LIMPOPO FM 21 JUNE 2024 NDI COMRADE NTANYIWAKU MAMAWA KUNO LERO FRIDAY

แชร์
ฝัง

ความคิดเห็น • 252

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm หลายเดือนก่อน +5

    The best Radio station in southern Africa

  • @promixphotography8056
    @promixphotography8056 หลายเดือนก่อน +5

    Apolisi ofoila, asilikali ofoila basi kumangomanga anthu mopanda dongosolo lenileni,chakwera wapha osatiso boza

  • @AnnoyedCheeseBoard-sm5nn
    @AnnoyedCheeseBoard-sm5nn หลายเดือนก่อน +3

    Keep it up Limpopo ndipo tikudalira inu ndi KALINDO mumatiyimilira kwambiri osafooka ndipo Kalindo mulungu amuyanganile kufikila atuluke ku police

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx หลายเดือนก่อน +3

    If we cannot stand up and fight for our lives as Malawians, no one is going to fight for us
    Wake up Malawi. There's no time to fear these idiots. It's time to take our rightful place.
    Let's unit and fight

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon หลายเดือนก่อน +3

    Mituyanu sigwira ntchito nonse amene mukuikira KUMBUYO mcp poti simunakumane nazo mcp enanu SIMUKUDZIWA ana obadwa ma 2000

  • @ZakariasintidomathengaMathenga
    @ZakariasintidomathengaMathenga หลายเดือนก่อน +4

    Zoonadi achipani atengepo mbali amunthandize bon kalindo atuluke basi chifukwa ndimunthu modzi otinthandiza tonse zikomo 24:38

  • @franklameck5700
    @franklameck5700 หลายเดือนก่อน +4

    Anthu mudana ndi limpopo kumalawi kuno kupanda anthu amenewawa ndindani angalimbe kumayankhula zimenezi its good kuti akuyankhula ali kunja otherwise bwezi pano tikuti afa so zikamalakwika limpopo ikuyenela kuyankhula basi

  • @LawrenceMsopa-ym1gf
    @LawrenceMsopa-ym1gf หลายเดือนก่อน +4

    Mulungu wakumwamba onetsani ukulu wanu a Malawi akufuna thandizo lanu kuzela kwa atsogoleli omwe inuyo mudawatsankha. Ndifendani ife popanda inu Mulungu wa moyo. Zikomo chifukwa chokumva mawu athu.

  • @mariamahamadu8402
    @mariamahamadu8402 หลายเดือนก่อน +3

    Bola adzamumpe chonde chifukwatu chipani cha kongelesi ndichakimpa nde chonde ambuye kumwqmbako muwoneni boni kalindo pamosi kalepo kaluwa chonde state🙏🙏🙏🙏🙏

  • @chrisboyce2
    @chrisboyce2 หลายเดือนก่อน +3

    Chakwera adzafa imfa yophweteka kwambiri chifukwa mizimu yambiri mudziko lino ikumudandaula kwambiri ndipo Mulungu mwini Zonse achite nawo bambo Chakwera ndi Nduna zake.

  • @blessingsnyalo-rp9ko
    @blessingsnyalo-rp9ko หลายเดือนก่อน +5

    Komadi nawo azipani zosusawa akuyenwra kumachitapo kanthu

    • @dalitson3558
      @dalitson3558 หลายเดือนก่อน

      Ukunena Zoonadi osusawa awonjeza kungoti zii

    • @user-ky4ce9gb6j
      @user-ky4ce9gb6j หลายเดือนก่อน

      Eti inu kungoti ndwii zoona mmm

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w หลายเดือนก่อน +4

    Bon Kalindo amtulutse, ngati boma lawalephela ndi zawo zimezo. Anthu akuvutika kunja uku, iwo akumanga anthu za ziiiii.

  • @AliceGeorge-il6ig
    @AliceGeorge-il6ig หลายเดือนก่อน +2

    Plz let's do something on winikos arrested, we don't have to be silence on this issue

  • @aloysiusdidymus7869
    @aloysiusdidymus7869 หลายเดือนก่อน +2

    Kodzani mademo tiwone ngat akugona

  • @HusseinMoffatt-mi1fl
    @HusseinMoffatt-mi1fl หลายเดือนก่อน +2

    MCP yafika pa manyi chakwela akupanga zapa nkholo kobas zamanyitu chakwelaiwe manyiako😊

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 หลายเดือนก่อน +3

    Ngati Pali anthu opepera ndiye ndife a Malawi mantha too much timakhala always ku ma stand kumaonenelera zinthu zikuonongeka as if we are not here in malawi pambuyo pake tiziyakhurapo very shamefull.

