💙💙💙APM you're my vote today. Kaya upanga kampeni kapena ayi. Ndidzabwera ku Malawi only to vote for you. But now start looking for a successor to maintain the party.
Yes , he is our hope but he is surrounded by some ill mannered individuals who also participated in bad behaviours during their past rule of government. They are quietly hiding behind him..
Very true brother and they're the main beneficiaries of APM's presidency. We don't need a leader who is as good as senile and who is being controlled by selfish minds. His time is past.
A professor nawonso analephela zinthu zina kuzikomza zimene Chakwela wazikwanilisa padzuko palibe wabwino Maka a ndalewa onse ndi zunkhanila zikha zika...
💙💙💙APM you're my vote today. Kaya upanga kampeni kapena ayi. Ndidzabwera ku Malawi only to vote for you. But now start looking for a successor to maintain the party.
Me too i will vote for him Ndipo ndikuona kuchedwa❤❤
Ineso ndikuona kuchedwa kwambiri 🔥🔥@@RiteRoderick
Waiting for you guys@@RiteRoderick
APM my vote. Tinanena Ife Kuti APM is a calm and visionary leader. 2025 APM BOMA
Gud thinking man,god blles you dad
We adore u,one in a million 😊
My vote
Time to focusing on new generations , he done his part already "Pamene anali boma sakaona zomwe a Malawi timasowa"
Watching for cape town south Africa
God bless you dad
Watching from Port Elizabeth
Our chiyembekezo❤❤❤❤❤❤
Tidyenso chimanga chaulere❤
Our votes
President in waiting...This is the kind of President we want. Intelligent and focused
Paja munavoteranso yemweyu last time
Apm my vote 2025
APM MY VOTEEEE
My vote❤DPP
With all due respect, APM, Biden, Trump, Museveni and other older leaders need to pave way for the youth.
APM my favorite😍💕
Ndipotuu ndikuona kuchedwa kut ndikuvotereniii dadiiiiii❤🎉
He has handled a certain crucial question well.
Ifenso pano pa Mozambique tili pambuyo panu bwana Peter mulungu aku sungeni mpaka tsiku la vote ndi
DppTu BASI my vote
Thanks so much malawi to support you 💙💙💙💙🙏
Watching from Cape Town!
Ziiiiiii
Mosongozedwa nd mulungu a dad ndinu ciyembekezo chathu
Waiting
Adad woooyeeeeee
Watching from Botswana
Background sound muzitsitsako wez ikusokoneza voice please
Tinakutuluka ....Namalomba ndi anzako masomwaa mutizunzilenso abale anthu alubino .....mbolizanu...
Watching from Durban
Well done
Watching from JHB
😊
💙💙💙💙💙💙💙
Ayenda ownawna APM
Our president
Uyiwaleko mr pulezidenti
Mchikulire ❤❤❤❤
Waiting baba
Adad akubweranso wina afune asafune
Kodi anthu mudzingoti kupita kutsogolo kenako kubwelela mbuyo
Momwe anthu munamtukwanila nthawi ijayo panoso aaà komatu Bola angolamulila Yesu dzikoli
Ayi koma Pali zinthu Zina Mulungu kuti zichitike kuti anthu atengelepo phunziro
Our Baba father Malawi ❤❤❤❤❤❤❤❤
Chimwemwe chanthu waseza nthumba ndiuyu chonde amalawi tiyeni timunthandize ponganiza ndiupangili kuti mwina antha kuzati pasa munthu oyenela ambiliwa agofuna kutchuka ndikuba bc
❤❤❤❤
Amalawi ataya zaka zisanu zaulele chopanda phindu president anagwila nchito kuchipiku vice sanajgale mp muyendesa bwanji dziko apengatu ndi mwazi wa kuchikangawa
Asamatinamize ice zaboza zimezo
Yes , he is our hope but he is surrounded by some ill mannered individuals who also participated in bad behaviours during their past rule of government. They are quietly hiding behind him..
Very true brother and they're the main beneficiaries of APM's presidency. We don't need a leader who is as good as senile and who is being controlled by selfish minds. His time is past.
Boma ilooo
Ulemu wanu adad?
Unakanika kale wabodza iwe suwina 😅😅😅
Udindo uwu ndikuona kuti adzaudyelele ndi vice president wake awa atha akula
Kulakalaka chigwa cha madzi chidulo chilipo udzayambe kugulanso mbalr imodzi ya mkaidi k100 ,000 ukuona ngt tidaiwala
Palibe zowina awa koma pa social media awina 😅😅😅
Choka iwe chikangawa
Apm basi
Chachekula ichi siziveka zimene akuyankhula akapume
Koma ndiye, kukakamira mtunda wopanda madzi- za zii!
A professor nawonso analephela zinthu zina kuzikomza zimene Chakwela wazikwanilisa padzuko palibe wabwino Maka a ndalewa onse ndi zunkhanila zikha zika...
Munthu wamkulu ndi inuyo ulemu wanu
Dzikolathu ndilomweli ena akuesela kung'amba koma bwana mulisoka
Azikoza munjila yanji ngati sadali mu boma koma malubino kumangofa ngati nkhuku
Ndilipano daaaa
Adzalowanso amcp ayamba kusanza😂😂😂😂😂😂😂
Munthawi yawo Magetsi amavuta vuta kwambili lero ndi mbili yakale ikakhala njala pa Malawi ndi culture yaba Malawi no wonder
Suka. Wen uthetha kaka
Tikukudikililani. Apm
Sizikumveka ntaaa
Chiyembekezo cha amalawi chokhachi basi
Athu. Akudikila inu adad
Please when you upload the videos make sure you take the shit sound out, doesn't sound sense.
Boma iloo
amalawi taphuzira sitidzayesanso
Ndipo tachimina😂😂😂 komaso tachilàpa, boraso kuika munthu osapemphera pa mpando😂😂😂😂😂.. Adad my vote❤❤❤❤❤
Kkkkkkkk salankhula zoveka abwanawa
Akuyankhula chizungu simungamve ndinu achewa ndevuto 😂😂chikanakhar Chichewa bwezi mukumva🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼😀😀
Ine ndikunva 😂
Adadi omwewo
My vote