ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Very interesting comedy , no one can separate Queen and Ganizani they love each other 😂😂😂😂 welcome back Mrs Mdyangu , where have you been hiding ?
Mwana wa Mkango wapezelera anthu akuyamba kufula uchi eishhhh kaya zitha bwanji Queen sakhazikika koma
Chipwanya ndi munyanyiwa Tom and jelly 😂😂
Camera man tizara tisamawonekesokaya😂,but all in all everything is perfect
𝕂𝕠𝕞𝕒 𝕟𝕕𝕖 𝕦𝕝𝕚 𝕟𝕕𝕚 𝕕𝕚𝕤𝕠𝕥𝕦 𝕜𝕜𝕜𝕜𝕜
Welcome back Mai mdyangu Very nice comedy
Kuphiri kopemphela mpaka 80 days hiyaa uku ndikuthawa udindo 😂😂😂
Kkkk mmmm
Mwana wamkango maso ndimaso queen akudyesa milomo kkkk😂😂 koma queen sazatheka
Queen uhule sazasiya ndthu, Mlelemba kupanda serious kwabwanj uku 🤣 Prisca mkuzangomasukano pamene paja after kumuona wathuyu kut mngouma 🤣 koma Chuma Mercy akangoziziwa izizi zikuvuta ndthuWelcm back Mrs Mdyangu akulu tinakusowa hvy
Welcome back Mai mdyangu
Welcome back mai mdyangu
Welcome back mai mdyangu moooo fire
😂❤ welcome 🤗 Mai Mdyangu apapa tijama ya queen 👑 sopano 🤣
Yavuta ndi wili😅😅😅😅 junior wabwela ndikufuntha😂
Queen sadzatheka,mayi Mdyangu welcome back
Eeee koma prisca amavala ma dress odabwitsa eishh,,, mlelemba m'busa wa chinyengo
Abusa maluzi too much eish mpaka akupita ku fasting ya 80 days 😂😂
🤣🤣🤣🤣🤣koma yofunsa will yokhayi yandibaya.......mbala koooopsaaaaa😊
Mdyangu ndi one palibeso😂😂😂
Mayi mdyangu sopano afika😂😂
Mimba yaphwa kkkkkkkkkk😂😂😂😂 Koma akupanga amulelemba
Yomweyo mayi mdyangu munasowa
Koma queen,eeeeeeee iweyo ndinkhani zina 😂😂😂😂😂😂
Kodi Mercy ndi Namoyo ndi munthu mmodzi or anangofanana ?
Munthu mmodz😂
Kungot amapezekas ku fumkaz
Mulibho guys keep on pushing
Queen muli miyendo yabwino More fire mabomba
Welcome back mamie
Now a queen akudyaso milomo ya Gan kkkkkkkkk
Ukoko nde mwachema😂
Koma Chinanchina a Mdyangu ndi ka handsome 😅😅😅
Mukanva wina wafa ndi kumpanda kwa amdyangu😅😅😅😅😅😅😅
Welcome mai Mdyangu 😋😋🔥
Komatu pulisika 😂😂😂😂😂 kwadyangu kumachitika zinthu eeeeeeeeee
Gani,anamwa tiyi azamwaso bola kusunga kapu 😂😂😂
Kkkkk km Mr dyangu akhalangat alipo mwana wina
Hule ndi hule samasintha kkkkkk look Queen ndi gani kudyana milomo
Yaaa wawa
Gan na Queen kumasukatu 😂😂😂
Takulandirani mai dyangu kkkk, kaya ku zambia anthu mwasiya alibwanji 😅
Good production
Kkk hlf man ndinu afage etii😅😅😅
Ozaaaah mdyangu
Apapa Nde sewero layambikadi next week kuchema😊
😂😂😂 chuma bwinotu osamupatsa mbama mmkaziyo
Km mlelemba mkazi akumva ululu akut kodi mukutani? aaaaaa 😂
Koma kusitha khani kwakeso ati umandisqngqlqsa kodi sitingqkhqle pa ubwedzi kkkkk zuthq bwanji izi
Kkkkk mlelemba aone mwana wake kkkkk
Komaso mulelemba kudabwa dzina la napumani akuti ndi chitsulo
😂😂😂 koma Amulelemba ayi taa 😂😂
😂😂😂😂 koma amulelemba
Komatu Eunice akufanana ndi Steve Junior kkkkkkk tawonetstetsani
Mwana wankango wagwila yekha kwini ndi Gan mpaka kiss 😂😂😂😅😅😅😂😂
Junior ndiye sakumbembesa
😂😂😂😂 Mr nepeman kukanika kufusila,
Kkkkk adakaphedwa mulelembatu
Kafula wabwera nd chisokonezotu kumpanda uziona😅
Half man akufuna adziwe ngt Pali will 😂😂😂
😅😅😅😅😅nepman welcome Mai mdyangu
Kodi Nepman mfundoso zimamupeta...😅
Kkkkkk komatu queen umenyetsana amuna
