ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
To those who waited for it to watch for free let's gather
We have meeting 😂
Here we are 😂😂😂
Amene timadikira aponye pa TH-cam let's gather here😅😅😅
This program sindimayitsata koma panopa mwandipatsa chochita ndiziwonera ziti zomwezi ❤❤
Yachina phwedo artist wanga iwe kaya uzatimenye koma umabebetsa mr❤❤❤
Akafika pamasewero ndi ochenjera koma like ndiwonkha
The confidence in Phwedo axe bullet 🔥
One of the best so far,,,,, yu got this kev, big up phwedo
Kkkkk eee kwayaka, aaa keev bas nafe mudzatitenge mwamv, tizamwe nawo gin yo aaaaa very fantastic hevy, i like ❤❤❤❤❤
Kkkkk phwedo
😂😂😂😂😂 koma phwedo 😂😂😂 ndimunthudi eya amatha kukhala chibwez🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
"chiprogramu chakochi ndichonyasa, funa anthu ayambane"🤣🤣🤣🤣.... Phwedo is smart.!!!!
Ati atsikana mitu sumagwira. Talakwaso chani😂😂
Kodi ndy osamwa mowafe mumatani nafe?
Fuso limeneli ndifuso lodanisa Fuso loipa🤣😂😂
Phwedo akolewa kkkkkk but not apwanye vintu ka kkkkk .@KAEVE ASE mafuso enawa azakuphwanya ndi botolo mmutu .kkkk careful😅😅😅😂😂
Koma phwedo kusokoneza eeeeeee ayi zikomo😅😅😅😅
Man phwedoo Gin si madzi. Mumakwanira keep fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Mphwedo kufatsa kwabodza😂
zinamveka ngat "kod unamenya aliseche iwe"😂😂😂
Ndili mweeeee ngat phedo nd ma hop anga😂😂
Mwinaso blind date ya Jetu ija muponya tidikilirebe 🤣🤣🤣🤣
😂😅😂😅😂 iwalan zimenezo, maybe next of next month tu 😅😅😅
Ati umayembekezera kt ndiziwelenga😂😂😂
The best Truth or drink ever😂😂
Straight
Ma cerebrity ambiri ndi achimasomaso 🤣🤣🤣 Ka Phwedoka ndi ka Mpakuli 🤣🤣🤣
Kkkkk wanzelu saiwala zomwe akuchita kom kev 😅😅😅😅😅😅
😂😂😂koma kwabweladi phwedo amwene eeeeh eeeh kkkkkkk
Khope yofatsa koma Eeee😂😂😂😂ndi chilombo😂😂
The best ever truth or drink dare😂😂
Mulungu ekha ndamene akudziwa 😅😅😅😅😅umakwana
Ndimutuluke manganya,kenako andimangee pano😂😂
Iyiyi ikufunika kuwonera daily eeeh.....Phwedoooo💥💥💥
This was dope for real😂🙌🙌
Apapa wabwela ngati coming aise, sozoti mpaka ma email address aaah iweee umati 🤣🤣🤣🤣👍
A kelvin akuti ndinu Ahule .Phwedo ndiye ameneyo. Wamuyamba dala
Gin ndakatundu😅😅😂😂 sapanganawo
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🥃🥃🥃anakoza
Mulungu yekha ndiamene akuziwa😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Amphwedo inayo bas Ndi champion Man wo kape mowawo mukuthima Ndinuyo so doesn't matter aku talker zo easy inuyo ❤
Best young actor kwathu kuno respect phwedo😚
A phwedo tsopano kuyipasa moto🔥🔥😹😹best truth or drink🍻🍾
Ever😂😂😂
I like jokes koma your the best actors ku malawi,nsanguluso wathu iwe
Za body count izi ineyo ndiinkawelengaaa??? 😂😂😂😂😂😂
Aaaaaaaah wanthaw!!! Iwe Kelvin tabwera😂😂😂😂😂Gin anakoza
Ndipo tana ndaku delita galu😂Nya uyu akulira😂😂
😂😂😂😂😅 ukadafufuzadi za ndege ija 😅 koma phwedo eich 😂
😂😂😂😂😂 iyiy inabeba heavy
Mowa simadzi we understand you di brother man ❤😂
Gwaladi bwanji? Zamuitaneni nayeso azazipepese
aaaah hahahaha koma ineyo ndaonela ma pg awawa koma na iyi aaah hahahaha phwedo azipanga act akamwa ali mwala heve
🔥🔥🔥🔥 mwala mwala
😂😂😂😂ati mwa ngozi mpaka kunabwera mwana km phwedo😂😂😂😂😂
Timadikira yaku TH-cam apa waiting for blind date aise😂😂😂
Ati amalawi ndopoila kkkkk😂😂😂😂😂 talakwaso chan nanga 😂😂😂😂😂
Koma ndishifukwa shiyani anthuwa amalezela ndi kabotolo kamozi kamowa?
