KODI NKHANI ZA LERO MWAZIMVA? YAPHEDUKATU UKU KWACHEMERATU KOMA INU MWATI MALAWI KWENIKWENI NCHANI?

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 4 ก.พ. 2025

ความคิดเห็น • 27

  • @PaulSanudi
    @PaulSanudi 18 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    ameneyo azingodikila kubweza chuma chathu bass balibeso kucoteledwa. akumama

  • @CharlesMatope-xg6ln
    @CharlesMatope-xg6ln 18 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Azibusa adyera awa,, angofuna kukhutisa mimba zawo not kufunila a Malawi zabwino,,,

  • @PempheroMoleni
    @PempheroMoleni 19 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Mwikho 😂😂😂😂 aaaa chakwera

  • @GeorgeMakina-j9x
    @GeorgeMakina-j9x 19 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Nkhoma Synod am one of the member CCAP dont pray for Chakwera God will punish you

  • @KondwaniChaponga
    @KondwaniChaponga 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Musiyeni Mulungu akhale Mulungu musatchule Mulungu pa chabe

  • @WonganiWongani
    @WonganiWongani 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Or tipephelele inu mwatulukakale mu boma pepani kwambili

  • @PaulSanudi
    @PaulSanudi 18 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    mumuwuze. asatilakwise kuti atimange tikusamala ana ife amalawi. pamene zafikapa Loko kungova Zina lachakwela mimba mukumapweteka chakwela wationesa zokuda sitizamuiwala

  • @StevenMsusa-h2l
    @StevenMsusa-h2l 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา +3

    Dyela basi zinthu mene zakwelelamo 50kg ya cement Mk35, 000.00, Nima Soap Mk800. 00 Bread Mk3, 500. 00
    Chakwela alephela

  • @ProjectHope-l1r
    @ProjectHope-l1r 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Mwikho

  • @charitymhone9983
    @charitymhone9983 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ine kamanganya ka sindimafuna kukamva mau ake Kamandibowa kwabasi palbe chanzeru chomwe wachita kakumangoba chabe misonkho ya amalawi pamoz ndi chikangawa😮😮😮 kuchikamwa

  • @LawrenceLev
    @LawrenceLev 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Azibusa adyera, malo molankhula chilungamo mavuto omwe aMalawi akukumana nawo, koma muli busy kuombera mfiti manja. Mulungu sanyozeka musamale ndithu

  • @MussahCassim-o6u
    @MussahCassim-o6u 19 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Kkkkkk atapembere ndani kod iyeyi mesa amati ndibhusa aphembere yekha

  • @phindiswatshibo7101
    @phindiswatshibo7101 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Azitsogoleri adyera amafunako ndalama

  • @benjaminjobo3525
    @benjaminjobo3525 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Why only nkhoma synod

  • @SylviaAunt
    @SylviaAunt 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Azibusawo si mulungu chimene mulungu wamanga palibe angamasule angakhale abusawo dyela basi

  • @EdwinHowardmkandawire
    @EdwinHowardmkandawire 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ife tikuzavotera chakwera ndipo tilipo ambiri
    kusowa kwa mafuta tinakuuziwa 2012 nthawi ya Bingu

  • @IdrisshSayiti
    @IdrisshSayiti 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zawugalu basi achakwela

  • @FelesianoKamwendo
    @FelesianoKamwendo 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Palibe chomwe angachite chanzeru .
    Malangizo sanayambe lero koma samalangizika
    Miyezi 3 angasithe chachani from 5year kkkkkkkkkkkkkkkk tikakumana kovotako basi kkkkkk

  • @MphindiraChimwemwe
    @MphindiraChimwemwe 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Azibusa awa ndi zitsiru amakasusuka paja azibusa a c c a p kususuka

  • @WilliamNhlane-fd9hi
    @WilliamNhlane-fd9hi 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Umphawi sizinthu , mmene zinthu zili azibusa mumakataniko ku state house ?

    • @JohnWame-u3l
      @JohnWame-u3l 19 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

      Anyapapi adyera😂

  • @JulioChiwalo-t4f
    @JulioChiwalo-t4f 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Mcp Akumayenda ndi zikwanje a mpingo azipempherera zimenezo

  • @JohnWame-u3l
    @JohnWame-u3l 19 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Koma umphawi,ndi usilu,sizabwino