KODI MWAMVA ZA BISHOP MSUSA UJA AKUKOKA NKHANI YA CHILIMA UJA? AMUTOKOTELA ABUSA ~ KOMA BOMA ILI EEH

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 13 ม.ค. 2025

ความคิดเห็น • 300

  • @MercyWillard
    @MercyWillard 18 วันที่ผ่านมา +16

    Msusa ambiri akugwilizana naye,ineso

  • @ChimwemweEEmwale-cz6nc
    @ChimwemweEEmwale-cz6nc 18 วันที่ผ่านมา +10

    Ndiye mukunenazoona kt ndege idayamwa magazi&mikozo ya anthu omwe adafa??nanga anthu chomwe chodawapha mundege isanagwe ndichani??
    Mafunso ochuluka akuperekedwa omwe alibe mayakho bola mukadangosiya osafufuzanso😢😢

  • @EliasYusufu-f5i
    @EliasYusufu-f5i 18 วันที่ผ่านมา +7

    This people we must demand to release black box this issues will come out slow by slow

  • @mbumbajilowele6511
    @mbumbajilowele6511 18 วันที่ผ่านมา +12

    Simple way ife tikufuna black box basi

    • @TakalaniGlenda
      @TakalaniGlenda 18 วันที่ผ่านมา

      Nkhani ili pa black box basi sizambiri ndiye asatipusitsedi agaluwa..

    • @KunjeFarouk
      @KunjeFarouk 18 วันที่ผ่านมา

      @@TakalaniGlenda bodza loyamba linaoneka ponenakuti komwe kunagwera ndenge ndikowilira koma zithunzi zija sikunali kowilira

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 18 วันที่ผ่านมา +5

    Msusa Bishop, Chakwera anapha Chilima. Bishop olimba mtima. Nkhani siotsekana pakamwa kuti wina asayankhule.

  • @ObviousLokoma
    @ObviousLokoma 18 วันที่ผ่านมา +6

    We need black box that's what we want not to please someone but the truth must prevail

  • @wendaemily3179
    @wendaemily3179 18 วันที่ผ่านมา +7

    Catholic the salt of the world. Bravo our bishop.

  • @AyebhoMfumu
    @AyebhoMfumu 18 วันที่ผ่านมา +3

    Bishop Msusa ..,
    Ambuye akudalitsen, ndinu chiyembekezo, amalawi ochuluka siokhutila ndi report labodzalo.
    Atumiki onyenga awo, adya ndalama.

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 18 วันที่ผ่านมา +15

    Bishop wanzeru Chakwera anapha CHILIMA

    • @philemontitusnkhoma7740
      @philemontitusnkhoma7740 18 วันที่ผ่านมา

      Ayi, adapha iweyo, amene ndi mnxukwa yopanda mnzeru, imene Bishop Nsusa waidzutsa kumanda

  • @NoelBanda-y4r
    @NoelBanda-y4r 18 วันที่ผ่านมา +11

    Abusa okuba awa zitsiru za anthu izii

  • @BrightonMkandawire
    @BrightonMkandawire 18 วันที่ผ่านมา +3

    Likhaka bwanji report yomveka without black box mukuzemba chani akupasani ndalama kuseli?

  • @rhodricksagawa7631
    @rhodricksagawa7631 18 วันที่ผ่านมา +5

    Anthu amene akuonongetsa Malawi ndiamenewa, a Msusa ananena momveka bwino kuti iwowo lipoti sadakhutire nawo ndiye makapewa akuzuzula chani? Nkhani ya anyamata azikwanje angoiyezeka osayankhapo bwinobwino. Adzafa infa yowawa kwambiri makapewa

