Koma kwIne zose mumapanga bwino koma kafuso kaja unafusa cct wangozo kuti zikutheka bwanji iwe oyera ngozo wakuda eee ndinaseka kwabasi koma my ngozo mumatha god bless your family
The video call was amazing....I also wanted to see who was really in the corner kkkkkkk, But Network nkhanza tinakanika kumaliza conversation (Ngozo vs Sangie)....mor fir guyz.
Ine ma p onse amanditsangalatsa koma banja la Ngozo ❤❤❤♨♨♨👏👏ndimalikonda kwambiri. Komaso mbusa wachinyengo ndi Ganiza alibo. Komanotu ndisayiwale Black Lina alibo kulimbana ndi abutsa. Komaso akolo a Ngozo Mulelemba alikuti analibhoso. Love you guys good job. Komasutu ulendo wakumalilo a Ngozo ndi nep man, amfumu hyphen. Pajatu mkazi wa Ngozo anapasidwa zina ndinayikonda kwambiri♨♨♨♨♨❤❤❤💖👏👏
Season inakoma kwa ineyo ndi practice/ training yomwe ankapanga ganizan yolawa mowa b4 asanayambe kugulisa kms yofuna kuwayesa ma baa girl kuti akukoma bwanji.Washing in capetown
Ine Koma pomwe pamandiwaza ndi pomwe ganiza ankapita Ku work shop malangizo Ake omwe ankapereka Patricia , mpaka pa video call pa aaaaaa guy's munakonza mumandimvesa moyo kukoma zoti ndili Kwa Eni ndinaiwala . Ine Patricia kuno Ku Botswana. More 🔥🔥🔥🔥
My name is Adam j j kazembe lneyo pa season 5 ya usauver yomwe inandisngalatsa ndi paja angozo anabwera kunyamba kumawa kwake ndikupeza mkazi wake atagona pa sofa ndikumafusa. Angozo kuti anagona kuti poti azawo onse akawafunsa Amati anagona Juno ndiye mkazi Amati kwenikweni iwe wagona kuti pamenepo inandisngalatsa kwambiri Koma madalo inuyo timakunyadirani mupitirize ndithu
Keep fire burning guys mukutichotsa nkhawa
My favourite part in season five was - WhatsApp video call between Patricia and Ngozo. You killed that scene, Sangie. Nicely done, big up!
Ine my favourite season patricia kumuyimbila ngozo nyimbo,, ndufuna ndi ulule za uhule wa ngozo l like that song❤❤❤❤
My favorite part mu season five ndyomwe Patricia anamuyimbra video call ngozo ❤❤ keep fire gyz mukutichotsa nkhawa
Sangie ndimakonda ma part ako onse 💓💓💓💓
My favorite scene ndiya ganiza akuvayila con. Con got dimples mmmm killing she beautiful.
Gyz this episode is super I like ur characters koma ya ku work shop ndi more komaso Jededai ndi nkhan Zina
Bwana piksy timakunyadirani
yakuwecheta yejinji ngakola ngambe kuti dyemanja wosope li👌
My favourite scene ndiya pamene ngozo ankachoka ku work shop, atangofka kumene pamene Patricia ankafusa za ma boxer kkkkkk, mmatisangalatsa continue
Adoro vossos vidio, continue assim e sucessos 🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿
I love you guys especially ngozo and Patricia. U guys ur so wow, keep it up
Iweyo ndiwe Yokopamala Sangie hahahahahahahahahahahahhahaahahahah Nancy azibwerabwera anakutsukuluzatuuuuuuu
Mumatha guys keep Up
I am enjoying season 5..... Ngozo wabwerako ku workshop ndi ma boxer awiri ochapa kkkkkk big up Usauver
favourite scene ndi ya Ganizani kuyambitsa nyimbo akut "tulutsani wanuyoooo, timuoneeee"
My favorite season is that of you have used😂
My favorite ganizani akut m busa wachingololo
keep the fire burning, mukuitha madolo. i loved all the scenes
