Komatu anthuwa adatenga Boma chifukwa cha ma bodza Namalomba you were very correct, This so called Tonse Alliance Government have absolutely failed, things are very worse.
A Wonder kukweza funso pamwamba pa funso lizake, what kind of an interviewer is that? Let them finish answering your first questions first from their answers. You could come up with other questions. Then chabwino ngati ili debate, make it clear so tisamaone ngati ndi azibambo amisala kupanga phokoso
Akukuyu vomerezan kut mwainu utsogoreli mulibe,mchifukwa ena akamakuunikirani malo mot mupeze mzeru mukulimbana naye vomerezan mwayinu ndi mafeliya anaferiya
Katangale ndendiwina aliyense atakhale pampando azapangabe zonamizana apa ai koma kungosiyana mmene analili mmbuyomu ndipanopa akusiyaniranapo ddp zinali two bad
What's the aim of this horrible interview if interviewees are being interrupted by the host. If you want credible information from them, let them finish answering your questions. Otherwise, don't brag about being a professional journalist if you are failing to put to work what you were taught.
Komatu anthuwa adatenga Boma chifukwa cha ma bodza Namalomba you were very correct, This so called Tonse Alliance Government have absolutely failed, things are very worse.
Kunkuyu nzeru alibe
A Wonder kukweza funso pamwamba pa funso lizake, what kind of an interviewer is that? Let them finish answering your first questions first from their answers. You could come up with other questions. Then chabwino ngati ili debate, make it clear so tisamaone ngati ndi azibambo amisala kupanga phokoso
Ifeso ndi a dpp komano wathuyu akana sankha wina uyuso ntola nkhaniyu wakwera boma
Namalomba number one ❤
Koma Namalomba zakuvutani Coz enafe zose zimene akukufusani timaziziwa kale ndipo ndizoona mumazilepheradi. Nkukuyu No one
Zeru ulibe
More 🔥 🔥 🔥 🔥 hot current ❤❤❤ you guys 👏👏👏👏
Unami welewo.
Kkkkkk Kunkuyu wati umalalikira kwina kwake have I got you wrong? 😅😅😅😅,,, koma ukhuluku umenewu mumalalika? ,, koma Mulungu tikusewera naye koopsyaaa.
Tizingodikila chiweluzo bas koma dzikoli lakanika achuluka anthu okuda ndimtima womwe😢😢😢😢😢😢😢😢
Namalomba ndi amuna
Lost opportunity due to bad interviewing. Wander is not a good listener, kwakke ndikukangana.
Guys kodi mkudziwa Ttv banja la kamuzu lili ndi shares yayikulu.?
Ttv yili ndi blood ya MCP.
Wonder ndi anamalomba kuti akhale limodzi tsiku lonse atha kupandana sure
Mukanamuuza inu a kunkuyu munamupha witika mwaiwala kale kodi
th-cam.com/video/o0g35X9MOE0/w-d-xo.htmlfeature=shared
😂😂😂😂😂😂
Kunkuyu ndiodekha wangokhala oipa kom ndiodekha i love him
Bola DPP
Hot current mwiniwake (amene amaipanga handle bwino ndi b.banda
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk koma ya hot curent iyi😂😂😂
Wonder mwadya bans
Akunkuyu moyowanu timawudziwa mudziwopa mulungu moyo ngt mwalabsi
Azipanga hot current Chunga uja
Anamalomba yankhan chilungamo inu 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Kodi anamalombawa amaganiza kuti zonse za dpp zinali bwino? Ndine oyikonda dpp koma ngati zinthu zimalakwika ndipofunika kuvomeleza, ndipo mukavomeleza tilimba tima kuti zinthuuzasitha.
Moses kuyakha zosephana munthu oyipa iwe witika alipakhomo kukudikira
Kukuyu ndi busa? Mm
Ndevu zamwayi akukondela kufusa mafusa
Wandra ndi Dolo alibe mbali kunkuyu zamvuta
This sounds really hot ndithu 😂😂😂😂
Akukuyu vomerezan kut mwainu utsogoreli mulibe,mchifukwa ena akamakuunikirani malo mot mupeze mzeru mukulimbana naye vomerezan mwayinu ndi mafeliya anaferiya
Kunkuyu usanamize anthu Inu munatenga BOMA NDI ma bodza
A kunkuyu kuchenjera kmnko 😂😂😂
I wish Brian was the host here... wonder talks kwambirinso penapake
Wanda ndinu chisiru kwambiri futso ropusa ngati akupasa ndalama machende anko
Kukuyu ndi satana ameneyo anatuthawisa ku malawiko
Katangale ndendiwina aliyense atakhale pampando azapangabe zonamizana apa ai koma kungosiyana mmene analili mmbuyomu ndipanopa akusiyaniranapo ddp zinali two bad
Koma yakudya katatu ija sanafotokozepotu
Mufuse nkukuyuyo kuti blackbox ilikuti mumati ilipo ija
Akumaneso anthuwa bwana Wonder 😅
Mr wander iwe ndi wa mcp mukukodela mafunso
Mr.Wonder you talk too much with one sided motion
Mr ndevu zamwai lero mwabweretsa program yofunikira kwambiri anthuwa atithandize pankhani imeneyi
Dpp find munthu wina aziku yankhulirani anthu osewa asaza bwelerenso
Program iyi siyapan et? Nakha aziti azawo asazaphe iwowa sanaphe
Wonder athu awa adzamenyana I think mudziitana modzi modzi,idzabadwa ndithu.
