Koma bakili muluzi TV kod ndingazakuwone ndi maso angawa ndipo ndimakhumba nditakhala your gud chilungamo Kaya ngt chani big up boss mumatiwunikila inuyo
Quite on point bro...Your observations are at another level...keep on exposing this visionless government...My plea to fellow Malawians is that let's not just listen to these messages but let's extend them to the local man who is at grassroot level and an easy prey for this autocratic gvt...Let's equip our fellow citizenry with the necessary knowledge by using whatever means so that when 2025 comes,this gvt may be shown an exit door...
Kkkkkkkk😂😂😂😂😂😂nyerere zimaposa chakwera ndi boma lake, ndipo saganiza chakwera, ndipo amaiwala kuti dzulo analankhula chiyani, vuto ndi bodza basi , madanje a boma amenewa, si noma ili ai
Zowona aise like me I'm really tired in South Africa i need to go home I wanna get married but I'm scared of this Garvement lust year i was soppose to leave but still I'm here Maitland cape town bcz of this person i hate these people
Big-up Bakili Muluzi TV
Reality of life
Eeeeeeeeee Koma ambuy pitilizan kutiululila zachinsinsi kudzela mwa pule
Chakwerayi zimene zikupanga iyi kumalawi akudziwa ndimulungu basi monga ineso ndamutopa nawo kwasalaku akufuna angotimaliza never give up big brother
APM my vote
Uyu sangawine uyu
Number one journalist
Exactly these is true boma ili palibe chabwino tilidi kubagamoyo
Koma bakili muluzi TV kod ndingazakuwone ndi maso angawa ndipo ndimakhumba nditakhala your gud chilungamo Kaya ngt chani big up boss mumatiwunikila inuyo
Umakwana brother pitiliza reality yomweyo❤ anthu akukonda ukatelo
Brother iribwino keep it up my vote for APM
From south Africa ndimakunyadiran big
Ulemu wanu big God bless you
Nyelele imaganiza kuposa chakwela😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂💪💪
kikikikikiki ziliko
😂😂😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂Ndipo akunenadi chilungamo brother 😂😂
@@RiteRoderick kwambiri kwake😀😀
Ulemu wanu brother we know so many things form to bakili have ur bless and more life ❤❤❤❤❤❤
Boma ilili litizunza.
Will say thank you mr BM tv
Nyerere yomweyo
Zisilu ndizomwe ndizomwe zimasusa koma umayakhu zoona ndi zonwe zikuchitika
😅😅😅😅😅😅😅😅 nyirere part impressed me 😅😅😅😅😅😅
Really bg boss iweyo makwana nditu tili mavuto oopsa dziko lino srs
Mbuzi za anthu awa ineyo ndye ai sindikuwafuna anthu oipa awa
Nyerere yomweyo😂😂😂
I love this TV siimasekelerayi zoputsa❤❤❤
Ulemu wanu big man
Quite on point bro...Your observations are at another level...keep on exposing this visionless government...My plea to fellow Malawians is that let's not just listen to these messages but let's extend them to the local man who is at grassroot level and an easy prey for this autocratic gvt...Let's equip our fellow citizenry with the necessary knowledge by using whatever means so that when 2025 comes,this gvt may be shown an exit door...
Big up bakili TV
inuyo mumayakhula chilungamo chokhachoka great job
We really trust your research ! keep it up bro.
God bless you bigy you make US know the truth ❤❤
Ulemu wanu big ❤❤❤
APM my next hope
My best television ❤
Apm my vote
Zilikotu😂😂😂😂😂....more fire BTv❤❤
Kubwelenso a pioneer
Thanks for updating us brother
Zoona big a kutiwonelera koma akhaula chaka chamawa
Amalawi zofuna izii 😅😅😅😅😂😂😂
You're most welcome brother man!!
Great job Mrs
Iwe ndimaso ammalawi aise. Umakwana pitilizanaise mwaiwe tizapedza tsogoleri weni weni
The true and professional journalist
No bro...He is always biased against MCP.. in short He is a DPP cadet maybe you havent seen yet
Big love brother ❤❤
❤ You bakili muluz
Bakili Muluzi is my best channel
😢😢 Malawi akuwawa🙌
Kkkkkkkk😂😂😂😂😂😂nyerere zimaposa chakwera ndi boma lake, ndipo saganiza chakwera, ndipo amaiwala kuti dzulo analankhula chiyani, vuto ndi bodza basi , madanje a boma amenewa, si noma ili ai
Big up broh anthuwa atipusisa😢
atitu Nyerere mbuzi chakwera
Zitsiru zawanthu ngati Achna chakwera ndiboma lake sinawone mmmm ayi
mumaitha bigy keep it up
Chakwera ndiwakuba straight 😮
Ulemu wanu Big man
Big tiuzeni mene zikuyendera Ku Senegal zankhani ya nyamata amene akuopedwa ndi boma ousmane sonko zili pati Wa wina chisango kapena ayi
Be blessed brother ❤
Kodi anthuwa ndi mzikadi‼️‼️mene akutumila dzikolitu ngati sakhala dzikolitu mavuto ali mbweee
Osangomuombera Mutu bwanji ameneyi ,,tizichita kuopa kubwera Ku Malawi chifukwa cha galu ameneyi
Zowona aise like me I'm really tired in South Africa i need to go home I wanna get married but I'm scared of this Garvement lust year i was soppose to leave but still I'm here Maitland cape town bcz of this person i hate these people
Mashop akuno ku RSA akupezekanso sugar wa kumalawi 😂😂😂
Wandikumbusa pa a pioneer pa unayiwalanso a youth zinali mfiti za anthu iweyo simunthu wamba tikufuna anthu ngati iwe.
