Malawi tikapusa tipitilira kuvutikabe President wanji wosapanga regret Mukamakavotera MCP kawiri zanu izo, Kodi bwanji sakutiuza percentage ya zomwe atipangila out of Promises????????? Time to vote for president based on region will no longer help us ....... Ine ndiye ayi Chakwera, Chilima akagwere ndi anthu onama zedi Komanso what we should know this is political battle, sangabwere poyera nkumatiuza kuti eya 2025 tizaluza that's why even those small small parties are promising that they will win come 2025. Uku nkulira kwanga ndatha ine wanu amalawi anzanga
Iwe ngodwala bwanji..... don't include kamuzu mukhani yako...he is the only guy that did good for Malawians ukafunse agogo ako...osati mbuzi zako Za dpp zo😂😂😂😂😂4get guys dpp will never come back muulamuliro
Ovota ndi anthufe kulankhula uku its like ma vote muli nawo mnyumba mwanu ,sitinaiwale ñjala ,kukwera kwa zinthu kubvuta kwa chakudya ,kukwera kwa chimanga mpaka 60 000 zomwe sizinachitikepo mu History ya Malawi ,ziwani kuti anthu ada nanu kukhosi kuyambira ku primary school mpaka ku collage ,ma civil servants ndi Ena onse ,aphunzitsi ndi ena onse ,kufikira munthu wakumuzi sakufunanso kumva dzina la tonse alliance and MCP tionana September 2025 ndipamene mudzaziwe kuti Amalawi anatopa nanu
Aaaaa ine mmene ndanvera ma speech awo kumeneku nduona kuti uyu unali mnsonkhano wa ndale wa mcp not mwambo okumbukila Kamuzu asamatinamizepo apa olo aja akuti achimwendo aja kulakhula kwanji kumenekuja ati akutchula Peter Munthalika ati sangatenge boma aaaaa zugwirizana chani ndi mwambo okumbukila malemu Kamuzu??? Eeeee koma guys ku Malawi mmm ayi zikomo
Makamaka chisilamAchakwera amadana nacho limodzi nd anthu akulilongwe,bas zingo khala zamutundu,tsopano msilam ndye ali paliponse,azichemwali anu onse anakwatiwapo ndi msilamu tili ndi anatu mwa kabudulamu, kuphiri la njudz,kwamasumba,ndye nkhondoyo ife tingo ona kucheedwa,kt tikuonetsen
Am a boy who belong to both two sides Lomwe and Chemwa because my dad from kasungu in Santhe and mom in thyolo Thomas .u like it or not .am a solution.
Wina aliyense amakondedwa ndi Mulungu. Ndiye osamanyoza mtsogoleri wathu. Ngati inu si a malawi samukani koma ine sindikuona chomwe walakwa pa zomwe wayankhulazi. Tisiye kusankhana mitundu ndipo uthenga uwu wa achakwela ndiowona ndinso omanga dziko.
Ine sindipanga nawo za ndale koma kunena zoona chakwela udindo alinawo nde wa church osakhala dziko. Ndipo akapitilila kukakamila mulungu akwiila dziko lamalawi chifuwa cha utsogoleli wanu. Inuyo mulibe chisomo cha utsogoleli wa ndale
Nothing you can say about election i will see kungowina iweyo uyembekezele nkhondo chifukwa sitizalola za manyi zakho mwaiweyo mulibe utsogoleri uzaona after all
Amene sakufuna chakwela Ngati ine . Come here.akunamiza anthu uyu
Mr pule mukuzinamiza zoti mupitiliza chaka chamawa mukunama kwambiri pa ground sipalichoncho baba muzakhumudwa kwambiri
😂😂😂😂😂😂😂
Koma na Dpp yokha zoti ingazalowensooo mmmm tikunamizanaaa
DPP boma chaka chamawa
DPP boma chaka chamawa
Dpp boma bas
Mbuziiiii Yakumwa Madzi Ometela Ndevu Galuuuuuuuuu Chikwanteleeeeee
😂😂😂😂 really😂
Only God knows the 2025 leader... May God intervene
Yes God knows what will happen tomorrow....I dreamt that Peter will be president of MALAWI
Mlungu atimenyela nkhondo bwana ngati mkudalira kuba ziwani ichi ku mwamba kuli mlungu
Malawi tikapusa tipitilira kuvutikabe President wanji wosapanga regret
Mukamakavotera MCP kawiri zanu izo, Kodi bwanji sakutiuza percentage ya zomwe atipangila out of Promises????????? Time to vote for president based on region will no longer help us ....... Ine ndiye ayi Chakwera, Chilima akagwere ndi anthu onama zedi
Komanso what we should know this is political battle, sangabwere poyera nkumatiuza kuti eya 2025 tizaluza that's why even those small small parties are promising that they will win come 2025.