    • @GeorginaChaduka
      @GeorginaChaduka 18 วันที่ผ่านมา

      Ndiye osapanga wake kafuku fuku bwanjii zaziiiii

    • @JJ-in-the-hut
      @JJ-in-the-hut 17 วันที่ผ่านมา

      M'buss wina akufuna kulila pompo

  • @PatriciaArchangel
    @PatriciaArchangel 18 วันที่ผ่านมา +4

    Archbishop msusa nde amawopadi mulungu ndithu

    • @NicksonMicheas
      @NicksonMicheas 17 วันที่ผ่านมา

      Kulimba mtima kwa msusa kumeneko

  • @Christopherchapeta-q2j
    @Christopherchapeta-q2j 18 วันที่ผ่านมา +3

    Angopatsidwa ndalama ndi a Mcp kuti apusise a malawi

  • @YamikaniMituka
    @YamikaniMituka 18 วันที่ผ่านมา +5

    Momwe akuyankhulila awa zot ndi atumika amulungu mmmm ,mwina Mulungu wake siiamene ndkumudziwai mmm

    • @ChimwemweEEmwale-cz6nc
      @ChimwemweEEmwale-cz6nc 18 วันที่ผ่านมา

      Ndipo inu mmm

    • @SliviaJosephy
      @SliviaJosephy 18 วันที่ผ่านมา

      Amatumikila ku midima

    • @VeronicaChirwa-ct4os
      @VeronicaChirwa-ct4os 18 วันที่ผ่านมา

      Indeeeee Mulungu tu anthu amangomunamizira zilipo zomwe akupempheza iwowa osati Mulungu weni-weni ayi

    • @VeronicaChirwa-ct4os
      @VeronicaChirwa-ct4os 18 วันที่ผ่านมา

      ​@@SliviaJosephyZoonadi otumikira za pansi pa nyanja izi

    • @chickob3859
      @chickob3859 18 วันที่ผ่านมา

      Naneso ndakaika

  • @IsmaelBilal-lh1pi
    @IsmaelBilal-lh1pi 18 วันที่ผ่านมา +3

    Ndalama ku mcp zapweka ...isi ndi sizelekwete zoononga dziko 😊

  • @MaggieMasiano
    @MaggieMasiano 18 วันที่ผ่านมา +5

    We need black box no blackbox no conclusion

  • @MacWilliamKaunda
    @MacWilliamKaunda 18 วันที่ผ่านมา +3

    Kuyeselera zizungu za apule,za ziii.just believe what you're believing,we & our Bishops don't believe what you're believing

  • @mbumbajilowele6511
    @mbumbajilowele6511 18 วันที่ผ่านมา +3

    Kodi agalu awa MA comments amawelenga zatumidwa izi si atumiki amulungu awa

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 18 วันที่ผ่านมา +2

    Ndili pambuyo pa bishop susa ena wo ndi ana afalawo ndichifukwa sakunena mipingo yomwe achokera vya satana vila vyamumalawi azerereza imwe

  • @BrightonMkandawire
    @BrightonMkandawire 18 วันที่ผ่านมา +3

    Msusa sanalakwise nosenu you are not enough to be abusa

  • @lesliematewere-dm1im
    @lesliematewere-dm1im 18 วันที่ผ่านมา +5

    tulusani report labwino bas osati zomwe mupangazo

  • @NoahPhiri-f7m
    @NoahPhiri-f7m 18 วันที่ผ่านมา +2

    Ambuye ndiwamphamvu kuposa satana mimbulu inu ukulu wa Mulungu ukubwer posachedwapa ndichilungamo pa ifa ya Achilma.

  • @MajiduMakiyi
    @MajiduMakiyi 18 วันที่ผ่านมา +2

    Bola mwanva agalu munamupha chilima akupaseni ndalama chakwelayo kuti muyankhulie pamtumbo panu agalu ndalama ikupwesani

  • @steveduwa6856
    @steveduwa6856 18 วันที่ผ่านมา +1

    Wonders Will never end in this poor Malawi.

