Aqīdah Kwa Akazi - Day 24 Part 1

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 12 ก.ย. 2024
  • Lero asilamu ena mu gulu la akazi akumapita mwa abusa nkumakapempha chithandizo (kumapemphereredwa, kupatsidwa madzi oyera, ndi zina zotero); ena mwa iwo akupita kwa asing’anga kukaombedza mu nthawi yomwe mavuto awagwera; ena akukhulupirira mu nyenyezi (horoscopes); ena akukhulupirira mwa mizimu pamodzi ndi ziwanda; ena akumapita kwa ma sheikh kukachititsa matalasimu; ndipo ena akumapempha omwalira ku manda. Kenako akachita ntchito imeneyi, iwo akumabwera m’mizikiti yathu namapemphera tsiku ndi tsiku. Enanso afika pomakhulupirira mbali imodzi ya Qur’ān ndi kumakanira mbali ina. Mtumiki wa Allāh (ﷺ) amamutsata pakamwa pokha koma osati mu ntchito zawo.

ความคิดเห็น • 1