ZAZIWIKA SOPANO KUTI JB SI MMALAWI PAMENE WAONESA ZIPHASO ZAKE ZA MAINA ODABWISA KU DZIKO LA MALAWI

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 21 ก.ย. 2024
  • ZAZIWIKA SOPANO KUTI JB SI MMALAWI PAMENE WAONESA ZIPHASO ZAKE ZA MAINA ODABWISA KU DZIKO LA MALAWI
    Welcome to our channel, where we dive deep into the intricate and evolving world of Malawi’s politics. From the rise of powerful political parties like the Democratic Progressive Party (DPP) and Malawi Congress Party (MCP) to the powerful impact of the UTM Party, we bring you insightful analysis on the key players shaping the nation. Explore the journeys of leaders like Lazarus Chakwera, Saulos Chilima, and the influential activist Bon Kalindo as they navigate the challenges of governance, power struggles, and the quest for a better future.
    Our channel is dedicated to unraveling the complexities of Malawi’s political landscape, offering you detailed breakdowns of alliances, rivalries, and the significant events that continue to define the country’s destiny. Whether you're interested in historical perspectives or current political dynamics, we provide in-depth coverage and engaging content that keeps you informed and inspired.
    Subscribe to stay updated on the latest developments, and join us as we explore the fascinating stories that shape Malawi’s political narrative.
    #MalawiPolitics #PoliticalAnalysis #DPP #MCP #UTM #LazarusChakwera #SaulosChilima #BonKalindo #AfricaPolitics #PoliticalActivism #petermutharika

ความคิดเห็น • 63

  • @GreciousMeleca
    @GreciousMeleca วันที่ผ่านมา +2

    JB is the best teacher

  • @HamidaImran-e2n
    @HamidaImran-e2n 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Truth JB his full but not full but very very full

  • @ebrahimisa14
    @ebrahimisa14 วันที่ผ่านมา +1

    The guy is spot on

  • @MarryNyilongo-s5x
    @MarryNyilongo-s5x วันที่ผ่านมา +2

    Muzinena zinthu zophuzitsa komaso poyankhulula kumaona mau ake osati zibwana zanuzi nose pangan kut tingatan kut tipulumuse malawi wathu osati zachabe zanuzo

  • @HappChiwanda-e6t
    @HappChiwanda-e6t 22 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    That's true bro inuyo mwathoka ngamo

  • @DigleDafter
    @DigleDafter วันที่ผ่านมา +1

    JB sakunama koma chilungamo ndipo amaphuzisa achinyamayafe sangafane ndi odya achuleyu

  • @chifundocharles2348
    @chifundocharles2348 วันที่ผ่านมา +2

    Kod munthu umakhala mmalawi chifukwa cha dzina???? Your town exposes ur foolishness honestly

  • @HerbartKaphamthengo
    @HerbartKaphamthengo วันที่ผ่านมา +3

    Nonsenu ndinu amisala palibeso zowalilana apa

    • @EvelynMasamba
      @EvelynMasamba 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Zitsiru zimalimbana zitsiru zokhazokha

  • @GeoffreyBakuwa
    @GeoffreyBakuwa 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zoona zake big man

  • @moosakamwendo1986
    @moosakamwendo1986 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    ulemu wanu big JB

  • @WilsonWalmatama
    @WilsonWalmatama วันที่ผ่านมา

    That's right

  • @frankphiri386
    @frankphiri386 วันที่ผ่านมา

    𝘛𝘰𝘥𝘢𝘺 𝘯𝘥𝘢𝘵𝘰𝘭𝘢𝘮𝘰 𝘤𝘩𝘪𝘯𝘢𝘤𝘩𝘢𝘬𝘦 𝘮𝘸𝘢 𝘮𝘷𝘦𝘵𝘦𝘺𝘶 ❤❤❤❤

  • @frankchimaliro5981
    @frankchimaliro5981 วันที่ผ่านมา +1

    Biggy

  • @SamisonLevison-z5p
    @SamisonLevison-z5p 17 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Jb ndi waku Malawi,dzina lilibe kanthu.Derick,Leonard ndi Dickson maina amenewa ndi akuti?Nde muzikanena za Fernando.Dzina la English nde m'Malawi likakhala la zilankhulo za kunja nde si m'Malawi life yabwanji imeneyo

