Fees yakwera Inu muzasitsa ndalama muzazitenga kutino palibe Cha nzeru chimene mungapange munaba kale ndalama mukufuna muzabeso mlungu si James kuteleko ndalama munaba zija zinatha Mukhalira zomwezo mukamayakhula mwa ukali kupanda kugwa ndege kaya mukanatha kumayakhula chani pamisokhano zitateni zandege anthu ataziwa chimene chinagwesa ndege ndiye imeneyo ndi null and avoid mupeze ina basi
Dziko ra malawi rina panga big mistake. But tiyeni tizinena zoona zokha zokha game ndi dpp. Mcp yationesa zokudya kuri dzuwa abare kunjaku paribeso nbusa amene angati ndabwera kuzasintha zinthu anzathuwa atukwanisa cauta komano game ndi dpp cikuni cacikuru cimasunga motodi nzoona
Powerful speech jomo💪🏻💪🏻💪🏻chisale palibenso💥💥💥tchayani kampeni anyamata💪🏻💪🏻💪🏻💪🏻💪🏻💪🏻💪🏻APM my vote💪🏻💙💙💙💙💙💙
❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Chisale the machine with the hard talk 🔥🔥🔥🔥
Watching from Johannesburg in south Africa but from machinga we support you here no doubts about that
MCP and DPP leaders must reconcile and bring peace in Malawi
Apm my vote ♥️♥️♥️♥️
Hon chisale mukukwana ndiye utsogoleri amayankhulidwa ndiwosafuna nkhondo ai ndiwomtendire Ambuye akudalitseni Amalawi nose
Fees yakwera Inu muzasitsa ndalama muzazitenga kutino palibe Cha nzeru chimene mungapange munaba kale ndalama mukufuna muzabeso mlungu si James kuteleko ndalama munaba zija zinatha
Mukhalira zomwezo mukamayakhula mwa ukali kupanda kugwa ndege kaya mukanatha kumayakhula chani pamisokhano zitateni zandege anthu ataziwa chimene chinagwesa ndege ndiye imeneyo ndi null and avoid mupeze ina basi
Aaaaaah fees yakwera km
Jomo The Machine
💙💙💙💙
ADPP muzipitaso kumupoto kupangisa misonkhano, chifukwa zisilu za MCP zikunamiza anthu.
Jomo.more fire
Powerful
Addp munduvesese kwambili ineyo khumbo langa ndikufuna kuzafotela Peter 1 chakudya kwamalawi guy chachiwiri mcp azalandidwe chiphatso chachipani ndi chipani chakhaza kwambili
Chisale is a powerful board guard
Anatuma APM bwanji okha alibe nzeru kuti apange sonkhano nthawi yawo
APM my vote
Piston yake pa mbalipo soldier upcoming Trawore wachi Malawi Norman chisale.
ineyo sindikonda chipani chilichose koma na uyu nomani chisale ndi selemani eeee amenewa andipangisa kulowa Dpp jomo osaopa ino ndi thawi yachinyamata
Sangayerekeze kupita amenewo
Onyoza zinyozani koma ine DPP my vote.
Jomo ndiwozindikila chisale akuteteza dziko amalawi chifukwa mbava zaonjeza dziko akulamulila ndi chimwendo osati chakwera
Bwana cisare ineo ndimanyadananu kwambiri
Jomo sanamwepo mowa chibadwire ine ndimboni
Inenso ndi mboni nkumudziwa bho bho
Dpp ndiyomwe ikutukwana maphulisa
I wishi nditakumana ndi chisale
I think ur doing it for dpp not for Malawians. No more second chance for madala
zoona zake adad salakwa
Zimenyeleni ufulu coz ndim'mene mumadyera .
We are cool with our lilongwe misewu ikukupwetekani 😂
Ines nzalorela kufera pompo. Bola ili latikwana
Akunama amcp tizawathanyera a mcp tatopa nanu
Dpp 2025 oyeeeeee........Chikangawa watikwana munthu oononga chitsilu cha munthu.
mukuwona,ngati,misonkhano,yanzanuso,sikukukhala,mukunama,,mwachepa,dpp,yatha,
Unaledzera ndiwe,osati jomo
Muuze kapeyo
Malawi pano tilibe utsogoleri wanzeru chimene amaziwa khaza,kuba ,kupha mpaka kugulitsa lake
Ofuna mupiteso ku lilongwe
Mcp ndiya kupha ,kuba,kupanga zanyansi palibe chanzeru chomwe ikupanga mcp ntchito kugulisa mapiri,komanso nyanja mungandilozere zomwe mcp wachita dziko lamalawi? Mwapanga chani osamangoyimbila mfiti mmanja ayi
Nthawi ya dpp tinkadya katatu pasiku panopa anthu tikudya paweek kamodzi ndiye wina uziti Chakwera alamulira mpaka 2030 ufiti chani? Anthunu a mcp Inu muziziwa kuti ukakwera pansana panjovu usamati pansi palibe mame
Nthawi zina ukakhala kuti sukudziwa sudziwa
Agogo woyeeeee😂
Jomooo more fired😂😂😂😂
😂😂😂😂😂😂😂😂
kd,kung,alula,ndi,kulankhula,,ndizosiyana,kapena,mumatsata,kulankhula,kkophyeka,timadabwa,nanu,
Kodi dziko lifuna kuti munthu azikhara bwanji?