Uku nkulira kwanga ndatha ine wanu amalawi anzanga
Ndipo you have said the truth anthu awawa mukut a MCP waaa God will give them a severe punishment
Boma la mcp limatinamiza kwambiri kamuzu palibe chomwe adachita mdziko la Malawi chimene tikudziwa ndikuba ndalama za Malawi makolo athu amakagona kutchire chifukwa kamuzu amafuna misonkho ndiye kuti chiyani lero
Ulibe manyazi komaso mwna umakomoka ma University, zipatara kkkkk Malawi tayani ndale
Zoti ma University or zipatalazo amangozinsintha mayina simukuziwa? Even Kamuzu stadium ija, bunda college kungonena zochepa anamanga ndi asamunda.
Tiziti Bingu uja adali ozungulira mutu akamati Kamuzu adapanga zinthu zambiri??
Iwe ngodwala bwanji..... don't include kamuzu mukhani yako...he is the only guy that did good for Malawians ukafunse agogo ako...osati mbuzi zako Za dpp zo😂😂😂😂😂4get guys dpp will never come back muulamuliro
K@@wisdom20mkango49
Chakwera ndi mbuzi yamuthu inu mwapanga chani mu 4 yrs ??? Ai lekani kunamiza amalawi
Kodi chifukwa chani amalawi timangopusisidwa apapa wbwera uyu ku blanttyre mukuombela manja ngati akupanga zinthu why!?
Vuto dzikoli mbuli zachuluka
Ndalama
Ndiye muziwe kuti zokonda za inuyo c zokonda za awooo.....ngati inuyo mumakonda Dpp musayembekeze kuti awo akondanso Dpp ayiiii .....ngati mmaombera mmanja Peter ...panopa ena akuombera mmanja chakwera.....ngati mwagona ndi njara pa khomo panu musayembekezere kuti kwa Neba nakonso agona ndi njara .....umo ndi momwe moyo umakharira ......simungawapange anthu onse kuti akonde Dpp ......koma wanzeru amakwera Timu imene ikusogora pa ground nthawi zambiri yoluza .........
Koma guys kod ku state house ku amasuta chamba eti nanga boza limeneli bwanji
Akuzinamiza amenewo
MCP ikuzinamiza Peter is already chosen to be president of MALAWI
😂😂😂😂
Apm my vote
Your president is another Bola Tinubu of Malawi, sorry he has pasted his sell by date, u can even ask Namalomba.
Chabwino
Koma mmene akumuyang'anira Anthu ake amene wabwera nawo kuchoka ku lilongwekowo akuwawona chifukwa akumuysuysatu zoti akhoza kuwinaso
Inu nde ayi ndithu za ziiii!!
Stadium sinadzadze or half nde simungadabwe?
