Ineso ndimaganiza kuti chakwela wasungq anthu aja chifukwa zikanakhala kt sizikukhuza za ngozi ija ndipo ali ndi chisoni chilungamo chitaziwika km masitetimenti akubwelela zachiwonekele kt chakwela ndi amene adapanga chiwembu chimenechija ndipo mukadangosiya osafuvuzaso bcz mayankhudwe akubwela ose ndiwonama tinazi2a kale ife kuti wapha anthu aja ndi chakwela ndi anthu ake km lino ndi dziko mm mulungu wamkulu akuziwa zonse.
Ndipo nsaname anthu awa a MCP akuziwa zoona zake,ine audio iyi yandivesa chison nsaname,ambuye munalolenji izi kut zichitike,ndipo kudziko kuno kuli Mulungu ndipo chobisika chizaoneka...zoona basi Chilima just like that abale ? Mmmmh ai ndith munthui anapha sure ma statement anachuluka osintha zonena,chakwera anat amundege anauzidwa kut abwelele yet akut denge siinafike ku Mzuzu airport,komanso ena anazat mu ndege communication munalibe,akut ndege inali ndimavuto yet report lati ndege inalibe mavuto,akut anthu anafela mwamba who killed them yet kufela mwamba imakhala kut ndege yapanga impact ndichinthu,guys Allah knows & he'll tell us the truth soon 😢
Nde mwati oyendesa ndegewa ma lincesi awo anali atatha ndichifukwa nao chinapangisa ngozi, nde mwaonjezeranso kuti aja amajambula zithuzi aja afufuzidwe amangidwe, so y amenee amatinamiza aja samangidwaa
Ulemu wanu the DC, anthuwa anachita kuphedwa, SKC and 8 others we never forget until for ever, now it's like history to us, we have questions without answers, why God u allow this thing to the innocent people
Chakwera sangapange action ili yonse coz him and his Cabinet they planned all this. Chakwera you killed Chilima ndi Anthu Ena Osalakwa Evil Man. Kupha Anthu eeeee Koma wina mukuti sathamanga misala
Guys moti Panalibe omuchenjeza chilima nthawi ija amazuzidwa kuchoka mu alliance? Akubanja komanso akuchipani zoona? Born Kalindo anamuchenjeza chilima soo many times koma sizimamveka.
En mesa ife timaona ngati commission of inquiry imayeneka ipeze enake kuti ngolakwa? But shame kuona winaliyense akuoneka wabwino rather than omwalirayo😢😢 Malawi wathui🇲🇼
Inu zoonadi mpakana Pano palibe olo mmodzi umangidwapo mma airport or atsirikali kusonyeza kuti ntchito inayenda bwino? They have to be arrested indeed so that they explain what happened
Yemwe ali responsible pa nkhani ya black box akuyenelanso kumangidwa ( analola bwanji kuti iziyenda yopanda black box). Anthu omwe akunenedwa kuti anamuuza president ma report aboza amangidwenso tiwaziwe (let them defend themselves)
Mutu wa pilot selemani unapita kuti? Poti anaikidwa opanda mutu sunapezeke. What happened in-flight from kamuzu International Airport to chikangawa?? Why is it that there was no blood or urine in the bodies of the deceased??? What did they do with it?
You are the true son of Malawi report ikutinso mfuti zinalu ziwili Koma inapezekapo imodzi inayo INAPEZEKA NDI asilikali ena pamalo ena ake Kodi anaitenga nthawi yanji nanga anachitapo chani?