Moto unandi keep it burning 🔥🔥🔥
Ati atsikana mitu siyigwira 😂😂😂😂😂
Chimvekera dzangongole dzikuwonera🤣🤣🤣💔
Ichi nchopengad not only mu movie😂😂😂
🎉🎉🎉❤🎉 mumakwana a Jaakev, udzipangapanga blaza, and don't forget to drop here these programs in gud time man, enafe tikumaona kuchedwa tikaona ti ma clip ku fb page kwako
😂😂😂😂
Program iyiyi ine itha kuthela mashots awiri sure,zinsinsi zonse nditaulura🤣🤣🤣🤣
Wa bodza iwe kkkk
Atiii ndine ofatsa 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 mr bwilubwilu mukhalitse mwava❤
Ati chiprogram chakochi nchonyasa kikkkkkk😂😂😂😂
Akut kuli achina lulu koma akuziwa kale kt ndiyemweyo😅😅koma phwedo
Azimayi imwani mowa😅
😂😂😂 🙌🙌 aulula zonse Wazionera Kaev
Mupiteko ku South bend mukajambule JB😂😂
Iwe Kelvin ine mmapanga kale subscribe before ..........Ndie priceyo isandiphonye oho
Ndipo likeso mnapangaI do to each and every madness guest of u
Ma shot aja amwene eish😂😂😂😂😂Phwedo suzatheka
This guy is funny without knowing his funny 😂
Kev ndihure 😂😂😂 unagwilira ka mwana kwa msundwe 😂😂😂 ukuthawa kkkkkkk 😂
Koma gin ndi redbul?😂😂😂
Ku relationship kwina kunja ngozi iii eshie😂😂😂😂
🔥🔥🔥🔥🔥🔥 muwonesese kt ayake bobo then timpase mafuso🤣🤣🤣
A pwendo aja km ndasangalala😂😂😂😂.........Kev next akhare kineo n aidfest
Mulungu yekha ndamene akuziwa 😂😂😂
😂😂a Malawi azanga😂
Girlfriend uja wakanidwa😂😂
Hahahahah Kumvetsa chisoni
Mmmm aphwedo mumasukatu😂😂😂😂
Mphwedo amatha,this is so entertaining
Aphwedo ndovuta mukalezera😂😂
😂😂😂😂 koma ichichi chaledzera😅😅😅
Mowa simadzi ndatsikimiza lero😂😂
Iyi yandikomela 😍😍😍😍
Agalu wo sikunabwere Tamia kma 😂😂😂😂😂
🤣🤣😆 koma
Ndasiya ine 😂😂😂😂😂😂😂😂
Akuti ndamwa a Kev 😂😂😂
Koma mphanvu zilipo,Gin anamwedwa uyo😂
Mmmm a phwedo andongwa ba 😢😢😢😢😢😢 palibe amawinadi
I really enjoyed this program 😊
Phwedo nyapako umatha😂😂
Ndiovuta fada😊😊😊Oh
Chigawenga chimenechi koma chimatimvetsa sugar keepit up broh
Madness you like stories lol What don't you understand on the fact that he cheated and ku cheating he had a baby with another gurl.