Kodi mukulota kapena kubwebweta? Nayensotu Kamuzu wanuyo ankatelo
Ovota ndi anthufe kulankhula uku its like ma vote muli nawo mnyumba mwanu ,sitinaiwale ñjala ,kukwera kwa zinthu kubvuta kwa chakudya ,kukwera kwa chimanga mpaka 60 000 zomwe sizinachitikepo mu History ya Malawi ,ziwani kuti anthu ada nanu kukhosi kuyambira ku primary school mpaka ku collage ,ma civil servants ndi Ena onse ,aphunzitsi ndi ena onse ,kufikira munthu wakumuzi sakufunanso kumva dzina la tonse alliance and MCP tionana September 2025 ndipamene mudzaziwe kuti Amalawi anatopa nanu
Achakwela musamathe mawu kumbukilani kt ovota ndife Malawi amene tikukumana nd mazuto muulamulilo wanuwu
Eti eti
Apule kuyesera kubayibitsa anthu ku Kamuzu Stadium, eti anthu kumangoyang'ana osabwezera kkkkkk! Koma m'Malawi anakonza ndithu.
Sanje akulu ndinu afiti eti mumadya matewera kwanu eti demeti or pitala angafike gulu limeneli mbuzi
Chakwela my vote kulibe opikisana naye uyo ndi owina basi
I support, chakwera is going to win❤
Zaziiiiiiii president osadziwa chimene akuyankhula
Kodi Ali ku kapeni 😂 ayiwala zomwe apitira mbuzi za anthu
Aaaaa ine mmene ndanvera ma speech awo kumeneku nduona kuti uyu unali mnsonkhano wa ndale wa mcp not mwambo okumbukila Kamuzu asamatinamizepo apa olo aja akuti achimwendo aja kulakhula kwanji kumenekuja ati akutchula Peter Munthalika ati sangatenge boma aaaaa zugwirizana chani ndi mwambo okumbukila malemu Kamuzu??? Eeeee koma guys ku Malawi mmm ayi zikomo
Cant you memorize the script and present as you not just reading...
Kodi Mnyamata woganiza bhooo basi amuchita tame????
Makamaka chisilamAchakwera amadana nacho limodzi nd anthu akulilongwe,bas zingo khala zamutundu,tsopano msilam ndye ali paliponse,azichemwali anu onse anakwatiwapo ndi msilamu tili ndi anatu mwa kabudulamu, kuphiri la njudz,kwamasumba,ndye nkhondoyo ife tingo ona kucheedwa,kt tikuonetsen
Am a boy who belong to both two sides Lomwe and Chemwa because my dad from kasungu in Santhe and mom in thyolo Thomas .u like it or not .am a solution.
Anthu akeso ndiwomwewa anali zulo ku DPP
Izitu sizinali za chipani
Kkkkkkkk zoonadi big
Koma ukudalira chani galu wamunthu iwe zakudya ukunenazo waziwona kuti ukuwona ngati Anthu angakwanise kugula fertilizer pa ntengo was 108,000 kwacha? mbava, mbala, chiphe munthu oyipa ngati njala
mwayambilatu kulila pack and go
Kom amalawi nd anthu onvesa chison kwambil 😂😂😂..anthu tikuvutika km still kuiimbila mmanja zinthu zopanda sogolo..
Osaiwala kut amalawi Fe Tu tangofuma kumudyela munthu kma awa antha
Eti makamaka azimayi chosecho usiku azikagona nd njala
Sindikuziwa kut anthufe timaganiza Chan,, mpaka kululutira garu ija koma😢
😂🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣😂😂😂😂 mawu ake ndi onvetsa chisoni kwambiri 🤣 apule 🙌🙌🙌🙌
Ndiye anachoseranji ma office ku Blantyre kuunjika ku Lilongwe? Waziwa liti kuti Blantyre ndi Malawinso? Wadabwa chani Lazalo, Nyanja Nyanja ua Zana?
Apm my vote 😂😂
God knows what comes next
Ana amahule inu mulibe ulemu kufatsa kutenga phone yako kumalembaa zotukwana zeru mulibe.