  • @patrickeldrige3740
    @patrickeldrige3740 หลายเดือนก่อน +3

    DPP sikufuna kulowerera kulephera kwa Tonse Alliance kuti asazaname patsogolo kuti a opposition amawasokoneza. Munali patsogolo kuti DPP ichoke ndiye tiye nazoni ndi nyasi zanuzi. Lero Mulungu wakuikani pambalambanda.

  • @user-pl2lj6mh1z
    @user-pl2lj6mh1z หลายเดือนก่อน +4

    Koma achakwela azachoka boma tizabweza zomanga athu osalakwa OK mulungu alinafe ndithu

    • @SaidiMbawa-st6bj
      @SaidiMbawa-st6bj หลายเดือนก่อน

      Iweyo mene ulilimo ungakwanise kumanga president

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y หลายเดือนก่อน +3

    Chakwela you mast go watikwana

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 หลายเดือนก่อน +3

    Vuto ndi azisogoleli osusa angoti pheee ngati kuti akumetedwa osalankhula china chilichonse chozuzula mchitidwe olakwika umene akupanga ng'azi ya mcp, koma akuti akufuna kuzavoteledwa 2025 for wat!?, shame on you opposition leaders

  • @user-pl2lj6mh1z
    @user-pl2lj6mh1z หลายเดือนก่อน +2

    Muzibwelabwela ntanyiwa timadandaula mukapanda kubwela timavela zambili❤❤❤❤❤❤❤

  • @MercyNyachi
    @MercyNyachi หลายเดือนก่อน +2

    I wish I was at my country as Malawian I could have die there too for bon

  • @user-er7ub4ug7y
    @user-er7ub4ug7y หลายเดือนก่อน +2

    Kma a Malawi tinagulitsa mtendere wathu ku MCP tilibe ufulu

  • @user-ci6zw3mj6t
    @user-ci6zw3mj6t หลายเดือนก่อน +1

    Mr born kalindo ndi freedom fighter just leave him alone please please release him b4 you put in trouble u a self chakwera

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg หลายเดือนก่อน +2

    Mr Ntanyiwa munditumileko uthenga Kwa zikhale ng'oma Kuti sarary yamwezi Uno akaguleko malaya

  • @besterlumbe4404
    @besterlumbe4404 หลายเดือนก่อน +3

    Zipani zosusa boma zaku Malawi ndizopusa kwambiri,zogona

  • @AhmadBridge
    @AhmadBridge หลายเดือนก่อน +1

    We are malawi , but lets joing together with opposition partie

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 หลายเดือนก่อน +4

    Mubwelenso amwene mutiwuze amene akufuna kuthawayo , tikamugagade asanathawe

    • @user-si7po9sd5i
      @user-si7po9sd5i หลายเดือนก่อน

      Kkkkkkkk

    • @user-nj4pn8gx7y
      @user-nj4pn8gx7y หลายเดือนก่อน

      😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂km ku Malawi nkokoma

  • @MzondiSydney-xz1zs
    @MzondiSydney-xz1zs หลายเดือนก่อน +3

    Lazarus you are aWIZARD

  • @TwayibuChimbama
    @TwayibuChimbama หลายเดือนก่อน +3

    Brz mwayakhula bwino ndithu koma nkhani yayikulu ndiyakuti osutsa boma akugona kwambili

  • @SebastiaoErnesto-mh6ec
    @SebastiaoErnesto-mh6ec หลายเดือนก่อน +2

    Apatu izi ndizofuna mmachita mademo thawi ya DPP ndiye lelo mukuti dpp yangoti pheee mmayesa mmachosa nonkha

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3q หลายเดือนก่อน +2

    Zoona zake asatana ari umu akubakira amcp zaoizo ife ndife adpp inu tiyeni mademo koma kumzuzu tikhase presidet wanthu osati chakwera uyo ayi nisataniki

  • @BostonMalisawo
    @BostonMalisawo หลายเดือนก่อน +1

    Ino mukuti anthu amangidwawo achita bwino panyapano pa amayi ano mashende anu chakwera apha chilima anagwilizana ndi manganya komanso azinduna nose ndino opanda maliseshe panyapano

