Daliso Kabambe watuluka ku DPP. Walowa Chapani cha UTM. Watero pouza Amalawi.

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 23 ส.ค. 2024

ความคิดเห็น • 47

  • @ChristianMtambalika
    @ChristianMtambalika หลายเดือนก่อน +5

    Utm chenjenjerani musanamizidwe kuti dpp ndiyofoira zaboza uyu akusokonezani

  • @KunyengaMoyo
    @KunyengaMoyo หลายเดือนก่อน +5

    Akufuna udindo awa mmm akufuna u president ku Utm

  • @AlexManuelMisomali-sv1vn
    @AlexManuelMisomali-sv1vn หลายเดือนก่อน +2

    Mwina upulezidenti omwe amaufuna ku DPP akautengera ku UTM komanso adziwe kuti a UTM siwopusa

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 หลายเดือนก่อน +3

    Tianyoze kwambiri DPP. Ambirife a ife a UTM tinachokera konko. Andale ndi anthu okakamira ma udindo komanso osakasaka maundindo. Tiyeni tikonde.

  • @davidlinerevelation3427
    @davidlinerevelation3427 หลายเดือนก่อน +2

    Ku south africa kuli Checkers ndi shoprite ndi company imodzi
    Kwinako mupitiliza

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc หลายเดือนก่อน +5

    😂😂😂😂😂,wafunako u president aaaaaa koma ku chenjela,kwinaku.

    • @mathewsnachuma8086
      @mathewsnachuma8086 หลายเดือนก่อน

      Ku DPP kuli anthu oipa amuzungulira bwana Uja anthu oipa kwambiri

    • @HarrisonMwanga-xy4sc
      @HarrisonMwanga-xy4sc หลายเดือนก่อน

      @@mathewsnachuma8086 inetu kuona kwanga watumidwa,kuti akatenge anthu onse,ali ku UTM awabweletse ku dpp tiyeni tisatile speech ya president wa dpp kuti'a president a UTM anatenga ma per cet ena kupita nawo ku tonse alliance,mr kabambe ndi a president a dpp ndi, family'pa, chimenechi UTM isamale.

    • @mathewsnachuma8086
      @mathewsnachuma8086 หลายเดือนก่อน

      @@HarrisonMwanga-xy4sc Kabambe wachoka chifukwa cha nkadza amwene kuli circle yoipa kwambiri anthu amuzungulira nkulu Uja atachoka Chipani chija chikhala bwino, Ali ndima self interest awo so sakufuna wina abwelepo koma akhale iwo basi

    • @HarrisonMwanga-xy4sc
      @HarrisonMwanga-xy4sc หลายเดือนก่อน

      @@mathewsnachuma8086 kkkkkkkkk, koma ndiyetu anadzungulilidwa ndi akhala kale

  • @samsonhavenoyayshonga2609
    @samsonhavenoyayshonga2609 หลายเดือนก่อน

    Ndi plan yoti azidziwa zomwe zikuchitika MCP azizazitumiza ku ma opposition party

  • @McAnthonyMbewe
    @McAnthonyMbewe หลายเดือนก่อน +1

    Inu wachoka ku thupi koma mumtima Ali ku dpp mukamamva ndale zokhwima mu ubongo ndi zimenezo.kutulusa Ronardo kut madifenda atase kenako umangomva in the goaoooooooo!!eeeeeeeeeeehhh.

  • @CharityChikomo-hl1gz
    @CharityChikomo-hl1gz หลายเดือนก่อน

    Dyela akufuna amusakhe akhale president coz waona kuti kulibeko mtsogoleli

  • @ChrisEnos-to5uv
    @ChrisEnos-to5uv หลายเดือนก่อน +1

    Akuziwana awa chomwe akupanga anthuwa ndi amodzi penyani patali

  • @emilynthite6545
    @emilynthite6545 หลายเดือนก่อน +2

    Ngati achoka kabambe alibe ntchito asaipise chipani cha dpp

  • @viennasamuel2976
    @viennasamuel2976 หลายเดือนก่อน

    U president awa ayi bolanso angokhala akweni president

  • @chisomokawotcha1766
    @chisomokawotcha1766 หลายเดือนก่อน +2

    That's the only way kabambe kukhala running mate without problems kuti alowe as running mate Ali ku dpp ndi zovut koma adzalowe ngati running mate from utm after alliance nde ndale zimenzo aziwerenga kale kale

