- 160
- 36 410
Free Online Madrasah
Tanzania
เข้าร่วมเมื่อ 26 เม.ย. 2022
Awa ndi madrasah aulele amene adakhazikitsidwa ndi cholinga chopititsa patali uthenga weniweni wa Chisilamu umene Allaah adautumiza kwa Mtumiki Wake (mtendere ndi madalitso zikhale pa iye), ndipo ndi uthenga umene adaugwiritsa ntchito asilamu oyambirira mu m'badwo uno (ma Swahaabah, Taabi'iin komanso ma Taba' Taabi'iin).
Kwa nonse amene mukufuna kutithandiza; mutha kutumiza Swadaqah yanu kudzera pa:
Mpamba: +265888275554
Airtel Money: +265995378705
Mo626: 1007234828
Ngati mukufuna kukhala nawo pa gulu la pa WhatsApp, tumizani uthenga ku +265888275554.

Âqīdah Iyambirire - Episode 4
Asilamu, makamaka maiko amene sitikutsatira Sharī'ah, tikukhala moyandikana kwambiri ndi anthu omwe ali a zipembedzo zina, ndipo izi zikupangitsa kuti ambiri mwa ife tisazindikire chikhulupiriro chathu chenicheni (ndife asilamu dzina lokha). Tikumangotsatira chikhulupiriro chilichonse chimene mtima wathu wakonda ndipo sitikulabadira za kutsatira Njira Yoongoka imene Mtumiki (ﷺ) pamodzi ndi ophunzira ake (Swahābah) adaiyenda.
มุมมอง: 122
วีดีโอ
Âqīdah Iyambirire - Episode 3
มุมมอง 1719 ชั่วโมงที่ผ่านมา
Asilamu, makamaka maiko amene sitikutsatira Sharī'ah, tikukhala moyandikana kwambiri ndi anthu omwe ali a zipembedzo zina, ndipo izi zikupangitsa kuti ambiri mwa ife tisazindikire chikhulupiriro chathu chenicheni (ndife asilamu dzina lokha). Tikumangotsatira chikhulupiriro chilichonse chimene mtima wathu wakonda ndipo sitikulabadira za kutsatira Njira Yoongoka imene Mtumiki (ﷺ) pamodzi ndi ophu...
Âqīdah Iyambirire - Episode 2
มุมมอง 1389 ชั่วโมงที่ผ่านมา
Asilamu, makamaka maiko amene sitikutsatira Sharī'ah, tikukhala moyandikana kwambiri ndi anthu omwe ali a zipembedzo zina, ndipo izi zikupangitsa kuti ambiri mwa ife tisazindikire chikhulupiriro chathu chenicheni (ndife asilamu dzina lokha). Tikumangotsatira chikhulupiriro chilichonse chimene mtima wathu wakonda ndipo sitikulabadira za kutsatira Njira Yoongoka imene Mtumiki (ﷺ) pamodzi ndi ophu...
Âqīdah Iyambirire - Episode 1
มุมมอง 1619 ชั่วโมงที่ผ่านมา
Asilamu, makamaka maiko amene sitikutsatira Sharī'ah, tikukhala moyandikana kwambiri ndi anthu omwe ali a zipembedzo zina, ndipo izi zikupangitsa kuti ambiri mwa ife tisazindikire chikhulupiriro chathu chenicheni (ndife asilamu dzina lokha). Tikumangotsatira chikhulupiriro chilichonse chimene mtima wathu wakonda ndipo sitikulabadira za kutsatira Njira Yoongoka imene Mtumiki (ﷺ) pamodzi ndi ophu...
Lesson 16 - Swalāh ya Mtumiki wa Allāh (ﷺ)
มุมมอง 13114 วันที่ผ่านมา
Lesson 16 - Swalāh ya Mtumiki wa Allāh (ﷺ)
Lesson 15 - Swalāh ya Mtumiki wa Allāh (ﷺ)
มุมมอง 9714 วันที่ผ่านมา
Lesson 15 - Swalāh ya Mtumiki wa Allāh (ﷺ)
Lesson 14 - Swalāh ya Mtumiki wa Allāh (ﷺ)
มุมมอง 152หลายเดือนก่อน
Lesson 14 - Swalāh ya Mtumiki wa Allāh (ﷺ)
Mitala ili ndi ubwino wanji kwa akazi? - Abu Hashmah
มุมมอง 362หลายเดือนก่อน
Abu Hashmah kufotokoza za ubwino wa mitala kwa akazi.
Aqīdah kwa Akazi - Day 40
มุมมอง 103หลายเดือนก่อน
Lero asilamu ena mu gulu la akazi akumapita mwa abusa nkumakapempha chithandizo (kumapemphereredwa, kupatsidwa madzi oyera, ndi zina zotero); ena mwa iwo akupita kwa asing’anga kukaombedza mu nthawi yomwe mavuto awagwera; ena akukhulupirira mu nyenyezi (horoscopes); ena akukhulupirira mwa mizimu pamodzi ndi ziwanda; ena akumapita kwa ma sheikh kukachititsa matalasimu; ndipo ena akumapempha omwa...
