Usauver Season 4 Intro - Yona
ฝัง
- เผยแพร่เมื่อ 21 ส.ค. 2024
- Welcome To My Channel..
Watch My Other Videos 👇
• Piksy Malawi Music Videos
#Langwani #Piksy #Asauver #Sangie #Music #Malawi #Comedy #Africa #Afro #Trending #Usova #hyphen
Subscribe To My Channel 👇
/ piksymalawi
Watch My Play Usauver 👇👇🔥
• Usauver Episodes
PLEASE NOTE: Unauthorized upload of this video unto any TH-cam channel is prohibited. (C) 2022. #CCNB. I didn't know that she is a non believer . I am very disappointed.
Enjoy USAUVER SEASON 4 INTRO
God bless you piksy umatichosa nkhawa.
One of my favorite episodes. Forever undefeated 😂😂😂
Ati iiiii iiiii Daviyndi Uliya hahaha....i love you my people watching from India waiting for the next one kkk
Sangie ndi piksy mwandibanda heavy,tsiku laenda bwino,enjoying from mbezi beach dar es salaam
Komatu ngozo uzinama bwino penapake iwe mmmmm ukuchita kukhala serious ndimaboza akowo kkkkkkkk uli nsomba yinakumeza kkkkkk langwani ngati iwe ufuna usalile miyendo chani kkkk
wow sangie this is so beautiful at all
Abwana siyan mabozao😂😂😂🔥
Koma ngozi upole moto boza basi Koma mmm amuna Ena maboza mpaka nsomba🤗🤗🤗
koma guys zikumafupika koma muli bhooo guys zibwere bas zinazo ife tingoti big up
nsomba 😂😂😅😆🙆♂️
Nde nsomba inali pachintchitotu nangano kumeza ngozo kkkkkkkkkk ngozo boza limeneli olo satana wamuposa kkkkkkkkkkk much love
Kkkkkkkkk koma somba
Mh komatu ngozo hahaha big up u always make my day 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Hahaha koma guys🙌🤣
iiii koma sisoko mpaka chidindo zoona😂😂😂
Hahaha can't wait for more
KD tingatan ndzisata leavol by leavol..plz coz ndmakonda gyz
❤
Kkkkkkk Ngozo bodza iiiiiiii
Hahahaha ngozo zinazitu kkkk
Yona wa lero ndi Ngozo
Mumawawa😁😁😁
nde kusinja nthumba lamango mwati et hahaha
2023 Koma still tikuonelabe ngozo anakoza
😂😂😂😂kma azibambo polan moto
🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Angozo inuyo ndi kawawa
😂😂😂ngozo kunama
Nsomba zikumatimezad🤣🤣🤣🤣🤣
Kkkkkkk afunika malilime ngozo
Haha.. komatu boiz
Hahaha 😂😂😂 big up guys, you are really entertaining
Angozo simudztheka
Eeeeee chinakumeza chambo ase siku lina izakumeza ng'ona ase kkkkkkk
I like this one. 🤣🤣🤣🤣
Zakutu
Koma mabodza ake abale 😂😂😂
Ngozo anakonza, eti thumba lamango lalowa umumu kkkkkkkkkkkkkkk
hahhahahaha koma ma gyz mumakwana kumezedya ndi somba yomwe yinameza yona kodi sinafebe??? 😁😁😁😁😁
hahahahahah koma madodza ake enaena eeh kkkkkkkkkkk
😂😂😂
Ngozo sadzatheka pa usavar umayitha bro kkkkkkkkkk
Nsomba inamumezabe Yona ija ilipo mwati 🤣🤣🤣???
Ndie thumba la 15 000 la mango lalowa mmenemomoo eti 😅😅😅?
🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Naye sangie pofika kulikhulupirira bodza loonekeratu ngat limenero... Chiripo chomwe naye amachita
Lol, hahahaha, Yona
Koma ngozo iweyo bola lisakuthele banjalo bodza waonjeza
Hahaha mpaka kumezedwa ndi nsomba
Kkkk koma ndafwa ndi kusekatu 😂😂😂
😂😂😂nsomba?
😂😂😂😂😂😂😂
😂😂😂This is hilarious
😂😂😂😂
Sangie 😂.
Ati somba🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Aaaa aaaa😂😂😂😂😂😂😂😂
Ubwela liti kuno ku mozambique?
This is not well organized😏doesn't even make sense
🤣🤣🤣🤣🤣🤣
🤣🤣🤣🤣