Mau mwawava kuti sachoka ndipo siichokadi
Yanga vote M C P
Paja peter anayamba kunzikonzera chifukwa chokalamba
Inunso ndi achisilu nso bwanji
Kamuzu sadamange stedium iyi ndi sir geofry cobby
Muthu ukamati nkazi uyu ndimukwatila umakhapa kuti madongosolo onse ofunikira manja wapanga Apure akukunaminzani pls konzani nyumba yanu yokapumila
Kwasonkhana zipani 9😂😂😂😂 Peter dzana lija aliyekha koma kunali chiguluuuuuuu❤❤❤❤❤
Kufuna osafuna iwe utuluka galu
Ndikufuna passport yanga mkulu zonamizana apa ai. Zinazo mukumanga kumalawi komwekuno?
Kkkkkkkkkk
Kodi mfana oganiza booo aphulitsa liti mabomba 😂😂😂
Anatha
Wojambula akupanga manyanzi akuonesa modumpha dumpha akuonesa Malo momwe muli anthu basi
Chakwela ndimbava amalawi akuti Zaka zitatu ndizazingono Kuti iye walemela ndi family yake pazaka zitatu.koma iñu amalawi masauka taganizani mozama amalawi zongoopela Manji tingozipasa mavuto tonkha
God can not do that much TO M.C.P again
Awaso koma akodzera bulangete sanayanike. Ayiwala kuti usiku ukubweraso
Komatu peter amayakhula osaonera palipose kumayakhuka zomveka.sono inu bwanj kukikose kumachita kuwerenga.amakupepelesanitu omwe amakulemberaniwo kaya simumaziwa
Mr President mukulankhula zakumapwa........ mwamva
Kkkkkk
😂😂😂pakamwa chilichonse ndi chotheka
Mulungu amamva mapemphelo ana akee
achakwela mudziyangula momalidza udindowo mwiniwake a kubwela bola yiweyo walawa nawo koma adzanu achilima eeee wauponda
Komasotu big wa samata kusanga or wa kazi awowatu kungo kala ngati nyapapitu
Chakwera akudziwa kuti sadzawina , koma angodzilimbitsa mtima hiya.
Amalawi zanga asazakunamizeni kamuzu sanapange China chilinchonse kumalawi zonse zimene akunene chakwela zaboza anamanga ndi atsamunda... Kamuzu amangodziwa kutsitha zithu maina zithu zoti sanamange iyeyo.
Ndizona tizivutikabe bas muziba ndalama muzilemba job aku banja lanu
Peter wa muthalika 2025 boma ❤
Pyoo9
Gadama
Matenje
Chiwanga
Sangala
Just to mention a few.
Sir Joffrey Cody planned Malawi
😭😭😭
The list is endless😭😭😭
He wasn't a malawian
Koma chakwera mwati ali ndi nzeru? Ndikuona ngati chomwe akuyankhula sakuchidziwa.
Abusa a Chakwera mukuzinamiza simungawine, nthawi yatha mumanga masukulu nthawi yanji..zikoli mwaliononga
apm.my vote baba palibe ncanzelu ndikunva.mwainu.sakho.hvy
Ukunama ase ng'ooo udye ndalamazo komaliza wopusa iwe
Mr Pule mwapanga chani choyanjanisa kuposa Kuba ndi katangale nzikomu njala thoo muzikomu
Apm he is the kind 👑
Chonchi DPP ingawine ndi vizungu zake izi
Kkk eti eti anyway Peter is already chosen for the president
Anthu amenewa adyesedwa chani kusekelele Chakwela mbuzi yamunthu anthu akuzunzika zinthu zakwela chakudya kulibe uchokapo pamenepo aise
Nyali unayasa zowunika ukamaba anthu wokumba mopanda manyazi chisiluyiwe
Awa akuzanimiza asiyeni aledzera mwina ku status house kuli ambuye mtengeni mowa obalalitsa uja
Wina aliyense amakondedwa ndi Mulungu. Ndiye osamanyoza mtsogoleri wathu. Ngati inu si a malawi samukani koma ine sindikuona chomwe walakwa pa zomwe wayankhulazi. Tisiye kusankhana mitundu ndipo uthenga uwu wa achakwela ndiowona ndinso omanga dziko.