M'talika angakhale ndi maganizo otuma anthu zolankhura? Ku DPP kungakhale munthu odyetsedwa ndi munthu monga zimachitila Zipani zina? Ndabvomeleza kuti Peter amawanjenjemeletsa.
Mowa akamwa alindinyala akufuna kupha anthu ndi mowa wawo
dpp,inati,kunpoto,sikungatuluke,mtsogoleli,wadziko,kulimbuli,zokhazokha,ndiye,achihana,musatitukwanitse,timakukondani,
A DPP tiyeninazoni koma kunyozana ayo
Muziziyang'ana Kaye....nkuyang'ana anthu mumafuna kuti akutsogoleli. Mbili ya munthu simasewela pa ndale. Ndiku Malawi kokha kumene mumasekelela zopusa....
Chikangawa wanya😂😂😂
boma,ndilomweli,otsutsa,ayi
ife,kunpoto,anatitukwana,apita,kt,ndife,mbuli,km,mupange,zosangalatsa,ntunduwanu,achihana,awa,siwomachezanawo,,alomwe,si,anhtu,
km,chihana,wa,afodi,musapange,misitek,kuyenda,ndi,dpp,mukhaula,mufuse,atupele,muluzi,ndiye,achihana,mukapusa,akugwilitsani,ntchito,zotsatila,inuyo,mukhazikika,
😂😂😂Zoonadi amfuse chilima kuti mcp nchani😂😂😂😂
@@SamKaposa-i5c😂😂😂😂😂😂😂🎉😂
Dziko ra malawi rina panga big mistake. But tiyeni tizinena zoona zokha zokha game ndi dpp. Mcp yationesa zokudya kuri dzuwa abare kunjaku paribeso nbusa amene angati ndabwera kuzasintha zinthu anzathuwa atukwanisa cauta komano game ndi dpp cikuni cacikuru cimasunga motodi nzoona
😂😂😂😂 chikangawa achoke🎉
Ma kape Ali konko ndichifukwa chake mukulora nkhalamba zilamule pamene anyamata mulinkonko.
Kape ndi amene anapha anthu 9 ija
Iweyo ukuimila chipani chanji??
Chisare mbamva. Akufuna azabetso mu boma kkkkkkk wanya naye tiona Ngati uzalowerowetso
Anakubela chani ,bachedwani muzafa amphawi lnuuuu
@MocambiqueMocambique pafuka usi Pali chani???
Pati biii Pali chani??? Ngati ukhulupilila mawu awa uziwa kkkkkkk 👍👍
achakwela,kutchaya,kugwetsa,sitikusintha,olamula,ndiwomwewo,otsutsa,ndiwomwewo,paka,2030,,wooooooooo,ishiiiiiiii
pagolo,la,mcp,simugoletsa,,
Munthu akayankhura musamathamangire kunena kut waledzera
Wakuwuzandani kut ndamene anatuma
iiiih pajatu Ma title akuno ku youtube amabwela motero, sabwela moyesa ayi. Koma zikomo powonela
Tsanatume kma akuona zimene zikutchitika
Chimimba choncho nde mungayankhule zazelu chakwela sakuchoka boma mpaka 2030
Mukungozinyenga ndi chala
DPP never again in Malawi mark my words, agalu inu mimba ngati mtsuko Jomo kkk
😂😂😂😂 Koma iweee
Nthawi yanu yatha, pack up your things, pompano mukupita
Zitsiru izi
nzake, wachimimbayo,akukhala,ngati,m,busa,inu,a,dpp,ndiekuti,anthu,awawa,apambana,wina,aliyese,ku,dpp,,nangasimukudiwa,kt,chisale,ndi,mbava,
km,zoti,chisale,anati,atengela,malamulo,m,manja,mwake,mwaiwala,,iye,malamulo,akut,samawaopa,kusonyeza,,kt,munthuyu,m,wakuba,ndinthu
Za zii basi kung'alula koma anzanu akulamula mpaka kale inuyo mukhalila xomwezo zonyoza ndipo ku oposition uko mukhalisakotu
kd,anthu,inu,mumamukondelanji,chisale,munthuyu,m,wakuba,mukukhalangati,simukudziwa,bwanji,amaba ,pita,muthalika,,osadziwa,lelo,mukufuna,azikabaso,nanga,apa,mwatolako,chiyani,
Dpp ndiyomwe ikutukwana maphulisa