ZISANKHO ZA 2025 ZIZABELEDWA CHIFUKWA KU MEC KWADZADZANA MA MAFIA A MCP OKHA-OKHA - BON KALINDO

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 21 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 30

  • @EmmanuelGasiten-fo5dr
    @EmmanuelGasiten-fo5dr ชั่วโมงที่ผ่านมา +3

    Bon Kalindo yu, tizimutsata bwino bwino.Siwachambatu munthuyu. Acting iyiyi sizama jokes.

  • @PoulJepterKwenda
    @PoulJepterKwenda 32 นาทีที่ผ่านมา +1

    Kalindo kupusitsa zitsiru zinzake km zinazi kkkk

  • @PatrickBastion
    @PatrickBastion 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Yehova mulungu amene munatilenga zonse tisiya mdzanja la mwana wanu yesu amen.

  • @IsaqueFernandoAntônioAntônio
    @IsaqueFernandoAntônioAntônio 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Kkkkk lero mwabwela ngati mwa drama koma zili zanzeru

  • @DoreenLivata
    @DoreenLivata 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Kkkkkk kmatu eeee dzikoli akulamuliladi ndi amafia

  • @chimzywyson2842
    @chimzywyson2842 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    The DC number one 😂😂😂😂😂😂😂

  • @OssmanAbubaker-v7t
    @OssmanAbubaker-v7t 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ulemu wanu the DC mumakwanila ifetu mumatiimilira ndipo tikuziwa zitsisi za boma ndipo Mulungu alinafe MCP singawine Mulungu alipo

  • @JohnKawondo
    @JohnKawondo 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kkkkkk the dcc boooooooon kalindo 💪💪💪💪💪💪💪

  • @JosephMandevu
    @JosephMandevu 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Kmatu kwachematu 😂😂😂😂😂😂

  • @dalitson3558
    @dalitson3558 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Vuto ndi a opposition ndimakape kwambiri anthu akuwapasa malangizo Koma makani, mcp ikangowinaso anthu amakhala pa mavuto a nyoo!!

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndiye inu a Bon KALINDO OSALANDITSA MALAWI.KWA ANTHU AWA OIPÀWA a MCP.WA..INUYO A BON KALINDO PULEZIDENT WA ANTHU OVUTIKA.@NANGA IZIZI SIZIMENE INUYO MUNACITA NDI A CHILIMA AJA .AGAINST PETER MUTHARIKA UJA .

  • @InnocentMlowoka-ew4lo
    @InnocentMlowoka-ew4lo 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma ndeee kalindo 😅😅😅😅😅

  • @DysonTummiesSajiwa
    @DysonTummiesSajiwa 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Komatu mupengetsa anthu

  • @FrancisMagombo-b5c
    @FrancisMagombo-b5c 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    🤣🤣

  • @ChifundoMissinjo
    @ChifundoMissinjo 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Koma ziliko

  • @RodgersMtonga
    @RodgersMtonga 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Misala ikudutse apa aa😅😅😅

  • @DeMu-t2v
    @DeMu-t2v ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ngati kuli koti azabera nde palibe chifukwa choti a opposition avutike ndikuzavota komwe

  • @augustinechibbalazi8897
    @augustinechibbalazi8897 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Longlive Bon

  • @nelsonmwanache8692
    @nelsonmwanache8692 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma the D.C

  • @mickyhassan3178
    @mickyhassan3178 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    😂😂😂😂😂😂😂😂😅😅
    ufo

  • @nelsonmwanache8692
    @nelsonmwanache8692 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    kkkkk koma winiko umantha

  • @MwaiKalinde
    @MwaiKalinde 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    😂😂😂taseka mmaso ndipo sindiyankhula

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mulungu atithandize ndithu

  • @FlorenceMudonjwe
    @FlorenceMudonjwe 30 นาทีที่ผ่านมา

    Ndiye palibe kuvotatu basi 😒

  • @Fanie-i7z
    @Fanie-i7z ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Unalikotamba ndiwe wopanda nzeru iwe Ku sapota chikangawa wakoyo Za xiii amako akuvutika kumudzi musiyeni Kalindo akutitsegula maso

    • @RusselleStanley
      @RusselleStanley ชั่วโมงที่ผ่านมา

      😂😂😂😂😂 za ziiiii

  • @patsonmdwazika3108
    @patsonmdwazika3108 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nama drama unali kotamba iwe usanamizile maloto

    • @Halima-i4x
      @Halima-i4x 36 นาทีที่ผ่านมา

      Iweyo galu fiti kod ulibe chisoni ndimeme anthu akumwalilila Malawi kooo manyazi akugwiren bambo

  • @RusselleStanley
    @RusselleStanley ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chokaaaa iweeeee kavule m'chenga

    • @Halima-i4x
      @Halima-i4x 35 นาทีที่ผ่านมา

      Nde muonatu musegula mimba Chaka chake ndichino 😮😮😮😮😮 muyaluka muonaso 😅😅😅😅😅😅😅