Zilibwino ndipo ifeso timasngala kwambili chifukwa timakhumudwa tikamaona oimba athu kuvetsa chisoni alibu koma apa zilibwino big up eli njuchi zilibwino ostopa osaopa
@Homeofpeace321 anthufe. We have different backgrounds.....you need to understand that a bicycle can be an achievement to someone, just like Njuchi.. having a car is an achievement, so eeeetu brother
Congrats brother Never give up tiye nazon.
Umakwana njuchi big up
Zilibwino ndipo ifeso timasngala kwambili chifukwa timakhumudwa tikamaona oimba athu kuvetsa chisoni alibu koma apa zilibwino big up eli njuchi zilibwino ostopa osaopa
This is a good and great achievement
Congrats❤😅😅😅😅😅
Nice
Congratulations bro
Very impressive boss congratulation ❤
Ndikhumbo lathu kiziwa kt oimba athu akupindula motani mu industry siunalakwise eli keep it up
Good one👍
Congratulations Eli
Congratulation 🎉
Big up ❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉🎉
You deserve respect
Congratulations 🎊
Congratulations mwana.keep it up.
Wow. Long live bro
congratulations njuchi
🎉🎉🎉🎉❤
Osamakhara ngat awa akumwa mowawa ai
Great achievement
Aaaaaa ndithawi yako imeneyo
Kumalawi kungogula Malo ndwe bwana
Ndimakufila njuchi
Congratulations
Pa size yake wachita chithu chachikulu tikuziwapo pomwe amakhala ambuye ndi abwino amasintha nyengo ya munthu ndipo ali ndinjira zambiri zimene amagwirisa ntchito posintha nyengo zilibwino pitilizani koma muzipemphera kuopa kulowa mmayesero ambiri tikachita bwino timayiwala mulungu tumaona ngati ndimphamvu zanthu osayiwala amalandaso akafuna komanso malawi ndiwokwiya uwu ena sakuonera kukondwatu nyumbayo ndi galimito pray for protection
Amen🙏🙏
It’s an achievement because he did put in the hard work in it that’s what achievement means
Wandisangalatsa mwana
well done
Big up
Zimenezi tu zisatibweletsele misozi😭😭😭😭😭😭😭
Galimoto is not achievement amalawi bus plot and nyumba is
Zili mushe koma den plan yake sili shap
Nzokonda zake
Akakulozani muzilira
Achievement galimoto?
@Homeofpeace321 anthufe. We have different backgrounds.....you need to understand that a bicycle can be an achievement to someone, just like Njuchi.. having a car is an achievement, so eeeetu brother
Congratulations
Congratulations 🎉
Big up
Congratulations
Congratulations