REPORT LIMENERI KOMA LITITHANDIZA ? ANTHU AKUDABWA M’MAGULUMU!

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 8 ก.พ. 2025

ความคิดเห็น • 27

  • @CharlesChalimba
    @CharlesChalimba หลายเดือนก่อน +1

    Buzi ya m'busa iwe

  • @SelinaMasangwi
    @SelinaMasangwi หลายเดือนก่อน +1

    Abusa mwaiwala Mulungu Kodi zimene munalonjeza kutumikila ndi zimenezo?

  • @VictorChunga-f1g
    @VictorChunga-f1g หลายเดือนก่อน

    Mmmm koma bundle yanga yathad chizungu chandivutakumva😭

  • @MarthaMbewe-uk5nn
    @MarthaMbewe-uk5nn หลายเดือนก่อน

    NO MANYAZI KUKULA KONSEKO?

  • @MusaMatola-r7i
    @MusaMatola-r7i หลายเดือนก่อน

    Tinalakwanji amalawi kumangotinaminsa zakha zonse 4 koma siku linsavika likwana la 45

  • @DamianoYohane
    @DamianoYohane หลายเดือนก่อน

    Kodi uyuyu ndi wa mpingo uti Thawale uy?

  • @AbsalomKambova
    @AbsalomKambova หลายเดือนก่อน

    Izizi chifukwa si m'bale wanga chikhala chilima anali m'bale nditaponya chiphe kalekale kwa agalu amenewa apapa tinganene kuti ndi report or lembetso

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 หลายเดือนก่อน

    NONSE INU MUKUTCHINJIKIZA CHAKWERA PA IFA YA CHILIMA MUDZAKODZEDWA MUKUWONA NGATI 1964 THIS IS 2024 AMALAWIAN ANAPENYA PATALI SIMUNGATI NAMIZE AI OSAVUTIKA NDIKUNENA CHILUNGAMO TINACHIDZIWA KALE CHAKWERA AKUWONONGA NTHAWI CHOTI AZIDZIWA CHAKWERA ALIPAVUTO KWAMBILI

  • @ShakiraDiness
    @ShakiraDiness หลายเดือนก่อน

    Koma muli ndiuzimu azigalu inu zitsilu za anthu

  • @JohnmjigoMalinda
    @JohnmjigoMalinda หลายเดือนก่อน

    Nonse ndinu agalu mudziwe kuti mukagona mawa mufela kutulo

  • @AbdulJohn-t7l
    @AbdulJohn-t7l หลายเดือนก่อน

    Tsiku lizafika anthu awa akubwelesa commission inquiry ya bodzayi mwazola manyi amwini chifukwa inuso muzafusidwa chifukwa chani munalola kupeka report laboza? 2025 ikubwela zonse zizaziwika poyela ndipo muzayimbidwa milandu chifukwa chobisa nkhani anthu inu nanuso mwayingongola nkhaniyi tikumana next year

  • @AdamJames-x7x
    @AdamJames-x7x หลายเดือนก่อน

    Ndizomwe adakuuzani Kuti muzanene zimenezi?manyi Eni Eni ,

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani หลายเดือนก่อน

    Akuwerenga ndakatulo kodi

  • @LloydBotoman
    @LloydBotoman หลายเดือนก่อน

    Nthawi izakwana kuti chilungamo chizaziwike

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani หลายเดือนก่อน

    Usatana uli ku Malawi panopa womvesa chison wochitisa manyazi Mulungu akuoneni nonsenu ndpo sadzakukhululukiran or asatana

  • @RossanaMitha-tl9in
    @RossanaMitha-tl9in หลายเดือนก่อน

    Nonsense.palibe chikumveka.

  • @danielstorey5655
    @danielstorey5655 หลายเดือนก่อน

    Trush lokhalokha anthu mwakalambadi ndithu nthawi yonsei mawadikirirutsa a malawi zau galuzi mxiiiii

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani หลายเดือนก่อน

    Only God knows ndpo misodzi yonse yomwe analira Amalawi onse aja dziwani adzapukuta ndi Mulungu siku lidzafika ndpo u will pay heavy price

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 หลายเดือนก่อน

    LIPOTI ILI MUKAWUZE AMANU

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 หลายเดือนก่อน

    NOSE MWQBWERETSA LIPOTI LABODZALI MUKUDZIYILA MAKALA AMOTO PA BED LANU SIMUDZAKHALA FULU MUNO MALAWI MUDZAZIWUZE NDALAMA ZOMWE CHAKWERA WAKUPATSANI ZOTI MUNAMIZE NAZO AMALAWIAN KOMA MUDZAWONA ANTHU INU MUKUSEWERA KWAMBILI

    • @MusaMatola-r7i
      @MusaMatola-r7i หลายเดือนก่อน

      This person's is killed 9 people in chikangawa

  • @InnocentMlowoka-ew4lo
    @InnocentMlowoka-ew4lo หลายเดือนก่อน

    Koma magazi amuthu

  • @TakondwaMainala
    @TakondwaMainala หลายเดือนก่อน

    It doesn't make sense

    • @ShamimuBisani
      @ShamimuBisani หลายเดือนก่อน

      At all and they wasting there tym

    • @AbsalomKambova
      @AbsalomKambova หลายเดือนก่อน

      True zaziiii

  • @Miracle-o1k
    @Miracle-o1k หลายเดือนก่อน

    Rubbish