Queen Ali siliyas dressing mbambande 😎😎😎
😂😂 koma mlelemba
Kwini ukuti banja la asisi ako limalimba chifukwa cha iwe.... ndekuti mwanayo ndiwa Shokoshoko eti😅.... iwe etiuza zoona😂😂😂
Yayamba kumabwera ngat scandal tu kkkkkk
Kuchema Gani ndi mwana Wa Mkango
Mulelemba chisilu cha muthu😂😂
Queen at it again 😂😂😂
Wayishosha uyuyu eeeh😅😅
😂😂😂😂 fear a woman prisca yoo
Mulelemba ndiwe galu kwabas
Queen amaniwaza alini figara ya mushe Koma mai shokoshono nde niwowama wamushe maningi
Kmatu mulelemba oho
Wow half man zake I think zida Ali ndi phuma
Sind ukuchila wasiye ukwatile ndi chipwanya😂😂
next weekend kukome ndikwa Mercy ko😂....iweeee🤌 Mumatha guys
Kwavuta Gani & queen awagwila uku😂😂😂
Nep man wafusilibwa kkk
😅😅koma mlelemba kkkkkk
Kukhomerera chiphwanya😂😂😂
😅😅😅😅 gani wagwidwa basi tili limoz next week
Haif man😂😂 alindi mzeru
mlelemba si mfiti koma kkkkkkk
Munyanyiwa soccer boots kuvalila descent 😅😅😅
Mulelemba mwana olonjezedwa kkk
Nep man kkkkkk dzina la chitsulo
Koma Gani ndi queen ayi zikomo
Komatsu ma junior asowa
Nice wow
Koma Queen iweyo 😂😂
Zilibwino kwambiri guys ❤
Mr hafu Muthu
Mumakwana madolo❤
Mulemba ndiwabodza,fasting 80 days kkkkkkkk
Sewelo la mfumu kazi lilibwino kwambiri koma wachibwi will uja uja akumatchedwa chuma akunyazitsa seweloli, Chibwibwi asiye sizikukhala bwino
Sorry not mfumu kazi koma m'dyangu
I love mdyangu
Kodi sindy muchira riti mpaka 30 months
Km week ikubwelayi kuvuta 😂😂😂
Mmmmm koma zinthu zake zosautsa kkkkkk
Mr mdyangu ku iphalula akuti mmimba ndi mchipala
Mwaikwapura bho😂
Tizalato pa camera.. 😂😂😂
Nepman kuchenjela konseko kufunsila kukuvuta 😅😅
Kwachema amwene 😂😂😂😂
Very interesting comedy , no one can separate Queen and Ganizani they love each other 😂😂😂😂 welcome back Mrs Mdyangu , where have you been hiding ?
Mwana wa Mkango wapezelera anthu akuyamba kufula uchi eishhhh kaya zitha bwanji Queen sakhazikika koma
Chipwanya ndi munyanyiwa Tom and jelly 😂😂
Camera man tizara tisamawonekesokaya😂,but all in all everything is perfect
𝕂𝕠𝕞𝕒 𝕟𝕕𝕖 𝕦𝕝𝕚 𝕟𝕕𝕚 𝕕𝕚𝕤𝕠𝕥𝕦 𝕜𝕜𝕜𝕜𝕜
Welcome back Mai mdyangu
Very nice comedy
Kuphiri kopemphela mpaka 80 days hiyaa uku ndikuthawa udindo 😂😂😂
Kkkk mmmm
Mwana wamkango maso ndimaso queen akudyesa milomo kkkk😂😂 koma queen sazatheka
Queen uhule sazasiya ndthu, Mlelemba kupanda serious kwabwanj uku 🤣 Prisca mkuzangomasukano pamene paja after kumuona wathuyu kut mngouma 🤣 koma Chuma Mercy akangoziziwa izizi zikuvuta ndthu
Welcm back Mrs Mdyangu akulu tinakusowa hvy
Welcome back Mai mdyangu
Welcome back mai mdyangu
Welcome back mai mdyangu moooo fire
😂❤ welcome 🤗 Mai Mdyangu apapa tijama ya queen 👑 sopano 🤣
Yavuta ndi wili😅😅😅😅 junior wabwela ndikufuntha😂
Queen sadzatheka,mayi Mdyangu welcome back
Eeee koma prisca amavala ma dress odabwitsa eishh,,, mlelemba m'busa wa chinyengo
Abusa maluzi too much eish mpaka akupita ku fasting ya 80 days 😂😂
🤣🤣🤣🤣🤣koma yofunsa will yokhayi yandibaya.......mbala koooopsaaaaa😊
Mdyangu ndi one palibeso😂😂😂
Mayi mdyangu sopano afika😂😂
Mimba yaphwa kkkkkkkkkk😂😂😂😂 Koma akupanga amulelemba
Yomweyo mayi mdyangu munasowa
Koma queen,eeeeeeee iweyo ndinkhani zina 😂😂😂😂😂😂
Kodi Mercy ndi Namoyo ndi munthu mmodzi or anangofanana ?