    • @JimsonChisi
      @JimsonChisi หลายเดือนก่อน

      Your righ mr

  • @Dorah-zl9uf
    @Dorah-zl9uf หลายเดือนก่อน

    Akufuna akhale apule ku UTM awa

  • @user-ji4xn6me8d
    @user-ji4xn6me8d หลายเดือนก่อน

    Akagwere komanso tinamupanga ndife kuti adziwe ndale

  • @JohnAsendi
    @JohnAsendi หลายเดือนก่อน

    Koma ndale mukufuna kuwasokoneza A UTM nanga kumeneko apitila kuchikonda chipani kkkkk nthawi yonseyi sapita koma manifesto ya UTM musaisokoneze kumeneko kuti tidzaonesana zomwe tikuonazi

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl หลายเดือนก่อน +1

    Awa alibe chintchito

  • @chifundocharles2348
    @chifundocharles2348 หลายเดือนก่อน +1

    DPP ija is using intelligence mafana ❤❤❤😂😂

  • @GiftChitsulo
    @GiftChitsulo หลายเดือนก่อน +1

    Kkkk akabambe kkkk 😢😢 asimungawine

  • @LindiweMoloi-wn5qo
    @LindiweMoloi-wn5qo หลายเดือนก่อน

    Akufuna akatenge Malo achilima ,apezelapo mwayi anthu ndiovuta amakonda mzawo akamwalila atenge mpando

  • @MaryJefry
    @MaryJefry หลายเดือนก่อน

    Afuna udindo awa asaipisepo dpp apa

  • @user-fq4kv8dj4t
    @user-fq4kv8dj4t หลายเดือนก่อน

    Utm chenjelani chipani chanu mwachoka nacho kutali wina asangobwela poyela yela nkukusokonezani zochita inu pangani zanu musatayane nokha nokha

  • @MaryChavula-jz3di
    @MaryChavula-jz3di หลายเดือนก่อน +1

    Sizingasokoneze dpp ai apite komwe afuna tilibenawo zochita ku dpp

    • @isaihmagani5697
      @isaihmagani5697 หลายเดือนก่อน

      Unena zimenezo ndiweyo Kabambe ndi m'bale wa APM nde sangakhale opanda ntchito

  • @louisbonongwe8537
    @louisbonongwe8537 หลายเดือนก่อน

    Zonse zomwe mukunena apaz ndimaganizo anu.zoona zake zenizeni akuziziwa ekha.inu dekhani.

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm หลายเดือนก่อน

    Akufuna udindo uyu mwinaso akufuna akhare president kuchenjera uyu

  • @user-vx5kv8dz3d
    @user-vx5kv8dz3d หลายเดือนก่อน +1

    Good move

  • @RobertChisenga-ci2mq
    @RobertChisenga-ci2mq หลายเดือนก่อน

    Akufuna upule

  • @user-ru1mm7bf4p
    @user-ru1mm7bf4p หลายเดือนก่อน

    Akuona ngati adutsa mosavuta

  • @KENETHMAJASA-ud5ee
    @KENETHMAJASA-ud5ee หลายเดือนก่อน +1

    Not bad, nipapopo

  • @EllinaBitto
    @EllinaBitto หลายเดือนก่อน

    Waìonera pataĺi😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @AlexManuelMisomali-sv1vn
    @AlexManuelMisomali-sv1vn หลายเดือนก่อน

    Kabambeyu wachita bwino kwambiri chifukwa amasokonedzako uyu

  • @blandinabonaventure
    @blandinabonaventure หลายเดือนก่อน

    A choke zilibe ntchito

  • @user-zm9nl8zn2b
    @user-zm9nl8zn2b หลายเดือนก่อน

    Dyere sichifukwa china

  • @jomochirwa
    @jomochirwa หลายเดือนก่อน

    Sadatuluke this is dpp plan its was planned akufuna utm ikhalebe ndi mphavu popeza utn idzapanga mgwilizano ndi dpp .ndiye planiyo .

    • @user-qp8kh2hj9o
      @user-qp8kh2hj9o หลายเดือนก่อน

      Wakuuzani ndani kuti utm izapanga mgwirizano ndi DPP musavutike ana agogo

  • @user-lw4hw9ce4w
    @user-lw4hw9ce4w หลายเดือนก่อน +1

    Akuzakhala running met wa APM iyiyo n mission ya ku dpp

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 หลายเดือนก่อน

    Ndimadabwa kuti bwanji kabambe akukakamila chipani cholephela

    • @edsonnyasulu5394
      @edsonnyasulu5394 หลายเดือนก่อน

      Amalawi chomwe tiziziwa ntchakuti kuphula dziko la malawi mu MIMBULU ilipoyi tisaone kuti munthu uyu akufuna udindo koma tiwone kuthekela kwa munthuyo kuti ndiothandiza kaya zikhala ngati as ufumu zilibe ntchito koma nkhani ndikuphula malawi

  • @user-xk3jd6ig8j
    @user-xk3jd6ig8j หลายเดือนก่อน

    Good move