  • @TarcisioDKasampha
    @TarcisioDKasampha 18 วันที่ผ่านมา +2

    Ambuye akuyendereni mwapaderadera, inu onyenganu

  • @MathewsMandutu-q9l
    @MathewsMandutu-q9l 18 วันที่ผ่านมา +3

    Ayelekeze kupha bishop wina aliyense katolika ndi boma paokha

    • @IssacMateyo
      @IssacMateyo 18 วันที่ผ่านมา

      Ayelekeze awone

    • @SimonLino-c1f
      @SimonLino-c1f 17 วันที่ผ่านมา

      No Justification that these people are clergy members. The money they might have swallowed is the cause of their get together. They are the bought lawyers trying to conceal the truth known to everyone even a younger ones

  • @LuckyNachongo-kg8oe
    @LuckyNachongo-kg8oe 18 วันที่ผ่านมา +1

    Bravo our Bishop

  • @StuwartKaunda
    @StuwartKaunda 18 วันที่ผ่านมา +1

    Kwakwakwa ndikuombera manja azibusa omanga dziko 🙏

  • @CLIFORDZAKARIA
    @CLIFORDZAKARIA 17 วันที่ผ่านมา

    Azibusa ammadzi awa, Msusa yemweyo kuti wawawa!!!! Idyani ndalama zamagazizo mufa nazo. Blood is in your hands abusa adyera inu, funso kumati, mwadya zingati? Composition ya enquiry inali ya anthu ngati unuyonso, adyera. We support our holy Bishop Msusa,Long Live Msusa!!!!.?

  • @PiasonAndrew-t7v
    @PiasonAndrew-t7v 17 วันที่ผ่านมา

    Kodi ngati nzanu wanena kt sanamvese pa report lomwe linatuluka ndiye inu mufuna amvese?

  • @gregchisuse830
    @gregchisuse830 18 วันที่ผ่านมา +1

    Onsewa alandilapo kale commission yanji yopanda black box paliena apa alingati mphepo

  • @PiterDeleza
    @PiterDeleza 18 วันที่ผ่านมา +3

    Yankhani funso nanga send off ndi dzina la mpingo?

    • @VeronicaChirwa-ct4os
      @VeronicaChirwa-ct4os 18 วันที่ผ่านมา

      Etii send off lingakhale dzina la mpingo mitu yawo

  • @RodgersMalaya
    @RodgersMalaya 18 วันที่ผ่านมา +2

    Mukatelo mwawona chithumba limbikilani muchitola nthawi ndiyomweyi mwayionela patali

  • @MaxwellChiwaya-i8q
    @MaxwellChiwaya-i8q 18 วันที่ผ่านมา +1

    Msusa Ali kumbali ya Amalawi

  • @EmmieM-kk7bl
    @EmmieM-kk7bl 18 วันที่ผ่านมา +2

    Umphawi kunyozetsa mmm

  • @TelezaNtodwa
    @TelezaNtodwa 18 วันที่ผ่านมา +1

    We need black box .no black box no concluion.

  • @johnsoldier
    @johnsoldier 18 วันที่ผ่านมา +1

    Ndipo oyakhulira azibusa asakha mbuli kwambiri,udzabwera ndiyazikwanje yazikwanje ndiiyi yayamba kubwera ndiitiyo nthaw zina anthu inu chisoni chidzikungwilani Mozambique simukuona et ndinu agalu kwambili

  • @NoahPhiri-f7m
    @NoahPhiri-f7m 18 วันที่ผ่านมา +1

    Ana anjoka inu Mulungu akukantheni inu anthu oipa inu munamupha Chilima osalakwa inu simukuwina 2025, you see in the name of Jesus Christ.