Ya video call ndi ngozo ija, lady you killed it🔥🔥
Emmie kuphoda eeeee😃😃😃 Komano ineyo Abusawa ndi Mlongo wake wa Sangie ndi omwe amandiwazamo koposa
The vedio call was the doppest I enkyed it to the max
Yanga favorite scene ndi ya mbutsa atafika kwa ngozo atalandilidwa ndi mlongo wake ngozo aise ndie abwata tu asakuziwa chomwe chilipo 😂
My favourite part in season five was - WhatsApp video call between Patricia and Ngozo
Video call ija aise its boom
This makes my days 🤩🤩, my favorite part,wen Ngozo was leaving kupita ku workshop n Patricia had all instructions Zama boxer 🤣🤣🤣🤣
Amandisangalatsa ndi abusa awo kkkk akuti akufuna kutapa chakhumi 🤣🤣🤣🤣
Zili bho gyz
Ambonera ndawaziwa mu usauver watsala nase i hope nthawi ilipo ndizamuona
Koma kwIne zose mumapanga bwino koma kafuso kaja unafusa cct wangozo kuti zikutheka bwanji iwe oyera ngozo wakuda eee ndinaseka kwabasi koma my ngozo mumatha god bless your family
The video call was amazing....I also wanted to see who was really in the corner kkkkkkk, But Network nkhanza tinakanika kumaliza conversation (Ngozo vs Sangie)....mor fir guyz.
Love you guys
Especially ngozo 😆😆andakwatibwa
Che mkobe takunyadilani zed
Black NiNa sitinamunve mbali yaketu kkkk, part yake inandiwaza heve ,he was serious like its reality.
my favorite scene is when ngozo lied to patricia that he was swallowed by a fish kkkkkkkkkkkk
The one gan decide to go to unknow after sangie recognise that at the plot there is no foundation , yes that one kkkkk
Patricia un Ngozo iwas sure kuti ndi banja 😂, ilike u guy's
Ine ma p onse amanditsangalatsa koma banja la Ngozo ❤❤❤♨♨♨👏👏ndimalikonda kwambiri. Komaso mbusa wachinyengo ndi Ganiza alibo. Komanotu ndisayiwale Black Lina alibo kulimbana ndi abutsa. Komaso akolo a Ngozo Mulelemba alikuti analibhoso. Love you guys good job. Komasutu ulendo wakumalilo a Ngozo ndi nep man, amfumu hyphen. Pajatu mkazi wa Ngozo anapasidwa zina ndinayikonda kwambiri♨♨♨♨♨❤❤❤💖👏👏
Inetu koma paja akazi angozo akafuna mazi naye ngozo kungobweresera chigubu chose chamazi no tambula amwene kkkk koma timasangalala Nanu guyz
Sangie ndinali ndisakumuziwa bwino bwino,kma nditajoina usav ndinazitolera
Guy's mumatiimilira 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
Season inakoma kwa ineyo ndi practice/ training yomwe ankapanga ganizan yolawa mowa b4 asanayambe kugulisa kms yofuna kuwayesa ma baa girl kuti akukoma bwanji.Washing in capetown
We love you guys keep it up
We love you guys
ine ma part onse alibhoo
Imandi waza ija mbusa anmunena Sange kut zebdaya kkkkkk mulogwache wa satana weniweni 😀😀😀😀😀 abusa muita
machine mtebede kubudula mmemo pagate kuzangoyamikila sistez ya ngozo kuona ngati new recruit ya ngozo ahahahah
Big up guys
Makamaka inuyo sister paka video call 🤣
Nkhani ndiyakuti zamkatizo wachapa ndindani mmmmmmmm mumatha gyz
Komano profile picture pa you tube sinasinthebe madam SANGIE mutiuza zotani
Kapena ndine wakuchikamwa
Ineso wanna join u guys
Nelson mr mumakwana
Jebedaya ndebede iweo umantha adha 🤐😂😆🔥
Watching
Victor umakwana umandimvesa kukoma
Video call 🔥🔥🔥🔥
Episode 3 eeeeeeh. Makamaka list ya malamulo kkkkk