  • @AminahMussah
    @AminahMussah หลายเดือนก่อน +2

    akuziwalila kt ndizosiyilana ndipo atsala ndi miyezi yochepa

  • @MphatsoKazembe-uv9ir
    @MphatsoKazembe-uv9ir หลายเดือนก่อน +2

    Osawopa Malawi ndi wa tonse

  • @EllinaBitto
    @EllinaBitto หลายเดือนก่อน +2

    A Chilimaaaaaaaaaaaa😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭

  • @TenahJustinnalia
    @TenahJustinnalia หลายเดือนก่อน +3

    Atimalizatu chakwera chipani chamwazi ichi

  • @gizzykondwani865
    @gizzykondwani865 หลายเดือนก่อน +2

    Olo amange bon kalindo bola ife tikuziwabe kuti wapha saulos chilima ndi chakwela from kasiya 😂😂😂

  • @Geraldmkwewu
    @Geraldmkwewu หลายเดือนก่อน +2

    Vuto utm anatiphera chilima manganya ndi chakwera ose ndi a mcp manganya wasangalara anangodekha maliro achilima kmso bon kalindo atulusidwa chilungamo chimapweteka

  • @user-dp7bc7yy6s
    @user-dp7bc7yy6s หลายเดือนก่อน +2

    Ai ndithu zikomo Mcp tikanatiso tizilota kut zizachitikaso izi kachiken sitikanalozedwaso kuvotera manyakawa

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg หลายเดือนก่อน +1

    Bwanji Sanasankhe. Dausi ..Nsonda ..kapena..uladi Musa Koma chakwera Ali ndi chipongwe

  • @user-xx4mt8ox8e
    @user-xx4mt8ox8e หลายเดือนก่อน +2

    I think apapa akufuna iye ali ku Police mavoti adutse

  • @JimmyIsaac-xd4ef
    @JimmyIsaac-xd4ef หลายเดือนก่อน +7

    Boni Kalindo wamangidwa Koma zipani zotsutsa Ali Phee! Osapangako kanthu

    • @user-ky4ce9gb6j
      @user-ky4ce9gb6j หลายเดือนก่อน

      Zomvesa chisoni kwambiri mmm

  • @user-xm1ic3nr9w
    @user-xm1ic3nr9w หลายเดือนก่อน +1

    Watching from Nsanje ndikutha kuona ma views akukwera mu ma minutes 😊 ocepa

  • @user-pb6tq4hs7u
    @user-pb6tq4hs7u หลายเดือนก่อน +2

    Ndizofuna izi munkayesa zachibwana munapanga mgwilizano wawumbuli koma muli ophunzira lero mukunong,oneza bondotu

  • @blessingsmwenela1308
    @blessingsmwenela1308 หลายเดือนก่อน +1

    Wayankhula bwino nyamatayo akuti osusa Boma akugona aiwala muma 2019 kumapita uko anzawo ankapanga mademo koma zinaliko bwino nthawiyo than Pano..Pano Malawi waipa koma azipani agona tulo..adzakuberani mavoti.

  • @user-vl5on2lj8b
    @user-vl5on2lj8b หลายเดือนก่อน

    Zifwamba 30 kulimbana ndi munthu m'modzi walakwa chani ? ndi udindo wathu aamalawi kulira pamaso pa mulungu kumphavu zake agwese upresidernt wa nkhadzawu amen

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 หลายเดือนก่อน +1

    Tiyeni tisatope tidziwaikidza ma pemphero Mulungu wathu amamva ndipo atimvera sakhala chete Mulungu wathu

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 หลายเดือนก่อน +1

    Mmene alongolera Manganya lero wangokhala chete ndipo ndikaonetsetsa plan yompha Chilima imachoka pakamwa pa Manganya sanayenera kuvora kukhala Vice ngati anali ndi chikondi ndi nzake Saulosi Chilima Manganya ndi mfiti too

