Can you imagine? What is it going to do with us about his cries? Why didn't he just ended the alliance since he had all opportunity to end it right there? This boy is just useless! Kkkkkk
Let the angels realise over Malawi. Ws declare unity, peace and safety. I will continue praying for Dr. Saulos Chilima. You deserve better. Its better to remind Tonse Alliance where you started. God bless you my honorable VIP. Stay bleed.
Mwayakhula zamveka, km inuyo kupusako mwazipusitsa nokha... poba ndalama za amalawi omwe lero lino akusowa ndalama yogula bonya. Ine nde ndakutulukani bas
Why are you insulting the vice president? He didn't insult you? Why are you so abusive with mal language? There is absolutely no need for insulting Jim bcoz all he is stating here is about the agreement which they discussed and agreed as a coalition government? Why kutukwana? Its not a wise idea kutukwana months wa mkulu.
Uyu asatipusisepo apa 2 years yoseyi anali kuti? Lero akubwela ngati ali care ndi Amalawi liliboza chipanda kumutchula pankhani ya sata sibwezi akutiyankhula lero. Galu wachabe chabe uyu😂
Don't take Malawians as stupid people. Don't bring your coalition issues now. Tell the Malawians where you get the money to buy those cars if you are not involved in corruption. Ndithu zoona mankhwala akusowa mzipatala inu mukuba ndalama.
Chilima ndi mbava yeni yeni. He is talking about their coalition nobody was there. Azikamba za katangale yemwe iyeyo ali mkati. Chilima akutola aMalawi ngati ndi zitsiru. Kuba basi.
Ife tikufuna kuva nkhani ya Kuba ndalama za malawi osati lelo nditsogola ndine mawa udzatsogola ndiwe za ziiiii ife tikufuna oba nkhuku atuluke ku jail kulowe oba ma million
@@dawahlilamastaubi1423 Izizi zomawatchula atsogoleri mayinazi ndi zolakwika. Ngati Papayo ali wabwinobwino bwanji sanasithe malamulo akuti papa asamakhale immune ku mirandu. Enafe pochonga tambala wakuda simkawona MCP. I am a Chewa but I cannot vote for a party that wanted to kill my mum called MCP. My mum had wounds for being beaten by MCP. So that is why I say I voted for them because of Chilima. Chilima is a human being and he has his weaknesses but don't underestimate us his followers. Even now his speech has brought back many of his followers.
@@cadohjabu5565 man, kikkkkkk hahahahahaha! Birds of the same feathers flock together! I was told not to argue with people like you hahahahahahha! Check commentators what they have said about you Boss my man! Oh Boy!
Kodi za mgwirizano anthu anayamba Kale kunena kuti mwauze za mkati mwa mgwirizano koma osanena nthawi yonseyi nde lero mukutiusza pakati pa nkhani ya data kuti mukukhuzidwa bwanji nde nkhani ikufunika apa zikomo
Koma chilima ndi munthu opanda chosini ndi mtundu wa amalawi sangayime kuyakhula lero koma palibe chimene mungakhule inuyo anthu ndikumva palibe chimene tingamve anthu amene amakutsatani ndi zitsilu komanso opanda Malawi panopa tinachangamuka osati nga mwakale iwe saulosi choka pampando wa vice president chigawenga ndaramazo ubweze kuti amalawi apume ndikutsawuka chitsilu Galu iwe komanso ulibe mfundo mtundu wa amalawi sanamve kena kalikonse chimene wayakhula lero mbamva iwe kufuna kulemela basi mulungu akulanga chifukwa amalawi kudandaula kwa mbiri
Show support ❤. Like and Subscribe for more 🇲🇼.
Zovuta. I used to like the guy. Not anymore. He didn’t even deny the allegations. He thinks he should be immune because he helped to win elections?
Can you imagine? What is it going to do with us about his cries? Why didn't he just ended the alliance since he had all opportunity to end it right there? This boy is just useless! Kkkkkk
Wait u will know the truth
Let the angels realise over Malawi. Ws declare unity, peace and safety. I will continue praying for Dr. Saulos Chilima. You deserve better. Its better to remind Tonse Alliance where you started. God bless you my honorable VIP. Stay bleed.
