Pepani kwambiri A COMRADE poluza agogo anu mzimu wawo MULUNGU aulandile ndikuusunga malo abwino,ndikuwankhululukila mu zofooka zomwe anali nazo Ameen 🤲 Tinachokela kwa MULUNGU ndipo kwa iye ndi kobwelela
Inu ndi zitsilu kwabasi. Mukuti mukufuna anthu apite ku mademo koma mukuwawophyezanso kuti kubwera mifuti. Koma nkhani yokhayi ya ku Barack, I believe it.
Nthawi yawo kuti tidziwedi kuti asilikali anthu Ali ndi mphabvu paokha ngakhale zolamulira dzikoli, ndiye tionera pamenepa kuti ndi ma under pitikoti kapena???
Radio ya mbuli program kuyamba mpaka kutha osalakhurapo chizungu ndiye Pali makape ena amatengeka zamabodza iwekumati Vp wamenyedwa kunamiza anthu ochuluka uchisilu okhaokha
@@mavutomwale6638 vuto lanu ndilimenero Mtanyiwa adapita ku school ngati ine or iweyo ine ndikugwira ntchito boma iye akugwila ntchito yogulisa zovala ganyu
Thanks for the updates proud of you always comrade Ntanyiwa🔥🔥🔥🔥
Pepani pepani Olemekezeka Mr Mtanyiwa poluza Agogo amene amakuthandizani nzeru mumve kupepesa kwanga Mzimu wao iwuse muntendele
Glory to God, Ause ndi mtendere
Pepani kwambiri A COMRADE poluza agogo anu mzimu wawo MULUNGU aulandile ndikuusunga malo abwino,ndikuwankhululukila mu zofooka zomwe anali nazo
Ameen 🤲
Tinachokela kwa MULUNGU ndipo kwa iye ndi kobwelela
Ntanyiwa ❤❤❤,, enawo ndi makape
Ifeyo tikapanga ma demonstration wo Mopanda ma DC wo
Inalillah wainah Lilah lajiunah
Sorry for the loss
Rip mai masika 😢😢😢
Mizimu ndiyokwiya kwambiri onse amene anatengapo gawo onse mulungu awakathe ndithu sikusinja mnzake yudas ndi uyo wathamangisidwayo kkkk pepani antanyiwa poluza agogo anu pepani mzimu wawo uuse muntendere
Pepani antanyura buye akhale nanu nyengo imeneyi. Koma dzuro usiku ndagona ndi kuseka za avic atathawa kkkk anawa hita bwino kwambiri anakangomupheratu ameneyo😅😅
Pepani kwambiri comrade😂
Pepani comrade😢😢😢😢😢😢😢😢😢
Inu ndi zitsilu kwabasi. Mukuti mukufuna anthu apite ku mademo koma mukuwawophyezanso kuti kubwera mifuti. Koma nkhani yokhayi ya ku Barack, I believe it.
Mayooooooo ineeeeeeeee Kubwera kwa Democracy kwapangitsa kuti tizidziwa zomwe zimachitika mdziko mwathu 😭😭😭😭😭 zikomo kwambiri Bakili pobweretsa Democracy😭😭😭😭😭😭 yoooooooooo
Sorry for the lose comrade
RIP mai masika ulemu wanu mtanyiwa
Mulipantchito... Ma,, forum anthawi... Ino..
Mnthumanzi
May she rest in peace
😭
RIP
Sorry Ntanyiwa for the loss
Ndakuvani
Koma ambuye mudzutseso munthu wina olimba mtima ngat chilima atipulumutse ife
Ndipo ichi ndiye chilungamo okuba sangalowe kumenekuja kukaba atsilikali gwilani ntchito yanu plz boma lisakutoleni plz
Nthawi yawo kuti tidziwedi kuti asilikali anthu Ali ndi mphabvu paokha ngakhale zolamulira dzikoli, ndiye tionera pamenepa kuti ndi ma under pitikoti kapena???
Sorry for that,
Koma zaku lilongwe izo inu mukunama
Ntanyiwa ma audio avungen ayaluke
Apatu ndiye asilikali aona poyambira ndiye poti ku MCP kuli mabanzi ambiri sizipita patali izi MCP chipani chankhanza
MHSRIP
Zoti VP wagendedwazo ndi zabodza zimenezo
Ndiwe mbudzi
Chaka chamawa kulizinthu
KOMA ANTANYIWA MUMADZI WA ZOBISKA ZAMBILI APA MWAWACHANGAMUSA ASILIKALI AYAMBE KUMUSAKA DALA KADULA BAS MWAING'ALULA BAS
Radio ya mbuli program kuyamba mpaka kutha osalakhurapo chizungu ndiye Pali makape ena amatengeka zamabodza iwekumati Vp wamenyedwa kunamiza anthu ochuluka uchisilu okhaokha
Pitani uko inu mudaphuzira kuti
ifetu timaziwa kuti inu chisiru kwabasi pamonzi ndimakolo ako kuvutika koyambira kwamakolo koyamwira ndichocho kuzolowera kuba basi ana asiye ngati inu
@@mavutomwale6638 vuto lanu ndilimenero Mtanyiwa adapita ku school ngati ine or iweyo ine ndikugwira ntchito boma iye akugwila ntchito yogulisa zovala ganyu
@@samanthamuller7643 kuvutika kwa chani ukundiziwa ine iweso ndiwe chisilu kwambiri kape ngati iweyo ungandiwuze chani
Mbuli yoyamba ndinu
Sorry for the loss