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg หลายเดือนก่อน +2

    Olimba mtima anali only chihana palibeso

  • @VeronicaChirwa-ct4os
    @VeronicaChirwa-ct4os หลายเดือนก่อน +1

    Ukuchitikawu ndi uchitsiru kwabasi Chakwera ukundinyasa kwabasi

  • @isaaczuze
    @isaaczuze หลายเดือนก่อน +4

    My vote is for Peter mutharika

  • @user-nz5jh1yk1g
    @user-nz5jh1yk1g หลายเดือนก่อน +2

    Koma boma la achakwera mmmm akudziwa ndi mulungu

  • @LeendaDeborah2005
    @LeendaDeborah2005 หลายเดือนก่อน +2

    Asatana ali mu ma comments section umu 😂😂😂. Ati kubakila MCP

  • @ivychithyoka1551
    @ivychithyoka1551 หลายเดือนก่อน +2

    Sure :DPP+Afford +UDF :::Fire Works

    • @sheila5812
      @sheila5812 หลายเดือนก่อน

      UTM alowe konko

  • @user-qo2cx1ee4y
    @user-qo2cx1ee4y หลายเดือนก่อน +2

    Amalawi mumati munthu akamalankhula mumamuchemelela koma akamangudwa ndiye kumuukilanso ,mutha muona,coz enafetu tili kunja muzivuyika NDINU ngati simukugwilizana,,inafe sangatipeze agalu amenewo siyili maiko okhala amalawi ambiri like south Africa,no koma dziwani mukapanda kugwilana manja mutha ,,matha akuphetsani amalawi

  • @user-yx6oo2pc3r
    @user-yx6oo2pc3r หลายเดือนก่อน +2

    Kodi nanga United Nation ili kuti? Chifukwa zikuoneka ngati sakunva zimene zikuchitika ku Malawi 🇲🇼. Kodi nanga African Union ili kuti? chimene chikufunika Mr Murder Chakwela achotsedwe basi. Komanso ma MP aku Malawi 🇲🇼 ndi ogona ndipo odontha. Chifukwa ma MP ndiamene angakwanitse kumuchotsa Mr Murder Chakwela mwachangu kupyolera ku parliament

    • @jameschiwanga
      @jameschiwanga หลายเดือนก่อน

      Sangabwele Kuno chifukwa anthu Ake amangoyakhula zopanda mutu

  • @user-tm3zh5zk4t
    @user-tm3zh5zk4t หลายเดือนก่อน +2

    😅😅bon kalindo niamene ali olimba mtima ndithu osati awa

  • @LawrenceMsopa-ym1gf
    @LawrenceMsopa-ym1gf หลายเดือนก่อน +1

    AKULU AKULU A MCP MUSAYIWALE KUTI KULI MULUNGU, PALIBE DOLO OPOTSA MULUNGU. MISOZI YA AMALAWI ILI NDI TANTHAWUZO PAMASO PA MULUNGU NAMALENGA.

  • @georgemponda
    @georgemponda หลายเดือนก่อน +1

    A opposition akumalawi agona ndithu kukhalangati adyetsedwa chibanzi chonsecho akufuna kuti amalawi azawavotere mu 2025. Mxm

  • @KelvinJpchimphepo-sh6nc
    @KelvinJpchimphepo-sh6nc หลายเดือนก่อน +1

    Inu mkut Peter abwelere muboma koma anthu akumwera mmmm, Kaya zanu izooo

  • @Leo-fj6gz
    @Leo-fj6gz หลายเดือนก่อน

    The main problem is we have weak opposition parties in Malawi and that’s why we will keep exploited like this….
    I wish Peter could leave the sit of the presidency for the young and brave person to lead the party, he is the only hope left but very old and he can’t act in these issues but a word would change these an acceptable arrest😎

  • @SamukLungu-zg7fl
    @SamukLungu-zg7fl หลายเดือนก่อน +1

    Amutanyiwa ndi kufunakuti mundi fusireko kwa chakwera kuti Kodi iyeyo chakwera ananena kuti ariyese ayenera kurira mumene angarire amafunakuti seka mumaso? Ine ndi mutumbuka

  • @AbuBakrIqrah
    @AbuBakrIqrah หลายเดือนก่อน +1

    Ulemu wanu a ntanyiwa mumatiyimilila ndithu
    Ife kupanda kubvela inu timadandaula kwabasi

  • @HarryKandani
    @HarryKandani หลายเดือนก่อน +1

    Chisankho cha amalawi...paja amafuna change ....change ija ndi imeneyi

  • @Pangolinimw
    @Pangolinimw หลายเดือนก่อน +1

    Nthanyiwa umakwana bwana

  • @EllahChikwatu
    @EllahChikwatu หลายเดือนก่อน +1

    Kunena chilungamo mukamayakhula zowa puta dala afiti amenewa mukuziwa kt azanuwo sakufuna kusokonezedwa pazomwe akucita .
    A born kalindo ndamene anali othandizira kusokoneza dziko lino panoso cilango chake chimeneci ali mphuleso okha samene akat zithu zisithe
    Anthane nazo aliphule yekhaso . Peter ananyozedwa ndpo ngat wayamba kukula nd peter sibwino ndpo osusa asalowerere anthane nazo