  • @jadakystanford115
    @jadakystanford115 18 วันที่ผ่านมา +1

    Bishop sadakakwitse vuto amalawi anthu oputsa ogona dziko lonse kusauka kumapangitsa kupondereza chilungamo.nawo otsutsa akuyankhura English osayankhura chichewa chokha chokha MCP yatenga aganyu paja khalidwe kawo

  • @KennedyBaton
    @KennedyBaton 18 วันที่ผ่านมา +1

    Quest for money makes people lose their dignity

  • @MacdonaldNzunga
    @MacdonaldNzunga 18 วันที่ผ่านมา +1

    Onse alipamepo makhruku okhaokha akuba muzina la mulungu or mumuone akulankhura uyo momwe wametera zikusonyezeratu kuti ndi tambwali ndiye ngati mwalandira ndalama tizakunama nthawi yikubwera ndipo mudzatidziwa amalawi kuti chibwana chomwe mukuchitacho chidzatha

  • @Ertyvhk
    @Ertyvhk 18 วันที่ผ่านมา +1

    Azibusa ake ndi awa amapasidwa ngongolewa

  • @ProspaDMitummba
    @ProspaDMitummba 17 วันที่ผ่านมา

    Remember after this life there's judgement mungathe kubisala kuseri kwa ndalama koma nzanu msusa real man of god he stand up on truth ndikuopa mulungu osati cikangawa

  • @ChikondiSabe
    @ChikondiSabe 18 วันที่ผ่านมา +2

    Ma busa achinyengo amenewo chikangawa ndi amene anapha chilima basi

  • @StevenDastan-f5y
    @StevenDastan-f5y 18 วันที่ผ่านมา +2

    Wometa mmbaliyu ndi mm busaso kod

    • @PeterNgalauka
      @PeterNgalauka 17 วันที่ผ่านมา

      Kkkkkkkka abusa akumadzi amametatu mbalimbali

    • @ProfessorLawn15
      @ProfessorLawn15 16 วันที่ผ่านมา

      😊amenewa si abusa koma hule.wa mmeta mmbaliyi anamuthamangitsa ku Swaziland. Amagona ndi atsikana 5. Tunena pano wqonongaso banja labeni ku matchansi uku amagona ndi mkazi wa abusa

  • @paulbanda9638
    @paulbanda9638 18 วันที่ผ่านมา +1

    Gulu la PAC ndikagulu kambava ngati inuyo shame on you, bishop msusa alibe banga, awa aoneni bwino bwino mbava zokhazokha

  • @bisweckchimphamba8497
    @bisweckchimphamba8497 18 วันที่ผ่านมา +1

    Kutereku akutumani kuti mutisokosere pano,false prophets,akupatsani zingati?koma inuyo mudzakayankha one day

  • @EliyassYusufu
    @EliyassYusufu 18 วันที่ผ่านมา +1

    Lipoti lopanda omangidwa mukatelo mwatapa tili pa mbuyo pa nu abishopo ngakhale siyine wa mpingo wanu koma poyima pachilungamo

  • @MayamikoMlenga
    @MayamikoMlenga 18 วันที่ผ่านมา +1

    Amsusa munthu wabwino kwambiri ndipo bambo msusa mulungu akudalitseni

    • @GeorginaChaduka
      @GeorginaChaduka 18 วันที่ผ่านมา

      Mulungu wake utiyo😂😂😂😂😂😂

    • @MayamikoMlenga
      @MayamikoMlenga 18 วันที่ผ่านมา

      @GeorginaChaduka mulungu wakumwamba amend analenga chilichonse amene anatipatsa moyo tili nawowu

  • @LiffaChinkhota
    @LiffaChinkhota 18 วันที่ผ่านมา +1

    Ndalama zaboma zaphweka awawa awatuma koma sakwanitsa achepa nazo
    Palibe amene aliwachipembedzo apa onsewa akuimila mabanja awo osati kuimila chipembedzo ndawakana ine azipembedzo ndia PAC bas

    • @VeronicaChirwa-ct4os
      @VeronicaChirwa-ct4os 18 วันที่ผ่านมา

      Akhale a mpingo akanatchula mpingo weniweni

  • @LiffaChinkhota
    @LiffaChinkhota 18 วันที่ผ่านมา +1

    Bungwe lazigawenga ili koma enanu musatinamize sindinu asilamu munangophunzila kuwelenga Quran