  • @PreciousSaidi-kd3we
    @PreciousSaidi-kd3we วันที่ผ่านมา +1

    Dolo

  • @Mussa-z9w
    @Mussa-z9w วันที่ผ่านมา +1

    Akuyakhulawa akunena zoona

  • @IqrahOmar-x6w
    @IqrahOmar-x6w วันที่ผ่านมา

    Jb is my vote

    • @bs-malawi
      @bs-malawi  วันที่ผ่านมา

      iiiiih nkhani ijaso abale

  • @FaithNchebe
    @FaithNchebe วันที่ผ่านมา

    JB is my vote ndi fana wabho!!!!

    • @MadalitsoChinkhonyo
      @MadalitsoChinkhonyo 18 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Imweyo kwanu nkuti tafusa agogo Ako akuza kuti anachoka komweko imeneyo s ikhani man

  • @YusufJimmy-v1o
    @YusufJimmy-v1o วันที่ผ่านมา

    Jb..ukunena zooonadi school simakuphuzitsa kupeza ndalama...walasadi....pali anthu ambiri ali ndalama koma savaye ku geli

  • @ThokohPrescotKalonga
    @ThokohPrescotKalonga วันที่ผ่านมา

    Yes nanenso dzina ndinadabwa nalo mm akuti Fernando's kaya ndani uko 😂😂😂 apapa mavyete afuna atiyende pasi 👍👀

    • @janschutte7515
      @janschutte7515 วันที่ผ่านมา

      Inuuu muzikhalako ndi kuganiza kaye.
      Ku MALAWI kulibe nzika ndipo nzika zeni zeni anasala ochepa tonse ndi obwera enanunso ndi aku DRS

  • @MussaLenard-s2t
    @MussaLenard-s2t วันที่ผ่านมา

    Jb❤

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh วันที่ผ่านมา

    Za tchito yanji ukuwonetsazo tili ndi ma friends ophula USA osati zamanyi zakozo

  • @DicksonKampunga-ot4bw
    @DicksonKampunga-ot4bw 19 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    JB analakwa physical science pa JCE

  • @chifundoalfred14
    @chifundoalfred14 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    inuyo amene mukuti ndiye odziwika kut ndinu amalawinu nanu mufunika school ndithu
    dzina latani
    kod achina simama transport aja ngakuti?
    achina Antonio transport aja ngakuti?
    achina Almeda transport aja ngakuti?
    onsewatu ndi mabwana mu Lilogwe mu
    mutiuzaso kut ndi a Mozambique???
    muzikhara serious ndi zithu

  • @FranciscoFabiano-ed6sj
    @FranciscoFabiano-ed6sj วันที่ผ่านมา

    JB amanena chilungamu kwambiri

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh วันที่ผ่านมา

    Matako ako iwe JB

  • @ronaldordinga6537
    @ronaldordinga6537 วันที่ผ่านมา

    Vomekezani chabe man kuti sukulu inuyo inakuvutani adha aja sukulu anapanga,,,,,,
    Inu mkakamire mbali inayo za sukulu izi zinakuvutani man

  • @FelixBoss-yn9pe
    @FelixBoss-yn9pe วันที่ผ่านมา

    JB ndi dolo koma zinazo padela

  • @HamidaImran-e2n
    @HamidaImran-e2n 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    J b ndinyapapi galu wa galu wamuthu

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh วันที่ผ่านมา

    JB chitsilu osapanga zatumbuka tamapanga za lomwe

    • @bs-malawi
      @bs-malawi  วันที่ผ่านมา

      Aaaah ndi mpwitikizi uyu asatinyase kkkkk

  • @GitiSakala
    @GitiSakala 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mavete mavete ukaliwanu

