ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Royalty to the party and not the people
Chilima simungamuthe Mwachepa Kauzaneni
Mbava yachabechabe
This figure pointing on the other it shows that all the parties know where this noise is coming from and why.
Nkhani siyamgwirizano koma yobela dziko.Achilima ayimikidwa chifukwa katangale ndi satar.
choka iwe palibe ukudziwa iwe Za Ndale
Lero akukana zoti sanasainilane
Ndinene mwambi monga amanenera a vice presidente: Ngoma ikariritsa sikharila kungambika
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Kikikikiki
Koma a UTM akanangotulutsa chikalata chimene chinasayinidwacho
Mkaka ndi satana uyu,bombocrat
Palibe wanzeru apa ayelakotu amkaka kudakonga mumtumbo kuja ayelako ( nungu nungu amwene 😆)
Years later mhu
Apa chilima akuziwa chifukwa akufuna mphanvu za a president zichepesedwe. Nde kuti nkhani ya a sattar a president a kuyiziwaso mwinanso ikuwakhuzaso.
Koma Chilima atakhala President angamabe ndalama zingati pa chaka ngat akukwanisa kuba ali Vice president kikikikiki
Ameneyi ndi abale aguputaz akumalawi 😄😄😄
Uzifusa mafuso eni eni ka.awo panopa akhoza kutero chifukwa akuva kukoma
Chilima ndi dolo angofuna kumuipisila mbili nkhani siyoona zangolowa ndale, panyapake nkakayo
Chilima ndimbava yachabechabe
Anakubela chiyani Umalipila msonkho iwe
@@cadohjabu5565 ndine mwini wa ma truck omwe anandilandauja
Olo aneneziwona tilibe Naye ntchito ndi wakuba chilima
kagwere uko anakubela chiyani
Ndiamizala awa there even dnt know what to speak
Aliyetse obadwila mu democy azitamandila zomwe zikuchitika panozi.koma apiyetse obadwila mudzaka zimeneso ayenela kudziwa bwino lomwe.democracy ndikuba ndikudzitamandila.tikudziwa komwe tachokela koma komwe tikupita sitidziwa.kaya akunena zoona kaya zaboza.the main point is,ukaba waba chifukwa udindowo unaukhumbila kuti ukabe osati kuthandidza amalawi.bvuto la amlawife,timaombela mania zilidzonse.ndichifukwa zikoli linagulitsidwa kwa satta mwenye uja.chifukwa amalawi tidakali mu konono mpaka pano.kumakagangalika ndikuthawa ziko lathu.kukakhala kumaiko ena.