  • @SteveTembo-q3j
    @SteveTembo-q3j 18 วันที่ผ่านมา +1

    To be honest guys tilindi atolankhani amzeru m Malawi muno.kufunsa mafuso a mphamvu azibusa a fake kukanika kuyankha mmm ma cadet awa

  • @ishmaelsiffah9900
    @ishmaelsiffah9900 18 วันที่ผ่านมา +1

    Anthu awawa akuyenera amangidwe ndi amene akudziwapo zambiri za imfa ya SKC ndi anthu ena 8 aja

  • @johnsoldier
    @johnsoldier 18 วันที่ผ่านมา +1

    Uyu olo utakhala unapanga mwambo ndiiweyo koma ndiwe ojiya kale ukuoneka ndipo anthu inu mulungu akuyendeleni mulibemo uzimu en zomwe mwapangazi ndizimemeso zingabweletse kukwiyitsa anthu ngt simukudziwa bcoz mukuonetsa mbali

  • @ChristopherMajanga-z5d
    @ChristopherMajanga-z5d 18 วันที่ผ่านมา

    Mabishopwo sakupanga za ambuye ai koma ayanja ndalama panjatu inapeleka yesu amen tisadabwe

  • @AventHaizea
    @AventHaizea 17 วันที่ผ่านมา

    Thank you so much for this amazing video! Could you help me with something unrelated: I have a SafePal wallet with USDT, and I have the seed phrase. (alarm fetch churn bridge exercise tape speak race clerk couch crater letter). What's the best way to send them to Binance?

  • @MosesMbale
    @MosesMbale 18 วันที่ผ่านมา +1

    Apo za wubusa palibe, onsewo ndigulu lazikwanje limenelo 😂😂😂😂
    Mubusa sangayankhule zawu bakha zo

  • @bisweckchimphamba8497
    @bisweckchimphamba8497 18 วันที่ผ่านมา +1

    Osabwera zanjala ili mdziko muno ,apa ndiye mukasokoloke chifukwa wina wayankhula chilungamo

  • @GoodsonGeleta
    @GoodsonGeleta 18 วันที่ผ่านมา +1

    Mukhale atumiki ake a Mulungu mametedwe ake amenewo? Koma Mulungu akuchapilidwa blangete pamutu ndithu eeee

  • @ShalomBernard-v4r
    @ShalomBernard-v4r 18 วันที่ผ่านมา +1

    Simazibusa awa ndiokuba awa azibambo ojiya awa

  • @DavieTombozi
    @DavieTombozi 18 วันที่ผ่านมา +1

    Komaso palibe chomwe walakwisa munthu mau ake anati ineyo osati onse kumvesa zinthu iye anati iye sakukhulupirira

  • @SophiePhalula
    @SophiePhalula 18 วันที่ผ่านมา +1

    Iwetu bambo ako ndi Chikangawa osati A bishop ayi

  • @GivenKitha
    @GivenKitha 18 วันที่ผ่านมา +1

    Mbunzi izi zadya ndalama za MCP izi

  • @VeronicaTime-jn7fp
    @VeronicaTime-jn7fp 18 วันที่ผ่านมา +1

    Ndinu ojiya mukukana chani jupanga mwamboko ndiye zikutikhuza chani inu anthu ooneka achipembezo koma mphamvu yake munaikana

  • @TobbiePahuwa
    @TobbiePahuwa 18 วันที่ผ่านมา +1

    Catholic Bishops always they speak Chilungamo ask Kamuzu Banda black box why the hide

    • @GeorginaChaduka
      @GeorginaChaduka 18 วันที่ผ่านมา

      Chilungamo anthu ake atiwo ma bishop mbavazo

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 18 วันที่ผ่านมา +1

    OSATISEWERETSA IFE AMALAWIAN DZIKOLI SI LOMAKE CHAKWERA AI MUMUWUZE CHAKERAWO ONE DAY ADZAKHALA MANJA MWA ANTHU TIDZALOLERA ANTHU TEN KUFA KOMA CHAKWERA ATAFASO

