JEG tElLeM - KWANU ndi KWANU ft 6th Mw , K Banton , LJ woyee & Earnestar || Dir. by P Kayz Mw
ฝัง
- เผยแพร่เมื่อ 5 ก.ย. 2024
- #KwanuNdiKwanu #malawimusic #JegTellem #KBanton #6thMw #LJwoyee #Earnestar #TrendingMalawi
Woyee yeah yeah
Osamayiwala kwanu
Tellem
Osamayiwala
Kwanu Ndi Kwanu mhuu
Nthengo mudalaka njoka aaah
Kwanu Ndi Kwanu mhuuu
Nthengo mudalaka njoka aaah
Kwanu Ndi Kwanu mmhu eh
Ndi kwanube
Kwanu Ndi Kwanu mhhu eh
Ndi kwanube
Kwanu Ndi Kwanu mmhu eh
Ndi kwanube
Nthengo mudalaka njoka aaah
Penapake zikavuta iwe
Ndikwanube
Usamachite manyazi
Ndikwanube
Utha kubwerera konko
Ndikwanube ah ah aaaaah
Osayi wala
Dzuwa likawala
Yemwe anakubala
Yemwe anakusamala
Pamene ukudwala
Usanakwela ladder
Kwanu kwanu nthengo mudalaka njoka
Uzakufunabe olo utachoka
Mukanyozela muzatenga matsoka
Osalora azako aziku locker
Kwanu Ndi Kwanu mmhu
Nthengo mudalaka njoka aah
Kwanu Ndi Kwanu mhuu
Nthengo mudalaka njoka aaah
Munachoka kunyumba kalekale mwati munatola Ka joker
Koma muzabwerabe kwanu nthengo munalaka Ka njoka
Mwasintha mawanga mwasintha khungu mapeto Ake ndi matsoka
Muzatipeza zinthu zikazavuta Pano tingopenya ndi maso
Pa maliro simumapezeka
Kumanda simumapezeka
Koma kuti mugone pansi lero lomwe kumanda omwewo mupezeka
Anapita kalekale kokawonekela eh
Koma kaphiri kakwawo sikaonekela eh
Pena nkumati njokayo mwina nthengo yasochela
Koma azatipezabe mizimu sikukondwera
Kwanu Ndi Kwanu mmhu
Nthengo mudalaka njoka aah
Kwanu Ndi Kwanu mhuu
Nthengo mudalaka njoka aaah
Yeah
Galu amanyada pakwawo nanga iweyo ulekelanji
Uzigomela Malawi kwanu kuno sungasowe mtaji
Funsa neba amasililanji
Mtendere umayambila chitipa kuthela Ku nsanje
Warm heart Ku mpanje
Uzingotakata mpakana uzatsegula maloko
Kutukula Dela lakwanu akhale ako maloto
Kwanu usakuluzile hope
Ukavaya abroad kusaka guap
Tsiku lomwe uzafike pa top
Kwanu uzakuyikeso pa map
Mukanabwera
Mwakhalitsa
Anzanu ochenjela
Goshen amangitsa
Lemme explain
Kulibeko Malo ngati pa den
Tufunika mindset change
Osangokhalila kupanga complain
Yeah yeah
Kwanu Ndi Kwanu mhuu
Nthengo mudalaka njoka aaah
Kwanu Ndi Kwanu mhuuu
Nthengo mudalaka njoka aaah
Kwanu Ndi Kwanu mmhu eh
Ndi kwanube
Kwanu Ndi Kwanu mhhu eh
Ndi kwanube
Kwanu Ndi Kwanu mmhu eh
Ndi kwanube
Nthengo mudalaka njoka aaah
Kamdothi iwe bwerera Ku nyumba iwe
Kamdothi iwe uthela moyenda iwe
Kamdothi iwe aaaaaah
Kamdothi iwe aaaaaah
Kwanu Ndi Kwanu mfana
Town ikasolobana
Ukumbuke padzana
Bwerera Kwa Amama
AUDIO
mikozinet.com/id/kwanu-ndi-kwanu-ft-6th-mwk-bantonlj-woyee-eaenestar/
www.malawi-music.com/J/1057-jeg-tellem/12728-me-vs-me-album/19024-kwanu-ndi-kwanu-ft-6th-mw-x-k-banton-x-lj-woyee-x-eaenestar
❤❤❤
😊
Ase iweo Ur gud man🔥🙌
Jeg ndiwe dolo 🔥🔥🔥🔥🔥
The guy after Banton ndi Faya umatha kwambiri ase!🔥🔥🔥🔥🔥
Lj woyee anaipha heavy
K-Banton got the bars for real
❤🙌 yeah!!!;
Koma chi LJ Woyee chi ndi chachabe 🔥🔥🔥
Fire guy's
Big up bos
Nyc ❤
This is♨♨♨♨
This is great sound
Iwe ndi shasha ase
tel dem nyamata umatha aise 🔥✌
K banton eish
My guy
Nonsenu mumatha koma k banton ndavula chipewa.❤❤❤
nice guys
Nice tune
Madolo🔥🔥
Fire guys🔥🔥🔥🏋️♂️🏋️♂️🏋️♂️
I love the mixture of old and new genres 🔥🔥🔥🔥🇲🇼🇲🇼❤️ we really need mindset change..... Nice bars
Thanks for listening
Jeg 🔥🔥🔥🔥
International moves
Thanks my bro
This track deserves a million views
Wa Gondwe mwanthyapula nyimbo iyi wapapi
Thank you
Lj woyee add the spice to make it sounds great 👍 🔥🔥🔥
Machine machine morefree
Creativity
K banton 🔥
zowonadi osadandawula guys sitiyala pompano tikubwela bola moyo titukula dela lakwathulo ndi2🙏🙏🙏 *respect* nice song guys 👦
Nce song
Eeeh boys akatu mwakonza!