M'maso motuwamo
Chilima ndi number 1 or zitavuta bwanji sindizamusiya ine 💪💪💪💪💞💞
Ndye munyatu agalu inu I think mukudyera limozi chilima ndimbava ndye Kuti iwenso ndimbava
Basi kumasanglla nd mbala iyi
Chilima ndi mbava ine ndiwa chakwela
Anthu akuba kuchenjera pakamwa...
Mudzafa ndi uphawi kupusa
Kupupuluma uyo, nzeru alibe, komanso no vision uyu.
This is senseless and useless press briefing, this man is the cause of all misery Malawi is facing today , he has porridge in his head
Koma zimenezi zikugwirizana bwanji ndi ndalama zomwe wabazo?
Mwayakhula zamveka, km inuyo kupusako mwazipusitsa nokha... poba ndalama za amalawi omwe lero lino akusowa ndalama yogula bonya. Ine nde ndakutulukani bas
Garu wachabechabe iwe ukazatinyozeraso president tizakumanga...ndalembane ndiwa police
Why are you insulting the vice president? He didn't insult you? Why are you so abusive with mal language? There is absolutely no need for insulting Jim bcoz all he is stating here is about the agreement which they discussed and agreed as a coalition government? Why kutukwana? Its not a wise idea kutukwana months wa mkulu.
Chilima is not a helo iyeyo Peter analiso wofoyila leloso achakwera akhaleso wopoyila ? zitithandizaji izi
Zachamba Amalawi mukutiwona ku pusa eti? How dare are you chilima?????????
Agreement yanu ya 5 years, inali yoti wina akaba 5 years winanso abwere adzabe,ndizomwe akutiuza apa,ndimaona ngati akufuna ķutiuza zoti anaba naye Sattar koma akuthawathawa ,afanawa ndi opoira kwambiri akutitenga ngati sitikuona ndipo sangakhale president
Kkkkkk
Koma ndiyeee... Nanga dzutukula dziko....
Aaaa mmene akubelamu zimadabwisatu kuti muchipatala mungasowe Panadol osaziwakuti anthu angopakulamo
Kkkkkk
Kkkkk 🤔🙆 🙆🙆🙆
Uyu asatipusisepo apa 2 years yoseyi anali kuti? Lero akubwela ngati ali care ndi Amalawi liliboza chipanda kumutchula pankhani ya sata sibwezi akutiyankhula lero. Galu wachabe chabe uyu😂
Don't take Malawians as stupid people. Don't bring your coalition issues now. Tell the Malawians where you get the money to buy those cars if you are not involved in corruption.
Ndithu zoona mankhwala akusowa mzipatala inu mukuba ndalama.
You’re right Tomas, this guy is dull. He thinks he knows everything and can fool Malawians.
Chilima Malawians are not fools
Sadziwa chimene amafuna uyu
Why ?
Why does all this start at this moment? A Chilima should stay in his office.
Chilima ndi mbava yeni yeni. He is talking about their coalition nobody was there.
Azikamba za katangale yemwe iyeyo ali mkati. Chilima akutola aMalawi ngati ndi zitsiru. Kuba basi.
Simuzakhala president wa malawi inu forget ndinu wokoma poyakhula munalikuti kale kuyankhula please osapusisa wanthu.
Zowonadi
Live ndichisilu ameneyi
Uyu amalawi akuwaonangati zitsilu kwambili
I know that chilima ll never be president in this country
A year later we here, may he rest peacefully 😢
@@matshepokhosa234 phuma ndilomwe lawapha kuthaagila zithu thawi isanafike. RIP
Chilima is my vote
Ndiwe chisilu ngt chilima ali vote yako
Wasowa womupatsa voteyo
Chizungu chimenecho eti?
Olo ndi 1kwacha yomwe sanakugailekonso.
Mr mbava chilima 🎃
Winiko asowatu why?
Kumenyanako muzimenyana Koma ife a Malawi zisatikhuze mumenyane mene mukudyela ndalama bomamo chifukwa ife a Malawi tikuvutika ndikale
Nkhani ndi yakuba pulayala abwera bwanji😅😅🤣🤣 linali funso la malemu zakaliya🤣
ndinu okula mtima ifeso tmaona ngat muyankhulatu nkhani za zunneth sattar
Akuchita mantha kt 2025 poeple will nt be able to trust him, kkkkkkkkkkkkkkkk
Ndipo kuzakhala kuinga mbava zonse zomwe zibisala mma office mu
Zimaulemu vip
Kwa omwe mumalankhula mbwerera mwaona zomwe amatanthauza Chilima zija????