  • @stevekhanje
    @stevekhanje 18 วันที่ผ่านมา +1

    Atumiki onyengawa

  • @BernadettaHalan
    @BernadettaHalan 18 วันที่ผ่านมา +1

    Abusa anzake nde kuti chani?? Zopusa, address him accordingly. Abusa anzakee??? 🥵🥵🥵 fwatseki

    • @GeorginaChaduka
      @GeorginaChaduka 18 วันที่ผ่านมา

      Tsopanooo Mesa mulinso ma catholics mmenemo

  • @dannynamacha4412
    @dannynamacha4412 18 วันที่ผ่านมา

    Kungonyozetsa dzina la Mulungu these guys are playing with fire karma izawatsata

  • @godfreyalberto7425
    @godfreyalberto7425 18 วันที่ผ่านมา

    Ayuda okhudzidwa anampha ambuye Yesu ndipo anawuza alonda akumanda kuti aziti Ophunzira Ambuye Yesu anaba mtembo.. komatu petulo sanaope anati iye ndimboni kuti a yuda ndi amene anapha ambuye ye Yeu sanaope.Ambuye Bishop Msusa ndi Petulo sangaope Catholic church is holiy sitiopa ifa tikamanena chilungamo

  • @dennisbvumbwe
    @dennisbvumbwe 18 วันที่ผ่านมา +1

    Msusa wachita bwino kwambiri report limene linja mafuso anga sanayankhidwe,Tikufuna kafukufuku wabwino.

    • @GeorginaChaduka
      @GeorginaChaduka 18 วันที่ผ่านมา

      Ulindi ufulu opanga wako 😂😂😂😂😂

  • @PiliraniDenesi
    @PiliraniDenesi 18 วันที่ผ่านมา +1

    Enawo ndi abusa achinyengo

  • @MoyendaChileka
    @MoyendaChileka 18 วันที่ผ่านมา +2

    Zaziii

  • @CharlesFeston-r1v
    @CharlesFeston-r1v 17 วันที่ผ่านมา

    Ndiye ngati Bishop akunama mangenitu azibusa ojiya inu zisilu za azibusa

  • @IbrahimUseni-p8f
    @IbrahimUseni-p8f 18 วันที่ผ่านมา +1

    Apapatu zizikuthekerani,koma chilungamo chizaziwika mukazatula udindo,,inu zoona ndege ikamagwa anthu mundegemo amapopedwa mikodzo ndi magazi mmmmmh

  • @DavieTombozi
    @DavieTombozi 18 วันที่ผ่านมา +1

    Oro mametedwe amenewa muli zaubusa menemo

  • @AaronDungadunga-ff2ny
    @AaronDungadunga-ff2ny 18 วันที่ผ่านมา

    Money can blind justice ..they've received money from chakwera

  • @SophiePhalula
    @SophiePhalula 18 วันที่ผ่านมา +1

    Simukuyankha funso tchulani mipingo azibusa

    • @SliviaJosephy
      @SliviaJosephy 18 วันที่ผ่านมา +1

      Akudziwa kuti atibulidwa kaye mayi wavala wiviyo eee ufiti ukumukhala

  • @VictorNkhoma-cq5ym
    @VictorNkhoma-cq5ym 18 วันที่ผ่านมา

    Yehova wachilungamo odziwa kuweluza azaweluza yekha mwachilungamo

  • @PaulcinFarming
    @PaulcinFarming 18 วันที่ผ่านมา

    Wakutumani chikangawa inu musatipusitsepo apa, anthu odana ndichilungamo musatibowepo mwapatsidwa ndalama, gulu lazikwanje lija ndilimeneli tifunilanjiso umboni apa chikangawa party.

