TSIKU LA CHRISTMAS AYING'ALULA

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 25 ธ.ค. 2024

ความคิดเห็น • 104

  • @JamesPhiri-h7p
    @JamesPhiri-h7p วันที่ผ่านมา +9

    Nkhani yachikangawa itha bwanj pamene kafukufuku wake ndi waboza

  • @yasiniKalonga
    @yasiniKalonga วันที่ผ่านมา +7

    We need black box finish and clala

  • @abwinoamatani4921
    @abwinoamatani4921 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Nkhani siidzatha afiti inu m'paka chilungamo chidziwike

  • @MustapherLino
    @MustapherLino วันที่ผ่านมา +3

    Mkukuyu alinaye mugulu akupha

  • @Spaw-BTheGogoBoy
    @Spaw-BTheGogoBoy 19 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Iyi yokha singathe mwachibwanabwana imfa ndiyopweteka

  • @TakalaniGlenda
    @TakalaniGlenda 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Koma kodi bwanji a opposition komanso mabanja anafedwawa sakufunsa za Black box imene kunkuyu anatu yasungudwa Bruno kuti Lili kuti???

  • @EnerstMwitha
    @EnerstMwitha 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndizoona Mr chakangawa ndioza sakunam mabishop

  • @aharayak4investment531
    @aharayak4investment531 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nkhaniyi siyitha mumve zimenezo Mr chaima.

  • @YusufuUsumani
    @YusufuUsumani 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    kwa anthu amwene Ali ndi zelu ndi maganiso aboh tsangafomele chifukwa kafukufuku ndi osakwanila bweresani black box tifomeresa bas

  • @StevenMasamba-y1p
    @StevenMasamba-y1p วันที่ผ่านมา +2

    Zoopyezana ai akunena chirungamo

  • @owenchikopa7266
    @owenchikopa7266 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kodi panagwera ndege paja ndi pa nkhalango yokhwithima? Mr Chaima chilungamo chimene mukunena ndi chiti mukamati nkhaniyi ithe.

  • @TonyMhone
    @TonyMhone 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Iwenso Chayima ukunena maganidzo AKO futseki. Tiopa mpaka liti galu iwe

  • @BenardKalilani
    @BenardKalilani 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    We need black box iwe kunkuyu history is the best teacher

  • @UPCChisomoChoir
    @UPCChisomoChoir 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Commisssion of inquiry yanuyo munali a mipingo omwe analandira ndalama mesa munawalipira ,mxweeee mitu youmayo

  • @GeoffreyEllias-m9l
    @GeoffreyEllias-m9l 22 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Coka kumkuyu Kodi black box ija ilikuti umkakamba ija.

  • @lacksonsiyadi943
    @lacksonsiyadi943 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nkhani iyi singathe pokhapokha black box ija mutaitulutsa.komanso kuyankha bwino mafunso omwe anthu akufuna kuti ayankhidwe pazomwe mumatiuza ndege itatsowa muja.

  • @DiveliousNyirenda
    @DiveliousNyirenda 23 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Munthu wa straight sangalimvetsedi lipoti lija poti mafuso ambiri sanayankhidwe for example apangidwa bwanj kafukufuku opada black box, komwe kuli black box sakutiuza chosecho anduna ananena mwaveveve kut yilipo ndipo akusunga bwino......

  • @MosesTangwe-q8o
    @MosesTangwe-q8o วันที่ผ่านมา

    Simungawanamize anthu chilungamo tikuchidziwa. sangapange kafukufuku opanda black box.black ilikuti?

  • @UPCChisomoChoir
    @UPCChisomoChoir 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Futsek Chaima sukuchidziwa chomwe ukukamba ,mpungwempungwe munayambisa nokha pokupha anthu aja ,, musazamudelele mkatolika ndi boma palokha limenelija ,, munya muonaso simunati

  • @AnyelwisyeSikwese
    @AnyelwisyeSikwese วันที่ผ่านมา +1

    Mayankho abwera Chaka cha mawa pa 16/09/24.Tizachotsa chikangawa

  • @WhyteSmart
    @WhyteSmart 19 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chilungamo chimawawa,nanga ndikunama kunena kut ndenge inagwera malo konkhwitima koma nanga pamenepaja ndiponkhwitima??