Aqīdah kwa Akazi - Day 39
มุมมอง 79หลายเดือนก่อน
Lero asilamu ena mu gulu la akazi akumapita mwa abusa nkumakapempha chithandizo (kumapemphereredwa, kupatsidwa madzi oyera, ndi zina zotero); ena mwa iwo akupita kwa asing’anga kukaombedza mu nthawi yomwe mavuto awagwera; ena akukhulupirira mu nyenyezi (horoscopes); ena akukhulupirira mwa mizimu pamodzi ndi ziwanda; ena akumapita kwa ma sheikh kukachititsa matalasimu; ndipo ena akumapempha omwa...
Aqīdah kwa Akazi - Day 38
มุมมอง 65หลายเดือนก่อน
Lero asilamu ena mu gulu la akazi akumapita mwa abusa nkumakapempha chithandizo (kumapemphereredwa, kupatsidwa madzi oyera, ndi zina zotero); ena mwa iwo akupita kwa asing’anga kukaombedza mu nthawi yomwe mavuto awagwera; ena akukhulupirira mu nyenyezi (horoscopes); ena akukhulupirira mwa mizimu pamodzi ndi ziwanda; ena akumapita kwa ma sheikh kukachititsa matalasimu; ndipo ena akumapempha omwa...
Aqīdah kwa Akazi - Day 37
มุมมอง 73หลายเดือนก่อน
Lero asilamu ena mu gulu la akazi akumapita mwa abusa nkumakapempha chithandizo (kumapemphereredwa, kupatsidwa madzi oyera, ndi zina zotero); ena mwa iwo akupita kwa asing’anga kukaombedza mu nthawi yomwe mavuto awagwera; ena akukhulupirira mu nyenyezi (horoscopes); ena akukhulupirira mwa mizimu pamodzi ndi ziwanda; ena akumapita kwa ma sheikh kukachititsa matalasimu; ndipo ena akumapempha omwa...
Lesson 12 - Swalāh ya Mtumiki wa Allāh (ﷺ)
มุมมอง 146หลายเดือนก่อน
Lesson 12 - Swalāh ya Mtumiki wa Allāh (ﷺ)
Lesson 11 - Swalāh ya Mtumiki wa Allāh (ﷺ)
มุมมอง 64หลายเดือนก่อน
Lesson 11 - Swalāh ya Mtumiki wa Allāh (ﷺ)
Lesson 7 - Swalāh ya Mtumiki wa Allāh (ﷺ)
มุมมอง 228หลายเดือนก่อน
Lesson 7 - Swalāh ya Mtumiki wa Allāh (ﷺ)
Lesson 6 - Swalāh ya Mtumiki wa Allāh (ﷺ)
มุมมอง 3682 หลายเดือนก่อน
Lesson 6 - Swalāh ya Mtumiki wa Allāh (ﷺ)
Lesson 5 - Swalāh ya Mtumiki wa Allāh (ﷺ)
มุมมอง 5712 หลายเดือนก่อน
Lesson 5 - Swalāh ya Mtumiki wa Allāh (ﷺ)
Asilamu adzatsatira zochitika za Ayuda ndi Akhristu
มุมมอง 5293 หลายเดือนก่อน
Asilamu adzatsatira zochitika za Ayuda ndi Akhristu
Lesson 3 - Swalāh ya Mtumiki wa Allāh (ﷺ)
มุมมอง 3713 หลายเดือนก่อน
Lesson 3 - Swalāh ya Mtumiki wa Allāh (ﷺ)
Allah azikulipilan zochuluka pano zikolapas kmaso ndisiku lachimalizilo
Ameen
Allahumma ameen
MashaAllah
Program yabwino kwambiri Jazaka llahu khaira brother zambir tikusinthika ndithu
Allahuma barik
Āmīn wa fīkum
Alhamdulillah...... May Allah protect you from Evil eyes
Āmīn inunso chimodzimodzi akhī
❤
❤
Ameen ❤ following
❤
Salaam alykum mwaswera bwanji Kod mulibe group PA WhatsApp
Walykum Salaam warahmatullah wabarakaatuh Go ku description mukayipeza number ayika kumeneko
@@BrendaMadinda oky chabwino
❤
Is this provide online learning madrasa study ?
May Allah bless u and your family
Āmīn and you too dear brother
following...... may Allah bless u and ur family
Ameen
Nyimbo ya mama wetu che mina kkkkkk kkkkkk Komatu azimai tisake sakedi maphunziro shaa aàaaa
Loud and clear
Jazakumullah Khair sheikh 🌸
❤❤❤❤❤❤❤ Masha Allah sheikh pititsani kutiphudzitsa
Jazakala khaila
Following
Jazakala khaila
Masha Allah ❤
Following
Allah akulipireni zabwino sheikh wanga
Aaamiin inunso chimodzimodzi
Jazakala khaila
Aaamiin wa iyyaakum
Barakallahu fika
Aaameen wa fiikum
Jazakala khaila
MashaAllah ummu sulaym
Taphunzirapo pamenepa ambiri timasogozadi maondo
Jazakala khaila
Jazakala khaila
Following
Ma shaa Allah Taphunzira nawo ndithu
Mashaallah
Jazakala khaila
Mashaallah
Jazakala khaila
Naam
Jazakala khaila
Mashaallah
Naam
Mashaallah
Mashaallah
Naam❤❤❤
Allah akulipire zabwino sheikh wanga
❤❤❤❤
Following