  • @Godwin-xy9rg
    @Godwin-xy9rg 17 วันที่ผ่านมา

    Asatanic inu musatiboweposo apa zisiru pamozi ndi chikangawa wanuyo corrupt bishops shame on you

  • @JJ-in-the-hut
    @JJ-in-the-hut 18 วันที่ผ่านมา

    Allahu Akbar!

  • @GertrudeMayuni
    @GertrudeMayuni 16 วันที่ผ่านมา

    Amususa please give a Malawi a break.
    Understand .

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 18 วันที่ผ่านมา +1

    Muone ose nkhope zao zausatana

  • @martintivalenji320
    @martintivalenji320 18 วันที่ผ่านมา +1

    Mbudzi za anthu

  • @mbumbajilowele6511
    @mbumbajilowele6511 18 วันที่ผ่านมา +1

    Busa angamete mbali choncho

  • @CliffordMtuwa-u8z
    @CliffordMtuwa-u8z 18 วันที่ผ่านมา

    Zomwe akunena Bishop Msusa ndi zoona awa akuti Faith leaders si oitanidwa ndi Mulungu koma anaziitana okha siochokera kumwamba

  • @EliyassYusufu
    @EliyassYusufu 18 วันที่ผ่านมา +1

    Lipoti ndilosakwanila

  • @MathewsMandutu-q9l
    @MathewsMandutu-q9l 18 วันที่ผ่านมา +1

    Apingo awa muone khopezo ndi okubanso kkkk

  • @OmegaMussa
    @OmegaMussa 18 วันที่ผ่านมา +1

    Iweyo mpatumbopanko iwe

  • @FortunateChimwaza-j4r
    @FortunateChimwaza-j4r 18 วันที่ผ่านมา +1

    Muli ndinjala basi

  • @michaelbaluwa1056
    @michaelbaluwa1056 17 วันที่ผ่านมา

    All those who are against Archbishop Msusa are the ones who got money from the ruling party. They are actually blinded by the bribes they got to the extent that they are able to speak against the truth. Anthuwa ndi agalu kwabasi

  • @HevenChiwaya
    @HevenChiwaya 17 วันที่ผ่านมา

    Apasidwa ndalama enawa ndioti agulidwa Chikangawa anakapeleka ndalama agawana gawana amenewa MSusa akumamba chilungamo

  • @LuciusScott-h7b
    @LuciusScott-h7b 18 วันที่ผ่านมา +1

    Akuba awa

  • @chickob3859
    @chickob3859 18 วันที่ผ่านมา +1

    Palibepo chilungamo apa zikuchita kuoneka zokha momwe akuyakhulira awa si anthu amulungu, I'm starting to think these Jamaican pastors are actually musicians, not men of God.😂😂😂

  • @PeterNgalauka
    @PeterNgalauka 17 วันที่ผ่านมา

    Press briefing imeneyi yopusa munalikut kut nthawi yonse anthu amayenda ndizikwanje concerned faith leaders anthu oyipa opanda chikondi chachibadwidwe oyera dzina lambuye wanthu yesu khristu. Tithokonze asusa poyakhula mobveka bwi no kut asatanikiwa atulukire poyera.

  • @CharityChirwa-v8v
    @CharityChirwa-v8v 17 วันที่ผ่านมา

    Ngati mudadya ndalama zikuvutani bishop msusa sanalakwe chilungamo chiziyenda ngati mazi chakwela adamohavchilima ndiathuena 8

  • @ChristopherJumu
    @ChristopherJumu 18 วันที่ผ่านมา

    Nonse a mene munabwela pa meeting iyi Patumbo panu nonse

  • @PachaloMwasinga
    @PachaloMwasinga 17 วันที่ผ่านมา

    Osamva chisoni ndi imfa zaanthu 9 zoona? Ambuye akuyendereni mwapaderadera zigawenga zazikwanjenu