Ati nfili mnchan ine kuti mpaka ndikhale ndi type ine
Ine mmimba mundiwawa plz😂😂😂😂
Ndakupanga stalk ku FB koma eeee ndiwe chikatundu chovaya aise 😊😊😊
Zinamveka kut "kod wamenya kale maliseche"😂😂😂
Siofasa uyu aaaah 😂😂😂
Jah kev umaonjezela shot wezwez 😂😂😂 ndiwe wachibwana
Kuseka sindidzasiya once i saw this video, Phwedo umakwana ase ndaikonda Conf yako umakwana
Kodi phwedo ndi size yanga eishhhh 😂😂😂
Akuti chi program chanuchi tchonyasa 😄🤣 phwedo ndi more
Mowa simadzi iiii😂😂🙌
Phwedo patali akuoneka ngat excess wakale uja😂
😂😂😂😂 gin simadzi kelv ndi husha akut 😅😅😅
To those who waited for it to watch for free let's gather
We have meeting 😂
Here we are 😂😂😂
Amene timadikira aponye pa TH-cam let's gather here😅😅😅
This program sindimayitsata koma panopa mwandipatsa chochita ndiziwonera ziti zomwezi ❤❤
Yachina phwedo artist wanga iwe kaya uzatimenye koma umabebetsa mr❤❤❤
Akafika pamasewero ndi ochenjera koma like ndiwonkha
The confidence in Phwedo axe bullet 🔥
One of the best so far,,,,, yu got this kev, big up phwedo
Kkkkk eee kwayaka, aaa keev bas nafe mudzatitenge mwamv, tizamwe nawo gin yo aaaaa very fantastic hevy, i like ❤❤❤❤❤
Kkkkk phwedo
😂😂😂😂😂 koma phwedo 😂😂😂 ndimunthudi eya amatha kukhala chibwez🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
"chiprogramu chakochi ndichonyasa, funa anthu ayambane"🤣🤣🤣🤣....
Phwedo is smart.!!!!
Ati atsikana mitu sumagwira. Talakwaso chani😂😂
Kodi ndy osamwa mowafe mumatani nafe?
Fuso limeneli ndifuso lodanisa
Fuso loipa🤣😂😂
Phwedo akolewa kkkkkk but not apwanye vintu ka kkkkk .@KAEVE ASE mafuso enawa azakuphwanya ndi botolo mmutu .kkkk careful😅😅😅😂😂
Koma phwedo kusokoneza eeeeeee ayi zikomo😅😅😅😅
Man phwedoo Gin si madzi. Mumakwanira keep fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Mphwedo kufatsa kwabodza😂
zinamveka ngat "kod unamenya aliseche iwe"😂😂😂
Ndili mweeeee ngat phedo nd ma hop anga😂😂
Mwinaso blind date ya Jetu ija muponya tidikilirebe 🤣🤣🤣🤣
😂😅😂😅😂 iwalan zimenezo, maybe next of next month tu 😅😅😅
Ati umayembekezera kt ndiziwelenga😂😂😂
The best Truth or drink ever😂😂
Straight
Ma cerebrity ambiri ndi achimasomaso 🤣🤣🤣 Ka Phwedoka ndi ka Mpakuli 🤣🤣🤣
Kkkkk wanzelu saiwala zomwe akuchita kom kev 😅😅😅😅😅😅
😂😂😂koma kwabweladi phwedo amwene eeeeh eeeh kkkkkkk
Khope yofatsa koma Eeee😂😂😂😂ndi chilombo😂😂
The best ever truth or drink dare😂😂
Mulungu ekha ndamene akudziwa 😅😅😅😅😅umakwana
Ndimutuluke manganya,kenako andimangee pano😂😂
Iyiyi ikufunika kuwonera daily eeeh.....Phwedoooo💥💥💥
This was dope for real😂🙌🙌
Apapa wabwela ngati coming aise, sozoti mpaka ma email address aaah iweee umati 🤣🤣🤣🤣👍
A kelvin akuti ndinu Ahule .
