ไม่สามารถเล่นวิดีโอนี้
ขออภัยในความไม่สะดวก

YONECO ED on Malawi Concourt Elections Case

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 24 ม.ค. 2020
  • Pamene Amalawi akudikila gamulo lochekela ku court pa mlandu okhuza zisankho, anthu ambiri ali ndi nkhawa kuti oweruza azagamula motani chifukwa zitha kukomela ena ndinso ndikusiyana ndi maganizo aanthu ena, zimene zitha kubweretsa kusagwirizana komanso kuzetsa mkwiyo.
    Ngakhale izi zili choncho, ndikoyenera kuti achinyamata komanso aMalawi tonse tilemekeze zotsatirazi. Kupanga ziwawa za mtundu uliwonse sikupangitsa kuti zinthu ziziyenda bwino mu dziko lino.
    Ralph Waldo Emerson anayankhulapo mawu, “Mtendere sungabwere kaamba koyambitsa ziwawa, mtendere umadza kaamba kakumvetsetsana”

ความคิดเห็น •