That’s what happens when u have a clueless govt……koma u will still see someone akukuwa ati boma ndi lomweli! Malawians let us trade carefully come sept, izi zomanamizidwa ndimaphulitsa kaye zithudzazi is a lame excuse……😡
Ana ama 2000 akuononga zinthu. Anaononganso kwambiri ku Nachitheme Secondary School ku Ntcheu. Ministry of Education mpofunika akhwimise ndondomeko za discipline mma school.
Ngati mmene inkavekera Times TV mu ulamuliro wa DPP. Ankadzudzula zonyasa za DPP en anthu tinkaona ngati mnga MCP,lero zatembenuka. Munva nkodzo wapyoooo. 7 months to go
Wabwino sakhalisa koma mr kaila mumagwila bwino nrchito....ambuye akuyemdeseni......bwino boss👏❤️
APM my vote 💙 💙💙💙
Kumalawi anakonza ndithu💙💙 my vote
Big up guys for always being there standing for the truth
The blues woyeeee
Boma ili likuzunza anthu😢 imagine 25Billion komatu akuluakulu uyu amayenera kuti azipita tatopa naye
Osati kupita akufunika angoferatu plz ambuye 👏👏
Mcp out of gavernment
Programe ili sharp iyi continue doing it beta
Keep it up guyz
Keep it up mibawa gwedegwede ikumatipasa phunziro
APM
My vote
Mumatha inuyo gyz ❤
😂😂zonse zili mwa iye maphunziro,malakhulidwe ,maonekedwe
Kkkk😂 ati kuseweretsa mbamu kkk koma selina.
Inu a overtnGolomba mumafuna kuti azinena cha chani....? Stv ndi Selina pitilizani kung'alura zandalezo...
A name inuyo musazafe or kusowa inu isakhale mbali yanu big up
Kkkkkkkkk mibawa 🔥🔥🔥🔥🔥
Mzipatala mukungopezeka KULERA ekha kkkkkkk ati boma ndilomweli🤸
Chakwera mboleyake anapha chilima
Ati boma ndi lomweli za ziiiiii
Mwabwera ngati coming
Ndizija anachotsa Tecnobrain, ndikubweretsa NickChakwe, ndikumapanga ma fake passports. Shame
Koma kunkuyu akuva izi ndimakanika ake aja
❤❤❤❤
Dpp woyeeeeee
Yes MCP must be alert 😂
Bip up Mr Kaira....
Ndiye amalawi ndimawadziwa
Kodi Steve sunkalongosoka chifukwa cha chidzanja nkhoma uja?
Gwede gwede yalowa ndale panopa aaaa munali bwino kumbuyoku koma panopa ndale zokha zokha
amangokamba nkhani mix zokhuza ndale pot owulutsa mawu koma alibe mbali yeniyeni cuz amatha kubaya mbalizose komwe kwagwa nkhaniko alibe kut uyu ndindan, so inuyo yaleroyi chabe yangobaya mbali yomwe inuyo mmayikonda nde kufotokoza kwawo kukutsutsana nzolinga zanu
Yalakwaso chiyani gwedegwe abale😂😂😂yabaya poti Boma lalandidwa katundu😂😂😂😂😂odiiiii ukooooooooo
Mmafuna azikamba zabodza?
Why don’t you talk about MBC if you don’t like it then leave
@dalitson3558 yes awuzeni kuti azikambaso za MBC,,,bwanji imangochemelela chakwela basi kkkkkkkkk khalani ndi manyazi
💙
Tikamati boma la buli ndiye la Achakwela😂😂😂😂😂Ana achikangawa ndiyemwati Boma ndilitilo??Boma kulandidwa katundu😂😂😂😂😂😂😂😂koma ku Malawi kosangalatsa
Kma kwamtere eeeeeee2 ai ndithu
Ndipo akugawa mokondelaa kwabasi always kumwera nd pakati n not mpoto kaya akugawako ndkmnee adzavote kaya
President Chakwela ndichitsilu kwabasi, Galu wamunthu osakonda anthu adziko la Malawi. Munthu opanda Mzelu m’mutu mwake muli Phala lokha lokha , munthu wanzelu zake sangalolere ADMAC kuti ithe choncho
Programe yanu ili mbambande mumatha kusukuluza khani kwambir
Musadzafe muzangosowa inuyo mumatha,Ulemu wanu
1 million job yasanduka 1 million yochosedwa ntchito anthu
😅😅
Kkkkkkk boma boma lopusa
That’s what happens when u have a clueless govt……koma u will still see someone akukuwa ati boma ndi lomweli! Malawians let us trade carefully come sept, izi zomanamizidwa ndimaphulitsa kaye zithudzazi is a lame excuse……😡
athu osadziwa chomwe akupanga awa munapasi udindo mbutumwa
Mulungu azikudalisani nonse
Kkkkk onekabwino
Ulamu wanu
😂😂😂🎉🎉❤
Ndife a DPP ndipo gwedeg gwede ndi a dpp
Ankasokoneza ndi chidzanja nkhoma uja kkk
Mbambande
Mumatha I nuyo
Umakwana guys
ok
Ana ama 2000 akuononga zinthu. Anaononganso kwambiri ku Nachitheme Secondary School ku Ntcheu. Ministry of Education mpofunika akhwimise ndondomeko za discipline mma school.
Awa asaname or kuti akavote ndi a DPP amasapota pitala
Mmene alili kasakula uja ndiwa mcp
Asaname ndichani? Chilungamo chakupwetekani Pali chamzeru chomwe akupanga munthu wanuyo?
Ķkkkk kwa Mtele motu za mvuta
Nde ndan opanda nzeru yemwe angavotere Chikangawa?
Ngati mmene inkavekera Times TV mu ulamuliro wa DPP. Ankadzudzula zonyasa za DPP en anthu tinkaona ngati mnga MCP,lero zatembenuka. Munva nkodzo wapyoooo. 7 months to go