Kamlepo is not just an ordinary person but person with vision even when he was speaking through channel Africa before multiparty reflect on the land he has always stand for the truth 🤝🇲🇼
I remember Hon Kamlepo Kaluwa being the first person to speak against the regime of one party state of MCP from Radio RSA kalelo chifukwa chake mpaka pano amayankhula za Nzeru
Thank you mr. Kalua for your explanation. A MCP akuti Peter wakalamba pamene iwowo adavola Kamuzu at 95 yrs! George Kasakula wa MBC ndi chitsulu cha munthu.
Kamuzu anali 100 something yrs not 94.Ndimachokera ku Malawi m'boma la Ntcheu koma Chihana and Kamlepo mumayankhula zinthu za nzeru regardless of wat pple say.
chisazo chabwino nda atupele muluzi wagwira ntchito ndi mayi joice banda and peter muthalika tawonani lelo atupele ali mundanda wa anthu 100 mu africa ali ndiwutsogoleli wabwino
Unfortunately the constitution was flawed in the sense that it gives the president a lot of powers. The clause that protects the president from PROSECUTION ought to be abolished.
But he also failed to take us to Singapore. On the economy MR Kalua, what did you have in the north? And why are you, thinking its wrong for Chakwera to pull these institutions centrally where they can easily accessed by all. Here you do not have a point in my view
Mr kaluwa you are very humble Man,is not easy to speak the goodness of someone, Malawi is full of jealousy God bless you sir
Kamlepo is not just an ordinary person but person with vision even when he was speaking through channel Africa before multiparty reflect on the land he has always stand for the truth 🤝🇲🇼
❤❤ Ulemu wanu Mr kaluwa
I remember Hon Kamlepo Kaluwa being the first person to speak against the regime of one party state of MCP from Radio RSA kalelo chifukwa chake mpaka pano amayankhula za Nzeru
Ambuye azikudalisani akaluwa❤
Thank you mr. Kalua for your explanation. A MCP akuti Peter wakalamba pamene iwowo adavola Kamuzu at 95 yrs! George Kasakula wa MBC ndi chitsulu cha munthu.
Mr kaluwa Thank you for sharing
Watching from south Africa and this is real,thanks hon kalua for your clarification
Congratulations 🎉
Big man Kaluwa
Iwensotu ukuonjeza ndizamakalala akoz tikusikatu this colour change bring back the old one
Tsoooooo kuwawa 😂😂
Thanks alot Mr kamulepo kaluwa
Kaluwa mumakwana hevvee
Chithupsya party zikuwawatu olo asakudzinvetsa kuno ku mchinji mcp takana
akaluwa ndimuthu wa mzelu kuchokela kale kale kuli kamuzu
Kamuzu anali 100 something yrs not 94.Ndimachokera ku Malawi m'boma la Ntcheu koma Chihana and Kamlepo mumayankhula zinthu za nzeru regardless of wat pple say.
Ulemu wanu akamlepo kaluwa
chisazo chabwino nda atupele muluzi wagwira ntchito ndi mayi joice banda and peter muthalika tawonani lelo atupele ali mundanda wa anthu 100 mu africa ali ndiwutsogoleli wabwino
Kamlepo Kalua machine
Unfortunately the constitution was flawed in the sense that it gives the president a lot of powers. The clause that protects the president from PROSECUTION ought to be abolished.
Constitution is not rigid boss it can always be amended, we are talking about its commencement here you have parliament that can always amend.
Mbuli zikudana nazo 😂kafufuzeni nokha ngati azibuyanu adaphunzira😂machine Peter, sibulutu
Who chose Chilima as Vice Presidential candidate? Is it Peter or Bingu?
Peter
Zazii
Kumva tsooooo 😂
Chitupsa party 😂😂😂😂 pitani ku MBC ngt mukufuna zachikangawa
Tsirani sugar ndi nchere kuti zikukomeleni
Kenako mutafune Ginger kuti bp itsike 😮😮
Zotentha mzithupsya eti
Zako zimenezo
Uyu akunama mcp simungachose boma 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
KWAMENE SIMUKUMUMVETSA KALUWA KOMA AKUYANKHULA CHILUMGAMO NOT KUTI KUMUKWEZA PETER 😅😅😅😅
Basi nkhani yonseyo basi kukweza munthalika muntengo basi zaiii akamulepo munatha inu basi tozinva zofoyilazo naweso wandevu ngati yudasi
Kapange yako iyi ndi ya DPP
Kumva buuuuu kuontcha 😂😂😂😂😂
😂😂😂😂
Lilime
Tulukani mu uvuni mwatenthedwamo 😂😂😂kumva chizungulire komanso kuwawa
Kuti tsoooooo ngati mwadya piri piri
DPP WOYEEE
UTM WOYEEEE
But he also failed to take us to Singapore. On the economy MR Kalua, what did you have in the north? And why are you, thinking its wrong for Chakwera to pull these institutions centrally where they can easily accessed by all. Here you do not have a point in my view
At least we have foundation of mombera university kusonyeza Kut anachotsedwa pampando ali ndi chidwi chomanga koma awa apanga chan kumpoto?
Congratulations 🎉