Ndikamuwona uyo ndimakumbukira munthu amagwira ku coca cola anapezeka atamwalira mugalimoto .
Witika
Namalomba ndiokuphya mtima saziwa kudekha
Wonder ndiwe chitsiru ukumubakira wamagazi manjayo nde munyatu chaka chake Chino kwasala masiku osati miyeziso mukhaula nonse
Ndimadikila 😂
Iwe ukafuse chocho? Adause ake at? Iwe kukuyu gahena akudira ndi chikangawayo anthu onuka mwanzi inu,mwanziwoso wakupengetsa
Komtu iyi wander uwatumizile akunkuyu iyiyo
Nose ndinu dzitsiru opusa agaru achabe chabe
Osamuuza kumkuyu kut nawoso asazatume munthu kukawombera munthu osalakwa chifukwa chazibeezi
MCP mwalephera ndinu nkhumba mmatope
Imagunika brian banda iyii awaa kufuss zikuvuta
Mcp yawonjeza pofuna kudulisa katundu
What's the aim of this horrible interview if interviewees are being interrupted by the host. If you want credible information from them, let them finish answering your questions. Otherwise, don't brag about being a professional journalist if you are failing to put to work what you were taught.
Aaaaa Malawi adaola kuyambira 2020 Pano munthu Thumba lachimanga mpaka K70 000 zaziiii
Anthu aboza osewa
Kwakwera boma koma B Banda bola
Namalomba waopa kuuza kunkuyu za Allan Witika
Mcp o% kkkķkkk woyamba kumangidwa nkukuyu 17September
Awawa a MCP anayankhura kuti azasintha zinthu akazalowa m'boma ndiye angosiya ku lankhula za mbuyo za katangale wa dpp apange zokhoza zinthu
Ankukuyu nzeru zoyendetsera boma mulibemo
Mcp Ali good pakulakhula koma tiyeni tichite 0
Kodi abweletsa akuluwo black box paja anati ili pamalo abwino
This guy on the middle is MCP cadet
Komano nthawi ya DPP zinthu sizi mandula a mcp za wonjeza kwambili
Mung'alure mr missing blakbox yooo
Mr wander kodi kunja anaku tenganiku kodi mwayambaso kukwera mbali imodzi timayi dalilatu Times chifukwa ikusiyana ndi zbs chenjerani mukalowa ndale ingakhale ngati zbs momwe inathera muja
Akulu akulu zowona mukuti mcp mulibe katangale kuposa dpp zowona zimenezo mukudziwa kuti kafukufuku watuluka kuti wolemera malawi yose yino mu 2025 ndi presdent chakwera ali ndi $300million dollars ndalama azitenga kuti a nalibe kalikose pano azitenga kuti sikatangaleyo
This is rubbish you can't bring a solution out of this un well prepared exclusive
Mr wander mukubalalika kkkk kom i like u mafunso ena mukubalalika
good Wanda. 😅😅😅😅😅
Ndiye mcp ndi nzelu zanu mwapanga chan panopa poti mwati inu ndiye muli ndi nzelu
program iyi ikanabeba akanapanga panopa kunkuyu sangamake ai akanagwa nd chikangawa
ine ndinalephera ku kch olo timankhwala ta mkhutu teniteni kunalibe wa ku pharmacy anandiuzilatu kuti pitani mukagule ku pharmacy.
Namalomba wangoona kupsa mtima km iweyo ndi one
Kod chilima alikt akumkuyu
Km ankukuyu ndinu muthu obadwa ndi munthu kkkk mcp nose ndinu agalu pls chakwra
Soya packet K800 mhuu
Akunkuyu amalalikira kuti?aaaaa mzimu wa Allan Witka ukupunthani sure😢
Namalomba eeeee
Kkkkk ndalama zabodza zobweleka ku Egypt. Kkkk
Host wakwera, a boma amupasa banzi
Kodi mumapanga program yi chilima alimoyo eti?
Ndevu za mwai ndi dolo ndikufunsa
Ma Dollar alidi nyumba mwa anduna ichi ndye chilungamo😅😅
Koma Wonder
wanda msiska anadya ndalama za mcp
Nayesotolakhaniyi andimanyaka
Wander kuopa boma kuti lingakumange
Political LIARS
Amalawi ake ndi mai oko akukuyu
A kunkuyu ulaliki wake uti bwana witika
Namalomba sayenela kukhala neneri wa chipani ayi DPP must shft this guy saziwa kuyankha mafunso am a DPP fun but am not impressed with this namalomba
Kumkuyu machende ako
Koma yomweyo
Figur yabozayo imathandiza 😂😂 kkkkkkk