Zili mushe
More🔥🔥🔥🔥 brother man
🔥🔥🔥achina JEG
Fire up 🔥🔥🔥🔥🔥🔥 unand gents mwaphaaaaaa
Palibe anapalamo munyimbomu guys keep it up
Apa mwakamba tchutchtuchu boss, onse amatha 🔥
K Banton🙌
Nice music my church met jeg
Thanks
Lj woyee ndiwe karundu🙌🙌🙌🎵
Lj anaipha heavy
Umatha nkulu iwe
It's crazy how everytime i come to TH-cam the first thing to pop up is this song. DAMN 🔥🔥
K b ulemu wanu hit
Wozaaa
One time me bro jeg
K Banton👌👌👌
Banger💥💥💥🔥🔥
Dolo kwambr.. Iyiyi nd hit kale🔥🔥🔥🔥🔥🚀
Zikomo
Video reflector yo sanagwile bho koma nice video, 🔥🔥
Thank you 😊
Hook waipha
This is nice 👍 big up to you all guyz palibe yemwe wapala apa 🔥🔥🔥🔥 moto unandi👌👌👌
Thank you
@@jegtellem you're welcome
U guys know how to do music, everything about this video is lit,much Respek,keep it up!!🇲🇼🔥🔥🔥
LJ ndi Mfana wachabe my role model keep going
Verse ya Banton... Ndiyamatsengaaa eeeeh
Siyachibwana
I always come here to listen to verse ya LJ then I go
K banton nyimboyi mwaisandusa kukhala yanu 😂
LJ woyee amatha aise amandiwaza
I like this song
K Banton wakhila
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Ukal wan k_banton
On the move❤
Music video ma part ina, simaoneka bho
We will do better next time
Jeg bas kasambe😂😂😂😂😂
Nice ase
Guys ur superb
kkkk oky anytime kumakumbukira kwanu
K Banton ndi akatundu omanga ndi mawaya 👏👏👏👏🔥🔥🔥🔥
Nyimboyi ndiye mwapha guys
Moto mesa 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
eeeeeeh nchachabeee🎉
More fire 🔥 mumatha inuyo
Nice video... Kodi a 6th analibe transport yochoka ku Kasungu🤣🤣
TRACKS IYI NDIDZAIPANGA KA VIDEO NDIKADZAVAYA KU UK! NICE TUNE
Ndikuimvera ndili mubus wakunyumba
Mumakwana man jeg
Nice
Last verse 💥
K-banton one fire 🔥🔥
We sleeping on LJ Woyee, Guy’s a beast🔥
Ndichocho guys
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
K banton umakwanira
Good music six kb morefire
I like you guys
Ndipo kbanton ma rylics amatha
Ilibho
Nyimbo Tellm
6 kuzakomesa chapasipasi
Matured song💥🔥
Umatha🔥
Lj woyee got my vote❤️❤️🔥🔥🔥
From Zambia sending some love this song is dope ❤
Thank you
Nice tune and massage
You guys you wanna us come back serious ndatha kuona,,,,,... Nice vibe big up guys
k banton aise umatha gee
Kwanu ndi kwanu zoona🔥🔥🔥
Home it's best
beat yachabe 🔥🔥🔥
K Banton wozzah 🔥🔥🔥🔥🔥