Sala uzipola moto 🔥
kanyimboka in the background katulukanso liti,, kakundiwanza
Waiting
Ngakhale ndachedwa km mkadzi Ngozo amandimaliza I really like her
From Tanzania ilov u guys
Ine usova yose imanditakasa
Ine Koma pomwe pamandiwaza ndi pomwe ganiza ankapita Ku work shop malangizo Ake omwe ankapereka Patricia , mpaka pa video call pa aaaaaa guy's munakonza mumandimvesa moyo kukoma zoti ndili Kwa Eni ndinaiwala . Ine Patricia kuno Ku Botswana. More 🔥🔥🔥🔥
Ganizani kuday ndalama zomangila shop
Ine pa video call pakhapaja ndiye eee pamandisangalasa havy
Banja la ngozo ndi #1 mupitilize kutisangalasa muli khe getting
Mumakwanitsa guys mumatimvetsa kukoma pitilizani mulungu akutsogoleleni musasiye
Kuzaimba ka video call esh kandiwaza nkuzathera u have used
Aaaaa koma ayi pitilizani
Ine inandiwaza paja Ganizani ankati abusa anammenya anampeza ndi nkazi waeni
Zaphavu💪💪💪
Ya video call
tazungulira mu room ndi kuona changati half pitikiti
Eh koma video call ija munayitha😂😂
My name is Adam j j kazembe lneyo pa season 5 ya usauver yomwe inandisngalatsa ndi paja angozo anabwera kunyamba kumawa kwake ndikupeza mkazi wake atagona pa sofa ndikumafusa. Angozo kuti anagona kuti poti azawo onse akawafunsa Amati anagona Juno ndiye mkazi Amati kwenikweni iwe wagona kuti pamenepo inandisngalatsa kwambiri Koma madalo inuyo timakunyadirani mupitirize ndithu
Zonse zili bwino ndithu
Ine part inandisangalasa ndi yaganizani ndi abusa akupita ku bus station
Inandisangalatsa mmene Patricia ndi Ngozo anamsekera wantchito atadindidwa ndinkaz wake kkkkk mmakwana guys
Video call ija ndi deal
Zebedaya mtebede amatha akamayankhula ndimangoyambiratu kuseka.Ganizani ndi massive amazakhala ngati opoira koma acting mkulu uyu ndi machine.Za ngozo ndi Jezebeli sitikachite kukamba awawa ndi akatundu.Koma Mtebeli asazamwalire
Wachapiranji ma boxer a mwamuna wanga
But pamene pamamisangaratsa nipaja malo momutsa madzi m,kapu anangotsa chi 5 ltr,,,😃😃😃😃😃😃😃😃😃😃 and man gani amanisangaratsa mayankhulidwe opola kupola
Kakakakak kma chomwe ndi kuziwa ngozo ndi patriciou amakhala kwambiri kakak angomanga oyera
Ine paja Patricia umamulangiza Ngozo be kumapita ku salima paja maka popasa 4n paja.
Ine padandiwaza pa abusa akumutchula Patricia kut Jezebel kkkk pitilizani kutisangalatsa guys😍
Na ya video call ija imandiwaza zimangondikumbutsa ex wanga
Patilitsha ndawona chithu chokhalangati hafu pitikoti
Mumaitha nonse ine imandisangalatsa ndi yamabokosa umaitha sang pitilizani koma funso njakuti ngozo ndi patri munakwatilana
Ku Lodge
Eeeee koma ya ma bokosa ochapidwa awiri eeeee
Ngozo suzamva
Video call was amazing 😂😂😂
ndizizungulira ndine ngulii? Piksy😁😁😁😁😁😁
Ma part onse a Sangie amandisangalatsa..
Komaso mkazi wasisoko atabwera kudzatenga poto wa ndio.
Video call anakonza sagie
Kamakhala ka dram kabwino kwambili
Pitilizani zilibho
Ine pamene pakunisangalasa pa mubusa wamangofikira kunena kuti jezebeli koma mubusa uyu zinazake umangowona waziyamba
Mtebe ndi Gani ndi combo ya nyatwa
Copying mark angel.😂😂 this is good thou
Paja abusa amadelela kut akawapephelela amayi aboxing aja adabwelako atatupa masaya