  • @RoseChimbwefu
    @RoseChimbwefu วันที่ผ่านมา

    Nkhani itha bwanji mafuso ena sakuyankhidwa bwino?

  • @TamandaniMaseya
    @TamandaniMaseya 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Iwe chaima kuli mulungu

  • @HassanMia-c2e
    @HassanMia-c2e 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kumalakhura ngat mulindi maudindo ozindikirisa anthu zoona pitan kumabwalo mukapeleke umbon nkhani osawasokoneza anthu mitu kapeleken umbon mulindiulu osawopwezedwa ife tiziwe nawo.

    • @HestingsEdward
      @HestingsEdward 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Abishopu akatolika akuti sakukhutitsidwa chifukwa choyamba adati ndikunkhalango yoopsa (thick forast is it so

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx วันที่ผ่านมา +2

    Nkhani yithe poti anafa aja si abale ako.
    Iyitu siyitha

  • @LukeMapukusa
    @LukeMapukusa 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Palibe kutha nkhaniyi apa black box ilikuti

  • @AmosShadreck
    @AmosShadreck 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nkhani imeneitu ndiyomwe chakwera azaluzile zisankho,amenei ndinkhumba yamunthu kwabasi ndipo tchende lake kwabasi ndiwe kumkuyu amene ma battery ako ndipo chakwera sitingamukhulupilile kumeneka from pachiyambi.

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mpomwe aziwa ku usi sufuka popanda moto eee kwasala akubanja😢

  • @ClementMunyolowa
    @ClementMunyolowa วันที่ผ่านมา +1

    Kodi chaima akupasa zingati tivomere bodza

  • @billymhoni9527
    @billymhoni9527 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Black box ikufunika basi.... Ndipo denge anati inakafika kumzuzu zomwe zikusiyana ndi report lawo lomwe

  • @MadalitsoChilinjala-f9v
    @MadalitsoChilinjala-f9v 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Bomatu likutiuza pa mbali afunse chimwendo yemwe anamuletsa kukwera ndege ndani nkukuyu anawauza anthu KUTI black box ilipo atulutse

  • @billymhoni9527
    @billymhoni9527 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Akubomaaa akukakamiza bwanji kuti nkhani ithe itha bwanji pamene zotuluka za Report zikususana

  • @MarkElia-i7q
    @MarkElia-i7q 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chaima undiyankhulitsa pambali ndipo nditha kutukwana ngati wadya ndalama ndipo ngati iweyoo unakhutira ndi report ife ai

  • @johnnyirenda5848
    @johnnyirenda5848 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chilungamo China pweteka zedi Frankly Speaking

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kukhuyu palibe chomwe angatiuze kodi muesa a malawi 🇲🇼 fe ndiopusa kkkkkk munamatu akukuyu

  • @StevenDastan-f5y
    @StevenDastan-f5y 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nkhaniyi ndiyovuta kwambili

  • @JOHNOlesmasCosmas
    @JOHNOlesmasCosmas 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nkhaniyi sikutha pokha pokha okuphayo nayeso ataphedwa ife a Malawi tidzakondwa ndipo tidzaiwara mpaka kale

  • @GhandNkhoma
    @GhandNkhoma 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    A akafufuze ndi abishopuwo zomwe abweretse ife tizava ngozi siona nkhope .

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Where is black box?? How can I bring out a report without mentioning the issue of blackbox???? Maboza basi anthu mukudana ndi kuuzidwa chilungamo bwanji????

