อน

    Aliyense atenge nao mbari baxi

  • @pauljosephmakaula6835
    @pauljosephmakaula6835 หลายเดือนก่อน

    Time wasters

  • @MwaiChikaonda
    @MwaiChikaonda หลายเดือนก่อน

    Aliyense amulole kutenga nawo ngati Mmalawi