Mumakwana bwana DC ,ati ine ndy ndingogula kasinja😢😢
Big up mr DC chilungamo chidzadziwika tikadzasitha tsogoleli anthu aja adachita kuphedwa m c p eeeee amalawi tidalodzedwa ndithu
The D.Ciiiiiiiiiiiiii zachita kuwoneka kuti wagwesa msozi kumapeto kulilira ife amalawi!!! Guys tiyeni tigwilane manja pochosa chakwela chifukwa zafikapa zafika ponukha kwambili!! Kwacha ikungogwa ngati magwava ovunda muntengo!! 😢😢😢😢
Nde anamubvura zobvara ndi boxer ndan ngat anafera mmwamba mommo mpaka kugwira kolona😢
This inquiry needs an inquiry for its own
Tikapanda kusamala amalawi boni kalindo atipwetetsa iyeyo chilipo akufuna zikomo mudzandinkhulupila patsongolo😊
Mwina akufuna atiwuzeso zachina matenje komaso agadama ndiazizake
True andu awa ndi afiti.....adapha anzawo, but God he's watching azipita m'modzimozi 😢😢
Zafikapa tizingonaniza enawa akufuna mbiri chabe Wawa booon palichaphindu akupanga ndinthu ovutika ndife
Chakwera is a monster 😭😭
Akubisa chilungamo anthu anja anachita kuphedwa ndipo President uyu aaa walephera ndipo anakakhala kuti ali ndi nzeru anakachita resign
He cant resign ndi opanda nzelu
Musanayambe kumanga amene amatumiza zinthuzi aja yambani mwamanga amene amatumiza umboni wonama kuti ndege inakafika kuti mzuzu
Zomvetsa chisoni, a Chakwela nenani zoona zeni zeni.
Malawi anafikapa zimafunika kumuchosa chakwela by force!! Koma timawopa kumangidwa
❤❤❤ chakwera machende ake sure ndipo lwe DC ukunena zoona
Ineso ndimaganiza kuti chakwela wasungq anthu aja chifukwa zikanakhala kt sizikukhuza za ngozi ija ndipo ali ndi chisoni chilungamo chitaziwika km masitetimenti akubwelela zachiwonekele kt chakwela ndi amene adapanga chiwembu chimenechija ndipo mukadangosiya osafuvuzaso bcz mayankhudwe akubwela ose ndiwonama tinazi2a kale ife kuti wapha anthu aja ndi chakwela ndi anthu ake km lino ndi dziko mm mulungu wamkulu akuziwa zonse.
Chilungamo chawavuta koma tsiku lina Mulungu adzachibvumbulutsa poyera
Ndizowona kuti anthu okhaka kufupi ndi komwe Kuna gwela ndege chilungamo akuchidziwa koma chilipo chimene akudziwa
Akuti anthu ena amapeleka ma report aboza, iwo anaziwa bwanji kuti ndi a boza? Nchifukwa chake tikafuna kuti zizikhala pa tv kuti tizizimvera tokha.
Ofunika kasinja basi kikkkk kom iweyo sudzatheka sure.....mpaka kulila munthu wamkulu lelo kuva chisoni
Tikapanda kusamala amalawi boni kalindo atipwetetsa iyeyo chilipo akufuna zikomo mudzandinkhulupila patsongolo
Very sad ending the DC...
God is watching öne day chilungamo chizaziwika ndithu
Ngat ulinawo umbon wako bwela poyera ngat ulibe matha
Ndipo nsaname anthu awa a MCP akuziwa zoona zake,ine audio iyi yandivesa chison nsaname,ambuye munalolenji izi kut zichitike,ndipo kudziko kuno kuli Mulungu ndipo chobisika chizaoneka...zoona basi Chilima just like that abale ? Mmmmh ai ndith munthui anapha sure ma statement anachuluka osintha zonena,chakwera anat amundege anauzidwa kut abwelele yet akut denge siinafike ku Mzuzu airport,komanso ena anazat mu ndege communication munalibe,akut ndege inali ndimavuto yet report lati ndege inalibe mavuto,akut anthu anafela mwamba who killed them yet kufela mwamba imakhala kut ndege yapanga impact ndichinthu,guys Allah knows & he'll tell us the truth soon 😢
Nkhani zovuta mvula ikagwa kuchuluka zoliralira Mizimu ya anthu omwe anatisiya pa ngozi ya ndege pa 10 june iwuse mutendere
Kalindo ndiwe dolo osawopa mumatiyimilira
Nde mwati oyendesa ndegewa ma lincesi awo anali atatha ndichifukwa nao chinapangisa ngozi, nde mwaonjezeranso kuti aja amajambula zithuzi aja afufuzidwe amangidwe, so y amenee amatinamiza aja samangidwaa
Zandikhuza kwambiri mpaka the DC kulira ayi Ambuye mulipo kumwambako
Ulemu wanu the DC, anthuwa anachita kuphedwa, SKC and 8 others we never forget until for ever, now it's like history to us, we have questions without answers, why God u allow this thing to the innocent people
Chakwela pa .......... pako pamodzi ndi parliament yonse....Ana oipa inu😭😭😭😭😭
Report yawoyi sikukwanirayi asaa tili mudziko latsoka Malawi anamuyipisa kale. Tagulani kasinjayo bwana DC tiwaphe face to face😂😂😂😂😂 dziko lathu linathimbilira ndichangawa😅😅😅
😂😂😂 ndipo iwe usazafe uzasowe yambisa chipani tizakuvotere ife
Dziko lathu ndilachete apapa ndipamene pamene pamafunika kumatcha chifukwa atiwonjeza anthuwa koma dziko lathu aaa turo
Ndipooo kwambir chifukwa tikumangoyang'ana ndikumvetsera tikupatsidwa ma report onama
To much sleeping
Chakwera sangapange action ili yonse coz him and his Cabinet they planned all this.