Phwedo ndiye ameneyo. Wamuyamba dala
Gin ndakatundu😅😅😂😂 sapanganawo
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🥃🥃🥃anakoza
Mulungu yekha ndiamene akuziwa😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Amphwedo inayo bas Ndi champion Man wo kape mowawo mukuthima Ndinuyo so doesn't matter aku talker zo easy inuyo ❤
Best young actor kwathu kuno respect phwedo😚
A phwedo tsopano kuyipasa moto🔥🔥😹😹best truth or drink🍻🍾
Ever😂😂😂
I like jokes koma your the best actors ku malawi,nsanguluso wathu iwe
Za body count izi ineyo ndiinkawelengaaa??? 😂😂😂😂😂😂
Aaaaaaaah wanthaw!!! Iwe Kelvin tabwera😂😂😂😂😂Gin anakoza
Ndipo tana ndaku delita galu😂Nya uyu akulira😂😂
😂😂😂😂😅 ukadafufuzadi za ndege ija 😅 koma phwedo eich 😂
😂😂😂😂😂 iyiy inabeba heavy
Mowa simadzi we understand you di brother man ❤😂
Gwaladi bwanji? Zamuitaneni nayeso azazipepese
aaaah hahahaha koma ineyo ndaonela ma pg awawa koma na iyi aaah hahahaha phwedo azipanga act akamwa ali mwala heve
🔥🔥🔥🔥 mwala mwala
😂😂😂😂ati mwa ngozi mpaka kunabwera mwana km phwedo😂😂😂😂😂
Timadikira yaku TH-cam apa waiting for blind date aise😂😂😂
Ati amalawi ndopoila kkkkk😂😂😂😂😂 talakwaso chan nanga 😂😂😂😂😂
Koma ndishifukwa shiyani anthuwa amalezela ndi kabotolo kamozi kamowa?
Moto unandi keep it burning 🔥🔥🔥
Ati atsikana mitu siyigwira 😂😂😂😂😂
Chimvekera dzangongole dzikuwonera🤣🤣🤣💔
Ichi nchopengad not only mu movie😂😂😂
🎉🎉🎉❤🎉 mumakwana a Jaakev, udzipangapanga blaza, and don't forget to drop here these programs in gud time man, enafe tikumaona kuchedwa tikaona ti ma clip ku fb page kwako
😂😂😂😂
Program iyiyi ine itha kuthela mashots awiri sure,zinsinsi zonse nditaulura🤣🤣🤣🤣
Wa bodza iwe kkkk
Atiii ndine ofatsa 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 mr bwilubwilu mukhalitse mwava❤
Ati chiprogram chakochi nchonyasa kikkkkkk😂😂😂😂
Akut kuli achina lulu koma akuziwa kale kt ndiyemweyo😅😅koma phwedo
Azimayi imwani mowa😅
😂😂😂 🙌🙌 aulula zonse
Wazionera Kaev
Mupiteko ku South bend mukajambule JB😂😂
Iwe Kelvin ine mmapanga kale subscribe before ..........
Ndie priceyo isandiphonye oho
Ndipo likeso mnapanga
I do to each and every madness guest of u
Ma shot aja amwene eish😂😂😂😂😂Phwedo suzatheka
This guy is funny without knowing his funny 😂
Kev ndihure 😂😂😂 unagwilira ka mwana kwa msundwe 😂😂😂 ukuthawa kkkkkkk 😂
Koma gin ndi redbul?😂😂😂
Ku relationship kwina kunja ngozi iii eshie😂😂😂😂
🔥🔥🔥🔥🔥🔥 muwonesese kt ayake bobo then timpase mafuso🤣🤣🤣
A pwendo aja km ndasangalala😂😂😂😂.........Kev next akhare kineo n aidfest
Mulungu yekha ndamene akuziwa 😂😂😂
😂😂a Malawi azanga😂
Girlfriend uja wakanidwa😂😂
Hahahahah Kumvetsa chisoni
Mmmm aphwedo mumasukatu😂😂😂😂
Mphwedo amatha,this is so entertaining
Aphwedo ndovuta mukalezera😂😂
😂😂😂😂 koma ichichi chaledzera😅😅😅
Mowa simadzi ndatsikimiza lero😂😂
Iyi yandikomela 😍😍😍😍
Agalu wo sikunabwere Tamia kma 😂😂😂😂😂
🤣🤣😆 koma
Ndasiya ine 😂😂😂😂😂😂😂😂
Akuti ndamwa a Kev 😂😂😂
Koma mphanvu zilipo,Gin anamwedwa uyo😂
Mmmm a phwedo andongwa ba 😢😢😢😢😢😢 palibe amawinadi
I really enjoyed this program 😊
Phwedo nyapako umatha😂😂
Ndiovuta fada😊😊😊
Oh