  • @Trancy-xt4py
    @Trancy-xt4py หลายเดือนก่อน

    Ndipo sakunama izi zikuchitika izi same like Zimbabwe di tikuziona

  • @user-fd1tu6ku1r
    @user-fd1tu6ku1r หลายเดือนก่อน +1

    Chakwera ndi Bagamoyo

  • @LukaMutikitha
    @LukaMutikitha หลายเดือนก่อน +1

    CHAKWERA NDIWOKUPHA

  • @leoleonard2103
    @leoleonard2103 หลายเดือนก่อน +1

    Bwanji kodi osango muphaso nayeso chakwelayo

  • @petertaulo8014
    @petertaulo8014 หลายเดือนก่อน

    Why we keep quiet let's stand together and rescue our country please.

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf หลายเดือนก่อน +1

    boma la zigawenga zokha zokha ili zitsiru asatana

  • @CharlesPhiri-ds1rk
    @CharlesPhiri-ds1rk หลายเดือนก่อน +1

    Iweyo bwela udzatitsogolelet ifetu tikuopatu 😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @MirriamRaja
    @MirriamRaja หลายเดือนก่อน +1

    Ambuye Malawi wanga akupita kut? Ambuye tithandizen poti ife timadalila inu patokha sitingathe ndinu Mulungu wachilungamo

  • @user-lb5gt4uv3s
    @user-lb5gt4uv3s หลายเดือนก่อน +1

    Amalawife ndiwogonadi timangolilira mmimbadi

  • @JUMAHSabiti
    @JUMAHSabiti หลายเดือนก่อน

    Atule udindo Achakwela kunena mosanyengela ndipo asadikile mpaka 2025 please musaone ngati mupeza mtendele ayi

  • @wilfredkazembe676
    @wilfredkazembe676 หลายเดือนก่อน

    What you must know " MCP" we are in exile out the country tsiku likubwera muzamuwone mmalawi weniweni wait and see as I said your days are numbered

  • @spargomw
    @spargomw หลายเดือนก่อน

    Limpopo🎉🎉🎉

  • @user-ky4ce9gb6j
    @user-ky4ce9gb6j หลายเดือนก่อน +1

    Zomvesa chisoni kwambiri mmm

  • @AhmadBridge
    @AhmadBridge หลายเดือนก่อน +1

    Komad a opposition chitanidi kanthu please

  • @user-vl5on2lj8b
    @user-vl5on2lj8b หลายเดือนก่อน +1

    Kkkkkkk siuziwa olo pang'ono kupatula kuba

  • @user-ty4pq5ub3q
    @user-ty4pq5ub3q หลายเดือนก่อน +1

    Zonse tikuona bwino ndinthu

  • @user-rz9rm4cb8x
    @user-rz9rm4cb8x หลายเดือนก่อน +1

    Inuyo amranyiwa komanso wa bakili muluzi tv mukungolalata koma munabisala kuopa mcp nde mukut anthu asaope

    • @JosephMwambe-rz2oy
      @JosephMwambe-rz2oy หลายเดือนก่อน +1

      Iweyo ndiye ndimbuz yamunthu mukifunanso muaphe anachendeinu mboli zaamanu

  • @ZakariasintidomathengaMathenga
    @ZakariasintidomathengaMathenga หลายเดือนก่อน +1

    Ife timadalila munthu yemweyo bon kalindo

  • @user-cd4df3vg4y
    @user-cd4df3vg4y หลายเดือนก่อน

    Ulemu wanu broo pitilizani kuuza ife amalawi chilungamo, osaopaaa chakwera watikwana kwambiri ana ang'ona awa misokho yathu yakoma

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj หลายเดือนก่อน

    Tatumizani ma message amene ben longwe adatumizawo musamangonamiza anthu inu pazifukwa zanu

  • @JohnConar-kq4hi
    @JohnConar-kq4hi หลายเดือนก่อน +1

    MCP 🤔🤔🤔

  • @user-lk8kj9zv6x
    @user-lk8kj9zv6x หลายเดือนก่อน +1

    Malawi😢😢😢😢😢😢

  • @WhiteRichard-cw2fo
    @WhiteRichard-cw2fo หลายเดือนก่อน +1

    Iwe wa mcp amene ukuika ma comments opusa usamare iwe chisilu eti bon kalindo amarakwa chani iwe wasateniki mukufuna athu azifa timawako beeeee nyani iwe