  • @MatikiMatiki-r7c
    @MatikiMatiki-r7c 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Anthu amaputa kukalapa kwa Amembe
    Amamva za mbiri

  • @Eqrah-hj2nu
    @Eqrah-hj2nu 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chilingamo chidziwika after 2025 elections

  • @ChipieIsaac
    @ChipieIsaac 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chikangawa 2024

  • @Mirriumkamwendo
    @Mirriumkamwendo 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ifenso sitikukhutila

  • @GuejendraMk
    @GuejendraMk 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kod a kpmiti anakaiona black box kumene kuli iyo. Ngat anamvera anvamo chani nanga muripot lao alemba zomwe anamvamo.

  • @wacksoniron
    @wacksoniron วันที่ผ่านมา +1

    Achayima inuso mukuzidziwa

  • @Alexanderdzungu-i5o
    @Alexanderdzungu-i5o 23 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    A Bishop apite akafufuze okha kuti atiwuze kuti tidzakhutile

  • @Muchipululu
    @Muchipululu 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Commission of enquiry yauchitsiru, yaugalu, yamanyi

  • @bisweckchimphamba8497
    @bisweckchimphamba8497 23 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nkhani iyitu sidzatha ndipo palibe report logwira mtima lomwe mungatiuze panopa.atsogoleri omwe anasankhidwa analandila chiphuphu

  • @edwinchilomba
    @edwinchilomba 23 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kodi ngozi imeney imafunika ichitike motani kuti anthu a ku Malawi akhulupilire?

  • @BrightPhiri-c6h
    @BrightPhiri-c6h 17 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Anthuwa akungo kutinamiza za report ya ndenge. Those guys akufuna kubela ma vote coz akuthawa report la Chilima.
    Guys tiyeni tisinthe Bomali.
    Kenako tinzamva zenezeni za Ngozi ya Chilima

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 วันที่ผ่านมา +1

    Kufukufuku wabodza angathetse bwanji nkhani imeneyi

  • @gibsonkhumalo6649
    @gibsonkhumalo6649 21 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Akulankhula molimba mtima ameneyo ndikuwona ngati akudxiwa bwino bwino za ngozi ya VIC president pafuka utsi ndiye kuti Pali moto eeetu

  • @TonyMhone
    @TonyMhone 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zonsedzi dzidzatha black box itatulutsidwa timve zili mmenemo ndipamene ineyo ndikhulupilira ziti Ngozi ija ndi ya natural come out Chikangawa iwe. Tiudze zoona

  • @GhandNkhoma
    @GhandNkhoma 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Vote ndi muntima .

  • @abwinoamatani4921
    @abwinoamatani4921 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Atsogoleri achinyengo analandira ma envelope asanayambe kafuku-fuku

  • @MacWilliamKaunda
    @MacWilliamKaunda 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    A Chaima ali ndi mbali

  • @johnnyirenda5848
    @johnnyirenda5848 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Black box Yopanda battery kkkkkk komanso Ilikuti black box panganinso ma Press conference ya black box Kaya ILIKUTI?

  • @edwinchilomba
    @edwinchilomba 23 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ku Iran nakoso mu May president anamwalira pa ngozi ya ndege kodi mukuvako za mpungwepungwe ngat zikuchitika ku Malawi zi?

    • @JustinLipipa
      @JustinLipipa 22 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Kuno ndiku Malawi, and Congress ndi chipani chakupha that's why

  • @RexElsoni
    @RexElsoni 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Bola ibale chilungamo

  • @Ertyvhk
    @Ertyvhk 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nkhani ya Agadama yatenga zaka zingati iyiyi siithatu izatha pa 2025 tikavota

  • @MatikiMatiki-r7c
    @MatikiMatiki-r7c 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Bishop anena anena basi

  • @CatherineMunthali-r1f
    @CatherineMunthali-r1f 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chilungamo chikadzaonka nkhaniyi idzatha

  • @YamkelaDamba-x5f
    @YamkelaDamba-x5f 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chakwera must tell the country the truth

  • @WonderfulMaulana-q6d
    @WonderfulMaulana-q6d 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Tidzakhutira nawo pakadzatuluka black box