Munthu mmodz😂
Kungot amapezekas ku fumkaz
Mulibho guys keep on pushing
Queen muli miyendo yabwino
More fire mabomba
Welcome back mamie
Now a queen akudyaso milomo ya Gan kkkkkkkkk
Ukoko nde mwachema😂
Koma Chinanchina a Mdyangu ndi ka handsome 😅😅😅
Mukanva wina wafa ndi kumpanda kwa amdyangu😅😅😅😅😅😅😅
Welcome mai Mdyangu 😋😋🔥
Komatu pulisika 😂😂😂😂😂 kwadyangu kumachitika zinthu eeeeeeeeee
Gani,anamwa tiyi azamwaso bola kusunga kapu 😂😂😂
Kkkkk km Mr dyangu akhalangat alipo mwana wina
Hule ndi hule samasintha kkkkkk look Queen ndi gani kudyana milomo
Yaaa wawa
Gan na Queen kumasukatu 😂😂😂
Takulandirani mai dyangu kkkk, kaya ku zambia anthu mwasiya alibwanji 😅
Good production
Kkk hlf man ndinu afage etii😅😅😅
Ozaaaah mdyangu
Apapa Nde sewero layambikadi next week kuchema😊
😂😂😂 chuma bwinotu osamupatsa mbama mmkaziyo
Km mlelemba mkazi akumva ululu akut kodi mukutani? aaaaaa 😂
Koma kusitha khani kwakeso ati umandisqngqlqsa kodi sitingqkhqle pa ubwedzi kkkkk zuthq bwanji izi
Kkkkk mlelemba aone mwana wake kkkkk
Komaso mulelemba kudabwa dzina la napumani akuti ndi chitsulo
😂😂😂 koma Amulelemba ayi taa 😂😂
😂😂😂😂 koma amulelemba
Komatu Eunice akufanana ndi Steve Junior kkkkkkk tawonetstetsani
Mwana wankango wagwila yekha kwini ndi Gan mpaka kiss 😂😂😂😅😅😅😂😂
Junior ndiye sakumbembesa
😂😂😂😂 Mr nepeman kukanika kufusila,
Kkkkk adakaphedwa mulelembatu
Kafula wabwera nd chisokonezotu kumpanda uziona😅
Half man akufuna adziwe ngt Pali will 😂😂😂
😅😅😅😅😅nepman welcome Mai mdyangu
Kodi Nepman mfundoso zimamupeta...😅
Kkkkkk komatu queen umenyetsana amuna
Queen Ali siliyas dressing mbambande 😎😎😎
😂😂 koma mlelemba
Kwini ukuti banja la asisi ako limalimba chifukwa cha iwe.... ndekuti mwanayo ndiwa Shokoshoko eti😅.... iwe etiuza zoona😂😂😂
Yayamba kumabwera ngat scandal tu kkkkkk
Kuchema Gani ndi mwana Wa Mkango
Mulelemba chisilu cha muthu😂😂
Queen at it again 😂😂😂
Wayishosha uyuyu eeeh😅😅
😂😂😂😂 fear a woman prisca yoo
Mulelemba ndiwe galu kwabas
Queen amaniwaza alini figara ya mushe Koma mai shokoshono nde niwowama wamushe maningi
Kmatu mulelemba oho
Wow half man zake I think zida Ali ndi phuma
Sind ukuchila wasiye ukwatile ndi chipwanya😂😂
next weekend kukome ndikwa Mercy ko😂....iweeee🤌 Mumatha guys
Kwavuta Gani & queen awagwila uku😂😂😂
Nep man wafusilibwa kkk
😅😅koma mlelemba kkkkkk
Kukhomerera chiphwanya😂😂😂
😅😅😅😅 gani wagwidwa basi tili limoz next week
Haif man😂😂 alindi mzeru
mlelemba si mfiti koma kkkkkkk
Munyanyiwa soccer boots kuvalila descent 😅😅😅
Mulelemba mwana olonjezedwa kkk
Nep man kkkkkk dzina la chitsulo
Koma Gani ndi queen ayi zikomo
Komatsu ma junior asowa
Nice wow
Koma Queen iweyo 😂😂
Zilibwino kwambiri guys ❤
Mr hafu Muthu
Mumakwana madolo❤
Mulemba ndiwabodza,fasting 80 days kkkkkkkk
Sewelo la mfumu kazi lilibwino kwambiri koma wachibwi will uja uja akumatchedwa chuma akunyazitsa seweloli,
Chibwibwi asiye sizikukhala bwino