  • @KassimIssa-bn3od
    @KassimIssa-bn3od หลายเดือนก่อน +1

    Km inuyo tapangan zot mademo achitike mosachadwamu ineso ndiphedwele ngat chilima

    • @jameschiwanga
      @jameschiwanga หลายเดือนก่อน

      Tangopitani nokha palibe atapange mademo mwagwanayo

  • @NastonVickta
    @NastonVickta หลายเดือนก่อน

    Ndigaireni nambala ya Limpopo fm

    • @CaptainNyenga
      @CaptainNyenga หลายเดือนก่อน

      thanks me too I want it

  • @AnaffSayamika-uh6vg
    @AnaffSayamika-uh6vg หลายเดือนก่อน +1

    Km guys Boma limeneli mmmmm

  • @DangerDanish-db1lg
    @DangerDanish-db1lg หลายเดือนก่อน

    Amen

  • @azunguauskay4903
    @azunguauskay4903 หลายเดือนก่อน

    Asafetu Born Kalindo sitithanako ku malawi kuno ohooo

  • @user-yx6oo2pc3r
    @user-yx6oo2pc3r หลายเดือนก่อน

    Chimene ineyo ndikuona apapa bola kungophwanyanapo ndi MCP chifukwa bomali ndi lathu. komanso zikuoneka MDF yathu ndi yautsilu chifukwa sikuiimilira a Malawi 🇲🇼 koma ikuiimilira a MCP. ndiponso bolaani Valantino Phiri achoke pampando wa ukomanda.

  • @user-vl5on2lj8b
    @user-vl5on2lj8b หลายเดือนก่อน +2

    Koma chomwe ndikufuna kudziwa ndi choti kodi momwe zikukhaliramu azisogoleri osusa boma monga ku DPP UDF AFORD AMBEWE simungatengepo gawo pofuna kuthana ndi n'chitidwe ukuchitikawu chifukwa kunena zoona zikuoneseratu kuti 2025 olo chakwera atati asapange campaign atengaso boma potengera ndimomwe wayalira maudindo ku MEC waikako okha okha a M C P mukuganidza kuti inu osusa muzaphulapo ?

    • @user-qq1uj7ct6n
      @user-qq1uj7ct6n หลายเดือนก่อน

      naneso ndikudabwa nawo.....Koma onsewa komaso amabungwee kuli ziiiii why dzikoli?????¿😭😭😭😭😭😭

    • @DoreenEmmanuelj
      @DoreenEmmanuelj หลายเดือนก่อน

      Akuopa chakwala ndioopsa kwambili 😢😢

  • @NefassiNefitarZaqueioZaqueio
    @NefassiNefitarZaqueioZaqueio หลายเดือนก่อน +2

    Kodi mukuti anthu avotere pita muthalika wasintha liti pakutu inu nomwe mukuti MCP sinasinthe pá zaka 30 zomwe yakhala kunja kwa boma.tsono Dpp yakhala kunja kwa boma zaka 4 yasinthila kuti liti????? Sankhani anthu oti sanalamuleko boma .Tamachenjerani a Malawi please.mukutsata zomwe zidachitika ku Brazil?? Pano Lula sakumufunaso koma ankamubwerezetsa .........musapuse a Malawi DPP sinasinthe ndipo zinthu zomwe zidakwera sizidzatsitsidwa mitengo chifukwa chosintha boma

    • @user-qp8kh2hj9o
      @user-qp8kh2hj9o หลายเดือนก่อน

      Zoona ndithu simukunama do koma a Malawi kupusa chabe amafunika munthu wina oti sanalamuleko osati pitala

    • @JosephMwambe-rz2oy
      @JosephMwambe-rz2oy หลายเดือนก่อน

      Galu wachifwamba iwe wa mcp mboliyako

    • @JosephMwambe-rz2oy
      @JosephMwambe-rz2oy หลายเดือนก่อน

      Ulowapo iweyo namachendeiwe

  • @Henry-vw2cz
    @Henry-vw2cz หลายเดือนก่อน +4

    Commander wathu Ndi mbudzi yeniyeni😂😂😂😂

  • @promixphotography8056
    @promixphotography8056 หลายเดือนก่อน

    Ndiye kuti kumwamba kulibe malo athu, tiyeni tipephere molimba kuti tigonjetse nyasizi