Luso lilimo chifukwa chake always nyimbo zake ndi pemphero kwa ine nyimbo iyi wandiimbira 2019 ndinadyetsedwa nthabwa mpaka pano any girl sindimakhulupilira kungoimba ngati ndinamufotokozerapo za nkhani yanga❤❤❤❤❤❤ oimba azitere WANGA NDI AZIZI
Uyimba yekhayo amene ndimayika nyimbo zake pa repeat pa ka 5 times I like this guy is songs 🎵 for real Azizi A2121 uyimba wanga I when are u going too came here south Africa 🇿🇦 cape Town
NDIMADIKIRA nyimbo iyi I saw a little clip of this tune few months ago been waiting. Wat a tune big up Bro Listening from Naweta village BALAKA One ❤ keep the fire burning Bro❤
Thanks for your messages fam please subscribe & share link
Komanso muphonye nyimbo zano mmasosho midiyamu bra
Achina albums anu
Kupanga seach nyimbo osapezeka ayibo
Nyimbo ndiyomweyi sitikusitha
Ilove your music
Azizi top fanz let's sign here
Nyimbo iyiyi 2024 ply list yanga imapezeka aftr nyimbo ina iliyose. Inaswedwa 🙌🙌
Azizi I love your music here in 🇿🇲 Zambia kuchalo Nimukali mumfana too much big up this is beautiful songs
Izi ndee nyimbo zabho🔥🔥🔥
Ineso ndinaona BANGWE ku MACHINGA ayise zachabe. Umakwanila AZIZI ulemu nthawi zonse❤
Dolo a2121
So nice aras heartbreak imaphweka Kwa wina koma ikhale Kwa iweo eeee 🙄🙄😊
Nice bro c l touch ndiyanu
I like the way way Aziz puts his efforts in his music career...his style is so unique
King mahn azizi❤
Iweyo ndi dhollo
Adha awa amatha kuimba 🔥💯🙌
My artist kuyimba ndiye ukuuu
Ndabwelaso .... Katswiri 🔥 kwambiri
Big tune, clean vids 🔥🔥
Big up punyaself
Azizi inu ndi size Yama legend
Eeeeee this song ikugunda pansi pa mtima zama love bola mowa
Luso lilimo chifukwa chake always nyimbo zake ndi pemphero kwa ine nyimbo iyi wandiimbira 2019 ndinadyetsedwa nthabwa mpaka pano any girl sindimakhulupilira kungoimba ngati ndinamufotokozerapo za nkhani yanga❤❤❤❤❤❤ oimba azitere WANGA NDI AZIZI
Zoti Azizi adzantha ndakayika🎉🎉😅
Mbambande dolo wanga with nice tune
Ndimadikira💔
Uli ndi voice yabwn yamaimbidwe ase keep it up
Nice song Big Up ❤
Azizi💥💥💥Nice
Azizi umakwana nice song ❤🎉
Beat yokhayo ndi Story payokha 🔥🔥🔥🔥🔥
Studio yagwira ntchito yotamandika🎉
🎉🎉🎉mumati yimilira big up
Here I am as one of the top fans for a2121
za nyimbo koma beat mwaimva .The guitarist❤
Uyimba yekhayo amene ndimayika nyimbo zake pa repeat pa ka 5 times I like this guy is songs 🎵 for real Azizi A2121 uyimba wanga I when are u going too came here south Africa 🇿🇦 cape Town
Adalah awa.💥✊✊ atangochoka kupita kwina 🙄💔
Abdul Azizi ....The Musician 🎉🎉🎉🎉🎉MANGOCHI PEOPLE LET'S GATHER HERE 🐟🐟🐠🐟🐠
Mkulu bg up u r super star❤
Sunapaleko azizi ili yose ya iwe ndi hit
Lucious Banda uja ndiuyu osala big up Azizi
Mwapha boss🔥🔥
After seeing the guy drunk touching his head I knew we gonna hear stories our granny used to tell us whenever we visit the village
Big up aziz
Eee iwe ndidolo wabasibasi❤❤❤❤ena akamazazindikira iye titasangqlalanawe time yaitali😅🎉
Zenizeni za moyo izi eeesh
Kom Azizi lero wapanga tsiku langa, it's a good vibe weldone.
