ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Ndaonera Betchani Tcheleni wa economy amayankhula bwino chonchi koma pano ali mu ground sakuchinya
Economist wankulu...so was the late Bingu..akudziwa chomwe akuyankhula uyu
Kabambe my vote, the real game changer we hv
Makina awa guyz.Ndimagwira vepi kwa iiyeyu,ndimakina awa
Chakwela amatelotu poyamba paja,ndiye poti amalawi ndiye timaoneka opepela mu Africa muno.
Mmmmm i dnt trust him chakweranso ankatero poyamba
Awa ndiye afunika utsogoleri za economy amazitsata osati abusa
Easier said than done. Mukalowa m'boma basi kumakangopanga zokonda inu!!
Chakwela ukuva koma munthu opanda mzelu
Uyu ndikatundu 😂
Sakuthamawu koma akuauza chilungamo paja ndi economist wankulu mmalawimuno
Tikumuvetsa munthu I koma chakwera sadziwa zimenezi kod nisukuru iti adaphuzira chakwera kut akhare mbiri chonch
😂😂😂😂😂 anthu andale abodza
Malawi muli anthu anzelu mukulankhula
Awatu alindichuma ndimakampany ndipo akhoza kuyendetsq dziko mukuoneka muli utsogoleri
Dolo kwambiri uyu akhalise Malawi
Uyu ndi katundu omanga ndi mawaya
Osakhulupirira wa2 andale inu aaaa sangakonze zithu awa. Onani akulamurira ku bocina faso siophunzira
Bola asatibele chipani cha utm kupita kwina
Vuto la ndalewa amayankhula bwino akakhala kunja kkkk
Eedi koma chakwera wanyanya
Boma ilo