Chakwera you killed Chilima ndi Anthu Ena Osalakwa
Evil Man.
Kupha Anthu eeeee Koma wina mukuti sathamanga misala
Guys moti Panalibe omuchenjeza chilima nthawi ija amazuzidwa kuchoka mu alliance? Akubanja komanso akuchipani zoona? Born Kalindo anamuchenjeza chilima soo many times koma sizimamveka.
Chakwela akudziwapo kanthu koma zoona mwaputa kwiyo wa amalawi 2025 osayiwala chikangawa.
VN ya kalindo lelo yandimvetsa chisoni kwambiri kumapeto kwa vn kalindo walila zopweteka kwambiri
Ndamva chisoni nawo nane
Lero the DC mpaka kulira zinthuzi sizili bwino sure
Achakwela oro mutabisa chilungamo muziwekuti la fourty lizakwana sikuchejela zomwe mukupanga ndinu dolo lero mawa ndinu kape😭😭😭😭
Bola kape mawa ndi mbuziimemeyi
Wamkulu waliratu uyu anthu akupha inu ofunika muzafe imfa yowawa
Chakwera, koma unabadwa ND munthu wa Mai iwe? Koma zoona kupha ana anzako
Ndi mwana wa njoka Chakwera. Sanayamwe bere
Wakupha ndilupanga lupanga lomwero ndilomwe lizamuphe muzonse timusiile mulungu
Katulutaeni lanu la bodza report
😂😂😂😂😂 umakwana bon kalindo
The DC for ever my support
Mizimu ikufuulabe pansi pa nthaka, Mulungu nde akudziwa zonse anthuwa apenga misala ndithu ichi anena ichi anena kusowa mtendere tu kumeneko
Katundu Mzito
😭😭😭Dc❤
Chakwera ndi Killer with MCP
En mesa ife timaona ngati commission of inquiry imayeneka ipeze enake kuti ngolakwa? But shame kuona winaliyense akuoneka wabwino rather than omwalirayo😢😢 Malawi wathui🇲🇼
5 mita ija adya ndani?
We love u mr bon kalindo don't stop to fight for poor Malawians
Eeeee 😭😭😭😭 ai zikomo ambuye akuone galu iwe panyini pamako ND ndunazako zomwezo
Ndipo ponunkha nkozo panyinipake
Kalindo ndinu munthu olimba mtima mumatiimila anthu osaukafe
The Dddddd Cccccc!!! Speaking the truth only
Amakana akudziwa chimene anachita
Ineo ndkanakhala osanglala thaw yomwe inagwa ndege ija athu ndkufikapo same time sibwez ndkufufuzaso chlichose ai😢
Nayo family ya Chilimayo kuli ziiii palibe chomwe akunena mmmm kaya
Ndipo inu aaaa
Chakwera ndi galu uyu mfiti ya kupha or kuchotsapo modzi mwanduna mulungu akukantheni agalu inu
Kodi anamuvula chilima zovala ndani
Yokhayi mwakwanatu bon kalindo😂
Pangatalike chilungamo chizaziwika September 2025
The DC tsopano auzeni chilungamo awatu mulungu awakantha
koma awawa ndiatumiki amulungu mulungu aziosera yekha ili ndidoza
Inu zoonadi mpakana Pano palibe olo mmodzi umangidwapo mma airport or atsirikali kusonyeza kuti ntchito inayenda bwino? They have to be arrested indeed so that they explain what happened
Infa yosayiwalika nkhani yake ndi ndale basi
Inu awamanga bwanji pamene anthuwa inali mission?
