Bambo aju nd humble man Koma kutenga Jokes + Ching'aning'ani in same house this is going to be wahala promax 😂😂😂 Nde ching'axy ali nd ma rules ake otsegulira get iiii 😂😂😂🙌
Koma Mukumachedwetsa ma episode... Ndikungomva bambo a Ju or Mayi a Ju koma Ju'yo sindikumuwonamo mnyumba muja kapena Ali ku school... Ngati palibe ine mzakhale Junior
Yalakwika pamodzi......sizingatheke abwana ake aakazi osamudzidwa yemwe anapanga chipongwe sister wawo......samayenera kumufunsa jokes kuti Kodi mukudziwana, mistake ili pamenepo....... acting yanu ikusowekera seriousness. A jokes akuyang'ana camera mobera which shows kuti iyeyu sakukhala serious!!! Komanso ma voice Anu sakumaonetsa kuti mukupanga zinthu ngati momwe mungazipangire in real life.....mukugulitsa ma voice amusewero.... Koma camera yanu ili bwino. Konzani moyenera kukomzamo...silibwino ndithu.
Nice work mr jokes
Koma please ma minutes akuchepa onjezeran please🙏
Ching'aning'ani ndi dolo kwambiri, Big up to Jokes and your entire team
Bambo aju nd humble man
Koma kutenga Jokes + Ching'aning'ani in same house this is going to be wahala promax 😂😂😂
Nde ching'axy ali nd ma rules ake otsegulira get iiii 😂😂😂🙌
Bambo a Junior ndi Dolo iwo amakonda anthu amagweru basi 😂😂😂 Big up guys.
Kkkkkk MA free range tsopano mutivesa kukoma gys
Mr joke receive you're flowers 🌹
Joke ndi chingaxy aja ndima Khang'a 🔥
Ndayamba kupanga follow tonight Koma ndigona mochedwa i like your acting guys keep it up
Nice acting obwande bwantasa 🔥🔥🔥
Mwatikhaulitsa yoooo mumatipatsa kukoma guys
Uku kuvutadi chiphwanya mix jokes 😅
😂😂😂 apo nde mwayiponyela kwakuyatu mungatenge anthu osokoneza okha okha akhale pamodzi hahaha azimayi akadavutikabe pakhomopo malo mokonza vuto mukuwonjezelaso mavuto ena
Komatu Bambo a Juh anthu amagweruwa, a bwinobwino sim'maona.
This episode ndaseka eeehhh
Ndichifukwa chani ching'aning'ani amangokhara mulonda 😂😂😂😂😂😂 anthu amagweruwa mukumawatenga kuti
He is good on that character
Aaaaa😅😅😅😅😅ATI choka apa magweru🤣
Kabanja akaka nde ndi mbambande kkkkk ati nde ndikuwuze....kamenekoo kkk
Kuzangoona ching'axy ndangoziwilat kuti bas abwana aputa mavuto nambala 2😂😂😂😂
Apalamula double wahala 😂😂😂
Kkkkkk😂😂😂😂😂 jokosi ndi chipheeee😂😂😂
Koma kt hoooooo ati freeee range😂😂😂
This season is the best
Kwayipa basi mpaka ching'aning'ani 😂😂😂
Head of the house on top of everything😂😂😂😂
Ching'aning'ani phuma😂
Akuti pa gate pa pali ma rules 😅😅😅😅🙌🙌🙌
😂😂😂😂😂😂 ching'ax wadza tsopano
Kkkk obwande live ati tachoka kuchikamwa
Koma Takondwa ,MA Ju ndi Thoko aziona kkkk alowesa nsikidzi mnyumba
Iwe umakwana 🔥🔥🔥🔥🔥
Tikumafupika❤ koma nditosangalatsa😂❤
Mukumachedwa... We enjoy watching Wachake
Jokes nd chingax madolo kwambili
Eee koma ching'axy yapageti yamulola
Zapamwamba guys ✌️
Amfumu athonyiwa tsopano. Moya MWafika apa? 😂😂😂 Go deeper Mr jox asamukepo onsewo usalepo wekha ndibwanawo
Gateman ching'ax ndamukonda take your 🎉🎉, ndimachedwa kuonera ma Nigerians actions koma izi, let's gather here 😂😂
Anyamata mupwetekana ati free range
Koma Mukumachedwetsa ma episode... Ndikungomva bambo a Ju or Mayi a Ju koma Ju'yo sindikumuwonamo mnyumba muja kapena Ali ku school... Ngati palibe ine mzakhale Junior
Kkkkkkkk😂
Nice
Tidikile Mutu kut watbweletsela zotan😂😂😂😂
Free of charge 😂😂😂iyayi amat free range
Every job has got rules,we see hre Mr Ching'axy have got his rules kkkkkk this Man iiiish
Yalakwika pamodzi......sizingatheke abwana ake aakazi osamudzidwa yemwe anapanga chipongwe sister wawo......samayenera kumufunsa jokes kuti Kodi mukudziwana, mistake ili pamenepo....... acting yanu ikusowekera seriousness. A jokes akuyang'ana camera mobera which shows kuti iyeyu sakukhala serious!!! Komanso ma voice Anu sakumaonetsa kuti mukupanga zinthu ngati momwe mungazipangire in real life.....mukugulitsa ma voice amusewero....
Koma camera yanu ili bwino. Konzani moyenera kukomzamo...silibwino ndithu.
Ching'aning'ani wabwera ndiyake ija kkkkkkkkkk
More fireeeeee
Jokes ndi ovutatu😂
😂😂😂😂dolo🎉🎉🎉🎉🎉
komano akumana nyumba imodzi kkkkk kuvuta
❤❤❤❤❤
nyumba izikhala yanu boss akachoka 😂
Kwavuta Ku mpanda😂😂😂😂
Kakoma ndi akaatu kkkk
Koma ching'aning'ani sazatheka ati tonse tikhale kumveselera mutu wabanja
Probably am first one to watch
Aaaaa Nthawi yomweyi yatha kale tidikilenso aaa😢
Muzikhala active poyakhula team yonse
3range😂😂❤
Koma jo ndi bwanawa mumanvana
It's too much sort ur series
MA facts a jokes😂😂😂😂
Kakuchepa kwambiri
😂😂😂😂 nice movies
koma anyamata inuyo ayi zikomo ndithu
Ching'aninga'ani😂😂😂😂
Yako ijaa dolo🔥
🎉❤❤❤❤wachake
Kkkkkkk koma jokes
Kuchikamwa😂
It's too much short why😅
Mukuchepsa ma minits
Ching'axy wadA iweyo kk
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣kwachema kobas
Mbambande inuyo
Here we go again
Jokes is that your sister? Mufananatu kwambr
4 range kkkkkkkkkkkk
😂😂😂
😂😂😂 koma nthawi ikumachepa atleast izikhalako 25 minutes not 12 minutes
Komano how come bosslady sankamudziwa jokes ??? ...mundiuza being her sister akakanike kupita nawo ku ukwati wake
😂😂Komatu
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
Kkkkkkkk 3 range
Free range
Anthu amagweruw a mukumawagenga kut😂😂😂
Ching'axy phuma😂
❤❤❤🎉
Ok
Kwaipa
Anasiya kodi??? 😢
😀
Eti anthu amagweru mumawatenga kut 😂😂
🤣🤣🤣🤣
,,😂😂😂😂😂
❤❤❤❤❤
😂😂😂😂
😂😂😂😂😂😂