Ukulu Wanu

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 25 ม.ค. 2025

ความคิดเห็น • 9

  • @memorymussa5610
    @memorymussa5610 2 ปีที่แล้ว

    You never disappoint ..kudos for the wonderful song🎵

  • @ChitaniSaineti
    @ChitaniSaineti ปีที่แล้ว

    I love this song ❤

  • @andyjoabe3816
    @andyjoabe3816 ปีที่แล้ว

    Amazing song

  • @epic2158
    @epic2158 2 ปีที่แล้ว

    I love this song, its a powerful Thanksgiving song

  • @ididimussa
    @ididimussa 9 หลายเดือนก่อน

    Nice song

  • @andyjoabe3816
    @andyjoabe3816 2 ปีที่แล้ว

    Amazing thanksgiving song

  • @dorothymatewere4352
    @dorothymatewere4352 2 ปีที่แล้ว

    May you please share the lyrics please 🙏

    • @chancellorcollegecatholica9067
      @chancellorcollegecatholica9067  2 ปีที่แล้ว

      Nthawi iliyonse ndaona,
      Zonse munalenga pa dziko;
      Ukulu wanu inu Mulungu,
      Uwoneka okha.
      Kuzigwiritsa bwino ntchito,
      Ndithudi zonse ndi zabwino;
      Ukulu wanu inu Mulungu,
      Uwoneka wokha.
      Chorus
      Ndikuthokozeni motani? (Tenor: Ndipo)
      Mulingo wake ndi wotani? (Tenor: Poti)
      Chikondi chanu n'chosefukira, Sindingachilipire!
      2. Ndikaganizira mavuto,
      Onse amene andiphonya;
      Ukulu wanu inu Mulungu,
      Uwoneka wokha.
      Munandilera pa umwana,
      Mundisamala nditakula;
      Ukulu wanu inu Mulungu,
      Uwoneka wokha.

    • @dorothymatewere4352
      @dorothymatewere4352 2 ปีที่แล้ว

      Thank you