Chakwera ,,,, ndimfiti ndithu lelo Chilima kulibe ngt bodza,,,, ...
Kumalawi tilibe tsogore koma tilindi busa wakupha
Chakwera sangachitepo kanthu chifukwa iyeyo ndye anapanga plan yonse
Chilungamo tichidziwa 2025
Osataya mtima mcp imangodwa mu 2025
Chonena ndilibe. Koma Mulungu yekha basi.
Komatu wayakhula mwana mwamuna uleme wako mulungu adzikudalitsa
Ing'alulen ife timveko nao
Yemwe ali responsible pa nkhani ya black box akuyenelanso kumangidwa ( analola bwanji kuti iziyenda yopanda black box).
Anthu omwe akunenedwa kuti anamuuza president ma report aboza amangidwenso tiwaziwe (let them defend themselves)
MCP at its best 😢
Anapha kulakwa koma mohavu zomwe akudalirazo nde ziti inu anthu oferedwa tayendayendani adzipita mmodzi mmodzi awa
4.5meters bwanji anafa ose?
Koma m'mozi ekha anakapulumukapo koma onse. Something is long showery
Ndipo mulungu a kuona ndipo tsikuku Lina tidzakasimba
Machimo mcp
Anatuma ndi chakwera yemweyo nde amanga bwanji
The will be A day for judgement
Koma ngati onse anali atafa ampezeka bwanji ndiboxer yekha😢
Mulungu akuona
Malawi wanga😢😢😢😢
Mutu wa pilot selemani unapita kuti? Poti anaikidwa opanda mutu sunapezeke. What happened in-flight from kamuzu International Airport to chikangawa?? Why is it that there was no blood or urine in the bodies of the deceased??? What did they do with it?
Anthu awa nda satana enieni 💔💔💔
Anya 2025
Anamupha bas mcp inapha chilima Khan yatha
Mcp inawapha anthuwa bas tikufuna mutu wa pilot ulikut Chakwera galu iwe
Kodi pilot analibe mutu? 😭😭😭😭😭😭😭koma guys!!!!
Kodi mutu wake unatengedwanso,iiiiiiiii.....zocitisa mantha.tsopano ndege ndimene inamdula mutu.
@@tobiuskeliophas4838Eya akuti analibe mutu💔💔💔
Ee! Zosayenda dziko lapansi Why? Ambuye tithandizeni mukuona mmene zikukharila musakhale chete Mmmm koma zoopswa kwambili.
Awa ndi a chitsiludi awa
You are the true son of Malawi report ikutinso mfuti zinalu ziwili Koma inapezekapo imodzi inayo INAPEZEKA NDI asilikali ena pamalo ena ake Kodi anaitenga nthawi yanji nanga anachitapo chani?
Zomvetsa chisoni
Ndipo Kwambr munthu ot asiya ma banja awo anthu akulira mcp
Zose z nd nickson chakwera
Kufuna kulemeka mwachangu adzitchuka asatana. 💔💔
Iweyo bwanji sudakaperekere umboni?, bwanji iweyo osalemba lako report ndikunenamo maina a omwe adapha chilima
Ndi kape ameneyu amangobisala pama audio ake opepela uyu
Oooh okay
Athu tamakhala ndi umuthu tiziti inu mukuona kwanu zonse zili bwino pa report yabwelayi??? Mulungu akuyakhuleni 😢
@@patsonmdwazika3108inuyo ndiye adolo? Ana a njoka inu😢
Eeeeti 4.5 onse kutha?
its true
Iweyo suumakapelekera umboni bwanji ngati ulindiumboni? Kupepera ndikumene ukupangako, ngati ulindiumboni bwanji suunapite kukathandizira kuti chilungamo chiziwikedi? Basi kumangokhala oloza zala chonsecho