May God bless His Word through you moderator and may He also plant a heart of philanthropy and patriotism in all political,traditional religious, and legal authorities in Malawi to be once again a Godfearing nation. Amen
A malawi sindimakumvetsani koma zowona after all what MCp has done to you in 3 weeks ago mwayiwala kale, kukuyitanani ku msinkhano inu nkupita,, mumati mukamvako chani chatsopano,,a oposition you guys are sleeping to much 😮h munayenela kukana osapezeka nawo pa chikondwelerochi,a MCP akukondelera their successful mission of killing chilima and the other 9, nchifukwa chake lero ali wokondwa,a malawi ndinu anthu osawona,how can you be invited for prayes to pray for the lives lost in chikangawa by the same man who orchestrated their death😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢 Malawians are you nomal ⁉️⁉️⁉️⁉️⁉️
Amene akunyoza Chakwera tsoka Kwa iye.uli ndi tsoka iwe onyoza munthu osalakwa, ngati ndi ulesi wakowo ongofuna kulandira go to page House khalamba yanu ikakupasani za ulele. Agalu inu
No message at all,this is not gospel ,for have "only and good things in God ,he is good all the time and he is cosistent,this pastor is ignorant that Job was doing all that in ignorance, hence this is jxt a motivational talk not gospel
Amen munthu wa Mulungu achakwera ndi nduna zanu a chimwemdo kunkuyu zikhale ng'omayo mukaka zisakhale ndwiii ziziva mawu a Mulungu ndizimene zikupangisa Malawi kukhala wawumphawi ndalama akuziononga basi.
😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😮😅😊
Munthu wamulungu wayankhula, wakumva amve zomwe Mulungu akuyankhula. ❤❤❤
Powerful words. We don't need to curse our nation due to painful situations. God will heal our nation
This man is one of men sent by God to deliver ❤
Amen, very powerful message. God bless you, God bless Malawi.
Munthu wankulu....powerful massage Glory to Jesus🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌
ABUSA alalikira osati zomwe ayankhula ndipo ndi phunziro kwa tonse osati a President okha
Tiyeni tisiye zonse mmanja mwa Mulungu popeza Iyeyo adziwa zonse bwino koposa mmene tidziwira❤❤❤
Mwayamba bwino zedi mbale. Anthu tonse tikanamaganiza choncho tikabakhala nidziko lantendere
For the first time seeing a preacher without recognizing POLITICIANS 😂😂
Abale ndi alongo timaseva zithu zopanda pake mmafoni athu. Zichotsenimo zoipazo komatu sevani uthengawu waphamvu muziwubwereza×10 kuposa zinazo. Tidzapeza mpumulo woyankhidwa kwa Yehova tonsefe tikawutsatira ndi kuwupempherera uthengawu patokha patokha
Powerful massage amen
Powerful message God bless you pastor ❤
Koma azanga mbusa uyu mulungu amupatse moyo wautali
Strong massage this is a lesson to the politicians who pushed a Malaysian people who's dying with hunger poverty
Chakwela yekha ndamene akutikhomelela Malawi siziko losauka chakwela must go
1q
@@ElizaMagombo very low
This eas beautiful and powerful sermon, great 👍💯
Mawu uphudzitsa ndipo achilimbikitso tingavutike motani titsataye chinkhulupiro yehovah ndiye zotse zanthu👏👏👏👏
Zoona m bale mulungu ndiye yanko tisanyozane pamene takumana nimavuto
Indeed powerful preaching God bless you
Powerful message ❤God bless Malawi
Great preaching
Rev Yasinami Gamma,Mwatiphuzitsa Ambuye akudalitseni kwambiri,
Great message Pastor.......God bless you
Ayi zkm man of god thank for good msg ❤❤❤
Amen i love this man of God 🇿🇲🇿🇲
Wat a wonderful preaching
Amene ali ndi khutu la uzimu uthengawu wawuva koma amene ali ndikhutu koma osamava, ndiwo ma comment ambiri tikuwawonawa. Amen pastor
Powerful message man of GOd
Ulaliki mbambande yobu mwayenkha munali kulimba mtima ndkukhala nacho chikhulupiriro chozama amen
Powerful Preaching
Y.G is the greatest Reverend of all time
Wonderful preaching
Powerful message ❤❤❤amen and amen
🤣😂 God bless you Gama
Koma anthu amalalika
Chonde amalawi tisatembelele dziko lathu chonde mau akulu ochokela mkamwa mwa abusa yasini gama amen
Big up brother man!!
Powerful message ❤❤❤❤❤😊
Ndipo zobvuta Zambiri zikubwela sakunama
Osayelekeza kuwapha awa ,taneneratu
I knew my rev: never go wrong.🇿🇲
Awa nde anadalitsika ndinthu
Nkazi wopusa Ngati Mayi gotani hara
Ayasin ndi mbambandetu ndi weniweni
Amen and Amen !!!!! Mau omveka bwino kwabasi
Great great great apstor of the year
Powerful massage
Amen amen kuying'alula abusa
True facts in life, ndaukonda uthengawu
Kuyakhula mopanda matha respect abusa a Gama
Amen paste!!!!