Olo mutati mvoteso ndani angavotera mambala iwe
Ife tikufuna kuva nkhani ya Kuba ndalama za malawi osati lelo nditsogola ndine mawa udzatsogola ndiwe za ziiiii ife tikufuna oba nkhuku atuluke ku jail kulowe oba ma million
Eti eti akungonjanja ngati tennis ball zazi achilima here you missed the point to tell us Malawian
Zigawengazija zikufuna zichapane
kkkķkkkk makawi uyooo
Ada awa ndikathyali
Blow fire....we are strugglin Guyz
..a one man shut down shit
Fundo yanu ilibwino big boss
Galu wachabe chabe, chitsilu chokondedwa nd zitsilu zi nzake
Lidayamba liti dziko LA malawi kukhala lokongola
The tension is growing 💀
okumba mbuna azagweramo yekha izo ndizomwe malemba amanena
Mutha kudzudzula Chilima koma kumunyoza ndikulakwa. I voted for him. So I respect him. Enanu simukhala ku Malawi koma mumalankhula xopusa
Ndi Galu uyu satana wachabe chabe
Ineso navotela chilima
iwe ndi nkhuku
@@dawahlilamastaubi1423 Izizi zomawatchula atsogoleri mayinazi ndi zolakwika. Ngati Papayo ali wabwinobwino bwanji sanasithe malamulo akuti papa asamakhale immune ku mirandu. Enafe pochonga tambala wakuda simkawona MCP. I am a Chewa but I cannot vote for a party that wanted to kill my mum called MCP. My mum had wounds for being beaten by MCP. So that is why I say I voted for them because of Chilima.
Chilima is a human being and he has his weaknesses but don't underestimate us his followers. Even now his speech has brought back many of his followers.
@ Patrick these people are bias tikuziona zinthuzi mosiyana
This man was honestly and genius ❤ but arrogant, gridy and selfishness among MCP party are not realistics
Ndikukhulupirira kuti panopa anthu azindikira kt MCP inali yakupha ndipo munthu uyu amapilira
Malawi always problems this is too much
😢
This guy got Pride , 💔 Chitsilu.
Iweso chitsilu
Ndi mbuzi
Ndiposo asalakhule mwachidure ayi kodi katangaleyo ndi iweyo kaya
Me here right now feeling sad for my country- Rest in peace
You went through the comments too huh😢😔
Nanga zokumana mu church mwa pastor Thom mpakana... Zugwirizana? 😂😂😂
Zeze uyuuu
Kkkkkk akukamba zosamveka uyu
Keep resting in power my Guy
Mwatingwilitsa fuwa lamoto inu 😔
Chakwerao Naye ndi mbava siopempere
Iwe ndigalu kwabas fusek
Lero wina kumakakana ndikupepha Mulungu alowerere
Kicks of a dying horse
Kodi 2063 iweyo udzakhala ulipo?
Akulu inuyo ndamene munapeleka dziko lanthuli manja mwanthu oyipa okupha akhaza okuba agulu, ndipo iweyo Chilima sitizakukhululukira munthu oyipa iwe 😏😏😏😏
💯👌
Takunyadilani vip 🙏🙏
Mfundo zosaiwalika zogwila mtima koma imfa eeee sizoloweleka koma tingoti Yehova oziwa zonse akule ife tichepe
Koma ndiye pandevu. ZotuwApo kuba kkkk
Muyetso omwe unayezela anzako,iwenso azakuyezela omwewo.
Kwachema khwinthi nd I mlili waukulu kwambiri.
Koma zotukwana nde sibwino.lets comment fairly
Belezebulu why you took this man why 😢😢😢😢
Zolembelana zanuzo tilibe nazo ntchito tikufuna Peter mutharika ife inu mwatizuza zinthu zakwela heavy
Awa ndi ndiye aindithu, kutsatila awawa awa ndiye kupanda bongo ndithu!
iweyo ndemene ulibe bongo Aise awa ndi Akamuna Adha
@@cadohjabu5565 akamuna kwa mbuzi ngati inuo. Anthu osazindikira kuti mbava zikukubeleni
@@cadohjabu5565 man, kikkkkkk hahahahahaha! Birds of the same feathers flock together! I was told not to argue with people like you hahahahahahha! Check commentators what they have said about you Boss my man! Oh Boy!