  • @FatimaKananji-kz6yx
    @FatimaKananji-kz6yx วันที่ผ่านมา

    Apunsila akuka lima nmaganyu wachiyawo 👻ndiso limakala pa mbiya basi

  • @JamesChimera-hw1nv
    @JamesChimera-hw1nv วันที่ผ่านมา

    Zofunika anthu amitu yoduka mawaya

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 วันที่ผ่านมา

    Zonse zonyasa nkhope zokhazokha

  • @kingtiles-g6q
    @kingtiles-g6q วันที่ผ่านมา

    ba apange akuona ndimwe chopupwa ndi ana awa

  • @MusaBukari1992-fd1ll
    @MusaBukari1992-fd1ll 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Iwe pwala lako

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy วันที่ผ่านมา

    JB ndi dolo osat Morgan kape wachabe chabe

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile วันที่ผ่านมา

    JB is a mozambican

    • @DigleDafter
      @DigleDafter วันที่ผ่านมา

      Ukunamatu iwe JB mmalawi weni weni ndi angati alindimaina ngati awa muziko lathu😂

    • @chifundoalfred14
      @chifundoalfred14 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      iweyo ndiweso Mozambique kumalawi kuno kulibe Gesho

  • @GitiSakala
    @GitiSakala 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Timakuziwa iwetusikape ifetakhalapoanamasikin usikulimbanandimakape ulindimafasiambili

  • @PatrickMandala-j6t
    @PatrickMandala-j6t วันที่ผ่านมา

    Komatu vyete muli kuseka kkkk umakwana

  • @mcdonaldchakwira3145
    @mcdonaldchakwira3145 วันที่ผ่านมา

    Jb chitsiru

  • @FaithNchebe
    @FaithNchebe วันที่ผ่านมา

    Maviyete ndi matchini not enawo

  • @SqueyaHosmane
    @SqueyaHosmane วันที่ผ่านมา

    Mukumveka kachipotikizi-potikizi....e

    • @bs-malawi
      @bs-malawi  วันที่ผ่านมา

      Ambiridi akutero kkkk

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete วันที่ผ่านมา

    😂😂😂😂 wagasi komano akuzinyelera

  • @davidjames9711
    @davidjames9711 23 นาทีที่ผ่านมา

    Kkkkkk

  • @robsontyg3928
    @robsontyg3928 วันที่ผ่านมา

    Koma chamba sizinthu 😂😂😂

  • @YusufJames-f5f
    @YusufJames-f5f 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    ❤😂😂😂😂mavyete #*1

  • @YellowmanMalawi-qe8zh
    @YellowmanMalawi-qe8zh วันที่ผ่านมา

    Chakwera tu ali komweko take care

  • @HamidaImran-e2n
    @HamidaImran-e2n 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    J b ndinyapapi galu wa galu wamuthu 21:14

  • @ThokoMsonkho-hy4uc
    @ThokoMsonkho-hy4uc วันที่ผ่านมา

    Ineyo ndi YAO ndipo ndinaphuzira ndipo ndimachita bwino kuposa Mtumbuka ndipo amandiziwa kukangolephera mkalasi wina sakhoza chimenecho koma sukulu si ntchito komanso si ndalama.
    Ndili ku Mbenjere National secondar ndimachita bwino

    • @XolanZungu-ye1rw
      @XolanZungu-ye1rw วันที่ผ่านมา +1

      Mtumbuka zamukhuza bwanji mmmm

    • @WeziChioni-d6u
      @WeziChioni-d6u 19 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Nde tisegule nazo mmimba poti wina ndimyawo

  • @HamidaImran-e2n
    @HamidaImran-e2n 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    J b ndinyapapi galu wa galu wamuthu

  • @HamidaImran-e2n
    @HamidaImran-e2n 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    J b ndinyapapi galu wa galu wamuthu