Ine sindipanga nawo za ndale koma kunena zoona chakwela udindo alinawo nde wa church osakhala dziko. Ndipo akapitilila kukakamila mulungu akwiila dziko lamalawi chifuwa cha utsogoleli wanu. Inuyo mulibe chisomo cha utsogoleli wa ndale
,😂😂😂😂ambuye atiyendele...awawa nde ahyi...mmmmhhh
kape chilichonse choyankhula kulemba basi kupanda nzeru galuu
Amakulembera ndani Kodi zomwe ukuyankhulazo chidzete iwe? Nose mbuzi
Nonse otsutsa tikuti nonse yiwalani mwamva kodi ?
Time is over enough is enough mbamva izi
Ngati tili ovota ndiiyeyo
Sadzadzitha
Kuyankhula momveka koma kusamala amalawi mukulephela inu a tonse alliance
Iweyo Chakwera ukuona Ngati Dziko la Malawi Ndi lako,kamuzu,chinali chimunthu choipa ngati Iweyo nkhope Ngati mvuwu pa Bumbu pa azibale Ako panopa Malawi aliyense wakalipa msili kariyo una bereka ñdiwe?gondwa mphawi mbava okuba ndalama za amalawi ULI Ndi nyàli iwee basop
Nothing you can say about election i will see kungowina iweyo uyembekezele nkhondo chifukwa sitizalola za manyi zakho mwaiweyo mulibe utsogoleri uzaona after all
Ukunama
@@user-gz3mi5bl1f let,s see after election because is not so far
Nkhondo😂😂😂😂😂😂 akulodza eti....umaidziwa nkhondo iwe
@@wisdom20mkango49 let's see
Ndiye iye wapanga chan ,zongoone likasa
❤❤❤. My vote m.c.p ennanu mwazolowerakudya zopempha
Dziko likamayenda bwino anthu amasangalala koma izizi ndiye ai mbuzi
Chakwera iweyo ukalamulira 2025 nyumba ya nkazako ndi ana ako pamtumbo pamako wamva
Ine zandale simbali yanga,chakwera samaopa Mlengi mwachidule mkulu wasanaki.
Azivotera yekha ndi nduna zakezo ...olo atabera zizitheka....
Ndipo ine utu sindimamva mfundo zzomwe amayankhula Koma mukuti olo ulaliki wake unali omveka bwino bwino?
zitsiru ndi zomwe zimanama zatelemu chakwera ndi. garu bass
😂😢😢
Tangoziwona nduna zakozo kukwiyako akuziwa kuti kwatha basi next year kusowa wakumuzi basi
Kkkkkk
Zaziiiii Chakwera ndi chitsiru kwambiri
ukupita wayambakulila galu ukupita u like or not u are going time is up
Çhakwela is good on preaching he thinking that Malawians are in church
Galuyii achoka bas afune asafune
This man is mede
Chakwera boma ,salute
Mulungu atithandize munthu uyu woipa mtima
Ukunama ndiweyo ife sitikupeleka mpata opeleka boma. Timalize zabwino zomwe tinayambazi
Mbuzi galu ngati iwe munthu umagwila ku chipiku ndiye ungakwanitse kukhala president panyo pako ukagwele
God will work it out next year,,,, we are tired with you Mr,, kungotiphaka phara pano....
Aliyetse angozifutsa kuti kwanthu kuno ndi chitukuko chiti chomwe alupanga ameneyu
Chenjezo kwa Malawi azanga gwileni mtima vote ndi chaka chamawa, uku mwapita uku mwapita punsi anagwa chagwada
Chakwera ndiwe mbuzi yamano pasi
kodi afiti kumalawi kuno tilibee,, akanangolozako nyaniyu iyaa😜
Chimwendo pemphero lakolo mulungu waanthu sangayankhe ndiponso upresidernt wa chakwera chaka chamawa ukutha mukulamulira kunyini kwamanu