Chilima ndi mbuzi ya munthu, amalawi tufuna atiwuze za katangale komaso atiwuze komwe watenga 3 billion yogulila ma galimoto
2025 tizangoyamba ufumu basi
Kodi za mgwirizano anthu anayamba Kale kunena kuti mwauze za mkati mwa mgwirizano koma osanena nthawi yonseyi nde lero mukutiusza pakati pa nkhani ya data kuti mukukhuzidwa bwanji nde nkhani ikufunika apa zikomo
Koma chilima ndi munthu opanda chosini ndi mtundu wa amalawi sangayime kuyakhula lero koma palibe chimene mungakhule inuyo anthu ndikumva palibe chimene tingamve anthu amene amakutsatani ndi zitsilu komanso opanda Malawi panopa tinachangamuka osati nga mwakale iwe saulosi choka pampando wa vice president chigawenga ndaramazo ubweze kuti amalawi apume ndikutsawuka chitsilu Galu iwe komanso ulibe mfundo mtundu wa amalawi sanamve kena kalikonse chimene wayakhula lero mbamva iwe kufuna kulemela basi mulungu akulanga chifukwa amalawi kudandaula kwa mbiri
Pa ground paipa
Kamunthu koipa aka
Mtsogoleli opanda chisoni mwaba kokwanila
I think this guy he need to fire his advicers they advice him wrong things I don't get anything from this young thug
Galu wachabechabe mbava...mbuzi yodyela amphawi ur time it's over
Where he was after too Long 😁
Wakuphonya utsogoleri chitsiru
My president
Big boy
Umaba yabooka uli ku airtel kuja nde ukayendese dziko iwe mtumbo wako
Umanva bwanji ukalowa nzipatala odwala kumagona pansi komaso kufa posawa makhwala when mugwiritsa poor Malawians tax buying personal expensive cars? Wicked pay back the money
Foseki chakuba,chisisi chakuba msogoleli ndiwe
Iweyo waziziwa liti iweyo kkkkkk kulibe so zimenezo zinachikako kut zolamulila anthu awiri dziko
Chilima remains my hero
What do you mean by saying,,remains? Kikkkkk!
Ok chilima and UTM forevermore
@@isaacchipatala1618 oh yaaa! He has started what he is not going to finish. I wish if he couldn't politicize what was obvious!
Zopanda nzeru mungofuna ku maliza Malawi basi5
Lion❤
Uyelekeze ndiwe galu kwabasi
uyu amatiimba amalawi
Chilima sitidza muiwala
Koma chonde Yehovah Mulungu wathu lowelerani
Inu Ambuye mumati zomwe tapangana pansi pano inuyo mumaziikizira chonde chitani pa izi
Bwana chilima simunakambe kwambili bwanji za katangale???? Khani yavuta ndi yakatengale osati mavoti ai?
Ndikutukwane pang'ono wandinyatsa chimbuyo chako waononga boma
Iwe utsaone anthu kuputsa chitsiru
Kodi mmene adasainiranamo Kodi mmene anamwaliramo ndiye kuti mfundo zapa alayanse yawonso inafa? Nanga 2025 tikafikako bwanji chifukwa winayo akuti aimanso moti ngati inali imfa Kodi sizingatheeke kuti 2025 oyimira kugwirizanowo achokere ku UTM?
Alindi zeluzoputsa uyu akutiona kupepela amalawi ife
Palibe chamzelu ndiwe kape wakuba waboza Palibe nthawi yatha uli ndiphuma lwe ukoza zithu zake zit Amalawi si ife zisilu ayi upeze Zina zochita sitngakupaseso sapoti tiwone Zina lwe basi panga zako lzi zakuvuta 😡
Ulemu akupasani bwanji mukuyamba noka kuzasipasa ulemu muthamangila kubela Malawi tsiku likubwera Loti muzayankhe ndalama zimene madyazo timazipeza. Movutikila
Koma nkhopeyi ikuyankhu yokha kuti something behind is wrong
Ichi ndi chitsiludi basi
Twabu
Chokani apa iwe chakwera nose ndinu vimbava