Powerful message
Hallelujah!🎉🎉🎉🎉🎉
Shehe uja amatinamiza koma uyu,
Amen man of God
Eeeeeee ulaliki ogwila mtima
May God bless His Word through you moderator and may He also plant a heart of philanthropy and patriotism in all political,traditional religious, and legal authorities in Malawi to be once again a Godfearing nation. Amen
malawi wathu ndipamene takhalapo. Amen abusa
Amen so powerful
Happy 60th independence Malawi and Long live.❤
Akulu mwati happy chani kkkkk kumalawi kulibe za happy mganize bwino
Eeee zako zili.pabwino Pali malawipa nkumati happy kakaka
60th independence and ufulu.
kumalawi Kuno kulibe akazi opusa
Ameen Abusa
Uthenga wabwino koma amaopako pangono a kambiri munthawi ngati iyi anaungalura uthenga .😂😂 a pule osawafunanso kkk.
My reverend
Amen amen
Wuthenga wabwino ambuye akudakitseni.
Man of God
Amene akukondwera ndi utsogoleri wa Mr Chikangawa ndiye kuti Mutu wake suyenda bwino
Amen
Ayasini inu ndi munthu wa mulungu ndipo ndinu mlangizi
M'busa ameneyu ndi wandale, ananyozapo zipani zina ndikuyamikila mcp,
Kutumikila mulungu mwachindinje, pamalawi panga pano palibwanj?🎉 Hellooooooo
Amalawi bvuto ulesi ndichikwa chake mtsoleli aliyese akakhala paudindo timati ndioipa akachoka wabwino kodi zooona atsogoleli onse. alamulilandziko linowa angakhale oipa ?
U might not mean what you want to say
Ayasini inu zitigairani mau amulungu anthu munawasitha
Chakwera akuzinyoza yekha aise😂😂 and inuyo mukugwira ntchito yanji if I may ask😂😂😂
Abusa a ku 49 ku nvama ccap church fumbi gheeto
Mwangozi
Malawi is not poor country
Koma Uyudi anadzonzedwa zedi
Muzeni zoona aleke kupha anthu
Amen ❤❤
Amen 🙏 🙏 🙏
Amen and Amen
Amen!
Khaniyotu ndiyona
Amen 🙏
Amen Amen
Kugunda kugwesa
Abusa ndye alalika kut amva tikunena kut zikoli timuchokeramo zikhale
Koma abusa Bible munalimvesadi ambuye akudaliseni
Chinyora
Abusa aku 25?
Nde mwati ABUSA aku 25 eti???😂😂😂😂😂😂😂
No the guy knows
A malawi sindimakumvetsani koma zowona after all what MCp has done to you in 3 weeks ago mwayiwala kale, kukuyitanani ku msinkhano inu nkupita,, mumati mukamvako chani chatsopano,,a oposition you guys are sleeping to much 😮h munayenela kukana osapezeka nawo pa chikondwelerochi,a MCP akukondelera their successful mission of killing chilima and the other 9, nchifukwa chake lero ali wokondwa,a malawi ndinu anthu osawona,how can you be invited for prayes to pray for the lives lost in chikangawa by the same man who orchestrated their death😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢 Malawians are you nomal ⁉️⁉️⁉️⁉️⁉️
Ndipo inu😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
Zosayenda
Koma azungu akumva?
Aimbileni phone muwafuse
Amene akunyoza Chakwera tsoka Kwa iye.uli ndi tsoka iwe onyoza munthu osalakwa, ngati ndi ulesi wakowo ongofuna kulandira go to page House khalamba yanu ikakupasani za ulele. Agalu inu
Iwe ndikape kwambiri
Nkazi opusa ngati mayi Yolamu, Monica Chakwera, Gotani Hara,
Tikamangosintha sintha ma president dzikoli lidzingosaukabe
Mwala oyendayenda siyanga ndele,
Zomati kusankha uyu,kenako kubwelela mbuyo,
Sizingathandize kulibwino kumusiya yemwe alipo ndikumapemohela kuti Mulungu asinthe dziko lathu,
Olo atabwelaso wina tidzati bolaso Achakwela omwe aja
Tiyeni timusiile Mulungu adzitisankhila ma president
Osati mumzelu zathu
Ai
Chakwera urichetengat urikuva koma ndiwe fiti yamafiti
Mulibvumbulotso mu ulaliki uwu,tiyeni timvetsere bwino ndi khutu la uzimu.Ambuye apitilize kukugwiritsani ntchito abusa.
No message at all,this is not gospel ,for have "only and good things in God ,he is good all the time and he is cosistent,this pastor is ignorant that Job was doing all that in ignorance, hence this is jxt a motivational talk not gospel
Uwu ndi ulaliki osati zomwe ayankhula look at you anthu okokomeza zaziii koma he's from 49 not 25 a fake journalist