  • @PhilipoGoji
    @PhilipoGoji 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nkani imeneyi ilipobe

  • @Alexanderdzungu-i5o
    @Alexanderdzungu-i5o 23 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Tiyeni tikambe za vula inu a Malawi

  • @DjshukulanGift
    @DjshukulanGift 22 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Pokut chakwera ndi mulungu koman zizatha

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Maganizo owona ndiomwe akunenedwa ndi a bishop

  • @OsmanIssajanatu
    @OsmanIssajanatu 23 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndipo aliyese sakukhutila ndi liport chosecho chakwela anapha chilima chifukwachani akuthawathawa kusayankha mafuso shakwela anati ndege inafika ku mzuxu komaso chimwendo anati ndege yazaza

  • @clairemyegha4315
    @clairemyegha4315 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mesa po signer tonse alliance mazibusa analipo. Koma anapangapo chani pamwne ena aja amanena kuti ife mpaka 2030. Why sanabwere kuzalesa
    .

  • @OsmanIssajanatu
    @OsmanIssajanatu 23 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Simungawanamize anthu mumalawimuno tikuziwa kuti chakwela anapha chilima chifukwa chawu president

  • @petertaulo8014
    @petertaulo8014 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chaima ndiwe mbuzi

  • @FelixKChisale
    @FelixKChisale 23 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Iwe ndiwe opusa kwambiri iweyo sungakhale mtsomgole

  • @WilsonMbendela
    @WilsonMbendela 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kodi iwe chaima umati chani matako ako

  • @Blessings-b7h
    @Blessings-b7h 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Waimba basi mbiri yawo inaipa a mcp anthu oipa.

  • @AmosNjoka
    @AmosNjoka 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Dpp kd mutan tazukan msanga mussngokhala cete kms taonan mukupanga kapen mbali imoz kupoto pakati mwasiila agangata okha

  • @GeoffreyEllias-m9l
    @GeoffreyEllias-m9l 23 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kulibe kutha choonadi mcakuti munatiphera chilima.

  • @JamesMaduka-wk8xi
    @JamesMaduka-wk8xi 23 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kufufuza zangoziyandege safunangati taxi imeneija imazifufuzayokha ndichifukwaanayika brack box and transponder ngati sakuulula brack box iweyooyikilakumbuyo bomawe ungathekuganizachiyani tokamalankhula mumatiyesaowukila koma malingauliiweungamvebwanji

  • @Alexanderdzungu-i5o
    @Alexanderdzungu-i5o 23 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    A kunja ndi abodza koma akuti ma bishop ndiwo amadziwa kaya zanu izo

  • @DjshukulanGift
    @DjshukulanGift 22 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Tivesese xichan? Kupusa basi !!!muphen pokut ndin ziphe,sitikukukuopan agalu in

  • @mchipengule
    @mchipengule 17 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Bishop wopanda zeru uyu!! Wodzetsa chisokonezo akufuna atamike? Mulungu akukhudzeni a Bishop mwapadera dera.

    • @theophiluschale5684
      @theophiluschale5684 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Apa nde Mwayamba kupembeza Chikangawatu . Wopani choona osati Bodza

    • @DereckSumbulero-i4z
      @DereckSumbulero-i4z 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Alimwana wako atamphedwa motero ungamve bwa? mukamayankhula zinazi muziyamba mwalingalira.

