A Samuel Lwara Akufotokoza Zifukwa Zimene A Kabambe Anawinila U President Ku UTM

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 2 ธ.ค. 2024

ความคิดเห็น • 24

  • @williamSaka-ep1qz
    @williamSaka-ep1qz 12 วันที่ผ่านมา +2

    Thanks u my brother very much

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 12 วันที่ผ่านมา +1

    100 percent Mr lwara ndipo ndimaona choncho nane.❤

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu 12 วันที่ผ่านมา +2

    Ndipo mr. Kabambe ali fit komanso amatiuza njila zothetsela mavuto ali mu Malawi. Ali ndi mfundo zabwino

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule 12 วันที่ผ่านมา +2

    Good Messnge ❤

  • @LinlyMatheweKufakwina
    @LinlyMatheweKufakwina 12 วันที่ผ่านมา

    Good message ❤❤❤

  • @billymhoni9527
    @billymhoni9527 12 วันที่ผ่านมา

    True Lwara....speaking Kabambe anapanga campaign ya Fundo....and angovomereza...

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 12 วันที่ผ่านมา +2

    Munthu uyu kabambe muli usogoleri

  • @paulbanda9638
    @paulbanda9638 12 วันที่ผ่านมา +2

    I support you

  • @IsaacBwanali-m8c
    @IsaacBwanali-m8c 10 วันที่ผ่านมา

    Tchaya Nganya

  • @frezarphiri3480
    @frezarphiri3480 11 วันที่ผ่านมา

    😂😂😂 iwe luwala uliwazelu kuyankhula chilungamo kabambe ndikatundu

  • @JamesChiphwanya-m4v
    @JamesChiphwanya-m4v 12 วันที่ผ่านมา +1

    koma kumamvomeleza zomwe akuyakhulazi ndizoona ineyo sinadyepo ndalama ya kabambe olo tsiku limodzi ndipo sindimamuziwa koma kabambe amaonesa kt olemekeza anthu omvutika

  • @LucyThambo
    @LucyThambo 11 วันที่ผ่านมา

    Inenso ndimaona choncho

  • @isaacchiwaula731
    @isaacchiwaula731 12 วันที่ผ่านมา

    Aaa iwe ndie kubwera lero apa nkumaoneka ngat wanzeru?? Zopusa zakozi ukuuza ndani? Opusa.iweti!!!

  • @Josephiriillovo
    @Josephiriillovo 12 วันที่ผ่านมา

    KUYANKHULA KWABWINO KWAMBIRI COMRADE LWARA AWUZENI ZENIZENI

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 12 วันที่ผ่านมา

    Enawa aaa kaya ukawone fundo zimene amakambq zambwelela zokhazokha

  • @zainabmsusa9054
    @zainabmsusa9054 12 วันที่ผ่านมา

    Zowonadi mukunyozana mulibemo phindu amawonjezadi asadabwe ndikuluza kwawo

  • @ChristopherManase-s1f
    @ChristopherManase-s1f 12 วันที่ผ่านมา

    Anabela zisankho uyo. Sizingatheke kusiyana ndima figure ngati amenewo. Akuti wapanga zonse,ndi Namalomba. Muona utm ikulowa ku dpp soon.

    • @RosinaPatel
      @RosinaPatel 12 วันที่ผ่านมา

      Muli ndi umboni?

    • @Josephiriillovo
      @Josephiriillovo 12 วันที่ผ่านมา +1

      Eti eti kabambe anali ndi zimfundotu ubwelele ukamvele mfundo za kambala,kaliati and mtumbuka nde utenge za kabambe uyike apo.
      Campaign ikakhale yongodandaula zamtundu wanji kubera ndi landslide aaaaa amwene palibe zovuta apaaaa delegate ndi munthu oopsyaaa

    • @LinlyMatheweKufakwina
      @LinlyMatheweKufakwina 12 วันที่ผ่านมา +1

      Zaziii chilungamo kuwawa imwani madzi mupume Kabambe 2025 Boma❤❤❤❤❤

    • @ElizabethMulinde
      @ElizabethMulinde 11 วันที่ผ่านมา

      ​@@Josephiriillovokoma ndipo Nde muve amtumbuka akut ine ngat anandivotera ku Nigerian inu ndindan kut musandivotele matama thoooo😂😂😂😂

    • @Josephiriillovo
      @Josephiriillovo 11 วันที่ผ่านมา

      @ElizabethMulinde matamatu EEEH