Anthu awad ngopenga...... best TV
Inuyo basi tinavomeleza kale za inuyo big man
Ur the best man all the time
Mutu mwakedi muli mphusi ndi mamina kkkkkk umakwana
Thanks for the video we have been waiting for this boss continue to give us the best
You are very true man Allah give you more knowledge
Big umakwana Ku bakili muluzi tv
Umakwana iweyo!!!😂😂😂😂
Eish koma ndiye nyeleledi❤❤❤😂😂😂
Big up bro timakunyadilani
Big up bro
Kkkkkkkklkkk koma mchimwene iweyo mantha ulibe
😂😂 Big mmati imilila chakwela amadwala mutu wanantogwe
Following 😊
Ndipo m,busa ameneu mulungu amuone ndithu
😂😂😂😂😂😂 Mmm kom bakili mulusi😂😂😂
Ndi zoona chakwera afuna anthu adzimugwadira ngati iye ndi mulungu
Ndizowona big
Well said ❤
Chakwera ali nga zipatso za mkuyu okhala ndi nyelele mkati
Ndigalu ameneyo chakwela
Panopa waitress yomwe ikutiziwisa zammbuyomu, za pomwetikuyendera ndi komwetikupita, ndi Bakiri muluzi 📺 🖥 basi❤😂❤❤
😂😂😂Iponden fadah😂😂😂
Ndee mwati nyerere ili ndizeru kupotsa chakwera😂😂😂zoonadi inenso ndavomereza nazo.
Chakwera ndithu ndi mbuzi yotheratu
Musongoleli wopanda nzelu uyuu Lazarus chakwera
Ukungozuza anthu
Adaa awa ndiwachipomgwe kumango tokota tulukani anthu akuoneni kunyoza❤ nsanje sizikuthandizani kumalawi Kuno iwe lomwe osokoneza komaso wamoyo oipa udziwe zimenezo ndiwe Santana pawekha or zomwe umapanga iwe kapena kulankhula ndiza satanic Malawi sili Ngati iwe udapusa nyani iwe
Mmmmh
Ndipo man Chanel iyiyi ineyo imandinyasa uthokoze kuti chakwera ndi m'busa DPP unakasowetsa
kkkkkkk akadapita kale wamoyo ndiwachibwana akusapota anthu ozunza komaso kupha malubino mopanda chisoni sadzalowaso agaru amenewa UDF kulibe inatha DPP yathaso kuwina MCP kosayamba
Mmm akulu yamula ndi sanje
Mcp ndi zitsilu za anthu machende awo
You are the best
Keep it up broo
Vote yanu zaziiiiiii amphawi inu
Big man inuyo mumatha
Manyaka boma la MCP
Ambuye tithandizeni kuchosa chilombo Chimenechi tatopa ndi kuvutika ife amalawi
Pulezident ovetsa chison😢😢
Boma lomvetsa chisoni
Chakwela atuka next year mulungu Alipo pite mutalika alowa iyeyo olo atanyengelela bwanji kulibe
Munthu wanzeru amayang'ana zipatala, ndende, amasiye okalamba,makanda ndiye chifundo koma awa kugawa ndalama chifukwa ndafiti
Nanga Sam Kawake zoti dziko likolola zochuluka anadzitenga kuti????...amene anamuthandiza kupanga ma statistics amene aja ndi ndani???
Sewero la achakwera kkkkkk
Iweyo chakwera Malawi siinatuluke kunyini kwamako kuti uzingopanga zomwe ukufuna tikukudxiwa bwino lomwe kuti unali mphawi omvesa chisoni lero waba usogoleri nkumasowa ndalama nkhati ndiiwe dolo pomwe kunkha panyo 😢😢😢😢
Nkhululukani amwene
Koma nakuda kwambiri Ndipo amayi mimba ya iweyo bola akanachotsa
Mbambande bakiri muluzi TV