  • @TachikoMwanamanga
    @TachikoMwanamanga วันที่ผ่านมา

    Ndipo khani imeneyi anthu mudzayakha. Itha bwanji anthu mukupanga research mobisa kumangotinamiza. Timaona ma research amaiko ena different with our country

  • @AlihIbrahim-s7v
    @AlihIbrahim-s7v 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma oliwoza boma akusowa kuti atulutse black box yomwe anatinamiza kuti ilipo,,,afufuza bwanji za ngozi ya ndege popanda Black Box??? This is rubish

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    IWEYO CHAIMA NDIWE OPUSA KWAMBIRI PALIBE ALOYENSE AMENE AKULHUTIRA NDI LIPOTI LA CHINYENGO LIJA NKHANI ITHABWANJI PAMENE BOMA LIKUPANGA ZA CHINYENGO IWEYO UKATI NKHANINI ITHE AKANAKHALA KUTI ANAPHEDWAUJA ANALI NKAZIWAKO KAPENA MAYI WAKO OLO NCHIMWWNE WAKO UKANAMVABWANJI ? ASOGOLERI A MIPONGO ANALANDIRA NDALAMA LIPORT LOONA TIDZALIZIWA MCP IKACHOKA MBOMA TIDZAIKA KAFUKUFUKU WATHU MWAKHALIRA CHIRUNGAMO AGALU INU ,BISHOP AKUYANKHULA ZOONA SAKUNAMAYI

  • @JuniorAllan-n1t
    @JuniorAllan-n1t 23 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    We need black box that's all

  • @TamUs-u2h
    @TamUs-u2h 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kodi za Imfa ya Isa Njaunjo why you bishops munakhala chete?

  • @ConradccjSokoSoko
    @ConradccjSokoSoko 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chindere, sikuti ukakhala opanda mkazi, Wana sikuti sufuna mtendere, Mtendere ndiofunika kwa aliyense dziko lonse Lino
    Mmali mobweretsa uthenga wa chiyanjano, mtendere, chiyembekezo iyeyo akupereka uthenga wopasula, wa mkwiyo. Iyeyo ndi Mulungu?
    Akufuna lipoti lolembedwa ndi Mulungu?

  • @rabisonpias5131
    @rabisonpias5131 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mwauze ACHAIMAWO mutu wawo udapenga.
    Tidzingomvomereza ndi za bodza zonse?. Where is a black box?.
    Who ordered searching isiyidwe.?
    Who told CHAKWERA zoti ndege idakafika ku MZUZU.
    Amene adamuwuza CHIMWENDO zoti malo mu ndege athamo, yet he/she knows zoti padali only 9 passengers. What was their intentions?

  • @AllanMumba-b9q
    @AllanMumba-b9q 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Pointless Mr Kumkuyu

  • @TamUs-u2h
    @TamUs-u2h 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Bishops Catholic watch your speech before your sermon.
    Tell Malawian the truth, otherwise ngati muno mungakhale ziwawa mwayambitsa ndinu

  • @HastingsBanda-m3z
    @HastingsBanda-m3z 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Iyeyo ngat akudziwa akanene ndipo akamupeze wasowa cholandila chomwe amalandila kwa chilima kulira ndikomweku basi

  • @HassanMia-c2e
    @HassanMia-c2e 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma abishop pena pake tangobwelesan umbon anthu adziwe zachibwana basi bwelesan umbon anthu adziwe ziko lizipita pasongolo sizachibwana mukulakhurazo basi

  • @TamUs-u2h
    @TamUs-u2h 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ine that's why ndinasiya kupemphera Ku Catholic aaaaaa umalowa mu church ndikutulukamo chimodzimodzi, ulaliki wa ndale okha okha za ziiiiii

  • @gibsonkhumalo6649
    @gibsonkhumalo6649 21 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Tamuuzaza bishop yo alongosole bwino chifukwa akuwoneka ngat akudxiwa bwino za ngozi imeneija

    • @danielmsowoya9107
      @danielmsowoya9107 21 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Kuganiza mofoila inuyo

    • @JeloJagot
      @JeloJagot 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Aliyense amene ali mmalawi akudziwa bwino zangoziyi kuti siyachilungamo. Mwakhala mukumangozikola mmayankhulidwe anu.mukufuna amalawi akukhulupilireni bodza lanulo. Inu amene mwakhutilanu khalani chete osakhutirafe tisiyeni tizilirabe kudikila Mulungu azatitonthoze. Hanania ndi Safira anafa kaamba konena bodza.