Tsono Bangwe mu Lilongwe imafunamo chani? Koma ichichi eeee ndi chiphe 🔥🔥🥳🥳
katundu amwene
Top fan waine
Shasha kangapo 🔥 🔥
NDIMADIKIRA nyimbo iyi I saw a little clip of this tune few months ago been waiting.
Wat a tune big up Bro
Listening from Naweta village BALAKA
One ❤ keep the fire burning Bro❤
Katakwe kwambr uyu ❤️🔥❤️🔥❤️🔥❤️🔥 ndimakunyadila azizi
Mr big up
Kuluka mwaluso100%
LIMBAN CHIBWANA AMADEKHA PA SOUND AMANDIWAZA ADHA AWA❤❤
NICE SONG NDIKABAMBEEEE MORE FIRE
ndakhala ndikuyidikila nyimboiyi mmmmm
Tinatopa ndikuyamikila ulemu wako azizi🔥🔥🔥🔥🔥💯
Azizi zako siza phuma zimayenda wez wez ngat fulu
This song just reminding me exactly what happens to me in2017 till now am don't even think again about relationship
Bola tizkatapitsa eti🤣🤣
Sorry bro
Talented man, big up my leadership 😂❤🎉
Ka verse komalizako🔥🔥
OUR OWN STORY TELLER ON THE POINT ❤❤❤❤❤❤
Fabulous boss👌🏻👌🏻
Inuyo mumantha hvy🎉❤
🎉🎉🎉 lots of love and support from here🇲🇼✌️
Fire umatiyimila bro chonchi ndimeneyi lero mpaka lilongwe to 🎉🎉mzuzu
Nic mwana wakwanthu iwe waing'alula imeneyo Zina ndichitikira
Ndaona bangwe mulilongwe✌️💯
More fire 🔥 in-law keep fire burning 🔊
Nyimbo ndi yomwei sitikusitha🔥🔥🔥
Keep the fire burning
mwapha🔥🔥🔥
Mumakwana bgy ,ife nde tkungofra ndmadkra kwnaku kachakumwa kazibambo
Powerful 1 2 1 2👍👍
Keep fire burn Azizi
A2121 and CL Touch Job well done 🎉🎉🎉🎉🎉🎉❤
Nyimbo Za matathauzo sizomangokuwa mu beat Za panozi
Uyuyu anabwera kuzakhala ❤
Powerful song ❤❤❤❤ by JACKSY
Super man uyuuuu🔥🔥🔥🔥🔥
Bangwe mulilongwe ibwera bwanji eeee azizi chiphe
One of the best and underrated musician here in malawi
Best musician wa nthaw zonse 🔥
This is one of my favorite artist and i always pleased with his lyrics...
Music yosakakamiza, voice pure , nice 📸 video
Ulemu wanu bro❤❤❤❤
🎉🎉🎉🎉mbambande
Keep the fire burning🔥🔥
The story master 🔥🔥🔥
Dolo 🔥🔥
Production top notch !!
Nice tune biggy 👍
😢 Ur my adviser azizi ur songs hit my heart 🎉
Luso losakakamiza ili❤❤
Dolo wathu🥰🔥🔥🔥
My therapist on it🔥🔥🔥
❤❤❤❤❤❤ mayimbidwe opatsa chikoka
Dolo katatu🔥
Top fan ine panoooo
🔥🔥🔥 bangwe mu lcity
The storyteller 🔥🔥🔥
My artist 🎉 Azizi
Azizi fire 🔥🔥
Mmisili wa luso lapamwamba zedi. Azizi receive your flowers Bro.
Azizi moto kuti buuuu❤🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Tamayesesani izikwana 7 minutes mwatisiyatu malele 🔥 📛 👨🚒 🚒 koma AZIZI
Azizi inu muntchuka basi musiyeno kuyimba 😊
Usazafe aise🎉🎉🎉🎉
Atsogoleri awawa alibe comparison 🔥🔥🔥🔥🔥
Uyuyu katundu 🔥🔥🔥