Ma bodza ONSE anakweza bus koma a Zake anakweza bus ya BT iyeyo anakwera bus ya Lilongwe chifukwa choti a nabwera mochedwa anapeza bus ya BT itadzadza, anakwera Ndenge ndi Louise yekha, onsamanama,, ine nali pompo momwe amkakwera bus anthu ONSE, Osama pereka umboni wabodza,
Zikomo tamvako Zina mwa izo koma nanga ndichifukwa chani nkhani yakufa kwake anthu akuyamkhula kut Mr L Banda akuziwapo kuthu chonsecho kusala Kwa omwalilayo anasalila ma programs Ake
Rember to subscribe
Nyc job
Iii
😭😭
thanks 🙏
Dzikomo potiziwisa chifukwa timangova achina Ben Longwe kutikota zithu zopanda mutu, Rest in peace chris
Thanks broh for the information
Always welcome
Zimu wake udziuusa muntendele 😢ngati anali ndi zofooka zake ambuye amuchitile chifundo tose tikudikila komweko😢
😂😢😢😫
Loud and clear
I liked it a good video
Chilungamo akuchidziwa ndi Mulungu basi😭
Koma only god knows
Nice video amakwana
Anthu Adana ndi Lucius Banda apa tadziwa chilungamo
Zonvesa chisoni dziko lanthu anyamata oimba akungopita kumanda mmmm
Fanai anayamba bwino koma tingoti mzimu wake uwuse mutendele😢😢😮😮😮😮
Mukoze
Mwalongosola zovek, mzimu wake uwuse mtendele
We really appreciate pofuna kutidziwisa chenicheni za imfa nothing to say RIP WalyCris Wanyengo
Mzimu wake uuse mumtendere only God knows the best.
Thanks potiziwisa bro
Zilibwino
Umaitha
Onse adakwera bus koma zosiyana. Yofikira ku BTz Ina ku LLz iye adakwera yo fikira Btz
Mesa akuti ankapita ku lilongwe ku show??
Iiiii zoona koma Ku la akwa
Bamboo inu ndopusa buaj😢😢😢😢😢😢😢
Kaya akudziwa ndi ambuye tingalakwitse mayankhulidwe
Zimu wake usee muntendere
Oyimba wabwin sakharitsa mzimuwake uwuse mumtendere😅😂
Thanks for ur information
So nice of you
Izo.mukukamba.zpmgova.kapena.ndimaganizo.anu.chabe
Wa moyo ndege ai ka wakufa ok
Bro …. Wanna ask some … Monetizetion ku Malawi kuno imathekaaa… Channel Yakoyii inathekaaa?
Give me your number .... On Facebook .. Sam Malvitha
Good explanation rest in Peace Achalume Walychris Kuchitekete
Zomvetsa chitsoni kwa mtundu wathu ambuye Mulungu ilandileni midzimu yawo ndi kuwakhululukira machimo awo wonse
Koma mumatha Bg ulemu wanu
Ndichifukwa chani atamufusa anakana koma akudziwa kuti ndalama yafikadi muphoni yake ndiwokuba ameneyo
Nanga nchifukwa A Malawi timafuna kuipitsa mbiri za anthu otchuka.
Ndipo inu,,,ine ndinamvanso choncho kunoko,mbumu unja ndi amene anamupangitsa asalile,,,ama panga record,,chosadziwa kuti,,,kusongolo kuzalanji,,,ndikukasakha bus,,maybe ama saver ndalama
iyaaaa mxiew
Rest in peace achalume,we Wu miss ur vibes
RIP wachalume
pitilizani man
Zikomo kwambiri potiziwitsa komabe mitima yathu ili yosweka😭😭😭
😥😥
Ma bodza ONSE anakweza bus koma a Zake anakweza bus ya BT iyeyo anakwera bus ya Lilongwe chifukwa choti a nabwera mochedwa anapeza bus ya BT itadzadza, anakwera Ndenge ndi Louise yekha, onsamanama,, ine nali pompo momwe amkakwera bus anthu ONSE, Osama pereka umboni wabodza,
Adam
Muhammad
Lucia wamanyi wathi Phela muyawo koma thizakumana kuno ku kujoni
Alright
Zikomo
Zovetsa chisoni kwambiri
Naice
Zomvetsa chisoni
It's time nathing more
Good
Mukonze vidios
How
❤
Atupele
God knows best🙏🙏🙏..
Good reporting!
Very 😭😢
Share
Azamutsatha
Zikomo potidziwitsa
Welcome
Uku Nde kufotokoza mwadongosolo, big up bro, channel yakoyi ambiri aitsatira pofuna kudziwa chilungamo,
RIP wachalume
Thanks brother ....
Achalume why😭😭😭😭😭😭😭
Thanks brother mumatha kuyankhula chilungamo
Thanks ... Check out madzulo ano for the last videoyofotokodza mbili ya Moyo wake ....
koma ifa iyi ngati ya mase...yemwe mukuti mukulu wa oyimbayu ndi chillombo
❤❤❤❤
R.l.P walycriss
Akudziwa ndi mulungu basi
Mmmmmm
Eeee
r u from South Africa?
I stay there
Ok Simone armineilo 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🇲🇼
Like
We have nothing tosay only God knows
Banda eee
Zoopwa
A 5:53
Lest in peace
6:06
Zabodza man zonsezo
uthengawo wamveka koma sizikumvetsetseka amta chowona cheni cheni wapita nacho mwiniwakeyo😭😭😭
zapweteka kwambiri
R. I. P
Tumizilen information yoika nthupi mmanda lero
Will do that.... Musaiwale kuchita subscribe Kut ndikaika video ... Mulandile notification....
Imfa sithawi , tichimwa chabe polozana zala rest in peace achalume
Only God knows the truth
So sad
Ife
May his soul rest in peace😢😢
Palibe chomwe mwayankhula chomvekatu apa
I got 504 likes ...
Nkhan inveseren mwachidwi big musaike blame Kwa munthu mopanda umboni
Rlp
Thank you breda
Big up
Google
😭😭😭😭
Only Jah knows
RIP
We have nothing to say, only God knows the truth
Watch my other video...
Very sad
Zikomo tamvako Zina mwa izo koma nanga ndichifukwa chani nkhani yakufa kwake anthu akuyamkhula kut Mr L Banda akuziwapo kuthu chonsecho kusala Kwa omwalilayo anasalila ma programs Ake
Rip
apa zamveka bwino
Imfa siithawika
Inna lillah wainna illah llajiunna
Only God knows may his soul rest in peace
😢😢😢
Linakwana siku lake
R,I,P
Thanx alot
Most welcome
Mmmmmmmmmmm rip
Zovesa chisoni kwambiri RIP